Nduna yakale mu boma la amayi imene tsopano ikutsogolera bungwe la ndale a Moses Kunkuyu achenjeza Mtsogoleri wa dziko lino a Peter Mutharika kuti athamangitsidwa pa mpando ngati sasamala.
Malinga ndi malipoti a olembankhani, a Kunkuyu ati a Mutharika atha kuthamangitsidwa mwa chipongwe pa mpando ngati sachita mwa kufuna kwa a Malawi maka pa nkhani yosintha malamulo a zisankho.
A Kunkuyu anati ukavuwevuwe wa a Mutharika ndi chipani chawo cha DPP upangitsa a Malawi kukwiya ndi kuganiza zothotha a Mutharika pa udindo wawo. Ngati mmene zachitikila ku Zimbabwe kwawo kwa Mugabe.
“Anthu amatopa, ndipo akatopa amalowa chiwewe. Nkhani iyi yosintha malamulo a zisankho si nkhani yaing’ono, ndi yofunika a Mutharika asamale nayo. Atha kupeza nayo mavuto,” anatelo a Kunkuyu.
A Kunkuyu ananenapo kuti mavuto a Mutharika atha kuyamba ndi zionetselo zomwe akufuna kuchita a mipingo pa nkhani yomweyi.
“A mipingo akangochita zionetselo, basi mavuto atha kuyamba pamenepo. A Mutharika ndikuona zimene akuona a Mugabe ku Zimbabwe,” anatelo Kunkuyu.
Ndibweledza kuyakhura mau amene anayakhura Ex President Dr BAKILI MULUZI Vutoraife a MALAWI ndikuiwarasanka PETER MUTHARIKA 2019 wamuboma ELECTRICITY BLACK again pokhapokha titazipeleka kwa MULUNGU WAKUMWAMBA 4 ndipo Yona anayamba kulowa mudziwo ulendo wa tsiku limodzi, nalalikira, nati, Atsala masiku masiku makumi anai ndipo Nineve adzapasuka 5 ndipo anthu a Nineve anakhulupirira MULUNGU, nalalikira cosala, nabvala ciguduli, kuyambira wa mkuru kufikira wamung’ono wa iwowa 6 pakuti mau awa anafikira mfumu ya Nineve, ndipo inanyamuka ku mpando wace wacifumu, nibvura copfunda cace, nipfunda ciguduli, nikhala m’mapulusa. YONA 3:4-10 auzeni a president tipange zomwezo muzaona MALAWI azayamba kucitatso bwinu vs 10
Malawi is Malawi, Zimbabwe is Zimbabwe. Peter will be our president till 2024…
TEL HIM JET-LI,RILY AN IDIOT CHINERE CHAKUFWIKAPO.
Atseke pakamwa pake ameneyo nzake ndi chakwela uja akumangotukwana ku parliament osakhala ngati anali m’busa sangawine ameneyo saiwona vote yanga abwelele ku ubusa konko osati president kulibe chake kumeneko
kodi kunkuyu ndi m’silikali?
Sizitheka zimenezo zibwano eeeeti
kodi mula ukufuna kudzankhala wandale m’tsogolomu?
Escom chaaaaaa
Iyi nde misala
Tachedwa nazo!!! Waionela patali chifukwa cha Mugabe. Munva posachedwapa akuluakulu athu a nkhondo akumwa tea wa mkaka Ku state house kwamagetsi ndi masana omwe. Ife tikuyang’ana ka MK10.00 mu mdima kuti tikagule machesi.
A classmate anga kupulaimale pa katolika insititute alakhula.
Ndakunvani ada. Ngati mungawelenge ndemanga yangayi. Mudipelekeleko moni kwa denesi tambala K omanso khilisitofala dambuleni.
Osaiwala lelana phiri.
Agolokipa anthu akupulaimale.
I was here read the comments
Pakamwa ngat pachimbuzi nonse mukut mlomweyu nd wabwino mmachende anu
KAMWAO AKUWAZA A ESCOM KUTI ATHIMISE MAGES AKUWAITAN PAMENEPO
Comment Reserved….
Amozy, titati tikubweretsereni a Mutharika kuti muwathothe, simungathawe? Mbwerera zimenezo?
