Yawo ija angoni: fisi wapangidwa ndiwo ku Ntcheu
Sadyeka uja lero wadyeka: Angoni a ku Ndagoma m’boma la Ntcheu adodometsa gulu pomwe achita ndiwo fisi yemwe wakhala akuwathera mbuzi m’mudzimo. Izi ndi malingana ndi kanema ina yomwe anthu akugawana m’masamba a mchezo yomwe… ...