A form four student at Lozi Secondary School in Nkhotakota, Cecelia Kazala, was found hanging in the early hours of Wednesday morning after committing suicide, Malawi Police say.
According to her family members, the deceased, 21 cited no reason for the act but left a letter which strongly advised the members not to accuse anyone for her death and asked the father of her child to take responsibility for the child she has left behind.
“Don’t accuse anyone on my demise. I have decided to do this alone. The father of my daughter Chrissie should take responsibility. I wish you all the best,” reads the suicide note.
The 21 year-old woman went missing on Tuesday, only to be found dead a few metres from her house the next day.
According to postmortem results from Nkhotakota district hospital, the deceased died due to strangulation.
Meanwhile, Nkhotakota Police have since ruled out foul play on the death of Kazala.
Muuuu zosakoma
Last days
bolani ngati anthu anadyamo : . . . Anaonesa umili wake
Ya maganizo onse ndiomveka koma ndisusane ndiomwe akunena kuti ndisatana akugwira ntchito musanamizire satana bible linati izafika thawi even satan azakukanirani kuti indedi ndine wosokoneza koma na izi ayi mufuseni mwiniwake ngati ndine mwaona ndiye tisamare mukamamutamanda chonchi satan amakodwa osamamutchura azazorowera sharp wapita wapita lets luk onither isues dts all its time no wry
Tingati mzimu wake uuse muntendele ngati?
go to hell
Tiyeni Tipempherere Nkhotakota Chiwanda Chimenechi Chaonjeza Anthu Awiri Ozimangilira Week Imodzi.Kuti Tiwerengere Chaka Chonse Ndiambiri.Mzimu Wake Uuse Mumtendere.
pipo commit sucide bcoz they want to eradicate the bitterness in their hearts…though its a wrong way…!
Zoona @Joji
Brame peter mutharika, ndiamene akulakwa, azimangirira ambiri atule pansi udindo zinthu zavuta kumalawi.
Eish so early!mulungu akukhululukire sumazwa zimene umachta!RIP.
Zomvetsa chisoni RIP
Aaa rest in peace,kkkk
so bad
Chodandaulitsa ndichakuti wathawitsa dinkamu amuna asanaigwire ntchito mokwanira,komabe she has created space 4 others to live in replacement 4 her,RIP.
ndi mnene waiverela size ya mdrogba
Zoopsa kwabasi wa?
MULTIPARTY NDI NKHONDO(H KAMUZU BANDA) INU ANA ASUKULU TISALOWELERE NDALE, NDALE NKANYAMA KOOPSA(JOSEPH NKASA) ~mau kwa amene akunena za CHASOWA.
Inna Lilah waina ilayih rahiun
Dont forget m’mene anafela Robert chasowa………God will judge.
Kukhuta
RlP
Mmmmm zovuta kumvetsa
sham sorry to her family.
A police yanu yija simunapite kukafufuza?
ine ndlibe polobulemu
Wathawa mavuto ameneyo ali boh koma eee asanakwatiwe eish
zonvesa chisoni
Anakhuta fodya
aliyese alindinjira yake yochokera pa dziko ngat adazimangilira Yudasi,only God knows
Very hard to believe.
waganiza bwanji nayeso samadziwa kuti kuzipha ndi straight ticket to hell?
Kkkkkkkk
akapume galu ameneyo
Luck of Critical thinking.
decision yayitali kungodwa xmas nanga 1 akuwona ngat akadwera kt
decision yayitali kungodwa xmas nanga 1 akuwona ngat akadwera kt
njelekezi wakugwilitsani ntchito ngati mwapanga izi ndinuyo RIP
njelekezi wakugwilitsani ntchito ngati mwapanga izi ndinuyo RIP
Only God knows the truth
Yap
Infa sithawikadi zowona,basi munthu kukangodzimangirila basi….
Infa sithawikadi zowona,basi munthu kukangodzimangirila basi….
R.I.P
Akanadikila awonekaye 2016
Anthu akumwa ma arv every day kufuna moyo iwe kutaya ngati ndalama,zilibwino
peter muthalika is to blame
FACT is if done by oneself, NO chance in HEAVEN.
