Sanachiteko olo msonkhano umodzi oitanila anthu ku chipani. Olo kuvala makaka a chipani sanachiteko.
Osewela mu timu ya Bullets amene tsopano walengeza kuti mtima wake uli pa ndale, Anong’a Fischer Kondowe wanena kuti iye ndi oyima payekha.
Kondowe wanena izi patangotha ma ola chabe a Sidik Mia atamulandila ku chipani cha Kongeresi.
A Mia amalandila anthu amene aonetsa chidwi choimila Kongeresi mu chisankho cha 2019 ndipo mmodzi mwa anthuwa anali a Kondowe amene akufuna kuyimila pa mpando wa uphungu ku dera la Kum’mwera mu boma la Blantyre.
“Ine anangondiyitana ku msonkhano wa atolankhani, sitinakambilane zolowa mu chipani,” anatelo Kondowe polengeza za kupotoloka kwake.
Iye ati tsopano ndi okonzeka kugwila ntchito ndi zipani zonse osati Kongeresi yokha.
aaaaa, kuvotera Jah man? votiyo ndie kungobetsatu! kkkkkk, ganja eti??
Jah man ukazawina uzakokele magesi kumanda
Koma abale fodya
Chamba chimkawapindulira achina Dube, Hill, Marley ,Spear koma awa ndiye ai
awa angotaya ndalama ngat ali nayonso that is
Ndudu.
Azachita manyazi akusemphana ndi boma
Page iyi cholinga chake ndikudanitsa anthu nkhani zolongosoka timadzimvera kuma page ena kuno kulibe admin olongosoka
Chamba
Koma MCP inakoladi Chule eti? shaaaa!
Anong’a nzeru zako siudakhwime and waoneselatu kuti azikugwedeza aliyense obwera, chifukwa chisankho siudapange. Dziwa kuti mmera mpoyamba ndipo ukachedwa anzako atola khobwe ukuliyayalo kenako udzalira madzi atachita kale katondo
kkkkkkkkkk mmesa dzana mumkati mcp yakola chambo ndie zataninso
Kkkkkk komatu utsiwu kumakoka bwino
Kongress ili ndi anthu amakhalidwe okhazikika not tossed by any simple winds that surely yours couldn’t match!
Ine mdanenapo kale kuti uyu mukuti Jahmanyu sangakalowe mparliament ndi tsitsi lake losapesa kuti adzikachita mbwerera zake zimenezi. Akungofuna kupusitsa anthu uyu kapena afuna achite fundraise… Mmmmmmh.
Chamba awa
koditu chambatu sifodyatu
FISHA PAMENE ANALENGEZA KUTI AYIMILA MCP AMBILI ANAYAMIKILA BUT NOW WASINTHA THASWHY AMBILI AKWIYA KOMATU MUWELENGE MAKOMENT ,PAMENEPO NDIPAMENE MUNGAWONE MAVOTI AFISHA ,MUNTHU SUNGASIYE CHIPANI CHAKO KUKAVOTELA WOYIMAPAYEKHA NANGA POTI ZAWONEKAKALE KUTI NDICHENJIGOLO MAWA AKALOWA KUCHIPANI
Chamba chake chimenechi azikapanga ku Parliament ndiye dziko lingtukuke??….a Malawi tikuyenela kuzindikila kuti ngati tikufuna kuti dzikoli litukuke tikuyenela kukhala osamala pa anthu omwe tikuwasankha kukhala adindo zomasankha munthu kamba kachisoni kapena jst for morale dziko la Malawi lidzakhala laumphawi mpaka kale kale, a Malawi sitimakhala serious pakachitidwe kazinthu that’s why Malawi amangozungulira malo a modzi modzi…Ngati tikufuna dziko lathu litukuke we need change our mindset and mentality we need to be strong in our thinking capacity and in decision making let’s be tired of dancing the same old songs anthu ngati awa tawayesapo ndipo atilephera ndipo ena ndi awa akutizunzawa we need to get a lesson and say enough is enough!