Iwe Nkuyo kaya ndi we Mukuyo za fodya ayi kuno ku Malawi tikuthotha iweyo, leave our President alone,
zachamba zimenezo , iwe kunkuyu uwuzane ndi anzakowo kuti : APM simungamuthothe , ngati ndi ndale mwachepa nazo . anthu olephera pa ndale inu .kuluza ndi u mp kwanu? kunkuyu ndiwe omvetsa chisoni
un empty tin makes alot of noise! zim and malawi are two different nations
The man has not helped us,as a country
TILI MOMOOO
Kumkuyuyo oro mzeru imodzi alibiletu,amuthotha APM ngati ndani,
Zonena Nenani Ine Pambuyo Pa MCP Tionane 2019 Basi.
sakunama ndilipambuyo lake ameneyo
Kunkuyu is another useless moron. His political grouping is devoid of substance.
A kunkuyu alive nzeru
Kunkuyu pamtumbo pako machende ako mbolo yako,mkongo wa mako,mavuzi ako, iwe undisamale nya mako munthu opanda nzeru mapwara ako
Palibe chipani chabwino chomwe ndimachiona chopotsa DPP
has he led the country for 37 yrs or the economy has become disastrous as in zimbabwe?
Malawi 24 now i understand why u failing to report facts its bcoz u still using bicycle
kunkuyu ndikachan ngat wasowa chokamba osangosatira maiwako adathawa uwa uja bwanji dzina lake ndaliiwala tandikumbuxa ndindam paja chenjezo udekhe uzazalakhuleso zopusa zakozo wamva!!!!!!!!!
Achoke pampandodi ameneyu..ozikonda
hayamba hale hayambale hale Ku njenjemera
Yoh
Kunkuyu is an idiot like chakwera and amai. Bunch of thieves who want to destroy our country, try that yuo idiot kunkuyu and you will end up in jail while rotten.
TEL HIM JET-LI,RILY AN IDIOT,CHINDERE CHAKUFWIKAPO
Ha ha ha ha! Chindere cheni cheni
I lost trust in Kunku because he is a failed politician
Timuthotha nyapala ameneyu….. I second you Kunkuyu
Iweso ndiwe kape mteshaa zoona nde kt uli Ku Zimbabwe mavuto osewo siukuwawona man mkunama uvote ndiwe osat ozindikirafeee
Well done kunkuyu ,only kamuzu was great sabuluziwa akungotizuza ndi umphawi iwo akudyerera
Cheya anathotha kale Kamudzu no way kuti muthothe ndani idiot unakukanika u mp iwe
Ndipo awa ndamene anaononga dziloli heavy.
Zaziiiiii, mix kusowa zolemba
aaaaa sillY
As chipani we can nay waste our time urging with senseless man like kumkuyu. Coz or atavuta bwanji sitingagule plumber ngt ameneyu
komandiye tu kunkuyu anthu akutukwana amaona ngati anthu amakukonda iwe ndiwe mbuli ya chabechabe
If you are musician I don’t see reason why you shld force thyself to comment on things that dils wil marketing. Akukumkuyu ndivuto la school and I hv nothing to say to him.politics ndi umbuli ndiyoopsa hence you die early while poor ask jb etc.
Kunnkuyu usanyengeke ndi kuyimiraMCP udalephera ndi amayi u like mboma ndi year UK a wine u like opposition
Who is kumkuyuuu
unapanga chAn wee mkukuyuu thaw yomwe unali m’mboma?zapamtumbo bas
Naoso a kumkuyu alindiudindo owona mavuto adzikolawo alakwachani?4tseki mulekele2.
Mauleeeeeee woyeeeeeeee
Akunkuyu zelu pa spoon!
Zongoganiza chabeeee
Kunkuyu you are un cultured barbarian, alunatic acomplete dundehead, chitsilu chomwa Madzi ometela, afailed politician .Dont take advantage of civilised leadership and make stupid statements, konza kachipani Kako Ndi Amako komw e aliko,dont be acoward
If you know what’s good for you just keep your mouth shut Mr kunkuyu………………sikaletu lija mumkawanyoza a chakwera lija
Zopanda nzelu,kungotengela zochita anzanu basi,pali zifukwa zokwanila ndi zoveka bwino zomwe akumuchotsela mugabe osamangobwbweta zinthu zosathandiza aaaa
Zoonad kut a Bungwe la ESCOM apanga ubale ndi azipani zotsutsa. Koma asamale akhonza kuluza ntchito kaya mwadya ma million koma mukunama ndipo muzakhumudwa.
Whats wrong with us Malawians. Why do we celebrate ignorance? Why is unpatriotic sentiments are being amplified and regarded as courageous. Why and how do we even find parallels between the situation in Zimbabwe and Malawi? Zimbabweans are just trying to do what we did two decades ago and we find that relevant? Really?
Kunkuyu are u also army commander mmmh tell me kapena you are a leader of lebels
Amaine Kangunje!!!!!!amaine Kangunje!!!!!!! a a abale pepanitu ndinangoyamba kulira ndinali ndisanawerenge nkhani yake ndimangoesa ngati ndiyampira wazulo kuti angondikumbusa ndie aaaaaa ndangolira ulere eti??????
Kkkkkkkkkkkkkkkk Atupele Muluzi Boma
Let you kunkuyu try we gonna burry you alive plus in Zimbabwe it’s the soldiers who did it not a mare civilian like you kunkuyu.asatilankhulisa pambali mbuli ya mwamanase iwe
Inu Moses kumkuyu munthu oti anakuza u Mp angatiuze chani zandale.kodi panopa ali chipani chiti?that idiot got nothing to share with us he just wanna be on the media since he is not a public figure anymore. I can’t buy his story .Idiot.
Kunkuyu mnaba ndalama sitikufunani. APM usadandaule umalizitse term iyi. Koma 2019 mavoti onse kuchosera voti yanga. Ndilibe nthai ya Kunkuyu komanso nthai ya DPP.
Kodi mukuti kankuyu kapena kunkuyu? NdikuMalawi konkuno amenryu?
Kunkuyu is one of the Malawian Idiots bcoz he is failing to call his former president to answer or defend her Cashgate Corruption and he is still making noises for nothing,
Aproverb says: ” An empty tin always makes alot of noise”, refers to KUNKUYU.
Mugabe amuthamangitsa ndi achipani chake ZANU PF inu ndi a DDP?
Who is Moses Kunkuyu afta all?
Kkkk akunkuyu Shaaaa mtsogoleriyu nde akupezeredwadi ndi inu nomwe mpaka warning haaaaaa
Kodi nanu a Kunkuyu osamapita Ku UK kogulutsa mowa kuja bwanji? Mwina mukabweleko ndi ndalama zina tidye nawo 2019, izi nzopanda nchere Muyankhula apazi, zinakulakani basi no mita now for you!!!
ZACHIPANI my foot bola bash DPP sitimayifila bola dash
Kunkuyu and ur fellow idiots u cant compare malawi Ndi Zimbabwe,, totally different… Umean millitary ilande boma coz of black out?? U are afool big fool…. ukuopa chani 2019,, muuzane anyani inu APM timuvoteranso 2019 kaya wina afune olo asafune,,,, ovota ndife,, zautsiru upse mtima zenizeni nyapaphi!
Akuluinuso Osacita Manyaz Bwanji Apm Leloso Nde Muzamuvotela Wot Sangawineyo Zawuchikapesotu
Zimbabwe2 Mwene idayambanso momwe ikupangila Lawiz panomu Ndiye muziganiza kuti Zimbabwe inali pati.
Zimachita kuyamba.
Mudakali ntulo amulakho inu mutharikanso nd ndani
Kkkkk ipondedwadi mbava imeneyi
Kukunyu ndie ndaniso finye ngati uyo akhare dolo bwenz atalephera kkkk
Tamuuzan ndinu
Wasowa zochita ameneyo mesa iyeso zinamukanika ndi mchemwali wake uja nde pano azioneka ngt wanzeru, kumeneko ndikufoila
Simuwinaso muwona
A president alephela awa . he is a total failure I have never seen. To hell with your president.
iwe ndi kape mbuli chabechabe mulesi kwa gwele uko
rikhedal..rikhedal
Aaaaaaah ndikunama ngati.
Akutivetsa pain
Aaa Iwe Kukuyu Unali Mboma Momwemo Ndi Amayi Oyipa Aja Mumangobaa Basi Ndiye Lelo Uzichuluka Mzelu Asiyeni Apwiyapwiya Amalize Mwabata
some where some people are gearing up to vote for a person who is just old as Bob…..kkkkkkk….Lord have mercy…..
Za ziii
Apakire zake ameneyu tatopa naye dziko lanji lokhala ngat president kulibe
Kkkkk
Pepa iwe Kunkuyu leka zimenezo kapena ukfuna usoweso kachikena ?
choka!!!kapolo iwe
Tazingonenani zakwathuko ku Malawi Mugabe palibe yemwe angamgonjese ali nganga m’boma
Ulemu wanu Mr Kunkuyu tiyeni nazo munthu ukakhala mtsogoleri sikuti ndiwe opambana ayi koma a fake Professor Muthalika ndi munthu osazindikira ngakhale adapitako ku sukulu. Kafunse kwa Mugabe akakuuza military yake yomweyo imakupatsa shawashayo izakununkha. You are a foreigner why Malawian accept a foreigner to run the country.
So shameful….
Tikamaseleula ndi apresident athu chakwela amaona ngat ndizenizen,chomwe angaziwe MCP singazatengenso boma ilindimbir zot anthu sazaziwala mpaka kale,ndpo asamasewele ndi Dpp sangamake”
2019 ndikila n mcp
hahahaha you are failing to manage a three bedroomed house ndiye uzikanena kuti uthotha munthu wa mkulu ngati uyu usawi .
kkkk mene mukuonemeramu mungayambile pat inu
Inensooo ..kunkuyu tikuthothaaa pamalawipano chabwino unapanga ndi chani?
Mentaly ill again….?????
Hahahaha who is Kunkuyu?? Opusa ameneyi ndithu. Akuona ngati nzophweka?? Ali ndi udindo wanji iyeyu?
Mr kunkuyu mudali kuti mwaona inu kuti anzanu ku Zimbabwe achita zamphamvu ndiye mwayambapo kunena zopanda n’zeru.Khala chete munthu wopusa iwe ndipo usadzabweredzenso kunena kawiri ai. Ifetu tikadalipo aDDP ndipo tiwinanso osati za inu aPp chipanichi chidatha ngati katani, kodi Mr kunkuyu m’tsogoleri wanu mayi JB ali kuti? Kkkkkkkkkkkkkkkiest ndikuyankhire akuti adathawa pomwe adaludza chisankho cha m’chaka cha 2014.
Za ziiiiiiiiii……..nthwi yonseyi anali kutko,kuyendesa2 boma ndi ufumu ndzosiyana
mul nd zochosera munthu pa mpando inu hahahahahhah…asilikal akungolimbana ndkulanda makala bac
Kumeneko ndikusowa chochita A Kunkuyu ndi mbuzi yeniyeni tell him asabwerese chisokonezo mmalawi muno akoza kusatira ambuyache,ndanyasidwa naye ala!
We are far behind than Zimbabwe
Kodi chifukwa chikupangisa kuzima kwa magesi, mukukhala ngati simukuchiziwa bwanji?zikukhuzana bwanji ndilumuthotha president, yakula ndi nsanje, mumafuna mutakhalapo Ndinyengo, dikirani 2019
Nde kuti a kunkuyu samva chingerezi….kkkkk mugabe sanathothedwe man…anathothedwa ndi iweyo ndi amai ….kunkuyu has nothing to offer to malawi….he is just frustrated.. What he is saying is just a kick of dying horse
Palibe chimene angapange uyu
Iyeyo zinamukanika bwanj mu nthaw yawo,ndiofoila ameneyo
I like Mugabe readership 100%
Nkukuyu ndi mbuzi yamunthu
APM akuyeneka kukhala ochenjera zedi chifukwa chakwera ali nganga ndi bungwe la Escom kuti magetsi azithima nde azinamizira kuti apulezidenti akulephera ati campaign chakwera tionana 2019 tambala wakuda muno sadzawinanso.
Aaaaaa a u sick?
bambo magombo muziona inu 2019 tambala wakuda sangawine taa and am reversing that question to you.
I mean aquestion u asked me
Inu Mukudelela Tambala Muli M’malawi Muno Koma Muthela Pamoz Ndi Pitalayo
Kkkkkkk km anthu enawa kumangolongolora ngati Ali ndi mphaso yautsogoleri enanu banja la ana awiri kumakanika kulidyesa ndiye 17 million kkk anthu angayambe kukusekani,mungothokoza ti manyuzi pepala tosaziwika bwinoti kuti timangopanga post zili zonse apo biii inu kunalibeko zamanyazi
Mtharikayo palibe akuchita bolaniso Mugabe muchotseni msanga
izo ndi zanu muisova ku malawi osathawako bwanji amene tili kwa zuma kuno mukuona ngati sitikufuna kukhara ku mw , my moyale, my team khudah continue doing the job
Machende ake kunkuyuyo..
