Police in Zomba have arrested four fellow police officers on allegations that they have been stealing money from complainants and suspects.
National Police Spokesperson James Kadadzera confirmed the arrest to Malawi24.
But Kadadzera refused to comment further on the issue saying it will jeopardise their investigations.
“Yes l can confirm that we have arrested four police officers but our investigations are still under way,” he explained .
The Spokesperson assured that the officers will face the law regardless of their status as officers.
He said that they will handled as any citizen of the country is handled when found to have broken the law.
Kadadzera promised that the suspects identities will be revealed once the investigations are over.
The spokesperson has since warned other police officers in the country to refrain from such malpractice as they will not spared .
Kodi inu anthu mungokamba! anthu amenewa amagwila ntchito yoophpya koma malipilo nde siya mau• munthu wazimangilila yekha kusaka pofela kauzeni apolice azatenge! wagwilila apolice azammange! koma mukalemela ndi wapolice ndiye chisilu! Mupite ku limbe kuseli kwa limbe police mukaone nyumba za ma offecer mabwana mabig a mapolice kuchitsa manyazi !mufuze police zambili mulibe galimoto agwila bwanji ntchito munthu mchifukwa amalandila ziphuphu ndipo sizingathe•
Set a thief to catch a thief theory, I don’t blame them but their employer.
Kkkkk anyani mbamva ndindani tiwaziwe
Ukakhala ndi ndalama umangodziwila kuti ndapulumuka.
Musadane nokhanokha nose mumachita zomwezo koma pot mbava ndyomwe yagwidwa bas anyongedwe ndithu . eeee dziko lathu ili!!!!! Nanga nkutan pot zdatero kale?
Dziko lili manja mwangalu,sindinadzionepo munthu olakwilidwa nkudzakhala olakwa,koma kuno dzikuchitika kamba ka ndalama,iwish god can panish you bad people,
Amene akulondela manda a Bingu ndi Kamuzu ndi amene sangatenge ziphuphu koma ena onse echiiiiii
zandmvekela bwino mwina ena atengelepo phunzilo an2 anji opanda cison?.
Apolise ambiri ndi mbava zikuluzikulu dikilani mumanga ambiri
Lamulo liwonetse ukali wake
Kumangana nokhanokha? Ndezodabwtsa2, chinyengo chili nd agalu inucho iwowo mwawamangawo nde matsoka mngotan? Eiisssshhh…..
Mbava izi. Most of the criminals in this country have connections with the police men. Shit!
Nsipu Wamela M’khola, Galu Wapakhomo Waluma Mwini Nyumba, Anjateni.
Throw away the keys let them rot eDANYANA
inu anzathu a ku zomba tiwuzenikoni mayina a mbava zamu uniform zimenezi!
plz,deal with them enawa atengelepo phunziro,tchupiti.
Kod ndizothekaso apolice kumangana et.
Amenewanso osawaleka mnsanga ayi, awa ndiye amadziwa bwino lamulo akwizingeni ndi unyolo wawo wawo.
CORRUPTION IT’S A SPIRIT FROM THE DEVIL ONCE YOU FALL IN THIS SPIRIT OF CORRUPTION IT’S LIKE YOU HAVE FALLEN IN THE DEBT CALLED KATAPILA THEN THERE’S NO TURNING BACK UNLESS YOU ARE DELIVERED BY STRONG PRAYERS OF THE SAINTS
Mbava Za Police Zambili Zili Pa Nayuchi Border.A Police Akutibela, Ndipo A Malawi Tikulila Pa Border Imeneyi.
Why u police always u stealing but ugot free shirt free trausor free hoes free socks free cups eish tchito zolembana pa chibale
Magani otse
Maluzi nda amene avuta pa malawi
Basterd officers
Apolisi ndiye mbavazo
pachoka nzako pali malo mwina nane mkupezako kaganyoko
This is common in most of our police stations, u can’t be assisted in police if you don’t have something to give them in your pocket, even if u want a below out u also need to pay if u want that below, but our laws says that below out its for free. Corraption won’t stop in these military departments!
We call it bail out not below kkk amdeza just write in our venarcular
Thanx for your correction, no one is perfect when it comes to this, even in our venarcular it cn be difficult!
Musaiwale kuti anthu amenewa amakhala mmaluzi daily. Zovala samakwanitsa kugula moti amangodalira uniform,fon sangakwanitseso kugula amadalira ma wireless msgs, akamapita ku ntchito kwao amakonda kupempha ma transport aulele coz amakhala kuti alibe yoti angalipire, mma plot amavutaso kulipira rent.
dzofunika kumangopha basi
Foos
Koma kumeneko…
MUKUWABISIRANJI MAINA AWO AKANAKHALA MPHUNZITSI MUTANENA KALE
Akavuwe vuwe ngati amenewa amanyazitsa boma mukawapeza olakwa fire and arrest them.
Nanga mukuti mwamwanga apolice 4,pakuti mwangomanga mmodzi apa
Kikiki
many police officers are nt working profesionaly.in this nation z de land of thieves mainly cival sevants especially police officers,polititians & wat u hv
Zilipo zambiri mbuzi za police zakuba
kudya pomwe yamangidwa.nice 2 hear
Okey musawapatse ballbond
alipo ambiri okonda zmenez
mbava in police uniform
Gravel Masinja
Maluzi
Last week mfuti,lero agwira
Kkkkkkk Malawi walero
Nazitere bwezi zikoma anthuni..
Maluzi
Don’t release them
Akutiyipitsira ntchito koma aaah very bad
zamanyazi
Zopasa manyazi
To Overcome Poverty,For Survival.
ndimakape ndipo zakhalabwno agwidwa
Gud gud, azichita bwino mbava eish!!! Munthu akulira kumudyeraso?? Mwina zichepa izi
Very good
NdKukula kwa dziko kumeneko
Zikamatele nthuni,,, ho! inu
Gud devopment
Bingo!