kkkkk kma guys
ine mdakakonda mtafunsako anthu akuchilobwe ngati mukundimva pano kd fisher kuyambila kale ndiwachipani chanji? vuto pa fb pano timangopusisanapo mwachitsano nd olemekeze alucius banda akangolemba nkhan yotsutsana nd boma macoment amakwana khumi mkumwendo pano koma akangolemba zoyamikila boma palibe amacomenta pano ndiye fisher ngati ukundimva panga zako usamvele zapafb pano anthu onse akuti chambawa sakhala kuchilobwe ndichamba chakocho panga zot usangalase anthu akwanu bas zitamveka kt walowa mcp dzana anthu ambir amat wanyika lerons akukamba zina malawi amoto ndi amenewo
FODYA wakoyo umangidwa naye.
Chamba chidamuphweteka kale kaaalee
Aaaaaaaaa akagwere uko nfichamba chakecho
Anong’a ndiwe chisiru and sudzawina,wayamba kale kuwapusitsa anthu fwetseki!!! shupiti’!
dyamani yakuona yereyi shaaaaaa?!!!!!!!!!!!!!!!!!!
Ubwino wake wake anthu amabwela okha ku mcp simagula anthu ndiye ngati anali fodya adzava kuwawa 2019 ife tikupita ku kenani mcp 2019ukudziwa kale wekha kuti ndi boma
Koma mutithandiza a shadow???
Ma player akasiya kusewera mpira amavutika mmalawi muno! mwina akufuna kutukula masewera a mpira kudzera mu ndale⚽⚽
Fodya si wa bwino, makamaka uyo asutayo eish.
Ndipo ku parliament kumapita anthu olankhula chizungu nde awa chingerezi chawo . (2) Kumapita anthu a descent, nde ma dreadi yalakwa. George Weah anapita ku sukulutu.
awa koma ngat ndi ganja apenga .komaso adzaluza sangathandize anthu .awa ayi mngampira +ganja osat izo ayambazo
Munthu uyu ndiwachambadi dzanadzanali anali ndi Zidik Mia,sanakuone ndani.
Musiyeni munthu kunali kuyamba kugwilana chanza ndili Munthu wotchuka komanso wandalama zake ndiye mwina amaganiza ngati amupatsa poyambila. Koma ndingomupempha kuti akhazikise mtima pansi & apange chisankho cholondola
He need to taught a lesson don’t let him to get away with it ngati chinali chamba awone polekera MCP khwiyaaaaa!
kukhuta chamba ukufakupeleka manyazi ku mcp eti komawachepa 2019 samala ndichamba chakocho
inu awa olo ataimila mafunde bullets ikamuvotera
Ngwazisodi akagwere
His advisors are driving him crazy
Under duress kkkkk
Eeee koma chambachi mukazawina ndiye kuti muzasegula mafakitale achamba kumalawi kuno mwina anthu azalemelako kkkkkkkkkkkkk sopano mia udakumana nawo utabandika kwambili ? Kuti sumaziwa chomwe chimachitika
Mphanvu ya utsi
waiting for mr fb robins john banda to comment!!
ANON’GA GANJA,CHANI?Inu mmaona ngati anthu sanakuwonen muli ndi nsena uja
anali atachisuta pomwe amakakumana ndi a Mia, ndi chomwe chimamtuma chimenecho!!
fodya anawapweteka awa
Fisi pankhani ya nsatsi
Waionela Pataki ndimadabwa ine ndiye mpaka mcp iiiiiiihyaaaaaa
Koma Jahman hahahahaha 😀 😀 :p wabanda eti
kkkkkkkkkk so fany
Kanundu eti! kumazimitsiratu!
kkkk ndiweyo kaaa anong’awe
Ndi wachamba uyu sazikwanitsa izi!! Nde amakatani kwa Sidik Mia?
kkkkkk