Wofalitsa nkhani ku bungwe lolimbana ndi katangale la ACB a Egrita Ndala ati a Hillary Chilomba yemwe anali wamkulu wachiwiri ku bungweli tsopano ndi omwe akhale akugwilizira ngati wamkulu kutsatira kutha kwa kontalakiti ya a… ...
Articles By Ben Bongololo
Apolisi ku Area 24 mu mzinda wa Lilongwe ati amanga mphunzitsi wamkulu pa sukulu ya sekondale ya Eagles Academy, pomuganizira kuti anaba ndalama zomwe ophunzira adalipira pofuna kuti alembe nawo mayeso a fomu 2 omwe… ...
Tension mounts at the Department of Immigration and Citizenship Services as staff intensify demands for the removal of Director General Charles Kalumo. The protesting staff say that they are not happy with Kalumo's leadership style… ...
Timu ya FCB Nyasa Big Bullets yadzudzula ena mwa otsatira team'yi pankhani yokhudza ziwawa zomwe zidachitika pa bwalo la masewero la Kamuzu itagonja ndi timu ya Silver Strikers ndi chigoli chimodzi kwa chilowere. Izi ndimalingana… ...
Wachiwiri kwa m'tsogoleri wadziko lino a Saulos Chilima, ali m'dziko la Korea komwe akuyimilira dziko lino ku nkumano omwe watsekulidwa lero wotchedwa Korea-Africa Summit omwe ukuchitika m'dzikolo. Cholinga chachikulu cha msonkhanowu ndikufufuza mwayi wamalonda ndi zachuma… ...
Mwana wamwalira ku Zomba makolo ake atakana kumutengera ku chipatala kamba kazikhulupiliro za chipembedzo. Mwanayu, yemwe ndi wazaka zisanu zakubadwa, anadwala mutu ndipo m'malo mothamangira naye kuchipatala, makolo amwanayu anayamba kumupemphelera kuti achire koma mwatsoka,… ...
A Malawi ayembekezere nkhani zakathithi komanso zothyakuka bwino zokhudza zokambirana komanso zomwe zimachita m'nyumba ya malamulo pofuna kuonetsetsa kuti anthu m'dziko muno akutsatira bwino lomwe za momwe zinthu zimayendera m'nyumbayi. Izi zikudza pomwe bungwe la… ...