Tiyeni tichepetse zoyaka mammawa izi ndi kuyamba kulimbikila tsopano chifukwa mowa otchipa uja auchotsa pa msika.
Anthu atadandaula za kapezekedwe ka mowa mu ma botolo a pulasitiki ndi mu masacheti, zikuoneka zamveka tsopano.
Kampani zopanga mowa umene umapezeka mu ma botolo a pulasitiki tsopano ati zayitanitsa mowa wawo atamvana ndi bungwe la Malawi Bureau of Standards (MBS) kuti atelo.
Malinga ndi malipoti otsindikizidwa mu nyuzipepala, kampani zopanga mowa zinakhala pansi ndipo mwa zina agwilizana kuti mowa onse wa mu pulasitiki usiye kupangidwa.
Padakali pano, agwilizana kuti mowa umene uli kale pa msika ukabwenzedwe ndipo ogulitsawo akalandilapo zawo.
Wina mwa mowa umene waitanitsidwa ndi wa Super Midori ndi Midori umene unakondoweza achinyamata ambiri mu makwalala umu.
Achina Boss Whisky, Flames Rum, Zero Gin, Blank Ponda Rum ndi Tyson Cane nawo awaitanitsa.
Shooter Premium, Vodka, Empire cane spirit ndi Chilwa manufactured by Chilwa kuphatikizapo Three Kings ndi Rio Gin nazo zaletsedwa pa msika.
Ng’oo Ife Tzmwa Kachasu Wachlokolo Osadula Msonkho
Sindisiyabe mowa uli mbwee otchipa
Precious kanjuchi
Bawa ndiyosayamba kuchita kuwuthawa. Musova life zinayela
AMA MIDO~MIDO
Zachita bwino zikaledzera zimangotukwana ife osaledzera zilibhooooooo
IFE TIZimwa kachasu
Tizingomenya Jadah mwamazilomu/kapena corner
Mowa otchipa ndiwambiri mmidzimu midoli ndkachan
Mowa otchipa ndiwambiri mmidzimu midoli ndkachan
Kunena zoona ngati ndi boma latero lachita bwino chifukwa anthu tayika kaamba ka midoli.
Tinayamba kumwa midoli isanabwere choncho sitida nkhawa sitisintha tizinwa chimozimozi
Kma apanga booo
kkkkkkk aitha
Achita Bwino Basi Bora Wathu Yemweyu Wa Madoro
zachmba akuona ngt tonse Tingakwanis mtengo wa vodka et??
Sha! Apa pakufunika kukatenga injaction basi.Amabungwe timenyeleni nkhondo pilizi.
Sha! Apa pakufunika kukatenga injaction basi.Amabungwe timenyeleni nkhondo pilizi.
Tilimbikira bwanj pomwe sitili patchito!!!! Even boma la2 silikufuna kutipasa chochita SO mukufuna kt titan???? Sitikudanda KACHASU ALIPO!!
Kkkkkkkkkk
Ife timadalira womwewo eish
diru ndi kachasu basi or muchose ife ya 100 tikusweka ndithu
Km nde aixo bwnj.Tiona km kt titan.
We ave musonzi ya pharaoh kachaso guts
NDE zachamba zimenezo,mukuona kut mwatelomo mwaitha kkkki mukunama ife ndi nganganga mpaka mpaka mamperemampere!
Palibe Nkhani Apa Guys Makosanawa Apeza Njira Apanganso Mowa Mwamtundu Wina This World Is Going Digital Mwazidziwa!
we still have beloved wine and kachasu in our villages ndie nothing to worry about
Kachasu ulipobe ng’oooo muisova
Nde tilimbikira chan sukulu tidasira 4m 4 chifukwa cha fees ya ku college idatikanika maganyu akusowa kt upeze ya ugwanya omwewu ati upeleke kenakake ndiye titan tidzingoyakabe kachasuyu mwina nkuiwarako mavuto boma lokondera nkhalamba ili
😀 kachasu oyeeeeeeeee!! Oyeeeeeeeeeeeeeee8-)
asamaname angonena upulukila mkwakale
Umbuli,,,chani anthufe,,hum? Kuti lesa kumwa zoipa wina akudandaula ndikuzuzula otilesao. Eishi,,,. I mean u!!!
koma tnazolowela.
Midoli tinaiwala kalekale pano ndi kachaso natural brew with natural ingrients and flavour
koma ndiye mwatilakwila tizimwano chani koma atsogo musadandaule tizipita kwa katalama kukamwa kachasu ndi mtojani kkkkkkkkkkkkk
24hrs No Mistake.Chikwesa
Guys Basi Tizingodya Chamba Nanga Simowa wathu Wa Anthu Osauka Aulesa.
jada amachipa man than midoli yanuyo,iwuzen zox city ndi mchesi ilekeso kachasu
Nkhani ndi low budget chikokeyani tamwaso mowa ndimmawa kumene ntchito mumangolembana nokhanokha
Tikamwe kachasu kwa ma mbilire
Kuno ulikobe diu diu
ndye malawi amene ndimadziwa ine,kukonda zo cheaper
kachaso sazathabee
Sa kuziwa zoti anthu amasuta petrol nkulezera, achina Cuba ndi kachaso
ndzmwelatu ndkaupeza
olo mutaletsa midoli palibe chomwe mwachitapo,nanga kachasu muletsanso?
