A Nkasa aikanso mutu wawo pa njanji.
Atayimba nyimbo imene inawadanitsa ndi anthu yotamilila nduna yakale yaulimi a George Chaponda, oyimba Joseph Nkasa tsopano wakwela ya a Pitala.
Mu Nyimbo yake ya tsopano, Nkasa watamilila Bambo Mutharika kuti iwo ali monga Yoswa wa mu Baibulo.
A Nkasa amene anayimba Nyimbo ya Mose wa Lero yotamandila malemu Bingu tsopano ajiya ya a Mutharika.
Mwa zina, a Nkasa akuyimba kuti Bambo Mutharika ateteza a Malawi ku njala ndipo iwo anasankhidwa ndi Mulungu kuti atsogolere a Malawi.
Nkasa nanga bwanji umphawi sukutalikila pa moyo wako chonsecho ukupembedza milungu yosemayi.
Nkasa usationjezere uluru
a nkasa odwala kale ngati inu, mukusowa pofera eti??
Ankasa umphawi ukupwetekani ngati mwatha ma plan chonde chonde pangani zina musalowerere za eni zikuvutani
maganizo a iyeyo ndi womukonda,inu vuto nd chani
Ndale at its best