Chamba chathilidwa moto ndi apolisi
Matani a chamba olemera makilogalamu oposa 1,150 omwe analandidwa kwa anthu osiyanasiyana chaka chino athilidwa moto ndi apolisi ku Mponela m'boma la Dowa dzulo. Malingana ndi mneneri wa apolisi m’bomali a Macpstson Msadala, apolisi atentha… ...