Bwalo lamilandu lamasula njonda ina pa mlandu wakupha
Tsopano Mavuto Phiri ndi mfulu popeza bwalo la milandu ku Karonga lathetsa mlandu womwe wakhala akuganizilidwa kuti adapha mchimwene wake mchaka cha 2018 pa mkangano omwe udabuka pakati pa abambo ake ndi mchimwene wake amene… ...