The Ana Patsogolo Activity (APA) Project has donated nine vehicles and 40 motorcycles to the Ministry of Gender, Community Development, and Social Welfare to boost support for children facing violence, abuse, exploitation, neglect, and HIV,… ...
Articles By Ben Bongololo
Rumphi East Parliamentarian, Kamlepo Kalua, and the leader of Malawi First, Bon Kalindo, are scheduled to appear in court today in Lilongwe to face charges related to cybercrime. National Police Spokesperson Peter Kalaya confirmed this… ...
Dzulo apolisi amanga mtsogoleri wagulu lomenyelera ufulu wa anthu la Malawi First a Bon Kalindo pa Kamuzu Road m'boma la Salima. Malipoti akusonyeza kuti a Kalindo awamanga pa mlandu okhudza kufalitsa uthenga osayenera pamasamba a… ...
Bungwe lopereka ngongole kwa ophunzira msukulu zaukachenjede la Higher Education Students Loans and Grants Board (HESLGB), lati likukonza vuto lakuvuta kwa tsamba la intaneti lochitira ndondomeko yopemphera ngongole. Izi ndi malingana ndi uthenga omwe bungweri… ...
Apolisi ku Chitipi m'boma la Lilongwe amanga mayi wina wa zaka 24 kamba komuganizira kuti wapha mamuna wake a Misheck Byson powakoka maliseche. M'neneli wa apolisi m’bomali a Sub Inspector Hastings Chigalu, atsimikizira za nkhaniyi… ...
Nkhawa yakula kwa ophunzira a msukulu zaukachenjede ochuluka omwe sadachitebe ndondomeko yopemphera ngongole ku bungwe la Higher Education Students Loans and Grants Board (HESLGB) pamene tsamba lochitira izi silikutsegula angakhale kuti bungweli lidati litseka pa… ...
Malawi Prisons Reform Schools have achieved a significant milestone by successfully sending five candidates, including one female inmate, to various public universities across the country. According to the recent university selection list released by the… ...