
Magulu a achinyamata m'boma la Chiradzulu apempha Bwanankubwa wa bomali kuti aimitse ndondomeko yosankha achinyamata oti achite maphunziro azamalonda pansi pa bungwe la USAID ponena kuti pachitika zachinyengo pa ndondomekoyi. Malinga ndi kalata yomwe maguluwa… ...