Tikuthotha ngati Mugabe – Kunkuyu achenjeza Mutharika

303

Nduna yakale mu boma la amayi imene tsopano ikutsogolera bungwe la ndale a Moses Kunkuyu achenjeza Mtsogoleri wa dziko lino a Peter Mutharika kuti athamangitsidwa pa mpando ngati sasamala.

Malinga ndi malipoti a olembankhani, a Kunkuyu ati a Mutharika atha kuthamangitsidwa mwa chipongwe pa mpando ngati sachita mwa kufuna kwa a Malawi maka pa nkhani yosintha malamulo a zisankho.

Moses Kunkuyu

Kunkuyu: Achenjeza a Mutharika.

A Kunkuyu anati ukavuwevuwe wa a Mutharika ndi chipani chawo cha DPP upangitsa a Malawi kukwiya ndi kuganiza zothotha a Mutharika pa udindo wawo. Ngati mmene zachitikila ku Zimbabwe kwawo kwa Mugabe.

“Anthu amatopa, ndipo akatopa amalowa chiwewe. Nkhani iyi yosintha malamulo a zisankho si nkhani yaing’ono, ndi yofunika a Mutharika asamale nayo. Atha kupeza nayo mavuto,” anatelo a Kunkuyu.

A Kunkuyu ananenapo kuti mavuto a Mutharika atha kuyamba ndi zionetselo zomwe akufuna kuchita a mipingo pa nkhani yomweyi.

“A mipingo akangochita zionetselo, basi mavuto atha kuyamba pamenepo. A Mutharika ndikuona zimene akuona a Mugabe ku Zimbabwe,” anatelo Kunkuyu.

 

Share.

303 Comments

 1. Ndibweledza kuyakhura mau amene anayakhura Ex President Dr BAKILI MULUZI Vutoraife a MALAWI ndikuiwarasanka PETER MUTHARIKA 2019 wamuboma ELECTRICITY BLACK again pokhapokha titazipeleka kwa MULUNGU WAKUMWAMBA 4 ndipo Yona anayamba kulowa mudziwo ulendo wa tsiku limodzi, nalalikira, nati, Atsala masiku masiku makumi anai ndipo Nineve adzapasuka 5 ndipo anthu a Nineve anakhulupirira MULUNGU, nalalikira cosala, nabvala ciguduli, kuyambira wa mkuru kufikira wamung’ono wa iwowa 6 pakuti mau awa anafikira mfumu ya Nineve, ndipo inanyamuka ku mpando wace wacifumu, nibvura copfunda cace, nipfunda ciguduli, nikhala m’mapulusa. YONA 3:4-10 auzeni a president tipange zomwezo muzaona MALAWI azayamba kucitatso bwinu vs 10

 2. Atseke pakamwa pake ameneyo nzake ndi chakwela uja akumangotukwana ku parliament osakhala ngati anali m’busa sangawine ameneyo saiwona vote yanga abwelele ku ubusa konko osati president kulibe chake kumeneko

 3. Tachedwa nazo!!! Waionela patali chifukwa cha Mugabe. Munva posachedwapa akuluakulu athu a nkhondo akumwa tea wa mkaka Ku state house kwamagetsi ndi masana omwe. Ife tikuyang’ana ka MK10.00 mu mdima kuti tikagule machesi.

 4. A classmate anga kupulaimale pa katolika insititute alakhula.
  Ndakunvani ada. Ngati mungawelenge ndemanga yangayi. Mudipelekeleko moni kwa denesi tambala K omanso khilisitofala dambuleni.
  Osaiwala lelana phiri.
  Agolokipa anthu akupulaimale.

 5. zachamba zimenezo , iwe kunkuyu uwuzane ndi anzakowo kuti : APM simungamuthothe , ngati ndi ndale mwachepa nazo . anthu olephera pa ndale inu .kuluza ndi u mp kwanu? kunkuyu ndiwe omvetsa chisoni

 6. Kunkuyu pamtumbo pako machende ako mbolo yako,mkongo wa mako,mavuzi ako, iwe undisamale nya mako munthu opanda nzeru mapwara ako

 7. kunkuyu ndikachan ngat wasowa chokamba osangosatira maiwako adathawa uwa uja bwanji dzina lake ndaliiwala tandikumbuxa ndindam paja chenjezo udekhe uzazalakhuleso zopusa zakozo wamva!!!!!!!!!