Ooooh mulungu wanga khululukileni munthu amenei, ife tilibe chiwelunzo. Inu ndiye mwini zonse, kwaife kupepha chikhululuko kwainu mwini zolengedwa zonse. Ameen
Mulunguwake uti amakhululuka tchimo limenelo?
wofa mu uchimo wakudzipha, wafa muuchimo bas, olo mutamulapira a million times Mulungu sangakhululuke chifukwa ndiye kut azitsutsa yekha pa mau ake omwe woti Kudzipha ndi Ntchimo. “Wafa wafa kulibe kulapirana (its a song)” Munthu wa nzeru amasalalitse chimaliziro chako Deuteronomy 32:28/Matthew 24:13
no need repentance after death
kapena tinene kuti nthawi yake inakwana?
God forgive this lady……
so sad
Is’t agirl or awoman? no problem anthu akuti ndizomwe umafuna, bwanji osazimanga chaka chamawa? RIP
A form four student? Why are we so stupid in this way Malawi’s? Read the Bible please so that we can get the ways to handle matters. It’s my plea to thee black stupid and foolish people who thinks that by killing our selves we’re solving problems.
I think this is not a time to shouting to a suicide girl/everyone who committed suicide. We never know what makes a great matter like this.
It could be better to pray for this problem than just to shout. I know for sure that demonic spirits is working hard. Is always there to force the people of God to do things which very contrary to our creator God almighty. Though it doesn’t mean that we be belongs to this spirits “no*
. Devil is taking the chances after discovery that we mustn’t kill ourselve. Is sin. So is forcing pple to get a sin & away from God.
We are still in God’s hand, & is the same God who will not let them (suicide pple) to go to hell.
Komano mpaka kuzimangilila mavuto ake ndiochuluka motani zingavute zingawawe i can’t to died chifukwa chozimanga auze anthuena mavuto akokuti athandizepo mzimu wake uwuse mumtendele
R I P.
pepani akubanja limenelo poti mulungu anati muzafandithu koma chofera sanachitchure kaya ulinyumba ukungona ungowona yensu wafika
That is a very bad. Lord have mercy on them because they do not known for what they are doing. Still almighty God have mercy on them coz is creation.
Burn her remains!
Low selfestem R I P
Mmmmm!
every problem has an expirely date so don’t comit suicide!
Mwanena mawu abwino anthufe ndiwofunika kumaunikirana kuti tizidziwa vuto lililonse lilinditsiku lothela.kunali ayobu anakumana ndizokhoma kuma zinawathera.
a yobu sanali amasewera wamtenga wina akuchoka wina akubwela ndiwina! amandipatsa nane chitsanzo chabwino
a yobu sanali amasewera wamtenga wina akuchoka wina akubwela ndiwina! amandipatsa nane chitsanzo chabwino
#R.I.P
nowadays anthu akuphana chonchi
Zonse aziwa ndi Jehova••RIP girl
Go to hell UNAKHUTA MOYO MBUZI !!!
was found hanging after committing suicide?
But why??????????
gud for her no need to feel pity it’s her choice!!!!!
Ndichizolowezi chake kuzimangilira pa 30 december every year sizachilendo
tikhoza kulankhula mmene tingathele koma chilungamo akuchuziwa ndi Mulungu, panopa ziko lafika poopsa kwambiri ngakhale kumbali imeneyi yopeza munthu atizimangililazi sionse amene akumazimangilila okha, zinachitikako kwina kwake anthu kuchokela limodzi pobwela kupezeka mmodzi wapezeka atizimangilila zosatila zake anthu paja ndemene anamupanga chipongwe nkumangilila pantengo, nde ineyo sindikulesa anthu kuti amazimangilila, koma ena amapangidwa chipongwe ndithu, koma zomvesa chisoni
awuzeni avese
Zoona
You Are Very Right. Some are forced to the note and killed. Chasowa case!
You Are Very Right. Some are forced to the note and killed. Chasowa case!
True
very shocking y ddnt sh do it aftr 12 midnight 2dae so dat her neighbours,family nd friendz celebrate dc new year in peace
Paja uku chamba amasuta ndi ana omwe ndizosadabwitsa.
do not judge God has final say
Inaalilaah wa inaailaahee rajeeeun,
zosakhala bwino, amakhala satana akuwagwilitsa ntchito anthu ozimangilira. Sikumakhala kufuna kwawo koma devil ndi amene amawapangitsa.
She did the same last year ndikhalidwe lake
kkkkk man felie musandsekexe ine kkkkk
kkkkkk….u mean next year azachita chimodzimodzi?????
kkkkkk….u mean next year azachita chimodzimodzi?????
Kkkkkkkkk Lol
Ha ha ha ha ha
Pipo commit suicide because they can face the society that reject them
Q
No nid to say RIP ukause malinga ndi zintchito zako wamva
Tizaonana uyende bwino
Wrong Turn ma sister nd judgement ahead. Eish bt why? Just. gone for nothing
Sad. Life is so sweet. Always share the burdens of your mind with a trusted friend or relative. RIP Cecilia. May the Lord have mercy on you.
OMG..this is what i heared when i was young that the world will be destroyed
mmmmmm their very few pple who cud understand u.others instead of listening they start judging u. I choose to keep silent but I tell u it hurts alot
So sad to those have same of killing themselves
Very nice
uyende bwino
paja mtima mulibe
kkkk zofuna zo!
oooooh pot mwatero ndinu.
joe nanga pali chfukwa chomvera chsoni?! 2016 sakuifuna
The reason we both can’t understand is that scientists have not been able to invert machines to measure mental pressure.
then be ascientinst
Ambuye munampanga ndi manja anu ndipo ndi ntchito yamanja anu
Tikukupemphani adayesetsa adakali moyo zamukanika kulimvesesa dziko lapansi ndipo wazikakamiza kuchosa moyo wache pazifukwa zoziwa iye ndi inu mulungu wozowa zobisika. Komabe musapepuse ntchito ya manja anu ambuye. Mulandireni ndi mtendere wosatha kuti waipayo achite manjanzi ndikiti azondikire kuti zonse ndizanu.
Ause ndi mtendere wosatha Ambuye. Amen
mr can never b.
nde siyan kumva chsoni pa znthu zopepera,,,
zopepera imfayo?
kuziphako,. thats being stupid,, c’mn joe u mean iwe mavuto ulibe? u do bt stil umapilira,,, nde uyu akuzpheranji? problems dnt last okay..! no need to feel sorry
as 4 me am lukn forward to 2016
ooooh moto unapita kuli tchire. muzisamala ndizomwe mukamba
Moyo womwewo ena akumwera mankhwala a tsiku ndi tsiku koma iwe ukuwutaya ngati tsisi lakumutu iwe R.I.T
Thats the power of the devil.May her soul R. I. P
amaleka kupanga zimenezo mawa bwanji…….a breake record
Becoz. …?
Happy new year!!!
Hahahaha anakakhala kut moyo amagula ndkanangomugula moyo wakewo bas.akudikula satana pachipata akulandile.
Amaopa Mantha ????
rip
Go wel
Kutopa ndi mgayiwa. Zake izo. Mulungu sakondwera ndi infa yotero äääääääääääääää
Ok tamva…kwaose wofuna kuzimangilira okha contract me pls ndili ndi zingwe zabwino zosaduka wamba…
No apparent reason,zovetsa chisoni.
Next plis
Very good,she must go
Kupepera nd anzake ali chipatala kufuna moyo,iye ndikuxipha dala?amaona ngati abwerela!mbuzi yamwana.
agues she oz afraid of facing this strange thing cald “2016”
R…I….P….
why shud she afraid of 2016.you are funny friend
mexa ali 4m 4…kuli mayexo2 2016 man..
mexa ali 4m 4…kuli mayexo2 2016 man..
why?
nde palibe zifukwa zachitisa?…eishh..so touching..
thats bad!