Wochemelera timu ya Nyasa Big Bullets m’boma la Thyolo watisiya pamene timu yake idachinyisa chigoli ndi timu ya Silver Strikers mu chikho cha Airtel Top 8 ku Mulanje sabata lathali, ngakhale kuti chigolicho chidakanidwa.
Mkuluyu yemwe anali Mfumu Lipulo mu boma la Thyolo anamwalira Lamulungu lapitali pomwe osewera wa Silver, Green Harawa, anamwetsa chigoli ali pamalo olakwika (offside).
Bullets imayenera kugoletsa zigoli ziwiri ndinso kuonetsetsa kuti asamwetse kamba koti timu ya Silver idali itapamantha Bullets ku Lilongwe 1-0 mu masewero oyamba.
Komabe, masewerowa sanatuluse chigoli chilichonse koma chigoli chokanidwachi sichidafike ndi uthenga wa bwino kwa a Lipulo.
Malingana ndi a Linos Phiri omwe amawaziwa a mfumu wa, lamulungu atachoka ku tchalichi cha katolika cha AAdololata, a Lipulo adapita kunyumba kwawo kumadikilira kuti amvetsele masewerowa pa wailesi.
”Amatsatila masewerawo pa wailesi ndipo zinalidi zokhumudwisa kuti Bullets simagoletsa. Iwowo adagwa pansi pamene olengeza mpira pa wailesi atanena kuti Silver yagolesa ndipo mmene amazanena kuti chigolicho chidakanidwa mkuti mkuluyu akatagwa kale pansi ndi kukoma, “ adatero a Phiri.
Ku chipatala cha Thyolo komwe anatengeredwa ndikomwe adauzidwa kuti mkuluyu wamwalila. Mkuluyu walowa mmanda dzulo.
Timu ya Bullets sidagolese chigoli mu masewera anayi yomwe yasewera.
Silver Striekrs yafikano mu ma semifinolo a chikhochi ndipo ikumana ndi timu ya Kamuzu Barracks pamene Be Forward Wanderers ipalana mamba ndi Moyale Barracks.
A thousand ways to die
Vuto ndi Danger kutetemula akamalengeza mpila kkkkkkkkkkkk
My fellow Malawians u need to agree with me whether you like it or not. Malawi teams should stop playing football. Because all they do all times is loose.
Ine ndaleka kusapota Bullets, Manoma ndilandileni ku Lali Luban.
The blood of that man will be in sulumba’s hands not in bullets fc
Mpira ndi masewero sizodzitengera mpaka mu mtima Guyz ngati mulipo anthu otero plz sithani ndi masewero awa.
May his soul rest in peace
Bullets kupanga mbiri yovuta kufufutika kkkkkkkk
Kodi Mfumuyi Yafa Ndi Mpira Kapena Bp?
anatukana mulungu awa
Ndi nthawi yawo inakwana
Ifetu abullets timavomereza .Koma inu anzathu mumavuta zedi
Mbuyache are u sure!
Ndiye Sanat Kumwalirakotu.
So sad
Analidi sapota weni-weni RIP
Kkkk Bullets siidzamva!!!
Woyikonda BB Sataya ntima
Nkhani ndi yomweyo basi paja a bb mukawina dziko limasowa mtendere .
Imeneyi ndi msembe yapaderadera neba yesesani
Bullets Pakufunika Iyankhe Mlandu Apa!
Zomvetsa chisoni.
R.I.P zimachitika,, zimu wamfumu wuuse mutendele .
360 minutes fc konzanipo pamenepo. Mpila umakoma wanderera ndi bullets zikamachita bwino.
360mins osachinya olo cha offside! pepani masapota + timu ya bb! ife(a silver) sitili moesa chaka chino! ndipo ma ref mu top8 anaesetsa kukukonderani.nafeso(a silva) sitili okondwa pomatikanira chigoli kawiri kose(home$away) tsono muonere matimu amzanu momwe akusewelera mu semi.
Angozo Mwayamba Kufa Masapota Anyasa B Samalani Ndi Bankers Kestern Turner
Mwina nd sembe yao NBB
Kkkkkkk iiiii koma ndiyetu chigoli chimoz mpaka kufa anthu awir. Ndiye mwasalanu ganizan bwino kusintha Chanel apo biii nonse mutha phsyitiiiii !!!!!! Coz BB ndiye izingoluzabe.
kkkkkkk Naa chaka chino inu a bullets mumwaliradi zeni zeni coz Noma ikubweraso komweko
Mutsale ndinu ife titha bac . Anthu oyipa inu mmasangalala ndikuluza kwanzanu
Hiiiii kkkkkk iwe waziiwala khalidwe lako neba? Unakakhala kut siumatokota tinakakhala chete koma tikufuna tiphwese bas
PALIBE TIMU APA YATHA BASI IZINGO KOZE KELA KUCHIPIKU BAS KKKKKK KOMA KUT YAAAA
kkkkkkkkkkkk koma nyasa 2010 kings fc imaliza ma chief malawi muno eti……….
Im wanderers fan …this just the opinions not facts …coz munthuyu sikut anakamba nd pakamwa pake kut nd chigol coz anthu anangodziwa kut amavera mpira ….I hate danger left winger mukazavera interview yake sikut nd munthu adanena zimenezo koma Mr Gondwa ndiamene anamufusa kut “Kapena tinene kut ndi chigol cha silver chinachitsa kut bp ikwere?” so you see the question sikut nd munthuyo ananena zimenezo koma ntolankhan …mmmm zinaz ay mabodza bas kusadziwa kufusa mafuso kumeneko.
Kodi munthu akamwalira amadzuka m’kufotoza chifukwa chimene wamwalira?
Ma doctor amadziwa chomwe chapangitsa kuti munthu amwalire, nkhani ndiyomweyo wamwalira ndi Chigoli chokanidwa. That’s fact
RIP chief Maule tikusowani
Winanso anafa LAMPARD ATALOWETSA CHIGOLI PA GOAL LA chelsea when man city vs chelsea
Kkkkkkkk Koma Times Radio, & Dager Left Winger, Williams Godwa Achimwene Aakulu ! ! ! Kkkkkkkk Pepani Mapale Koma Muziziwakuti Zibwana Zanuzo Muphanazo Anthu.
Timu Mpaka 6 hrs Osachinya Olo Cha Off Side Ngati AMasewera Atamwa Midoli Kkkkkkkkk
RIP
ndye mwat mfumu??? kumwalila? nd off side goes ause mu tendere ndye iwe gilin harawa usanamenye short pa golo uziona upha nazo
sibwino kuyankhula motumbwa choncho ayi aliyense adzafa kodi zikanachitikila m’bale wako ena mkumanyoza choncho ungamve bwanji, zamasewera tipange zamasewera zachisoni tipangenso zachisoni dzimvele ntolo.
inde tizafa koma osati ifa yake ya bullets yi apo ndiye wanama akanakhala mfumu wabzeru bwezi akusapota Manoma the blues
R.ip
R.I.P diehard.
Uko ndiye kuifera team kummaikonda ndi mtima onse tomorrow we w’ll hear something.
Bp inashuta siBullets wadandaula choncho coach wa bullets
Tsiku Lake Lakwana, Draft Yokha Yakufa Kwake Ndiyo Ikupangisa Anthu Kulankhula Ngat Aduka Mitu Apai Koma Mwini Moyo Ankaziwa Kut Akuluwa Azafa Motelemu. Nanga Iwe?
koma zovuta
so bad,kumaona ma team okwera kkkkk
bullets yikufunika kuyimbidwa mulandu wakupha kklkk
rest in piece great papah I ll miss u
Mizimu fc
team ya nyasa bb izingomphabe masuppotar chocho mpaka onse kutha kt “peeeee’cuz chmemecho ndchiyambi chabe mpaka izafika ma ma sub kumasapota cuz of there bad resuits
A bullets tikonze mwambo wazovutazi chifukwa ndi munthu wathu ndithu.
igweee wagwa nkukomoka nkumwalila
nde ngati chigoli cha offside anamwalila mmozi nde chigoli chenicheni amwalilaangati
Mabanja asokonezeka, mabizinezi avuta, matenda sakuchilitsidwa, anthu akungomwalira. Zosezi chifukwa cha Nyasa BB. Eeeeeeeeeeeeeee!! Napepe
a bullets muzayankha mulandu wa ifa ya mfumu chenjezo mukamakaonera mpira muzimweratu mankhwala a bp
kumeneko ndiye kupusa nkhani yake yampira yomweyo mpakana kufanayo, akapume.
Kodi palibe nkhani zina kupatula zakusachita bwino kwa bulets mxiiieeew
AUSE MTENDELE !! KOMA NGATI ZILI ZOONA
Siyekhayu winaso wafa ku mzuzu
Apa ndavomelezadi Kut bullets ndi team ya athu eeeh……
igweeeee
Zachisoni.
bullets yaonjeza…ngat siyisitha tipita ambiri..kkkkkkk…RIP
Koma ngati anthuwa kumandako amafusana kuti “inu mwamwalira chifukwa chiyani, a mfumu amenewa akayankha zoona? Ndie pamwambo wamalilowo amati chawapha a mfumuwo ndichani?
Bp
chigoli chokanidwa
kunama yawapha anfumuwo ndi bullets
Kuthawa kulima
Azifabe Choncho Amatumbwa Kwambri
zovetsa chisoni kwambiri
Eeeeee chakachino manda adzadzatu ndima supporter a MAHULE FC, Oooops! sorry MAULE FC chifukwa kuluza kukanapitilira. Boma lingolesa masapota onse a CHINKHOMA FC’wa kuti asamapite kumabwalo amasewero or kumvera mpira pa wailesi pomwe LIPIPA FC ikusewera game yawo coz BP ikupha anthu ambiri a ZIKWANJE FC.
I Love Bullets Koma Ikutionjeza .Amfumu Naonso Mpaka Kufa!!Anakadikira Pompano Tiyamba Kucita Bwino. Peoples Team Muzayankha Kwamfumu Kikikiki.R I P
R.i.P igweeeee
mavenda kkkkk kumwalira ndi nkhawa
Zonvetsa chisoni kwambiri,
lest in pice