Njonda ina yafa pomwe imafuna kuba Nsomba
Njonda ina yazaka 30 zakubadwa m'boma la Mangochi yatsikira kulichete itamira panthawi yomwe iyo imafuna kuba nsomba mumisampha ya asodzi amzake pa doko lina mnyanja ya Malombe. Nkhani yonse ikuti mkuluyu yemwe dzina lake ndi… ...