Koma zili kumalawi
Hon. Kunkuyu some times silent is better than nosense
Maloto a chumba
Mr, kunkuyu stop smoking expired weed
Izoooo izooooo!! Atimliwe huyu mzeee
I second, APM this electricity issue it’s just too much
Koma Nyimbo zagwaladi zimanveka bwino
Kunkuyu ndichitsiru kwabasi, ukafanize za ku Zimbabwe ndi kuno?
Besides, is Peter a dictator?
Ngati unakulaka u MP ndiye uzikachuluka mnzeru?
Unathawiranji ku BT?
Anthonthedwe osagwila mutuyi
This is another mad man needs medical attention he is frastrated tayerekeza tione
Kkkk thats the meaning of “Presure Group” in Malawi.
Nsanje basi mukuchiziwa chomwe chapangisa kuti Mugabe amuthothole inu
kikikiki mugabe still in power
shaaa.. Nde mwati Bullets yatani?
Iwe vaya uko
ukhaula neba.Wagwanayobe ng’oooooo
Haaahaaa kunkuyu lol
nzamanyazi munthu amene analephera u mp nkumanena moteromo,,,ngati simutha kuyankhula just keep quite!!! Achinyamata amene tikufuna si ngati iwe aaaiiii,,tikufuna the likes of Vp Chilima,,Hon Atupele ndi ena ambiri ,,
et wachamba ngt ameneyi
Kodi munthu oti analuza kumudzi kwao angatiuze chani.he is desperate for sure.
Komansotu ndi kape wachabechabe.Ngat uli dolo bwanj sudawine pa zisankho zija??usatilakwise okanidwa ndi anthu akwanu omwe iwe
kkkkkkk ndi zoba kkkkkkk akungofuna kutchuka
Hheee a kunkuyu ndi manyaka enieni angokhala chete kumene aliko iyaaaaa
Aaaa Naweso Bola Mene Unatchulako Chilima Zinaveka Osati Atupelezo
Nde kupeperako kumeneko. Kumadalira zoonera basi?
Kulanda dziko mwaupandu sibwino tisawononge dzikolathu tingadzalile mawalino tisatengere kuzimbabwe,
kumkuyu ndi mbuzi zikuchitika ku malawi ndi ku zimbabwe zikufanana osakamba za mapenate anzulo bwanji za mkutu
Loading….
Timu ikamaluza anthu amakamba zambiri. Koma atakulowetsani palibe mungachite kumangozikolakola. Ndiye aKunkuyu kaya mwaiwala kut boma lanu linangoba ndalama nkuika amalawi pa mavuto? Mukuganiza kut inu mungasinthe zinthu?Muthalika ndi katakwe akuyendetsa dzikoli popanda chithandizo cha maiko ndi mabungwe. inu mabungwe ndi maiko ankathndiza dziko lino mmalo molitukula munabamo ndalama Kunkuyu ndi wopusa kwambir
Mutu onyasao iwe unganene kt pitala akuyendesa bwino ziko lino. Agalu nonse muzaona mmene azanu amayendesela ziko by 2yrs to come ndpamene muzaziwe bwno lomwe
Uyu Kunkuyu ndi chitsilu analephera ndi mayi wake uja ndiye akuona ngati DPP angayithe?
Kumalemba pano zopusa ayi ife aMalawi tikubvutika chifukwa cha mantha Bwanji Bakili Muluzi sadaope Nthawi imene ija kuti tilandile matipate. inu mudali kuti zimenezo mudzikapanga ku mbumba yanu osati ku mtundu wa amalawi onse ife tatopa ndi Umphawi komanso Bodza kumasangalala munthu mmodzi chifukwa chomuvotela. zopusa ayi.
Thats good I dear ineso sindimamuonera kukondwa mr mutharika yu
Kkkkk….. kaya zanu
Musiyeni president wathu wokondedwa alamulire,coz anamusankha ndi mulungu amene anaona utsogoleri wabwino mwa iye.
After all Mugabe is still President of Zimbabwe, therefore his reference is invalid…
Where does he get the authority to utter that nonsense?? His authority expired through the ballot box and he is just a mere citizen whose influence can’t be felt or atayima pachulu
Za Ku Zimbabwe ndi Ku Malawi zikufanana?sudziwa kuti anthu aku Zimbabwe amaoneka ngati ochenjera Ali wopusa,wosayamika??inu a kumkuyu,u, president mungauthe?
Thumb up Mozy!
Malawi police & soldiers tulo, busy kulanda makala nd fodya wamkulu,
anzathu ku zimbabwe akulanda ulamuliro mnanja mwa anthu o4ira
ndipo ngati iwo saphikiraa makala. chonsecho nawonso magetsi alibe
Ku Kamuzu Barracks magetsi samazima. Ndimakhala line yomweyo.
Nanga mukalanda makalawo mumawatan
mmmmm comment iyi ndi ya mbuli hvy u can’t compare zim situation and Malawi
Iwe mzako ndi wandale,muzikachezela limodzi ku mental
Palibe ali perfect,,, APM woyeeee
Woyeeeee
Kano Kali phe kumvetsera ndikuonerera
moto umapita kwa sala ntchile kkkkk
mfundoless
IWE UDALI MBOMA MOMWRMO NDIMAI AKO ATHAWA AJA MUNAPANGAMO CHANI SIMUNANGOBAMO NDICHITUKUKO CHITI CHOMWE MUNGACHISONYE KUTI MUNAPANGA 2years time munaononga mosaneneka anthu kudzunzika ndinjala ndiye lero ufuna ukhale wanzeru
Is Mugabe chased away?
Wachepa kumkuyu iwe Ndale sukuziziwa nde bolanso Vincent Wandale osati iwe
Where were u kumkuyu before zimbabwe sagga?
Battle of the cowards.
Inu ngati munalephera ndi Mai wanuyo ndizanu.Kupusa kapena kulephera pa ndale musapezelepo mwayi okamba za msogoleri wamalawi.Ameneyi ngati muli okwana pandale muzamchose mu 2019,kuno sikuzimbabwe.Amene ali mamuna azamchosa ameneyi pachisankho.Osadandaula ndipompano.
apiteso ku mental…
A chewa ndichocho ndi anthu okonda ziwawa Kunkuyu(Dedza)
Akufunika Ku mental ameneyi !!!!! viva mutharika!!!!!! osamutengera kunkuyu ndi openga!!!!!
I don’t know Malawi I know South Africa ndiyemwe ikundithandiza ndikusunga moyo wanga mwa ambuye
amalawi simukuona zitukuko zomwe ndapanga? miseu yozira ya area 24 ndi 23,malata ndinalonjeza aja pano ndikupangisa ku japan,simenti ndipangisa ku brazil,za magetsi musandifunse sindinalonjeze
Ineyo chipani cha DPP ndimachikonda koopysaa I don’t know why
ndiwe chitsiru
Ameneyu Nd #CHINDERE!!
Umafuna Akonde Zofuna Iwe?? Nde Chitsilu Ndiwe, Ife Nda Dpp President Wanthu Ndi Wanuso Apo Bwa
Siwathu man…ndi wanu
ineso ndimachikonda moti come 2019 ndivotera dpp chipani chowina baba peter kt chongi
Inenso ndachikonda heavy, let’s keep on living this successful party, bravo DPP
Anthu opanda nzeru odzikonda osaganizla zaena! Nkumat ndmakonda DPP ndizavotela Pitala, Lingalilan bwino, kumapanga znthu zot apindule ambiri, ngat muli pabwno stay quiet! Munthu wanj osamva zaena??
You have to see a doctor right awyt
Wow wow guzy we dot need to swears each others here lets works together to buld our beautfull country Malawi
Ine ndi DPP ndi one family
Ndikutha Kuona Kut Anthu Amene Mkuti Mmakonda Dpp Munalozedwa. Apo Ai Akakuoneni Kuchipatala Cha Anthu Amisala
No problem with loving DPP but if you love the president, go and see the doctor something is wrong with you ok.
#Vio umachikonda chifukwa ur one of those thieves & ur Prince Is Apm,dats De Reason U Love Dpp.
Losers are catching emotions already…..mupsya mtima simunati……DPP is here to stay
Osangomwa tamec muiwale bwanji/ osangodikira 2019, mutha mpweya mukulimbana m’driver pa chiongolero
kkkkkk auzee ilove Blue
ZOMVETSA CHISONI KUKONDA MBAVA MAG
hayamba hale hayambale hale ku njenjemeraa!!!
Ada kunkuyu ngati wakutuma ndi agalatiya othawa tchalitchiyo dziwa kuti akupweteketsa
Mapazi ake kunkuyu. Zeru zabwera liti? amakanika kuwauza amayi ake aja anabanawo ndalama ajana
Kufuna kutipwetekesa aphawife poti athu andalama inu zikangoyambika ndege mukuixiwa kare kokwelera , musati nyase munkati muthuyu ndiwabwino leroso oipa,Bakiri munkamutcha mbuli lero wakoma, come 2019 my vote goes to MCP
Haaa ukuona ngat mcp yakoyo idzasintha kanthu?
Ndi vote yanga siyako an idont care cause idont eat politics
All i want is ddp out and mcp in….
Ure with me
Be yourselves guys. APM is a President and no one can change that
Who cares
that can not change smting com bakili anaipa bingu anaipa amai anaipa uyu waipa ndye ngat mun2 akuipa asawne!!
Then lets change this paty if its like that
Patapezeka wanzeru like Late Michael Sata of Zambia zikhoza kusintha.
Kapena ngati President wa Ghana nzotheka.
Koma to say the Fact Petala ndi DPP yake aononga Malawi for sure
Kaya mmati dpipi zanu izo MCP yomweyo boma chatipatsa mphamvu ma bi election ma resources di pi pi inali nao koma zakuvutani basopu
guyz amene ali ndi charger cha sumsung galaxy andibwereke nditchajire phone pliz!
peter more fire…haters atilila
noxe kuphatikiza kunkuyuyo muuzane sizingatheke mukunenazo tayexan muone …… ine nd wa Dpp 100%
(Y) waiting
Kunkuyu ndi chitsiru anathawa ku blantyre zoba ameneyo palibe angamumvele
Kkkkkkkk pitara
IS THE PRESIDENT WORKING AT ESCOM?
the president controls statutory companies…escom is a statutory company therefore the president controls escom. Fotseki go to xul and learn premises and facts…mbuzi
no wonder ndiwe chaku thyolo
This one is indeed #Goat ya Mano kunsi
I see you don’t respect opinion from others boxer chirumba whatever you call your self ,if you know better it doesn’t mean is all of us.if you don’t want to comment keep your stink comments for yourself
If you don’t no electricity please don’t comment anything,,, when your phone battery shows low battery and went off do you know the cause? why can’t you make it full battery all the time?
Nobody has his own generation of power if u have reasources make your own machine,cause your noise may change nothing
dymon has a right to opinion
whom r u asking?
I havent mention any name bwana,whats the problem
IMBWA YAMUNTHU
Ask yourself
Ndayamika mulungu polenga ine kukhala imbwa.
Kkkkkkkkkkkkkkkk comment loading…………..
A kumkuyu ndiofunika kukawapima ngati ali ndi misala
Iwe ungathe kuyendetsa dziko?
Dont change the subject admin bullets penalty fc yaswedwa dzulo kuyesa kuwapatsa penalty koma zosathandiza
U Do Confuse Pple! Anthu Nkhani Si Ya Mpira Wa Dzulo!
Yampirayo ndiye yofunikira kwambiri man
Kkkk Kangunje
kkkkkkk yes yampirayi ndiye yofunika heavy kusiyana ndi izi cz andalewa palibe wabwino onse ndichimodzimodzi koma mateam yabwino ilipo imodzi baasi pa malawipano the plps choice not kangunje fc kkkkkk.
Kkkkkkkkk kma guys
Or Abraham Bandah akudziwa za shasha ka ngunjeeeeee
hahahaa ref anabelekera neba nsalu yong’ambika.wagwa neba.
AKA Pigs fc get ready for Fisd cup finals against Moyale coz KB has withdrawn for unknown reason
kkkkkkkkkkk paja ñdamva çhoñçho kuti ñkhumba zoñse zafika muma fiñals a fisd kkkkkkkkkkk
Khuda mankhwala ophela bus ikubwela Friday fc
Humble Ishmael Ahoyie olo magesi asayake bola bullets yatuluka kkkkkkkkkkkkkk
Watuluka Fisha fc ahahaha
bullets ayipanga mugabe kkkkkkkk
Iwenso tachoka apa munaopa mzuni mmafuna free points mwanya
Nkhumba ndi bullets osati noma wamva iwe alick kazembe
Bola mwatulukabe inu a kampopi fc
Kuteleku mtima umakupweteka mmene tinkapitilira paja eeeti? koma iwetu ndiye unagwa mwauchikape bwanji..? round of 32 komansotu kuluza ndi 2 kwandanda…kkkkkkkk thats why u have taken 12yrs wthout grabing asuperleague yes…u are indeed makape of football here in malawi…#SHAME!
Salute to pples team
the post is about politics dont post foolis on others post #Stevie Kampezeni
I dont eat politics mr phiri kkkkkkkkkkkkkkkkkkkk
kkkkkk wapenga ameneyo
Yap lil talk kunkuyu osamaonelela zopusa anthu Ena anakula mopusa komangoonelela pamene zithu zikuonongeka
Mapazi ake zeru zabwera lero! bwanji sankaganiza that time ankaba ndi jb
akanakhala kuti amaba nawo bwenzi ali ku maula uku hahahaha
Ife Tinamuthamagisa Kuno Ku #Chilobwe, Kt Mbuzi Ya Munthu #Kunkuyu.
hahahahaha tiziona chaka chake ndichino
kunkuyu more fire ofunika kuchithamangitsa chopanda manu mkamwachi chatikwan t
Bambo ako angathe kuyendetsa dziko?
ayi koma anu.
Izi zandalezi enafe sikwenikweni koma izi zinali pa Civil dzurozi! akuti khaya #Moyale inagolesa ma penalty awo wose pomwe aneba anga anamupasila mmanja goloboyi wa moyale m’pira m’malo mochinya kkkkkkkk koma yaaa!!! zaulendo uno!.
Wrong packing wrong timing!.Let Moyale celebrate alone!
oky, but some tyms is better to join some1s cerebration.
Nkhaniyo Koma Mwaimva Kapena Mukungolemba?
Ndi ufulu wathu a Malawi kuchitapo kanthu ngati mtsogoleri wa dziko akulephela kuchitila zabwino anthu. Kodi tidzakhala olira mphaka liti? Iwe dzuka Malawi !!!!!!!
Upanga chiyani iwe piter iyi ndi team yoyamba. pomwe mugabe akunenedwayo anayamba kulamula 1980, ndizomveka kwa wanthu wa ku zm, osati ife tasintha atsogoleli kangati from 1994?
stupid comment aixe ndiwe mbuli Khala phee
iwe ndi kape opanda nzelu mbuli wa chabechabe nditu
Or atawina chakwera dziko silingasithe… maiko ambiri nkhani ya China inalowa pansi kale kale ngakhale kuno ku south Africa zikuvuta nkhani ngati zomwezi…. uthenga wanga ndiwakuti tstiyeni tizingolimbikira kugwira ntchito or tima bussines Kuti tizitha kupeza thandizo lathu president sadzagawa chuma kwa mtundu wa anthu mpaka kale kale
Rubbish, what do you mean kulephela is he the first president of the Republic, he is not namalenga,ndizosiilana, what others started others continue so on so forth,
Welcome Zimbabwe crisis. …its better in Zimbabwe there’s no president but magetsi alipo
pamenepo ndipamene muziziwira kt its nt de president amayakitsa magetsi
Muuze #Ruth, Kma Sava Kma Vuto Ndiumbuli 80% Pa Mw Ndimbuli Pamodzi Ndi #Lazalo.
U have to keep your mouth, point of zim how can u bring in malawi? Blacks pple are always think nagative way why? Can u see in zimbabwe anytime war can start so are u happy that to happen in malawi?
I can see that this man is full of nonsense
Wow thx to reply, come on
Who to fight who in Zimbabwe? No signs of war there.Be patriotic dude.Mavuto avuta ku Malawi pano
But fighting it is not solution always distroying, solution is every has to be in solution tabe to see how to solve this matter. A point of coup cant help pls brothers
Iwe Ndiye zungu eti? Pitanitu kumangalandewmu
Komas tili kale pa war
KOMA KAMKUYU NDI GALU WAKUDYA MANYI, IWE SIGULU LIJA LA PP MUNABA NDALAMA M’BOMA?? UKANENE ZA KU ZIMBABWE NDIMAYESA AKUCHOTSA DICTATER AKUIKASO DICTATER? MBUZI YAMUNU GALU WENI WENI. STUPID.
ok!
Magetsi wathedwa nawo nzelu pitala chimenechi ndi chimene chitamuchotse pomwe alipa basi
kkkkkkkkk
Akunama ameneyo mkona amangoti Ku choka uku kulowela uku kumangosintha osakhazikika
kathote ambuye ako
Akumkuyu m ukunamatu kazingokhalani kunyumba kwanuko musaiwale kumavala magalasio
write a comment
Kkk Kma Madolo
We still love him…Even if he can die today his ancestors will still remain President
We??
His ancestors? ?
Not u dude cadet!
Kunkuyu wakhuta mkute. APM ndi more
Long live APM