Police in the commercial city of Blantyre have arrested a patient and his guardian for stealing blankets and bed covers from the Tuberculosis (TB) ward at Queen Elizabeth Central Hospital (QECH).
The couple, Frank Duli, 44, and his wife Sungeni Duli are reported to have stolen blankets and bed covers at the hospital on several occasions.
Confirming to Malawi24, Blantyre police deputy police spokesperson Andrew Mayawo said Frank was admitted at TB ward in September but, together with his wife, he devised a plan to steal the blankets.
After visiting her husband at the hospital, the wife used to take some hospital blankets home.
The theft was revealed after another person who was also admitted in the same ward reported the matter to security personnel who tipped the police.
Police arrested the couple on Monday this week and charged them with theft since they acted contrary to section 278 of the penal code.
The two however pleaded not guilty to the charges when they appeared before Blantyre magistrate court on Tuesday.
Frank and Sundeni come from Kudza village, Traditional Authority (TA) Changata in Thyolo district.
That’s sign of poverty
Kklkkk kodinso kuli ma blanket omangilana???ukapitakotu osamutengera blanket patient wako aonjedzera matendawonso Chibayo pompo
mwawamanga oba blanket nanga aja anaba washing machine aja munawamanga?apolisi apa malawi mumalimbana ndi zazii pomwe a cashgate akungonjoya bola kukhala opanda polisi
Kuba sikuchepa,mwina amafuna zizimba koma yalakwa.
Anakangowasiyila osati mpakana kumangana,zomvesa chisoni
Zingoonetselatu kut umphawi wafikapo pa nyasaland
Akakhala wakuba ndalama zaboma kumangowayang’ana mmmmm malawi sadzathekanso
Iiiiiiii
Mh, jst leave them plz, they dont hav money dats y,
kkkkkkk lol
Mmmmmm
komaso zina ukava,sumatha kuvesatu.
Ndachita manyazi ndi Dziko langa Malawi , pali zinthu zoti mungalengeze kuti anthu onse padziko aziwe. mukanawonjezeraso awiri kuti mwina akathandizidwe akachoka kuchipatala.
Dziko la mbava,Abale amene samaba ku malawi ndi ndani? tangowasiyani mutengapo sambi chabe akakuferani mu cell or pa khnti.
Tangomusiyani nanga munthu akabe zomwezo ndiye Ali bwino mavuto basi
Mukuchita kulemba ndimuchizungu manyakakanyakawa even maiko ena akuwonankhaniyi angoseka
Kkkkkk zazi zinazi zokhala Nazo busy kulengeza pomwe anthu oba ma billions mungowadusa osawalengeza.izi zokha pangani nazo manyazi
The latest Malawi news mukunena ya bulangeti la chiperoni? Koma chambadi ndi nthawi ya chilimwe zimadana eti
…mlandu woba nkhuku yomweyi, dziko lonse kudziwa ena akaba mamiliyoni mmangopondeleza….(by charles nsaku). Apolisi asiyeni awo, akanakhala aba ndrama mkanagawana nawo kapena kutenga zonse inu.
popeza odwala 3kota ya odwala omwe amapita ku QECH ndi amphawi ndiye aliyense aziba chomwe chamusangalasa katundu wapachipatala akhalapo Mulungu samukhululuka munthu chifukwa chodwala ndiye dziko likatero
Nanu Apolice Mwasowa Zomanga Etiii??
Guyz anakuuzani ndani kt wodwala kapena mphawi akalakwa samangidwa? zili bwino kwa iwo agwidwa ndipo akuyenela kugamulidwa monga mwa malamulo,kd kumwamba ena akapulumuka chifukwa cha umphawi kapena kudwala? ndiye ngati zili tero aliyense aziba mablanket akhalako chifukwa ena samagwidwa ali musalimbane ndi aCASHGATE iwo chilango chawo chili kumwamba
leave them,why not go 4those in cashget zausilu apolice in ndinuso mbava zoba matewela ku maternty
Amenewa Akakhare Kundende Moyo Wawo Wonse. Mpaka Kuba Ka Bulangete Konunkha Panado.
Mwamangilanji tatuluse osamanga mbava zinaba ma million andalama mukulimba ndaamene waba bulangeti ahaaa muzigani
Arresting someone just coz of blanket why not arresting Rotten Cabnet for that K577 billion be patient guys leave those poor to go to their home . Feel pity
Angomuuza kuti atenge wabazo koma akazadwalaso azatenge zofunda wabazo kuti azizafunda chifukwa zamusangalatsa zedi
poor malawians,,, kuba zakuchipatala, koma nde zakokamanja
Koma ku Malawi ndiye umphawi wafikapo di ee mpaka ma size amenewa abale kkkkk olo wa police omangayo ndiye kungomangila kuti poti naye ndi ntchito, ali ine ndingangowasiya kunyumbako zawo sizili mukanthu.
Akazadwalanso azafunda chani?
Kkkkkk shame
Yalakwa zedi
Nanunso A Police Mumabanso Makamaka Okala Kuno Kumbayani, Ndilande, A police Okhala Malo Awiliwa ndimbava Zenizeni, Futi Zanu Muma Pangisa Lenti, Iya , Atayeni Anthuo Chatapu, Nanunso Anakubala Bansi Mdziti Munabeleka Mwana Ali Ku Tnchito, Tsiku Lina Muzanva Kt Nayenso Ndimu Kaidi,
Hahaha zafika poipa mpaka kuba
Kkkkkkkkkkkkkkkk
Kkkkkkkkk umphawi wabvuta
#kkkkk
Recently Human Rights Activists condemned the habit of wheeping pupils by some teachers.Here we are,the law enfircers & hospital workers are violeting the rights of sick people we need to hear your voice.How could someone who has just been discharged from the hospital appear before the court of law while cashgate offenders are given rights to recover from their various illnesses before appearing in court.What kind of Malawi are we developing?Where are Human Rights Activists?Is this how our judicial system going to handle the poor?
Cash ? gate guys are walking taller they’re busy arresting someone discharged from hospital ? it’s either he was mentally disturbed.that’s pathetic
Very pathetic indeed bro
Umphawi ndiye wafika pena paketu mpaka kukaba zofunda za chipatala koma yah
Thats Too Bad, It Indicates How Malawians Are Desperate And Living In Poverty
Umboni woti kumalawi kuno kuli umphawi oopsa ndi umenewo kulibwino kungowasiya chilango chake ndi manyazi omwe achitawo..komanso mukumbukire kt onseo ndokuba omangayo ndi omangidwayo zonse ndi mbava km winayo kusagwidwa
Kkkkk Kom Mada
Kkkkkk amon mbava yaikulu ndiyomwe yamanga nzakeyotu..kuteko ndikunena pano wamubelanso kale nzakeo
Kkkkkk kusonyeza kuti mbava zagwilana?
Kkkkkkk apa nde zagwirana tiwone kt amuimbe mlandu nzake ndan-
Kkkkkkkkk! Very fantastic! please, I beg, jst leave them
Nawo apolisi kumalawi amalimbana ndiwoba mkuku kusiya mbava zikuluzikulu esh zovuta
Osalimbana Ndi A Cashgate Bwanj Zomwe Abazo Zikukwana Ma Million Ndende Ikudzadza Ndi Aphawi Ndithu.
Umafuna asekelele zimenezi anthu aziba zofunda zaku chipatala zoona
Agulitse chamba kuti apeze chofunda kum’manga kutenga zogula gula kale kumanganso shaaaaaaa!!!!
osangowasiya bwanji
amasuleni azipita kwao ndi amalawi osowa amenewo.