Former First Lady Callista Mutharika has said Democratic Progressive Party (DPP) members will force Vice President Saulos Chilima to contest in the 2019 elections. Callista made the remarks in an interview with a local radio… ...
Articles By Kondwani Mkhalipi-Manyungwa
Wamisala anaona nkhondo. Ataopseza kuti ayenda buno bwamuswe pofuna kukakamiza boma la Malawi kuti lizinyonga anthu onse opezeka kuti apha albino, a Winiko akuoneka ngati tsopano atha kumvana Chichewa ndi Mtsogoleri wa dziko lino a… ...
A Kongeresi kodi mulipo apa? Musapite kutali chifukwa tili ndi uthenga wanu. Zija za Konveshoni mumadikila zija kuti ichitika lero pa 5, ku Mzuzu, ati muziiwale kaye. Mtsogoleri wa chipani chotsutsa cha MCP, a Lazarus… ...
Wamasuka tsopano m’busa Brown Mpinganjira. Wayambapo zija zokhuthula mawu pa misonkhano yandale. Nkhani pano si ya PP anaisiya ija koma ya DPP. Ndipo iye wachenjeza anthu a kummwera kuti asazayese kuvotela Kongeresi. Amene anali wachiwiri… ...
Anthu awiri amene amatsogolera anzawo pochitila mtudzu President ndi kumema anthu kuti achite zionetselo anjatwa. Izi zachitika mu dziko la Tanzania limene Mtsogoleri wawo John Magufuli wayamba kuonetsa makhalidwe achilendo ofuna kupondeleza ufulu wa anthu.… ...
Deputy Inspector General (DIG) of Police responsible for administration Duncan Mwapasa is expected to be appointed Inspector General of Police to replace According to reports, Kachama is supposed to retire in May this year and… ...
Forget all the rhetoric of beating Chakwera in the 2019 polls and holding on to the Presidency until 2024, this is President Peter Mutharika’s last term. According to a self proclaimed man of God who… ...