Police at Ndirande Township in Blantyre city have arrested a 37 year-old man for being found with Indian hemp locally known as “Chamba”.
According to police, the suspect Francis Khoza was arrested after he was found with Indian hemp weighing 300 kgs in a vehicle registration number KU 1751 on Thursday.
Confirming to Malawi24, Blantyre police deputy spokesperson Andrew Mayawo said the officers had a tip about the suspect who was packing the Indian hemp to sell it outside the city.
“The suspect was packing the illegal stuff at Makata and people of goodwill tipped the police who managed to stop his vehicle when he was about to leave Blantyre,” said Mayawo.
Mayawo added that the police have since sent the Indian hemp to Bvumbwe Research station as part of investigations on the matter.
The suspect comes from Mataka village, in Blantyre and he is yet to appear in court.
Kkkkkkkkkkkkk chamba ndi deal koma ukakodwa
ndi mbola
Apolice athu uchita kugundika ngati zoona onani uniform yangati chamba cha Nkhotakota
Am a buyer aliyese amene ali mlimi wa chamba i buy dont wory azanga market itsegulidwa pa 2july nkhotakota
a chana inu osamaga a cushgate
dis is bullshit!kumanga munthu cifukwa ca chamba, inu mmafuna aziba mmesa achimata ambiri akusowa tchito cifukwa cha ndyelalanulo,mukagwila wogulasa chamba nde mmanews ndi maradio kulengeza pamene mukulephela kuthana mbava/zigawenga cfukwa choti mumawabweleka nokha mfutizo?
Nyonyonyo Haigrade Dukse Gangsta sanalakwe uyu
Haha haha Ine nkhani zimenezi ndinasiya kuyankhila . Zimandikwiyisa kwambiri . Ndimawopa day ina nzayankhula mosakhala bwino
Haha..I know the feeling.instead of focusing on albino killings n sht..
Eti man . Kaya anamvapo kuti zoti wina wafa akusuta chamba
hahaha..Never
Za dziko ndi chocho palibe wabwino poti apolisi akugulisa chambaso ok
Why arrest innocent people? The man didn’t create the plant.
Why the police contineu arresting good pipo, like this chamba saller?, onbehalf of arresting those who are now killing innocent pipo/like albinos? Apolice aku malawi ndinu mbuzi kwambili mukummanga opezeka ndi chamba? Okupha albono ndemukumawasiya poti #4million?
Kkkkkkkk
Chamba chili ndi ndalama kuposa fodya aliyese tsono, mukumangiranji munthu poti iye amafuna ndalama zozithandizila pa moyo wake.kodi mudzamvomeleza liti ulimi wachambau? tatiyeni amalawi tizilima ulimi woti tizipeza ndalama osat uwu amangotibela azunguwa.
Police ya kumalawi imagwira ntchito ndi mbava
Kkkkkkkkk koma mastain mukuwalephera
Aaaa! Shit who do dis
Kkk mpaka mfuti kukagwira osuta chamba
Kkk mpaka mfuti kukagwira osuta chamba
Nanga aja Mumasuta nawo ku Blantyre market aja muwagwira litiiii???? Timakuwonanitu ifenso tidzachita report a tip!!!
Nanga aja Mumasuta nawo ku Blantyre market aja muwagwira litiiii???? Timakuwonanitu ifenso tidzachita report a tip!!!
Palibe mulandu pamenepo
Palibe mulandu pamenepo
It’s Healing Of The Nation Don’t Criticise It U Are Failing To Catch Di Thieves and Criminals Bt Rush On Useless Things DemtBlust Jah Will Arrest U Too
Zopusa, its legalised! Wat about albino kiling
Fuck the police. Fuck the government. Free Chamba free the people . power to the people.
Chamba ndi chani what abaut cat and coco
Kkkkkkk akuti akachisiya kuti chambacho? osangonena kuti tachigulitsila munthu wina bwanji ku Bt kulibe warehouse zaziiii
Kkkkkkk akuti akachisiya kuti chambacho? osangonena kuti tachigulitsila munthu wina bwanji ku Bt kulibe warehouse zaziiii
A police amakakamula za ziii
A police amakakamula za ziii
What is wrong with chamba plz leave that man alone nxn
What is wrong with chamba plz leave that man alone nxn
Thanks 4 the story but that pic eeeee is that the only one!
Thanks 4 the story but that pic eeeee is that the only one!
Kkkkkkkkkkkkk koma wachamba yemweyo mpana choncho
Kkkkkkkkkkkkk koma wachamba yemweyo mpana choncho
Eeeeeeeeeh bwanjiso mwina anakanika kukukongozani mesa ndiamene mumakonda kusuta chamba inu bwenzi tikukambapa mwina anagawana kale chambacho kkkkkkk aaaaah
Eeeeeeeeeh bwanjiso mwina anakanika kukukongozani mesa ndiamene mumakonda kusuta chamba inu bwenzi tikukambapa mwina anagawana kale chambacho kkkkkkk aaaaah
Ine nimadana mkumaika chithuzi chosagwilizana ni zimene mukunena malo moti muonetse zachitikazo inu muikazina
Ine nimadana mkumaika chithuzi chosagwilizana ni zimene mukunena malo moti muonetse zachitikazo inu muikazina
kumamenya ogulisa chamba zazii anthu akupha ma alubino apolice a malawi hahahaha
kumamenya ogulisa chamba zazii anthu akupha ma alubino apolice a malawi hahahaha
f**ckn police brutality ligalize # Dagga. live poor man alone
kkk ndirande sazatheka !!! Thumb up my fellow ndirandians ku makata,safarao,mapulot,newlines,malaysia,nyambadwe,majiga,mpembu gamulani and many more
fucken shiti malawian police mukuononga mabisiness athu too mutch
za ziiii kusiya kugwila ma alibino killers kulimbana ndi wa chamba basi,, abakha
pali nkhani apa? Chamba chili bweeeeeeechi!
kodi bwanji bomali osapanga kalondolondo kut adziwe komwe munthuyu anakagula, kenako akathane ndi mlimi wa mbeu imeneyi?
eish eeeeeee kaya
Eish
But you said it is legal to cultivate it then why do you arrest those who poses it ? This is really ridiculous guys
It is shame to see the police arresting one found in possession of Indian hemp setting free one found in possession of bones of an Albino….that’s not fair!….or maybe am missing something on indian hemp,I ever since I was born,have never heard of any death caused by marijuana…but look at those u setting free,they’re taking the life of fellow. humans…Wise up and free everyone found in possession of MARIJUANA
zeen raster
police yathui mmm
police yathui mmm
Send a thief to catch a thief
ku malawi kuno umphawi uzatha pokhapokha atayamba kumalowa ma bussines obweresa ndalama. Chamba sikusuta kokha ma products ambiri omwe timapanga import ndiopangidwa from chamba
ku malawi kuno umphawi uzatha pokhapokha atayamba kumalowa ma bussines obweresa ndalama. Chamba sikusuta kokha ma products ambiri omwe timapanga import ndiopangidwa from chamba
We can’t success if you still doing like that smuggling ndiyomwe ingathandize kuti dziko lathu anthu azinva kukoma koma ñgati ndi choncho tizakhala ovutika mpàka kale anzathu mmaiko mwao anadalisidwa ndizàchilengedwe zomwe zimawabweĺeseĺa chuma komwe kwathu kuno ayi ndiye ngati wina akuźilimbiķila mwaiye yekha mukufuña mumubwezelese m’buyo eish my nyasaland wañtasadi ndi ntima omwe

Uchitsiru basi akazakhazikisa lamulo lolimalo tizakuonani muzagwira ndani
Uchitsiru basi akazakhazikisa lamulo lolimalo tizakuonani muzagwira ndani
Kodi iye waba? Musiyeni naye ndi ntchito yomwe amapezera ndalama,
Kodi iye waba? Musiyeni naye ndi ntchito yomwe amapezera ndalama,
Chamba Mmalawi Muno Chidayamba Kalekale Kusutidwa Mwagwila Yekhayu Bwanji? Kalimbanen Ndi Opha Albino Uko Ameneo Akugulitsa Chilengedwe
Chamba Mmalawi Muno Chidayamba Kalekale Kusutidwa Mwagwila Yekhayu Bwanji? Kalimbanen Ndi Opha Albino Uko Ameneo Akugulitsa Chilengedwe
Apolice akumalawi ndinu mbatata zosawa,Mukusiya wokupha Alubibino kumalimbana ndi zamziiiiiiiiii.
Apolice akumalawi ndinu mbatata zosawa,Mukusiya wokupha Alubibino kumalimbana ndi zamziiiiiiiiii.
Kusowa tchito basi koma tikaimba foni kuti okuba kuno ndie mumabwera akubao ataba atapita kale Kenako kuzamafutsa mafutso a tchayina.
Kusowa tchito basi koma tikaimba foni kuti okuba kuno ndie mumabwera akubao ataba atapita kale Kenako kuzamafutsa mafutso a tchayina.
Ganja yomweyi…….
koma apolice akumalawi kukonda katangale kwambili alimbana ndi munthu wa chamba moti azilimba ndi anthu amene akupha alubino koma pa nkhani ya ndalama eeeeeeee ndi chifukwa dziko lamalawi ndi yosauka sizachitaso bwino ayi
Nde zausilu, which one is a criminal, having human bones and one having plants?
Nde zausilu, which one is a criminal, having human bones and one having plants?
leav him kod walakwa chan?? Mesa amapanga bussnes cifukwa can boma silifuna anthu azilemera LIGARISE IT PLIZ
leav him kod walakwa chan?? Mesa amapanga bussnes cifukwa can boma silifuna anthu azilemera LIGARISE IT PLIZ
Bolani kulemera munjira yogulitsa chamba,kusiyana ndikupha albino.Munthu mtayeni uyu sanalakwe,aMalawi nsanje safuna mzawo kudya thukuta lake.

mulibe dzeru apolice because mukanamusiya iyeyo
Ogwirawo ndi mbuzi za athu inu chomwe mumabandacho mumatenga kt?kungokhala ndi umoyo wa umbava musabisetu china kt muzisuta muzalangidwa mulungu ali nanunanu
kenako timva ayamba kulanda mowa
Asiyedwe munthuyo mwachangu we all cannabis
amalimbana ndi zazii apolisi akuno
Nanga osapezera ntchito bwanji bwerani kwathu mutenge china koma mulimbe chifukwa muzathamanga l swear.
achilanda kma azikachisuta ndie
Oky chabwino tamva koma funso langa kwa inu apolice bwanji mukulimbana ndi ogulitsa bwanji osathana ndiyamene akulimawo bwanji? pamene kukufesedwa njeleko mukuziwako zachinyengo basi tiziti mukugwira ntchito bwino muthana nazo bwanji zimenezi pamene njele zake zikufesedwa mom’muno ndipo mukuziwako. mbola imeneyo malawi police is poor
Alakwitsa kumugwira munthu akupanga bussiness kuti adye ndibanja lake sinanga boma silikulipira anthu
analima monga njira yopezera ndalama zosamalilira banja lake akakagulisa kuma company omwe amapangira mankhwala a asima kukana kukaba za anthu ena kapena kuwoongera bongo la munthu wina, mwasiya mbav
Demeti mumathamangila patinkhani ting’ono ting’ono koma akati akuba amfuti kuno ulendo okalowa m’bulangete nkonono ngati usiku…….koma masana #u_alwez_piss_me_off u akapokola
Muzalande Cha Ine tizawone Muzasanduke Akazizi
Cha bwino
Ok tamva
Kkkkkkk okay?
Chabwino tamva!! Nanga amene akupha nzathuwa ma albino mwagwirapo angati???
kupanda dzelu apolice malo mulimba ndi anthu amene akupa anthu azawo umalimbana ndi chamba nde chani chimenecho
Ligalize Marijuana… why we hesitate to?