
Mwambi woti tsoka likalimba amakuluma ndi galu wako yemwe wapherezeka lero mnyumba ya malamulo pomwe phungu wa chipani cha Malawi Congress (MCP), Yona Mkandawire wadera la Rumphi West, wazukuta bajeti ya 2025-2026 m'nyumbayi ndikunena kuti… ...