Mzuni have rubbished claims on social media that they have been promised money to win their match against Be Forward Wanderers.
According to the rumours, Mzuni has been told that they will be given K1.9 million as a top up for player allowances if they beat Wanderers.
Mzuni Head coach Alex Ngwira told Malawi24 on Thursday the reports are false.
He said Mzuni are going to play as usual not because people have promised them money.
“Nobody can force us or tell us how to play, we started the league with a mission and that mission we are going to fulfil,” he said.
He added that the team will work hard to win the match because they want to finish in top eight of the league.
The game between Mzuni and Wanderers was originally expected to be played last month but it was abandoned after the Mzuzu based side refused to enter Balaka Stadium saying Wanderers supporters had assaulted Mzuni’s officials.
This weekend’s game will be played at Civo Stadium in Lilongwe.
You mean Mzuni doesn’t want to win?
Zisiru inu u just write rubbish. You write stories based on rumours. You don’t out to fetch raw news
Inu mumayesa avomera koma Malawi 24 ndi panja penipeni
Apatu zaonetsa kuti bullets simatengera leage chilungamo,zinyengo basi.
Ndikupepela kumeneko angobesapo dolazo coz Noma will carry the game
Is being promised incentives match fixing? Koma journalism ya Malawi.
Ok Tamva
Bullets yalonjeza 1.9million kuipasa mzuni ikawina
hahha tiwagagada Ana amenewa mpaka akasimba zoona kwa a chancellor awo
”We’re Manoma, we’ll crash mzuni like a thunder, no matter what !”
Pali amene amafuna kuluza? Ma team anakati aziti akalandira ndalama aziwina ndiye zikanakhala bwanji? Za zii Mzuni more fire tiri pansana pakopo iyaaa. Noma mukuchuluka zokamba kamba bwanji? Mukamenyrnso ma official a Mzuni mukaona pplekera.
Are you Adimn telling me that a certain team has promised 2 pay Nzuni so dat they win the coming game?? Where on earth did u c such a thing happening in football history?? Can’t u c dat yo post has got nosense?? I think u must go 2 d hopital 4 medical check up b’coz u r totally insane.
inunso apatse zina kuti akaluze
palibe team yingakwanitse kugula Mzuni..
Matha amenewo neba wayamba kubwebweta zopanda pake
Sono mmaganiza angavomere while they knows kut match fixing ndi mlandu???
Kupereka ndalama kuti akawine?zosamveka zimenezo
Oro neighbour utapereka ndalama ifebe league tikutenga bas
A Wanderers mitu yawo sikukoka angobwebweta zili zonse vuto lozionera kuukulu ndilimeneli kuwina kwawo league season ino timva nako mbwelera
Ngakhale atalandila ndalama koma nzuni siingaphule kanthu ngakhale atabwerekera maplayer akampopi.
Aaaa Tkawapatse Ndalama Yachani,amene Akutchukitsa Izozo Ndi A Noma.Ngat Kwalembedwa Kut Azawina Nde Kt Zizatero Ngt Ayi Basinso.A Noma Msanjenjeme Chikho Chili Mmanja Mwanu N Zili Ndi Inu Kuwina Kpena Kuchitaya.
hahaha Mzuni nde kachaninso?
kodi mzuni ikadzaluza adzabweza ndalama kapena adzatani bola mzuniyo ikanakhala kuti ikukasewera ndiina koma osati noma
League Ku Bullets si zachilendo nde palibe chifukwa tingachitike chinyengo izi ndi zopasana wina akatenga chaka chinaso wina atenge nde timati league ikukulano
Mzuni sinandikhumudwisepo ineeee …..sopo ina amagokula koma ili yosalimba !!! Go Mzuni go
Koma Sundy Wina Azafa Ndi Mtima Kkkk..Noma 4eva
Tiwanyenya ana amenewo…apange fix za manyi zawozo kma ife tukwapula ana wosasambawo
aliyense akusuka yake
kkkkkkkk am a nbb fan komano mukuti yapatsidwa dollar kuti ikawine ????? lol mukanati mwina kuti ikaluzetu if happens kut sikawina azatani lol only God knows amene atenge super league
ukasuta chambatu siungaone reality on the ground…dele ukulotabe utatenga league?? aaaaa..fodya siwabwinodi…league yapita basi ku Nyerere..wake up from your slumber
u missed my point brah
Neighbor wamagalimoto sindimatha kumunvesa wayamba mantha2
@ atenga kale mmmmh zabhobho koma
Kapado fc mantha kaya 10 yrs osatengako super league
Belanani ndalamazo
hahahaha Mzuni nd Riesta City ife a Noma timaziwa koma tikayesesa
Whether rcvd money or not Nyelere will beat them up by 2goals to nil
Am #KB fan but am with Nyerere aka Manoma
aganyu mulira nonse tooooooooo
Go Mzuni, draw yokha ndiyokwanira