Mkulu wa a polisi m'dziko muno a Rodney Jose atsindika kuti akuluakulu omwe akutsogolera kupanga zionetsero zokakamiza mkulu wa bungwe la Malawi Electoral Commission a Jane Ansah kutula pansi udindo, asiye kupangitsa zionetserozo. A Jose… ...
Articles By Archangel Nzangaya
Boma lati liyesetsa kuti mu ndondomeko ya zachuma ikubwerayi aikemo zinthu zomwe zikomere anthu ochuluka mdziko muno. Izi ndimalingana ndi nduna yazachuma a Joseph Mwanamvekha omwe amayankhula mu mzinda wa Blantyre pakutha pa mkumano omwe… ...
Dedza police are hunting for charcoal burners who are believed to have killed a community volunteer working in Dzalanyama forest. This is according to Dedza police publicist sergeant Cassim Manda who identified the deceased as… ...
Bungwe la Malawi Law Society lapempha mkulu wa bungwe la zisankho m'dziko muno a Jane Ansah kuti atule pansi udindo. Izi ndimalingana ndichikalata chomwe bungweli latulutsa lachinayi chomwe watikitira ndi mlembi wa gululi a Martha… ...
Organizers of post-election demonstrations slated for Friday have refused to cancel the protests in Mzuzu. The development comes the Mzuzu City Council on Wednesday asked organizers of the demonstrations to think of changing dates for… ...
Mamuna wina wa zaka 49 m'boma la Rumphi ali m'manja mwa apolisi ataombera ndikupheratu chibwenzi chake kaamba koti makolo a awiriwa amawakaniza kuti asakwatilane chifukwa ndi pachibale. Watsimikiza zankhaniyi ndi mneneri wa apolisi m'boma la… ...
The Zimbabwe government has deported 13 Malawian nationals who were in the country without proper documentation. Mwanza border public relations officer Pasqually Zulu said the 13 Malawian nationals arrived at Mwanza border on Tuesday from… ...