ndithokoza apo apanga bwino kwambili mwina ana azipitako ku school
Kuno ulipoo be
So what!! Is there anything goimg to change? Mmalo mopanga zot anthu azipezza ntchito ur bzy. Doing nosense mxiilll
tizingokhal kwa bush-D tizingo banda basi then ku kachasu simungapoilise ghetto yut
iiii midori alibe job pano deal ndi chikokeyani cup K100 odi ine ndipite kwa mayi mavuzi
Ndix
mbayani
kkkkkkk ife tili ndi mayi chithako Lz
Kkkkk kuno kuli mayi Yaya
Ndingolira wez iiiiiiiiiiiiih fwiiiiuuuu mayoo mayooo midori yatisiya mayo fwiuuuuuu anthuoipa andiphera midori mayooo! Mwakafira
Ndiye Midoliyo watha zaka zigati achinyamata akumwa end midoli uxanabwere panalibexo mowa wina umene amamwa ngati nichoncho mungoletsa mowa uliwose kupanga dziko muno muone ngati m’malawi muno mungakhale makwacha poti ndi anthu omwewo opanga mowao amabweretsaxo ndalama tamaonakonixo zinthu zoletsa inu,,,mukumagulitsa makondomu matenda osachepa kumangopitirirab osaletsaxo bwanji kugulitso makondomuwo.
TiZimwa kachasu.
muti kuchosa midori mukutifunira zabwino? aaah ife tikukufunilani zoipa zonse ndipo chipani chanu sitizschivotera
ine pano ndkumwa midoli yomweyo
Zanu izo ife kuno ukanapezeka , kudzipepesa daily. Nyimbo ya Atoti manje#mavuto.
hang’ala alipo Ife tilibe problem
Ndiye Tidande? Timamwa Amarura Ife Zanu Zimenezo Muyisova
Tizimwa kachasu sitikudanda
Kkkkkkkk mickey uzingothila kachaso basi?Kkkkkkkkkk
Kkkk ndiye yake Big kachusu basi
Kkkkkkkkk ok big man sangatikwanise ife ndachikulile kachasu alipo iyaaa
Mumatikhomelera bwanji!?
Aaaaah mayazi kachaso alipo
chamba, Cuba ,kachasu , masese, mtonjane, matokoso, wine, still available @ cheaper and affordable prices………….. mazoba mwaletsa midori inu mwatilira hahahahaha
Sukunama aise ….ma plan awathera chabe mitundu ya mowa ndi lwanyazi…..Timwabe malire nseru
Ghetto child sopano ..
Kkkkkkkk ukuziwa kale Chimzy getto siyimaphweketsa dhilu .
.
Kachasu alibwino
pamenepo boma laluzanso ndalama zambiri zomwe limatolera ku ma company amenewa
Atipweteka kwambiri ife a nbb,unali otnchipa omwewu.
Kkkkkkkkkkk
tizimwa kachasu ndi mtonjani simungatithe wea thea is a will thea is a way hahahaha sitingasiye bawa
tiyamba kusuta chamba vuto palibe amisala tichuluka kkkkkkkk
Kachasu Alipobe lol
Nkhani yabwino kwa ogulitsa kachasu…msika wakachasu unasokonekera pang’ono chifukwa cha competitive ameneyu
hahaha tizakamwa pa den pawo kkkkk
Kuchotsa midoli Ife timatcha,ifenso ndi achinyamata amene miyoyo yathu ikusintha kamba kogulitsa midoli yomweyo
Sha koma midoli yokhayo ndiye ayilakwira bwanji. Achinyamata akanena kuti akumwa wa mame, mowa wake umakhala super midoli.
Kkkkk ntonjani kwa mambewe
Atleast, waudzu ulipobe.
Ife tima-fila non % beer, kachaso
Akumaika mabotolo a galasitu tsopano
chambaeti
Klkkkkkkk
kachaso still exist
tinayamba kubuka ndikale midoli yakoyo kulibe.ghetto sinama kachaso umatisunga amwene moreover midoli ndekuti aichotsa ku mtsika wakwanu. kunoko nde midoli splash xxx shooter akanamwedwa hahaha #team_kuyaka.
tizimwa wakhuni womwewu basi
Man midoli sanachotse k300 ndiye kuti achotsa
Zinanyanya kusanache achinyamata kumabawika mfundoyi ilibo!
Kaya omwe amadonyokao ndi kusweka ayisova
Tibwelera ku kachaso,kaya ati pano akumanthira ma ARV tilibe nazo ntchito zimenezo ife bola kuyaka bax.
Ndakwiya nanu nde ofunka kuoderatu makaton 10 ndizingomwa pa den
Ok fine
Kachasu ndiotchipa heavy kuledzera kulipo
Anganga! mwatsya pa mphepo! tzmwa chaponda yemweo mwatultsao
tkakumweran kut
kkkkkkk……. jada thandize bas…….lol
Ok Ok Ok Palibe Vuto Pamenepo Kachasu Alowe M’bwalo Basi Iyaaaa
tizimwa jada
pamene ukulemba zakozi ife tikusweka midoli yomweyo panopa ku Limbe
kkkk getto yut smungamuthe tiziyakabe wamudz,mikunda
Ife kuthima nkosayamba bwana wanga,Pelese Ku local industry ndi diwazi.
Ndiye mwati midoli kkkkkkkk
Awuchotsa kuti? Anyamata akumwabe tayendani ku Kawale ndi mmakwalala muone nokha.
Achita bwino achinyamata umawatupitsa
Masiku ano nd collabo bax..tikumangosonkhetsana ndkukagula gin oro midoli aichotse we already found a solution
Kkkkkkkkk kumeneko ndiye kuyaka kwa ma member ozindikira big up!
Kkkkkk
ndeyake kkkk
Kkkkk
Nde auzen atsise mowa wa carsberg tizigula 200 special,green
Achita bwino
tizimwa kachaso. hedec kkklkkkkkkkk