Ikakuona litsiro sikata.
Patatha masiku chabe ataona mbonaona kumpoto, Neba wakumananso ndi mazangazime mu mzinda wa Lilongwe pamene wapamanthidwa ndi a Silver Strikers.
Pa masewelo amene anachitikila pa bwalo la za masewelo la Bingu National, timu ya Silver inaonetsetsa kuti Maule apitilize kumwa wa mandimu.
Chigoli cha Victor Limbani chomwe chinabwela patangotsala mphindi zinayi kuti mpira uthe ndicho chinadzetsa misonzi ku banja la ma palestina.
Mu nyengo ino ya mpira, Maule aluza kachiwili kotsatizana.
Dont speak too much poti mwamwera mkaka lero bcos u dont know about tomorow. Pendapenda sikugwa koma kuchalira ulendo
Kkkkkk ndipo sanati neba, azingoumbuzidwa mpaka adzatipepetse
Ndikutha kuona Ramadhani akuthamangitsidwa
Kampopi fc u must look new players leave thosw madala azikalima fodya kumudzi
Its part of a game, penda penda sikugwa,Maule,Man u more fireee!!!!
palibe chachilendo
Koma Neba zinavutadi!!!! Mpakana kufika pothawa ma Interviews Coach????????
Ndipo neba chaka chino ndi chako
Koma yaa akungokupatxani mpata kt mwina mutchukeso ngt bulltx mbuyomu kma ine nganga pambuyo pa maule maule oyeee!!!amene zikumuwawa akakolope nyanja!!!
Ndipo sizaleka kuisapota ndili ng’ang’a
Amupukuta neba amukangatha neba,amuchotsa chimbenene nene,amukuzura neba, amuwoonetsa zakuda neba, too much matama,neba 2017 wachilowa ndi minyama.
pepani amwene zimachitika
Sichinatu nebayu anazolowela ma galaundi a kapinga ndye pa carpet pakumatelela chimizi mumuuze azipanga training pa chisaka mwina angasinthe kkkkkkk
Neba kunsava
KKK Akuti Neba watani ku Lilongweku? Osamakweza mawu atimvera shhhhh
Pepa Neba “bad startn”!
Neba matukutuku atha kkkkk
Kodi inu a Malawi 24,ife ndi a neba anunso?
Yakuwona litsiro moti siikata! Asaaaah! Musovenge!
Aaah! C’mon guyz..Ikanatiliza Noma , Eagles or KB zikanandiwawa.Not Siliva ndiMoyake
So what?
Mphuno Yako,.Nawe Lero Ukufa 2 Kwa Duu
kulibeso kuiphula neighbor zanu zada inu basi ma nkers woyeeeeee!!
mwaluza basi matama agalu inu
Kkkkkkkkk kkkkkkkkk kkkkk!!!!!! Mazangazime,,,
Neba osadandaula zizayenda tsogolomu komanso wayamike anyamata piter mponda awatibula ana amwano anja
Akuti refuu sanali bhooo sanapeleke penaty kkkkkk
Koma ndiye zamuvuto neba alowe kaye mu fasting
Uziona chaka chino.not yet kkkkk..
tionezako neba usanthamange kumeza
kukhala kuchilendo nde timat musova mapale….
It never rains,but pours
*BEFOREGAME:Tukawina mupirawatu ndi wa silverniwofanana.AFTERGAME:Twaluzachifukwa FICHANI sinasutefodyayabwino+GABA inatopa inafikamamawaomweuno..kkk komaneba
Ndiye ukuona zachilendo?kumenyedwako yayamba ndi NBB?
kkkkk zikuoneka ngati achimva kuwawa chaka chino akakati walimbikira idzikhala draw basi
Kukodza Ndikukodza Basi Mulira.
Mvuto La Anthu Ikamenyedwa Team Yayikulu Nkhani Xiimantha
Or zilichocho koma ine pambuyo bb bax 4 ever
Kungoti silver yawina chifukwa mwayi owina unagwa kwa iwo,admin ndiwe mboni ya dzulo ku Bingu Nationel Estadio
kkkkkkk kod inu nde simufuna mwayi wo?kkkk
Kkkk timaufuna koma unatikana,that’s why unagwera silver
Neba wandani, wanu inu Malawi 24
Tioneseni log table
Tioneseni log table
its part of the game
Inunso a Malawi24 ndinuopepera eti tazioneni Nkhopezi.
Abale kulemba samalemba choncho kuonesa mbali
Ndiye? Inu chikukhuzani ndi chani? Leave us alone.
Inu mukusangalala ?
Ngakhale malemba amanena kuti “Muzonse Yamikani Mulungu”, ndiye winawe umvekere “Yamikani Fodya” mungawine choncho? kikkkkkk
kkkkkkkk mavuto ndaabwino amwene mpaka mwakumbukila malemba?kkkkkkkk
kkkkkk like it
Kkkkkkkk Yamikani Chingambwe kkkkk
Yamikani kampopi
Kkkkkkkkk adha
Uli ndi nzeru zachiwala zoika manyi pakhosi
Kikkkkkk! Yakukwana
kkkkkkkkk iiiii koma ndaseka
Kkkkk kuganiza kkkkkkkkk
Kkkkkk mwaganiza bwanji malume?!
Kkkkkkkkkk koma nde mwanditseketsa kkkkkkkkk .
kkkkkkk etiii yamikani kampopi
kkkkkkkkk…
kkkkkkkkk
ndinu atolankhani mwina sapota kukhakhale kulemba nkhani kumeneko
Gaba anasewela nao?
nde zikukuwawani? eni ake tazoloweratu..maulee 4eva. nde mpirao umeneo
nebanebaneba mutu sukugwira
Ndi news iyi osati uzichita kuwotsa kuti ndiwe neba ayi usazapangeso
Ndiye so what? nawe Admin ndizachilendo kuona wina ataluza game wopambana amayenera kukhala mmodzi basi? taluza koma next time tidzaiphula
kkkkkkkkkk usova bas kkkk
kuyambira mu Dec 2016 tizingoluzabe???????
Kkkkkk Koma Taonjeza Abale
Kudzilimbitsa mtima kumèneko?
Kkkkkk eya kuikondetsetsa team
Ok ndakumvetsetsa
Etu Man ndi team yafuko sitingainyoze ayi
Lero ndipo wadziwa kuti mpira amawina mmodzi basi Mulungu wakufulatilani mumadzimva kulankhula mokhuta ngati dziko munalenga ndinu, ana anjoka inu simunati mulila keeeee ngati galu
Kagwereni Uko Inu mesa mwa wina basi khalani chete mtunda ukanali musathe mau
Ife a noma zathu pheeee
Tichite Naye Tikamukang’anthaso Ku B Town Konko Akathana Ndi Sibale,tete Akapuma
VUTO NDI KUZIKWEZA!!!!!
chaona zako chapt maw chilikwaiwe tvomeleze zvut
ukakwera pa nsana panjovu osamat kulibe mame,mesa mmayankhula motumbwa aja inuyo…muvekere team ya pfuko….
The Peoples Team Kkkk
Wamenyedwa ndi neba mmafuna admin alembe zabodza
Xazawupezanxoh Mpumulo….Kkkkkkk
Panyapako muntumbomo adimn wa Noma iwe mxiiiiiiiii
Mmmmmmmmm its 2 much Gift Banda zamasewela izi bcool kkkkkkkkkkk
Wationjeza
Kkkkkkkkk pepa neba
Nukupepesa inu ukumukunyoza mma status anu
Thats bankers kkk
Yandiwawatu loss imeneija,Sulumba ndi mlozi mabi enieni aaaa
hahaha
Azalimba ku B town. Kungoti anthu a ku LL ndiwoipa sanamuuze kondowe komwekumapezeka nganja yabwino hahaha. NOMA for life
Ku BT kulibe ground paja kamuzu anatsekatu muziti ki balaka
Lol mzinda ukulilenji uwu opanda stadium
Ndipo rive
BB iyandama chaka chino
Kutsogola sikufika mark ma words
Liwiro Lamumchenga Sayambira Limodzi,kutchola Khobwe Ndimmawa,fodya Ndi Uyu Ali Pamphuno,mwana Ndi Amene Wabadwa Sawerengera Mimba
Ndekuti mumasapota nyerere nonse kumeneko eti?? Kkkkkk
ndinu a noma eet
Kkkk
neba osadanda zizakhala better
madzi acita katondo
Maule sanati azingoona za kuda. Pepani ndithu tilakhurana pochoka pa siwa tione kuti titani.
KKKKK!!!!
Iiiiiiii nebaaa pepani ndithu
kkk bankers 4eva,,,
kkkkkkiikkkkkk osamatelo nanga choncho ndibwino
Eti man
Mpaka usiku past 1 nkhani yokha yokhayo@ kodi mulibe maguza? Kapena akazi? Kuluza kwathu kusala tulo malawi 24
Kkkkkkkkkk