Bambo wamangidwa poponyera ana ake awiri m’chitsime
Bambo wa zaka 32 yemwe anayambana ndi mkazi wake, ali m’manja mwa apolisi mu nzinda wa Lilongwe pomuganizira kuti amafuna kupha ana ake awiri powaponyera muchitsime cha madzi momwe akhalamo masiku atatu. Wofalitsa nkhani pa… ...