 8. Kunkuyu is an idiot like chakwera and amai. Bunch of thieves who want to destroy our country, try that yuo idiot kunkuyu and you will end up in jail while rotten.

 9. Iweso ndiwe kape mteshaa zoona nde kt uli Ku Zimbabwe mavuto osewo siukuwawona man mkunama uvote ndiwe osat ozindikirafeee

 10. If you are musician I don’t see reason why you shld force thyself to comment on things that dils wil marketing. Akukumkuyu ndivuto la school and I hv nothing to say to him.politics ndi umbuli ndiyoopsa hence you die early while poor ask jb etc.

 11. Kunkuyu you are un cultured barbarian, alunatic acomplete dundehead, chitsilu chomwa Madzi ometela, afailed politician .Dont take advantage of civilised leadership and make stupid statements, konza kachipani Kako Ndi Amako komw e aliko,dont be acoward

 12. If you know what’s good for you just keep your mouth shut Mr kunkuyu………………sikaletu lija mumkawanyoza a chakwera lija

 13. Zopanda nzelu,kungotengela zochita anzanu basi,pali zifukwa zokwanila ndi zoveka bwino zomwe akumuchotsela mugabe osamangobwbweta zinthu zosathandiza aaaa

 14. Zoonad kut a Bungwe la ESCOM apanga ubale ndi azipani zotsutsa. Koma asamale akhonza kuluza ntchito kaya mwadya ma million koma mukunama ndipo muzakhumudwa.

 15. Whats wrong with us Malawians. Why do we celebrate ignorance? Why is unpatriotic sentiments are being amplified and regarded as courageous. Why and how do we even find parallels between the situation in Zimbabwe and Malawi? Zimbabweans are just trying to do what we did two decades ago and we find that relevant? Really?

 16. Amaine Kangunje!!!!!!amaine Kangunje!!!!!!! a a abale pepanitu ndinangoyamba kulira ndinali ndisanawerenge nkhani yake ndimangoesa ngati ndiyampira wazulo kuti angondikumbusa ndie aaaaaa ndangolira ulere eti??????

 17. Let you kunkuyu try we gonna burry you alive plus in Zimbabwe it’s the soldiers who did it not a mare civilian like you kunkuyu.asatilankhulisa pambali mbuli ya mwamanase iwe

 18. Inu Moses kumkuyu munthu oti anakuza u Mp angatiuze chani zandale.kodi panopa ali chipani chiti?that idiot got nothing to share with us he just wanna be on the media since he is not a public figure anymore. I can’t buy his story .Idiot.

 19. Kunkuyu mnaba ndalama sitikufunani. APM usadandaule umalizitse term iyi. Koma 2019 mavoti onse kuchosera voti yanga. Ndilibe nthai ya Kunkuyu komanso nthai ya DPP.

 20. Kunkuyu is one of the Malawian Idiots bcoz he is failing to call his former president to answer or defend her Cashgate Corruption and he is still making noises for nothing,
  Aproverb says: ” An empty tin always makes alot of noise”, refers to KUNKUYU.

 21. Kodi nanu a Kunkuyu osamapita Ku UK kogulutsa mowa kuja bwanji? Mwina mukabweleko ndi ndalama zina tidye nawo 2019, izi nzopanda nchere Muyankhula apazi, zinakulakani basi no mita now for you!!!

 22. Kunkuyu and ur fellow idiots u cant compare malawi Ndi Zimbabwe,, totally different… Umean millitary ilande boma coz of black out?? U are afool big fool…. ukuopa chani 2019,, muuzane anyani inu APM timuvoteranso 2019 kaya wina afune olo asafune,,,, ovota ndife,, zautsiru upse mtima zenizeni nyapaphi!

