Ife tikuti kunsewu toto – atero ophunzira
Ophunzira msukulu zaukachenjede mdziko muno atemesa nkhwangwa pamwala kuti sapita nawo ku msewu kukachita zionetsero sabata lamawa. Bungwe loyang'anira zipembedzo mdziko muno la Public Affairs Committee (PAC) lamema anthu kukachita zionetsero lachitatu likudzali pofuna kukakamiza… ...