Zafika pano mzawo wa a Chaponda atha kukhala a Peter Mutharika okha ndi oyimba uja Joseph Nkasa.
Anthu otsatila chipani cholamula cha Democratic Progressive (DPP) apempha mtsogoleri wa dziko lino amenenso ndi mtogoleri wawo a Peter Mutharika kuti amuvule unduna George Chaponda amene ndi nduna ya za malimidwe.
Malingana ndi chikalata chimene Malawi24 yaona chopita kwa mtsogoleri wa dziko lino kuchokera kwa anthu omukonda, iwo akupempha kuti a Mutharika achotse pa udindo a Chaponda.
“Ife ndi mzika zenizeni za DPP ndipo mukudziwa inu kuti sitinayambe takuponyanipo miyala,” alemba choncho mu chikalatamo kuuza a Mutharika.
“Akulu anu aja atatisiya, ife tinali nanu. Mayi Joyce Banda atakumangani, ife tinali nanu. Pa nthawi ya kampeni komanso ya zisankho, ifenso tinalipo. Ife timakonda chipanichi,” alemba chomwecho mu kalatamu kufuna kuonetsa kuti iwo ndi eni a chipani.
Anthuwo anenanso kuti ngakhale iwo ali okonda chipani motere, koma akhumudwa ndi mmene ikuyendera nkhani yokhudza nduna ya za ulimi a George Chaponda.
Iwo ati ali okwiya maka ndi kuti President Mutharika sakuchitapo kanthu pa ndunayi ngakhale bungwe lofufuza limene anakhazikitsa kuti lifufuze za kagulidwe ka chimanga ku Zambia linauza a Mutharika kuti a Chaponda akukhala ngati amafuna kuchita utambwali pogula chimanga.
“Bwana munalonjeza kuti muchitapo kanthu pa zimene bungwe limeneli lifufuze, apa labwela ndi zotsatila tikufuna muchitepo kanthu,” atelo mu kalatayo.
Iwo ati ngakhale akuvomeleza kuti Bambo Chaponda ndi msanamira wa chipanichi koma zafikapa madzi achita katondo ndipo palibe kuchitila mwina koma kumupitikitsa basi pa unduna.
Anthuwonso anena kuti a Chaponda akusokoneza zhipanichi chifukwa adani onse a chipani cha DPP ndi utosgoleri wa a Peter Mutharika akupezelapo mwayi onyoza kudzera mwa a Chaponda.
“Akutinyozetsatu mtaunimu Chapondayu. Adani athu a zipani zina, enanso obisalila mu mabungwe ndi ena onamizila kuti ndi atolankhani akupezelapo mwayi otinyoza,” atelo anthuwo.
ndye mwat mutu wa nkhan nd,Mukhiyen chaponda kkkk koma kuwelenga nkhan yonse nd ku khiya sizifanana
Chaponda aphedwe basi
Nkasa wayaluka basi
ine ine zaunyani ine ndatopa ndi okuba aphunzitsi aphunzira aja adikilira ntchito osatenga ayiko chelete what for baibulo linati mutailanji ndalama ndi zinthu zosadya agaluwo anawelenga koma
ataninso achaponda? asova ndimomwe amadyela pano ali ziii agalu mwaona chaka cha 2018 azanamenso anyani
Nanga a Nkasa ndiye akuti chiyani tsopano. Poti amabakirawo ndi amene awonekera poyerawo
Nkasa ndi wadyera
Akuti Chaponda ndi treasurer wa Bank Nkhonde ya ma minister .. Basi nkhani yatha.. Za village bank ya ma biggy izi tiyeni tizitaye..
A Joyce banda mulikuti azanu akumaliza ndalama munasiyako zinja bwerani musawawopeso pano mumanena zowona kuti cash get anayambitsa ndi aDpp Malawi uja wathadi
Mkasa pamutu pake spamayenda amazfuna zobedwazo umphawi ngat ine unamkwana koma samazkumaniza.haaa!!! Changamuka iwe!!!!!
Don’t f*** as around mbava sizimangana nawe nkasa u don’t know nothing about politicians ufera zaeeni
Inu tawasiyani anthuwa zawo nzimodzi inu mukumuona peter akutututmuka
Nkasa tsopano
koma MCP inaribwi chifukwa achikulirewa akanasowa popanda ku kambirana
Pamene zafika apa,timati zinthu zavuta.Khoswe wapasidwa aulura makoswe apazala.WHEN TWO THIEVES HAVE MEET IN THE SAME HOUSE STEALING,NEITHER OF THE ONE CAN SHOUT.
Pitala Pitala..Chaponda Chapomda A Lomwe Alomwe No Piya Kodi Ndalama Sizinakukwane..Nde Mukuwona Ngati Ife Tipita Kuti ..Chimanga Waba,ndalama Waba, ..Vuto Siiwe Koma Pitala Amene Anakupasa Udindo…Shame On DPP GVr
time bomb
Oh!oh?kodi nkhani yake ndi ndalama? Akhiyidwe basi ndiwo pusa ameneyo khiyani
Zokhiya anthu ndiye ayi tatopanazo,mukhiya angati aaaaa
Inenso ngakhale ndilibe nyota koma kalatayi ndikugwilizana nayo kotelo kuti ineso mukalatamo ndilimo
#TeamChaponda #corruptionMalawi #cashGateCountry malawi kuvesa chisoni
Kkkkkkkkkk DPP is no more popular coz of Chaphwanya,,,kaya mukuti Chapinda kaya Chaponda
Kkkkkkkkkkkkkkkkkk
A Nkasa nawo azafela za eni ake dyela ndilo likumuvuta mkuluyi, aliyense wandale amafuna atamudyelapo… Samala pakamwa Nkasa tsiku lina uzaona ngati malodza…ngati nyimbo zinakuthela ndibwino uyambe ndakatulo
INDE BIG NGATI NYIMBO ZAMUTHELA AYAMBEDI NDAKATULOKKKKKKKKKK!!!!!!!!!
Nkasa chimutu chake ndichachikulu nde nthawi zina zoyankhula zake zikumafanana ndianthu openga mngomuzolowera
MAVOTI MUNABA AJA AMALOSELA KUBANDALAMAXI.ASOWE AMENEYO!
Malawi must wake up fo wat tomorrow myt bring
Malawi must wake up fo wat tomorrow myt bring
Chaponda amangidwa tsopano ngati pamalawi tikuyesesa kuti tidalisidwe ndi Chauta yemwe analenga dzikoli.Peter Mutharika ngatidi akusata chilungamo chofumira kuchipani cha DPP ayenera kumanga chaponda.Aziwe kuti ndalama amaba chaponda zazuzitsa osauka komanso okalamba omwe alibe thandizo lililonse.
Nkasa ndi wadyera amasata kwapita thumba iyaaaa
Kodi chikuvuta ndichani osamumanga Mpana pano?ndaona vuto ndi pitala ,chandiponda ndi pitala onse asowe
Kawasowesetu nanga
Chaponda man of the yr.
Dont arrest da guy send him fo exile,atalowera chapa Zimbabwe zingatichitireko ubwino,do something Mr Preident,;show da europeans dat we r very serius,reform
very simple man
TEAM CHAPONDA tilipo, bring me umboni I will hate him,
kkkkkkk Nkasa
Akufunika tameki mbava yamunthu kuzuza amalawi
Komatu paja nkasa ndi njoka alibe 2 koloko,amasintha anytime.
Ine sindikumva kuwawa ndipo moyo wanga uli m’malo chifukwa sindinavoterepo DPP tiyeni tonse tivomereze za ulamuliro wa Dpp mpaka 2024,kufuna oro osafuna 2019 boma kulamulanso Malawi mbali zonse.
Galu Ndi Peter
A Nkasa chawakulira ndi dyera how can u Support a criminal
Mzake wina ndne !! Musatinamize apa ngati anthu onse mwawafunsa !! Apa ndye mwanama mwawanamiza anthu kuti mzake wacaponda ndi peter ndi mkasa ine mwandifunsa ? When posting dont generalise everything . Dont forget even jesus was the son of god but during his time its not all the pple who like him its not also all the pple who hate him. Ndye sianthu onse omwe amagwirizana ndizomwe mukuganiza . This r my ideas idont want citsilu camunthu cikunditukwana if u want to argue with me argue with acts not hate . Iwe robins banda idont want ur comment here .
Munthu wopanda nzeru amasekelera zinthu zopanda nzeru
kkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkk #Welcome_to_Malawiana
Malawi.com
Eeeh koma chiChaponda chitha kuvala Bomba la timkenawo kuti chiphe gulu amwene eeh eeh!!! Kakaka osazitaya bwanji? Money chikazidyeladi ku Manda sure
and come 2019 the hypocrites will vote for the same goats…kumakhala pa line mkumati ine ndi wa ujeni ine…but this is really disgusting!!
akhiyidwe basi,kkkkkkkk ife tagwirizana nazo
Chaponda kukamila zinthu ndalama mukdyera kumanda
Joseph Nkasa ndi mfiti yodya maliro,Joyce Banda ndazinzake akutibela ndalama zamisonkho yathu ndi Nkasa yekha yemwe amati JB ngwabwino lero ndizi tonse tuti Chaponda asowe iye yekha akuti ayi a Chaponda alibe problem.
kkkkklkkllkkkkkkkkkkkk
Kkkkk pano mkasa waituluķanso wasala yekha pitala
apatu a Malawi awadziwe eñañso kut atengere phunziro
Njatani!
indedi amumange kumene iyaa kubela anthu ozauka
inuso a malawi24 zima link zanuzo mmatibowanazo mukapitiliza zomaikama link zanuzo ndikublokeselani page lanuli
zaoneselatu kuti inu baba ndinu mulesi pakuchitazinthu,ongofuna zothaitha,
Yevova musavomereze kuti anthu oipa anonge chipani cha fuko DPP.
Apatu ngati ali munthu wamaganizo yekha akuyenera kutula pansi udindo, posadikira kuti a president kapena amabungwe kumuuza kuti tulapansi udindowu. Uyu akufunika, apite kudera lake anthu akamukoke masaya mwina angamve galu ameneyu.
Chaponda atha ngati makatani , kwangosala pang’ono kuti chomgwera chija chigwe
Akhiyidwedwi ndi petulo yemwe
All im doing is crying for my party dpp.(why mr presdent is failing to isolate this person from my beloved party.
amangidwe kubela ovutika e okalamba stupid kuipa ndi ntima omwe
kkkkkk zanu izo mmaesa amalawi ngat opusa eti.kuchedwa kupangapo kanthu,apo ndi izo chipan chikunka naipa chifukwa cha munthu mmodzi
with me is Hon Dr.George Chaponda, Dpp Included.
kkkkkkkkkk akhiyidwe CHAKONDAYO inde
chaponda www. com
https://www.facebook.com/drchaponda/
kkk ko malawi 24 kukometsela!
kkkkk