 23. Aaa Iwe Kukuyu Unali Mboma Momwemo Ndi Amayi Oyipa Aja Mumangobaa Basi Ndiye Lelo Uzichuluka Mzelu Asiyeni Apwiyapwiya Amalize Mwabata

 24. Ulemu wanu Mr Kunkuyu tiyeni nazo munthu ukakhala mtsogoleri sikuti ndiwe opambana ayi koma a fake Professor Muthalika ndi munthu osazindikira ngakhale adapitako ku sukulu. Kafunse kwa Mugabe akakuuza military yake yomweyo imakupatsa shawashayo izakununkha. You are a foreigner why Malawian accept a foreigner to run the country.

 25. Tikamaseleula ndi apresident athu chakwela amaona ngat ndizenizen,chomwe angaziwe MCP singazatengenso boma ilindimbir zot anthu sazaziwala mpaka kale,ndpo asamasewele ndi Dpp sangamake”

 26. hahahaha you are failing to manage a three bedroomed house ndiye uzikanena kuti uthotha munthu wa mkulu ngati uyu usawi .

 27. Mr kunkuyu mudali kuti mwaona inu kuti anzanu ku Zimbabwe achita zamphamvu ndiye mwayambapo kunena zopanda n’zeru.Khala chete munthu wopusa iwe ndipo usadzabweredzenso kunena kawiri ai. Ifetu tikadalipo aDDP ndipo tiwinanso osati za inu aPp chipanichi chidatha ngati katani, kodi Mr kunkuyu m’tsogoleri wanu mayi JB ali kuti? Kkkkkkkkkkkkkkkiest ndikuyankhire akuti adathawa pomwe adaludza chisankho cha m’chaka cha 2014.

 28. Kumeneko ndikusowa chochita A Kunkuyu ndi mbuzi yeniyeni tell him asabwerese chisokonezo mmalawi muno akoza kusatira ambuyache,ndanyasidwa naye ala!

 29. Kodi chifukwa chikupangisa kuzima kwa magesi, mukukhala ngati simukuchiziwa bwanji?zikukhuzana bwanji ndilumuthotha president, yakula ndi nsanje, mumafuna mutakhalapo Ndinyengo, dikirani 2019

 30. Nde kuti a kunkuyu samva chingerezi….kkkkk mugabe sanathothedwe man…anathothedwa ndi iweyo ndi amai ….kunkuyu has nothing to offer to malawi….he is just frustrated.. What he is saying is just a kick of dying horse

 31. APM akuyeneka kukhala ochenjera zedi chifukwa chakwera ali nganga ndi bungwe la Escom kuti magetsi azithima nde azinamizira kuti apulezidenti akulephera ati campaign chakwera tionana 2019 tambala wakuda muno sadzawinanso.

 32. Kkkkkkk km anthu enawa kumangolongolora ngati Ali ndi mphaso yautsogoleri enanu banja la ana awiri kumakanika kulidyesa ndiye 17 million kkk anthu angayambe kukusekani,mungothokoza ti manyuzi pepala tosaziwika bwinoti kuti timangopanga post zili zonse apo biii inu kunalibeko zamanyazi

 33. izo ndi zanu muisova ku malawi osathawako bwanji amene tili kwa zuma kuno mukuona ngati sitikufuna kukhara ku mw , my moyale, my team khudah continue doing the job

 34. nzamanyazi munthu amene analephera u mp nkumanena moteromo,,,ngati simutha kuyankhula just keep quite!!! Achinyamata amene tikufuna si ngati iwe aaaiiii,,tikufuna the likes of Vp Chilima,,Hon Atupele ndi ena ambiri ,,

 35. Timu ikamaluza anthu amakamba zambiri. Koma atakulowetsani palibe mungachite kumangozikolakola. Ndiye aKunkuyu kaya mwaiwala kut boma lanu linangoba ndalama nkuika amalawi pa mavuto? Mukuganiza kut inu mungasinthe zinthu?Muthalika ndi katakwe akuyendetsa dzikoli popanda chithandizo cha maiko ndi mabungwe. inu mabungwe ndi maiko ankathndiza dziko lino mmalo molitukula munabamo ndalama Kunkuyu ndi wopusa kwambir

  • Mutu onyasao iwe unganene kt pitala akuyendesa bwino ziko lino. Agalu nonse muzaona mmene azanu amayendesela ziko by 2yrs to come ndpamene muzaziwe bwno lomwe

 36. Kumalemba pano zopusa ayi ife aMalawi tikubvutika chifukwa cha mantha Bwanji Bakili Muluzi sadaope Nthawi imene ija kuti tilandile matipate. inu mudali kuti zimenezo mudzikapanga ku mbumba yanu osati ku mtundu wa amalawi onse ife tatopa ndi Umphawi komanso Bodza kumasangalala munthu mmodzi chifukwa chomuvotela. zopusa ayi.

