Millions of cash found in Chaponda’s house

563

Under fire Agriculture Minister George Chaponda is finding the going tough as millions of cash have been found in his residence during a raid conducted by the Anti-Corruption Bureau today.

The Bureau has seized $58,500 and K124 million Chaponda’s house in a raid that also saw Admarc CEO’ Foster Mlumbe’s residence being searched.

Further reports indicate that the Minister also had various currencies including South African Rand, Botswana Pula and Zambia Kwacha.

The ACB deposited the money at the Reserve Bank of Malawi.

The raid followed the ACB’s continued probe into the Minister’s feared role in the procurement process of maize from Zambia.

Separate reports by commissions of inquiry had asked government to consider separately probing the Minister.

Share.

563 Comments

 1. Nothing strange to me, that is malawi,where there is no real freedom. No one will speak out if you do, u are under arrest, and sent to life in prison, pple of malawi are dying of hunger you don’t mind, the price of fertiliser is increasing every single day. If you pay for having electricity in your house, u must keep waiting until jesus comes, its not him only keeping money on his pillow, most politians there do the same

 2. Achaponda pamulandu wanu muyenera kupedwachifukwa kumidzi kwafa anthu ambiri chifikwa cha nzeru zako zimene makolo ako anakulipira ku sukulu .wapetsa anthu ambbri muyenera kupedwa mulungu atiyankhe pempho lathu

 3. I told you that this DPP people all of them is criminals u see now Chaponda he did what about others’ ministers and president also doing the same .

 4. The r the fucking leaders we don’t want in our country, people can’t even afford three meals but these foolish leaders r seriously keeping money in their houses. Where is Magufuli?

 5. Ndizonad kt tisamango khuluprra chlcose cos nthaw ina tidzakhala kumbal ya satana & Amalaw stdzatukukay coz umbava ndumbanda enafe tkamavutka scholnga cha Jehovay bt anthu kupondereza ,,,,,,,,,,! ndiongofunika kumukhweza

 6. chomwe ndikudikira kumva ngat mzika yokhuzidwa ndi liu lochoka kwa ‘chilungamo’. chifukwa pamene chilungama chalankhula chinyengo chonse chimaululika.kungowamanga chabe achaponda sizikutanthauza chilungamo ai, chifukwa chinyengo nthawi zonse chimazibisa kuti chioneke ngat chilungamo. ACB itifufuzire kuti ndalamazi zinabedwa bwanji chifukwa nzotheka kuti achaponda sali okha.

 7. Malawi ndizuko lopeza ndalama pa sizeyake chifukwa bhirazibera anthu boma likutha koma angoika mmatumba mwao vuto anthu amakhala pa mpando ncholinga cholemera iwo ndimabanja awo osati kuendesa dziko kuyambila president mpaks pomwe mungatchule zausiru azisogolerinu mtima ukundiwawatu mot ndinggende kut ndiphe mwai utapezeka ogenda chapondai

 8. Nkasa watulusa nyimbo… ananenso nditulusa yanga. ndipo ikunveka motele…. #Usalire_waba wekha…… (ujeni) #usalire_waba wekha! #Usalile_waba wekha!

 9. Amalawi sazathekaso umbava wanyanya zoona munthu kumasunga chuma chambilirimbiliri pamene ena akufa ndnjala anthu opanda chisoni eish mulungu azangotiweluzapo bas

 10. Big shame … While people are suffering in Malawi .. Big boys are sitting on top of billions in their homes .. Its not the only one .. More …..

 11. Ndikadakhala Ine Kuti Ndaba Chimanga Chimodzi Chonkha Mmunda Wa Aneba,kale-kale Ndikadakagona Mu CELL 51 Pomwe Chonyasa Mtima Ndi Nkhopechi Mwachilekereraaaa Ndakwiya Nazo Kwambiri

 12. chokhacho chondinyasa kumawauzà anthu a kumudzi amphawi kumawauza azilima misewu ndikumawapatsà very smallest amount of money while you just staying in your office but kumaba ndalama zaamphawi for your own information mukamakhala mma office mwanumo ziwàni kuti you are there just for the poor people and not only that you must know that God is watching you one day you will answer for that

 13. What kind of selfish is this Malawian leaders whilst you have all the treasures the mansions expensive cars and everything in your mansions but still you stand and robes the poor’s kodi tsiku lina mudayamba mwaganiziroko about your background where you are coming from???? I come from the poor village of poor people and I have experience the poverty you must thank God coz you just born from the rich families nchifukwa mukuchita mchitidwe onunkhawu

 14. That’s DPP government, if you can go to every house of DPP ministers you will find more cash even to the house of Peter mutharika there is Millions of foreign currencies

 15. No secrete under the planet earth;akulu dziwilani2 kt apo mwailowa ndende;chauta simunthu amaiwalitsa munthu papang’ono,zoona ndalama amasungila nyumba? Tiona kt zitha bwanji

 16. Vote ikabwela ndi nomwenu oyambilila kuzipatsa vote zitsilu zimezi, adali ku America akulila ku America lelo nkumati alamulile dziko? Shame……

 17. Oooo Malawi, instead of raising the country in some other problems, you bsy kubisa ndalama zoti zikanathandiza uphawi wonsewo.shame on you. Iwe ndi banja lako nkumapeza ntendere. Apo Malawi akumva zowawa.Go to hell chakwera.

 18. Kodi Mmesa Mumanena Kuti Cash Ndi Ya Pp Nanga Lero Bwa? Mbava Zazadza Ku State House,what Type Of Malawi Shal Our Sons & Have?

 19. Izi ndizina zomwe zikupangitsa kuti a malawi azipita kumayiko akunja kaman ka umphawi pamene ena abu
  sa ndalama.taonani tikuphedwa kuno ku south africa

 20. Malawi wachuluka nsanje, kuzikonda komanso liuma. mmene anayambira kunena kuti anyamata ndi atsogoleri amawa muja mpaka liti? look the ministers and government officials of today. they have been there ever since till they die just like our neighbour Zim. Malawi am very sorry for you!! greedy is here to stay. shame on you!!!!!

 21. if we talk shit here then u will start tracing us n arresting us…I can’t start to imagine many Malawians eat on less than a dollar per day while u HV millions in ur house…instead of helping the poor ur busy enriching ur self am so ashamed with Malawi politicians so selfish ur even rich than the govermrnt

 22. Choncho nkumalankhula motumbwa anthu akamathawa mDzikomo kukafuna maganyu dziko lina, ufiti wanuwo ndi omwe ukutithawisa ife. Pa nkhope nkuoneka omvesa chisoni komanso ngati ofatsa koma muli mfiti akulu.

 23. Malawians are starving no proper roads,no medical equipments in hospitals,no proper schools,yet our honourable folks are harvesting money from all angles,God must intervine seriously we’re dying.

 24. zikundiwawabe……………..BOMA ILI LIKUZIWA KUTI SILINASANKHIDWE LINALOWERA PA WINDOW CHOLINGA CHAWO KUNALI KUZATIBERA BASI NDIZOMWE LIKUPANGA KOMA DZANJA LIKALEMBA LALEMBA CHAUTA SANGAKONDWE KUTI TIVUTIKE CHIFUKWA CHA ANTHU LESS THAN 50 OMWE AKULAMULIRA

 25. This is so sad, I do believe our country is such poor at all. the problem is leadership. we can’t have a situation where by we let criminals govern the Republic, thieves who just care about themselves shame! let them face a total mighty of law before they sink the whole ship down!

 26. kuba koteleko ndikumene kukupangisa kuti dziko lathu lizikhalabe pa umphawi….koma chondiwawa ine ndimisonkho imene boma likuika pa ma salary anthu muzina la Pay as you earn, pa madzi okuma ati VAT, akatolera misonkhoyo ndikumakapasa anthu awo…ati Ma ministers,talk of Chaponda, Nakumwa, gondwe and the leader himself kumakasunga mma nyumba mwawo ndalama zathu eni ake tikuvutika…muzipatala mankhwala zipangizo mulibe ati boma lilibe ndalama chonsecho mukusunga nyumba.

 27. Koma ndiye akakamiratu welldone anti corruption .these is what we need fighting corruption without fear who ever is,until Malawi government became clean again next House should be Nakhumwa ,leason must be lean .media is playing a good role to expose these culprits

 28. Anthu Ambiri Aotchedwa Chifukwa Chakuba Foni,mbunzi Ndi Zina Zing’ono Zing’ono Adapita Koma Ena Kuba Mamillion Kukhala Mfulu. Eee! Zomvetsa Chisoni Dziko Ndi Anthu Ake

 29. These guyz dpp are fucking fifth let us to rule In transparecy & accountability how can donors help wth such behaviour kumpanje ndakhumudwa osaukafe tidzingosauka olemelanu mudzingolemela.masiku omaliza

 30. izi dzakhala zikuchitika for long time in Malawi but a boma amangozimilitsila jst becoz they all know what they anthu mkumafa ndinjala mmamizimu no msewu magetsi kuvuta wogwila ntchito zaboma osalandila malipilo awo ndalama mukumaba mkumaika mmanyumbamwanu God is watching all this simunati

 31. Misonkho Yathu Imeneyo?Mphunzitsi Akulira Kufuna Ma Areas Ake Koma Akulephela Kupatsidwa.Komatu Mphuzitsiyo Ntchito Adagwira.Akanyanyala Ntchito Nkumamuwopseza Kuti Mumchotsa,akuti Ma REFORM.Kodi Ndunazo Ma Reform Sawakhuza? Mmhu! Chabwino, A ACB pitaniso Kunyumba Ya Fabiyano,kuli Ndalama Zathu Kumeneko Mukatitengere Mutipatse.Amphawi Tikulira Ndi Kukwera Kwa Katundu Iwo Nkumaunjika Ndalama Zokuba Mnyumba Zawo? En I Qot, Malawi Will Never Develop Becz Of Selfishness Of Our Leaders.

 32. No where to runthis is my home land i feel like i can hire osama just to destroy them at oncemy malawi watani
  Iwe pitala ndi nzakoyo chapman am warning u

 33. Mwina ndalamazo anayikapo ndi a mzake a DPP kuti amusase kenako nkuntumizira a police kuti amugwire nazo, ndale nzobvuta

 34. I said cashgate started by udf then dpp those two party are the master and bakili is a cashgate father. PP was just caught up in the system things were already in motion. Chaponda with his troops just continuing where they left. Peter knows what is going on

 35. Kaya Zanu Izo,mkanakhara Kuti Ndaba Minkhaka Mdimba Mwachaponda Ikanakhara Life Imprison With Hard Labour,koma Achapo Anaba Ndalama,ayi Ndithu No Unyoro.Dziko Limayanjana Ndi Dzitsiru.

 36. Ndalama munthu angasunge nyumba ngati zimenezo bodza ilo! Ngati ndichoncho tipephe ama television azionetse zili pomwe azipezelapo zoipitsilana mbili si bwino!

 37. Nanga bwanji president sakuchitapo kathu,mwina iye zikumusangalasa zakatangalezi eti,poti mbalame zofanana nthenga zimaulukira pa modzi zosachita kufunsa apa anthuwa ndi amodzi,koma ngati kuli kulodxedwa analoza Malawi yo game ana iponyela kosafikira achisodzera

 38. Akumudzi Atangoganiziridwa Kuba Nkhuku Amakagona Kupoceli Podikira Kufufuza Chilungamo, Nanga Uyu Sakutengedwa Bwanji Iyi Ndimbava Itengen Ikalowe Basi, Muzifufuza Atasekeredwa.

 39. Sinu aja mumaima pachulu kumatukwa kuti JB wakuba .taonanitu lelo sarary yanu ndi ndalama zomwe mukupezeka nazo paralel.mene mumalowa pa udindowu musaiwale munalengeza chuma chanu kuchuluka kwake .lelo manyazi bwa ndende ikununkhilatu spa.ndikanakonda manyumba a anthu amenewa azisechedwa pafupi pafupi .

 40. greedy learders are source of poverty in mother land fellow countrymen lets vote wisely in election time. Pple like him must not given avote. good morning malawian in gauteng provice

 41. Osawukafe tikaba K50,000 mumatigamula kuti tikakhale kundende zaka six pamene olemela olo abe ma million sumawamanga kodi ndende munapangila anthu osawukafe.

 42. With this kind of attitude, there’s no way Arsenal can win any Cup this Season ……infact I don’t see any difference between Chaponda and Wenger….precisely

 43. Man chapomda nde mwanyanyanso mukadyera kut njombwazo man,hahah mungokhaliramo kuba m’bomamu bas mwina jeketeyo munachitanso eeeee bas.dambfounded

 44. Achoke ndalama za misonkhi thoo mukutibera nthawi pang’ono mwakweza ichi ayi misinkho ikhale chomchi nkhani kuba basi achoke kanulepo kalua great man

 45. Mulungu Wamakamu ! Inu amene mudatuma Mose kuti akaombole anthu amtundu wake ku egypt.Ifeso Atate tikupepha kuno kumalaw tipatseni atsogolire omwe adzaombole mtundu wa amalaw ku ukapolo 1: kukwera mtengo kwa katundu 2:olandira salary change komaso mocedwa 3:kukweza mtengo wachimanga 4:kubedwa kwa makhwala mzipatala 5:kupsa kwa ofesi misika 6:kuzimazima kwa magetsi pamene nduna ikusandutsa nyumba kukhala bank yosungira ndalama zakuba nonse a dpp mulungu akuoneni mwazuza amalaw mokwana pokhutsa mimba zanu shame on u.

 46. Pliz ACB Pitilizan Kuyendera Ena Monga Kuchipinda Cha ,Pitalalala , Nde Nkumanena Kuti Ndizavotere D P P..Bola Osavota ..Malawi Will Never Be Poor But Poor People Will Be Poor 4 Ever ..Chaponda Pat ..Pako

 47. O Lord! why have you forsaken us? I would love God had repeated the punishment of the era whereby ukachimwa kukanthiratu pompopompo. Uyu Chaponda ndi Pitala akuyenera atasowa. Thanks to Jesus that he died on the cross to save sinners like these locusts. Kodi Yale university amaphunzitsanso za umbava eti! Anthu awa si amalawi, ndiakunja. Now i can feel and smell the tears of late Maxon Mbendera(MHSRIP). This is the meaning that Malawi shall continue cry with problems due to its leadership. APM and DPP how do you feel? Are you satisfied with your ruling? Thanks ACB, gwirani ntchito mosakondera. Tikudalira inu.

 48. zonvetsa chisoni.. exodus14;14 God wil fight for us.. akuona zonse God z nt asleep… achumanu dyeranitu chanu pansi pano… tidyereni aphawife koma mathero anu ndionvetsa chisoni..

 49. No medicine in hospitals cash in chapondas house how do you justify this? May be Nkasa and Mutharika can tell us something.

 50. WAMISALA ANAONA NKHONDO
  ~JOSEPHY NKASA~
  *mumnyimbo yake iyi ya
  KULIRA KWA DZIKO=Anati
  nkulota kwake anaona chinyumba[Malawi ] chitagwa amaona
  wina aliyese akulira,ngakhale
  ku Phiri kumene [kubomako]
  analira,lero ndizimenezo zayambika kubomako,aliradi.
  This is 2017 ndikati ndione 2018 kukhala nsamuko ku Dpp
  anthu athawako,pano aliyese
  akunyasidwa nao.kuti apite ku
  nyumba ya goodall gondwe akapeza ma $ ambiri zedi.but
  why Malawi ???

 51. Mulungu amalikonda ziko ili si izi kuchita kuonekeratu kuti president nayeso akuziwapo kanthu suspend this fool to pave way for investigation mkuti palibe analakwa iye serious??

 52. acb mupite ku kamuzu palace mukapeza zina zambili chifukwa anagawana samabakilana ku airport zanali ati chani sham on u peter

 53. No_no that’s not gud,amalawi ziko tikumkanalokuti ndiumbava! ithink a ACB tiapemphe kuti apitilize kufufuza mmanyumba a ma minister ambili athakupezamo zambili,chimene ndaona peter akumagwilisa ntchito ma minister kuba,nde akufunika kumakidwa bad,oo!! paja amkati ndiophunzila kwambili ndekuti xool yake alinso profeser pa umbava ndithu

 54. Patrick Nkhoma, we are not saying chaponda should be poo but why keep such a huge amount in the bedroom? You are both thieves. ACB should investigate you as well.

 55. Did you ask him where he get those money??? Where is those people thy was burn people in Lilongwe? Why don’t you burn this idiot? We are sick and tired with that man he must be very stupid

 56. This is the system of dpp government to keep the stolen money from poor pipo apa chaponda wawuponda umvamubebe ukalowa basi

 57. HeeeeeheeeE odi ukoo alikuti a dpp tayankhanitu apa zana mumati mphezi ndiyomwe inayambisa moto nanga za cash mutiuza kuti ma bank anali oseka kkkkkkkk mbava progresive paty

 58. Ameneyo Aponyedwe Mndende Bax Cz Waononga Mbli Ya Malawi Kmso Anthu Ambli Trimumavuto Nd Njara Iye Kucita Kusintha Ma Prasma Cifukwa Cha Maize Gate Kkkk

 59. You cant fool all the people all the time. La fourty likakwana lakwana. Atsogoleri opanda chifundo ndi anthu awo ngati awa sindinawaone. Cry my beloved country. Kuno ku Joni akutithamangitsa, kwathu kumalawi akutilengela umphawi pomaba ndalama za osauka. Tipite kuti. Ambuye chitani njira yanu ija yothana ndi mbava zikulu zikuluzi. Mulibe chisoni ndi mmene ife anthu anu tikuvutikira kunja kuno komanso mdziko lathu lomwe. Inu nkumasunga ma Million mnyumba while your people are dying due to shortage of mankhwala ndi zakudya. Ndamulira Kamuzu!!.nyama komanso nkaka zimapezeka. Amatinamiza kuti kudula kadi nkulakwa pamene pano aliyense akuyenera kukhala ndi khadi kumati ID. Ambuye timvereni chifundo ife ana anu. Tidaika mikango kutitsogolera pano ikutidya.

 60. Poor donors. The land is fool of tears of the suffering Malawians, and their tears bring curse along to the Warm Heart of Africa, and Mother Malawi is becoming cold.

 61. Kupsa kwa office ya agriculture a #Chaponda akudzwapo kan2 ha ha ha nde kt amafuna ma umboni asapezeke kkkk Chaponda mwala wa ndele wateleleka ndpo wagwela madzi.. ACB proceed with yoh investigation

 62. Now mitima yathu yaamba kuzizla chifukwa chilungamo chayamba kuoneka,big up to ACB it must go deeper.the money in chaponda’s house isn’nt abig shock because zizndikilo zinachuluka zosonyeza kuti ndi mbava

 63. Komatu sichaponda ekha amene akusunga ndalama mnyumba pali nduna zambiri zimene zikupanga izi. Inu a acb fufuzani nsomba zina zikodwa

 64. So you think if it is true that he has 124 million cash, the money enough as a minister. Then I see him a poor minister because some minister has more than that

 65. Chapondayo mmafuna akhale ndi mamillion angati? Minister ngati uja ndipo sinior minister 24million ndindalama? Mukati muziti ma BILLION koma million? Mwangosauka ndipo muona ngati ati ammange AKUKUTUMANIYO AKUPWETEKESANI CAPONDA OYEEEE

  • Ndi 58;500 dollar,,,, kodi babawa ndalama zimavuta? kuwelenga eti ? nchifukwa chake mumangotapa mopanda nzelu,,,, anzanu amaba lelo shortage kuzagwela obwela i ye atachoka,, apa zingoonesa kuti chaponda sukulu inavuta,…

 66. Okondendwa amalawi azanga olo mutalakhula chotani apa palibe chomwe chingasithe ofunika kupangapo kathu aziwe pitalayo kuti takwiya

 67. kunena zoona boma la Dpp ndi la athu akuba okha okha mbuzi za athu kuphatikizapo pita munthalika koma kulimbana ndi Joyce Banda

 68. The problem is with us ordinary people these shit are happening bt we dnt do anything we just watching and keep on posting funny shit of these scandal #dzuka malawi dzuka

 69. Every Year In Malawi
  Story After Story, all these Stories about Corruption. Damn!!!!!
  Ngati m’Malawi muni tilimo anthu 45 Million bwanji Boma chaka chino ipeleke 1 Million Kwacha nzika iliyonse ya Malawi kuti nafeso tidyeko thukuta lathuu mukungolisambaalo?

 70. how true is this…..if ye mmmh mwemo ndikukhala kwathu Ife achiMalawi,tikamaona otere akupanga zitukuko nkumatiuza ife kuti tizilimbika kuseweza tizalemera mmmmh,mwemo

 71. he is not alone..why gathering such courage of justifying himself when the will of pple is demanding his out of public Office but stil clinging.

 72. Fuck chaponda mbuzi yamunthu,,tawonani mmene liliri dziko la Malawi wina ndikumabaso nde ngati zili chonchi njala tiyithetsa bwanji..Fuck chaponda

 73. Hy my poor Malawi….Law abiding citizens are living in abject poverty jst because of some prominent in office is living a lavish life to such an extent of keeping huge amount of money under the bed….mmmm hayi this is a circus and he is one of the crowns and i’m pretty sure he is not alone #cashgate2 THE RETURN

 74. Koma galu ameneyo its better akanangodulidwa mutu..mwatikwana kwambiri..Escom yayambaso zake zija 16hrs no electricity..nde mbuzi izizi zikutikwanaso .adulidwe mutu ameneyo…zachamba..

 75. nde ife zitikhudze nmanyumba mwathu mwagwa chaponda or kuti zatani siziti thandiza nawo nose si akuba nokha nokha afiti ku gwilana ufiti anyani kusekana zikundu

 76. Mukuwapatsa anthu chonena, nde timve wina akuti chaka chino takolola bwino chifukwa cha boma lake ,,mulungu akulangani , mulungu potimvera chisoni amalawi wagwetsa mvula yochuluka ndipo tikolola , nde tidzangomva kuti wina ali boma lanthu lathetsa njala mbamba deee mudzadzitemberera,,, tazionereni mbava za anthu, ,, mulungu akukhululukireni,,,

 77. Zikuululilatu kuti ndalamazo ndizakuba ndichifukwa chiyani ndalama zambili ngati zimenezo akusunga munyumba? Manyasa inu simudzathekanso.

 78. Mbuli yachuma, zowona ndalama zonsezi kumazifungatira nyumba ndithu? Iwe tisakumane mawa, ndikukoka masayawo wandichititsa manyazi.

 79. Amalawi tilindivuto pankhaniyi pafon panga ndaona macomment 97 koma zomwe ndaona mumacomment amenewo asheee zikukhalangati kuti anthu ene samalawi mpaka umayamikila munthu wakuphayu.Amalawi tiyeni tizikondana osati poti anthu salukuonani nde muzikomenta zausilu ayi ngati mulibe chonena muzingokhala.chaponda wakumanda osateso kundende ayi.kapena ngati ndikundende kukhale kupozimu asakawone komwe walowela akakhaleso room No 4 yomwe kumayenda madzi wamchele galu wamunthu

 80. Mankhwala akusowa mzipatala aja dola zake ndizimenezo, escom ikungobwebweta ija kusowa chonena kumangonena mbwerera..dola zimapita kumeneko.. zaku agriculture sitichita kunena…..nanga chipanda zina kuotchedwa

 81. Mankhwala akusowa mzipatala aja dola zake ndizimenezo, escom ikungobwebweta ija kusowa chonena kumangonena mbwerera..dola zimapita kumeneko.. zaku agriculture sitichita kunena…..nanga chipanda zina kuotchedwa

 82. Probably the other rotten ministers have such huge sums of money in their bed rooms. Mob justice would be a better way go. This chaponda will walk free in no time.

 83. on behalf of moble justice,we r ready to tear him into pieces.Petro is ready,within min we turn him into ashes.We need him no mo,,,,,,,

 84. Ndalamazo ndi zochepa, kumbukilani, amagwila ntchito ku african development bank komaso word bank ali ndi ma track oposa 20, komaso ali ndi Victoria hotel kodi munthu oteleo ngalephele kukhala ndi 150 million kwacha?

 85. Akukulengelani ankolo n’dima ukachuluka kwasala pang’ono kucha.ine nganganga pambuyo panu 2019 boma ilo.zikumuwawa akolope lake mw

 86. Apa ndiye kuba aonjeza aDPP.Kodi muzasiya liti kuba? Zinthu zonse zikhale zokuvutani anthu kuphana,njala,imfa mzipatala,,,,,,,,,,

 87. With such huge amount of cash why cant u Chaponda buy another face mkuchotsa yonga kaziziyo! black mamba!! Anthu opanda chisoni

 88. Pakatipa mukagwira munthu ali ndi mafupa a albino mumaotcha munthuyo , aneneyi bwanji cause ndi amene wapha anthu ambiri ndi njala kumalawi kuno, musamusiye , mukamusiya ndiotcha ndekha na izi zandikwana. Monse muja amalawi akufa ndi njala iwe ndalama unabisa mgututu.

 89. Akakhala woti waba mbudzi nde kuthamanga kumumanga Aboma muti mufuna umboni moyo wanji umenewo kuteloko chapondayo mulandu wake ndi okupha munthu nie

 90. CHOYIPA CHITSATA MWINA, MWANYANYA KUZIKONDA, MUNTHU WASANKHO UYU, WAZIONA? GOD HAS ANSWERED MALAWI VICTIMS!! MA KADETI MUKUTI BWANJI LERO? KUKHALIRA KUMBUYO MBAVA, MWAZIONA????? KKKKKKKKKKKKKKK

 91. ndalamazo ziotchedwedi chifukwa kafukufuku wachamba akachitika chimaotchedwa,koma zodabwitsa ndichakuti makosana omwe azipeza ndalamawo chibadwilini sanagwiliko ndalama ngati zimenezi ndipo samayembekezelaso,lero azipeza mmalo moti agwilitse tchito umwayi umenewu ndipamene aku iufanz kuti atchuke kuti agwila bwino tchito.izi ndizomwe amadanazo azawowa zomangotchuka ndidzina lokha koma kumatchuka ndi ndalama akuti GET RICH OR DIE.mudzafa osauka mukamapusa

 92. People are dying in hospitals,civil servants are earning pea nuts,hunger,and yet some one is stealing such a huge amount of money.so what if all politician’s NGOs can also be investigated Malawi is rich but due to selfish leaders makes the Nation sinks.

 93. Choncho otithandiza angapitirireso kutithandiza iiii koma Malawi ine ndikangootcha nyumba yake bas coz ndikumva kuwawa kaya ndikundende ndipita koma na apa ndikayiotcha bas

 94. You Dpp Cadets, you have always backed Someone with very dirty Stealing Record, now what have you to say? Mwati zii maka inu mukuchuka kutukwana apa anthu akamanena za Umbava? Manyazi bwanji? Kuli ziii !!!!! Kkkkkk we know your Dirty Names, you Brutes!! Si izi mwaziona? Kkkkkkkk

 95. Tingamasauke ife kuno potidulira misonkho yanthu tikumadya movutika wina akusunga ndalama mnyumba?abale anthu mkumafa ndi njala ndimatenda ochizika mankhwala mulibe mzipatala zanthu.Mulungu achite nawo ndinthu.

 96. When the going gets tough, the though gets going on, once u r dirty, the rain never quit pouring on you. #Geordge_Chaponda is filth, let him have his fate. Aponyedwe m’ndende basi. Wanzuza Malawi mokwana.

 97. I am thinking that it’ll take a very long time for God/Allah to punish these crooked officials. I mean God must be absent minded about Malawi’cause of its pretence of being “God fearing nation”.
  Therefore, my fellow Malawians the time has come, its everybody for themself. Lets loot, kill, lie, and all that mess. Those of you who get caught, know your defence, and you who’ll go unseen, let satan be with you!

 98. Honestly I wish him dead… imagine an individual keeping such amount of money.. oshiii masiku omalizadi awa anthu azakhala ozikonda okha,komanso okonda ndalama…….. shame Chaponda…. iwee? andale zanzamva!

 99. Petty to us ordinary ppl suffering frm hunger and diseases chifukwa cha anthu monga awa.Koma tikuziwa kuti even ndalama zapeka koma adyaso ndi ena while anthu akufa akusowa chakudya komaso mankhwala mzipatala .#MALAWI

 100. I feel sorry for my home land, donors are busy helping malawi with food crisis yet they keep money in their homes while pipo r dying of hunger. God will never forgive u pipo with high profiles in government.

 101. Tinanenapo kuti tsiku lina Chauta yemwe anatilenga kuti tikhale osaukayo azachitapo kanthu poganizira anthu okalamba omwe akusowa chakudya komanso anthu owathandiza.Tangoganizani anthu okalamba kutenga voti yawo kuvotera munthu yemwe akuzawabera patsogolo.Amalawi akuvutika koopsa,ndiye wina ndikupezeka ndindalama ngati zimenezi m’nyumba.Ayi Chauta sanamalize kutimenyera nkhondo zioneka.

 102. कृपया ध्यान दीजिए !
  अब हर कोई अपने android mobile से घर बैठे हजारों रुपए हर महीने कमा सकता है और वो भी बिना कोई पैसा लगाए।
  ये झूठ नहीं है। मैं इससे 10000-15000 रूपए हर महीने कमा रहा हूँ। आपके join होने के बाद मैं आपसे contact करके सारे proof दूंगा और आगे कैसे काम करना है, वो भी बताया जायेगा।
  Join होने के लिए
  1. अपने android phone के play store में champcash लिखो और उस app को अपने mobile phone में install कर लो।
  2. अब app को open करके sign up with champcash पर click करके अपनी details भर दें।
  3. Refer id of sponsor पूछेगा वहाँ पर 919209 डाल दो।
  इस I’D (919209) को खाली पेपर पर लिख लें आगे जरूरत पङेगी।
  4. complete challenge और अपनी id activate करके business से जुड़ जाओ।
  …..जय हिन्द…..जय चैंपकैश…
  Wtsp 9953611562

 103. Dr chaponda i really think lawson chaponda body is really turning in the grave..after what you did to grayson and the entire ofamily i think you deserve it …u are such a greedy man,its pay back time,i cant judge u but God only knows your downfall….all the best bwana

 104. Atleast malawi’s agric minister is under probe which means malawians are not to be taken for granted.our’s-the infamous dora siliya’s life is going on just fine.no probes and not a single statement from our president pertaining this fraudulent zambia-malawi maize deal.it is a big shame to have dogs that will only bark and not bite as your leaders.

 105. We both know he is not poor n for the fact he is so highly educated you wouldn’t expect to find masiliva in his house …..what am trying to say is if he stole money he wouldn’t be stupid to just lay it there n being a top official he would have been tipped that something will happen at his house his is not an opposition member he belongs to the government …think big if you wona catch a big fish

 106. Wapasindwi anaulula wapadzala.ACB was going for maizegate issue and here is money laundering.Pple told him to resign and pave way 4 investigation but he didn’t want. $58, 500 could hv boosted the forex reserves but he was keeping all this money in the house.Hw many ministers are also keeping huge sums of money in the house? Will Malawi develop with such kind of behaviour.?

 107. Ng’oma yolilitsa siichedwa kusweka ndi izotu. Chaponda mfumu ya mbava ndiye munkati ndimanena za chimbavachi andi njata nanga umboni upose apa? oyenera unyolo yani? akafere kundende konko.

 108. Nothing strange …cashgate began with these ddp guys…now the end of ddp…..Mulungu amabwereretsa mpungwepungwe dala ….kut wamaso aone yekha komanso kut chilungamo chioneke

 109. pepan aDAUS and PETER bola ife tikudya Gaga tikatelo kugona pasaka ndikukagula soap wodula misonkho tho!! ena nkumaba ha!chauta alowelerepo.AMEN.

 110. Mmmmmmma Chaaa Ndalama Zonzo Munthu Mmotzi Mkumatigulitsa Chimanga Kwadimaci K12500 Zowona Zimenezo Iwo Mkumati Zitingatsitse Mtongo Wachimanga Zowona Zimenezo

 111. hahahaha makape amwenye akatsunga ndalama mmanyumbamu alibe vuto mmalawi akamatsunga ndalama nyumba waba shame nsanje basi

 112. Anthu amakhala ndi money mnyumba inu kafunseni ma Burundu akuzani momwe amasungira ndalama….komanso akuluwa nthawi yonseyi samafuna kuthawitsira kwina bwanj dollarzo? apa nde sanaithe

 113. Kkkk naye chaponda ndi ofoira bwanji samaziwa kuti kukubwera ACB bwanji samabweretsa Kwa ine kuti ndimusungire ………..aziona Kkkk amaona ngati ndimubera ayi ine sindidya za chimanga ndiye ndi izoo wazionatu

 114. This is what we call Money laundering. such amount of cash in your house why can’t just deposit them instead of hiding them, There fore you have to answer Money laundering charge and where do you get them?

 115. Ndalama zokhazo musiileni ndimalipilo omwe amalandila patchito yake, salaey+ alawasi ndizomwe zikupangisa kuti ndalama zakhale zochuluka choncho

 116. Amangidwe, anthu akufa ndinjila kuvutika mpakana kukalowa mayilo a kunja. Inu kumabisa ndalama.anthu opanda chifundo inu.

 117. Mufunilanji umboni wina?? Mbava iyi…. and weeks, months will still be going without getting him behind bars,,, koma ndingoba mwanapiye wa aneba muzanditenga pompopompo. hehehe! Malawi waola

 118. Mufunilanji umboni wina?? Mbava iyi…. and weeks, months will still be going without getting him behind bars,,, koma ndingoba mwanapiye wa aneba muzanditenga pompopompo. hehehe! Malawi waola

%d bloggers like this: