Malawian midfielder Robert Ng’ambi came from the bench for Platinum Stars to score in the 87th minute sealing a win over Highlands Park in the Absa Premiership yesterday.
Ng’ambi was well positioned when he headed home from a corner kick taken by Ndumiso Mabena.
This was his 5th goal in the league this season.
Just at the start of the second half, Mabena had his thunderous shot hit the woodwork and it remained tough for both sides to score.
There were missed opportunities for both teams in the match no wonder it needed the heroics very late for Nga’mbi who replaced Sibusiso Msomi in the 70th minute.
Nga’mbi’s side are now eight points clear of the relegation zone with three games left.
Highlands Park however still anchor the the log table with 22 points from 27 games.
Ma shini baba
Izi ndi zampira all the best
Well well thanks man ntchito wagwiradi nyamata
Ma player abwino tili nawodi amasewera bwino kunja,koma akati 2mikirani flames goo!
nice keep it up men!!!
Zowona man ng’ambi
Ndinyamata osachititsa manyasi kudziko lachayinake kuno woza woza ng’ambi
Mankhwala ndi dilu!
Amatiimilira pali Anyamata awa Mzava, Ng’ambi, phiri ndi Gaba amapezeka mu first 11 ngat achokera pa bench imakhala plan ya coach koma so far they represent us!
Inde zoona koma zimadabwitsa mu flames sakupezekamo ndi Gaba.
Apezeka ma game a June tikamazamenya ndi Comoros
And me
Kkkk
Umatiimilila
Alibho
Malawian Kanganya
Nyc one
Ndimkadabwa ndi ma coach ena amamusiya time ya ma colifies aku afcon aja
Mumatitonthoza ndinu
Salute abambo
That’s gr8
He is the best
patheba pano tili ndianyamata awili osayendela season …
limbikani ndi Ng’ambi …
Ukunama iwe better ukadanena Phiri jr osati mzava
sumausata mpira phiri wakhala aliku loan coz chosachita bwino.. mzava unamuonapo alipa bench chiyambileni lig?
Guys Gaba naye ndi akatundu
ine ndi madziwa ng’ambi ndi mzamva enawo kkkkkkkkkkk amakhala ngati amayendela season
Mzava wakhalisad
mzava ndi Nga’ambi sayendela season akakhala bench ndekuti ali injury
Gaba amayendela season koma amatha ndithu