  • Where does he get the authority to utter that nonsense?? His authority expired through the ballot box and he is just a mere citizen whose influence can’t be felt or atayima pachulu

 37. Za Ku Zimbabwe ndi Ku Malawi zikufanana?sudziwa kuti anthu aku Zimbabwe amaoneka ngati ochenjera Ali wopusa,wosayamika??inu a kumkuyu,u, president mungauthe?

 38. IWE UDALI MBOMA MOMWRMO NDIMAI AKO ATHAWA AJA MUNAPANGAMO CHANI SIMUNANGOBAMO NDICHITUKUKO CHITI CHOMWE MUNGACHISONYE KUTI MUNAPANGA 2years time munaononga mosaneneka anthu kudzunzika ndinjala ndiye lero ufuna ukhale wanzeru

 39. Inu ngati munalephera ndi Mai wanuyo ndizanu.Kupusa kapena kulephera pa ndale musapezelepo mwayi okamba za msogoleri wamalawi.Ameneyi ngati muli okwana pandale muzamchose mu 2019,kuno sikuzimbabwe.Amene ali mamuna azamchosa ameneyi pachisankho.Osadandaula ndipompano.

 40. amalawi simukuona zitukuko zomwe ndapanga? miseu yozira ya area 24 ndi 23,malata ndinalonjeza aja pano ndikupangisa ku japan,simenti ndipangisa ku brazil,za magetsi musandifunse sindinalonjeze

 41. Kufuna kutipwetekesa aphawife poti athu andalama inu zikangoyambika ndege mukuixiwa kare kokwelera , musati nyase munkati muthuyu ndiwabwino leroso oipa,Bakiri munkamutcha mbuli lero wakoma, come 2019 my vote goes to MCP

 42. Izi zandalezi enafe sikwenikweni koma izi zinali pa Civil dzurozi! akuti khaya #Moyale inagolesa ma penalty awo wose pomwe aneba anga anamupasila mmanja goloboyi wa moyale m’pira m’malo mochinya kkkkkkkk koma yaaa!!! zaulendo uno!.

 43. Ndi ufulu wathu a Malawi kuchitapo kanthu ngati mtsogoleri wa dziko akulephela kuchitila zabwino anthu. Kodi tidzakhala olira mphaka liti? Iwe dzuka Malawi !!!!!!!

  • Upanga chiyani iwe piter iyi ndi team yoyamba. pomwe mugabe akunenedwayo anayamba kulamula 1980, ndizomveka kwa wanthu wa ku zm, osati ife tasintha atsogoleli kangati from 1994?

  • Or atawina chakwera dziko silingasithe… maiko ambiri nkhani ya China inalowa pansi kale kale ngakhale kuno ku south Africa zikuvuta nkhani ngati zomwezi…. uthenga wanga ndiwakuti tstiyeni tizingolimbikira kugwira ntchito or tima bussines Kuti tizitha kupeza thandizo lathu president sadzagawa chuma kwa mtundu wa anthu mpaka kale kale

  • Rubbish, what do you mean kulephela is he the first president of the Republic, he is not namalenga,ndizosiilana, what others started others continue so on so forth,

 44. U have to keep your mouth, point of zim how can u bring in malawi? Blacks pple are always think nagative way why? Can u see in zimbabwe anytime war can start so are u happy that to happen in malawi?

 45. KOMA KAMKUYU NDI GALU WAKUDYA MANYI, IWE SIGULU LIJA LA PP MUNABA NDALAMA M’BOMA?? UKANENE ZA KU ZIMBABWE NDIMAYESA AKUCHOTSA DICTATER AKUIKASO DICTATER? MBUZI YAMUNU GALU WENI WENI. STUPID.

%d bloggers like this: