
Abambo anayi amangidwa powaganizila kuti anapha mnyamata wa zaka 18
Apolisi m'boma la Balaka amanga abambo anayi powaganizira kuti ndiwo adachitira chiwembu komanso kupha ophunzira wa pa sukulu ya sekondale ya St.Charles Lwangwa Gift Libuda. Ophunzirayu yemwe adali ndi zaka 18 zakubadwa adachitilidwa chiwembu pa… ...