Ndizipanga hayala apolisi a mfuti – Mpinganjira wachenjeza ochemelera Wanderers
Mtsogoleri wa timu ya Mighty Mukuru Wanderers Thom Mpinganjira wachenjeza ochemelera timuyi makamaka aku Lilongwe pa nkhani yoyambitsa ziwawa, ndipo wati masewero aliwose aziyitanitsa apolisi okhala ndi mfuti kuti akathane ndi maliwongo aliyese. Izi ndi… ...