An 18-year-old man has been sentenced to 66 months imprisonment with hard labour for raping two boys.
The convict, Chikondi Banda, was reported to have invited two boys to a rest house at Linthipe Trading Centre where he promised to give them money.
State prosecutor Levi Mangani told the Lilongwe senior resident magistrate court on Tuesday that the two boys complied with Banda’s invitation and followed him to the room where he ended up raping them.
Banda was later convicted after he pleaded guilty to the charge of sodomy, which is contrary to section 153 (a) of Malawi’s penal code.
Mangani pleaded for a stiff punishment arguing that sodomy is a serious offense, hence the rapist had to be dealt with.
In his ruling senior resident magistrate Chisomo Msokera slapped Banda with five years and six months in jail.
The convict comes from Chiutsa village, Traditional Authority (TA) Chikowi in Zomba district.
Zachepa zakazo kwambiri bola akanati 66 years
Akaz ali mbwee ena akumandfunsira okha bas wna bizy nd amuna anzako mxeew
5 years basi mwina amAmajestrate ndi alamuake
Komande Defilement Ya Shupa2 Pa Malawi.
That’s being foolish!! Akana khalakuti wagwiririra asikana nde 15 years, kodi mesa kugwirira ndokugwirira, waapasaso matendatu amenewo.
Chigamulo chimenechi tidabwepo
Bola anaufila akapitiliza kundende komko poti zili common zamathanyulazi kundende
66months???
Isn’t enought amuonjezere asaaaa
Imeneyo ndi mbuzi,zina nzofuna kuzisaka nkukaziponya mundende,zizikagonana kumeko.
Zachepa zakazo waphwaniraso ufulu azimai nanga galu timampatsa msipu mbuzi mkuipatsa nyama amangidwe ndithu wamisala ameneyo
Amuchepera sentence ameneyu
Shameless he goat!
absurd!
Amuna nde akutichitisa manyazi paziko pano
Devil! Atenga malo;shit,shit satana wonyenga.
Zachepa zaka add more
born 2 woman
Shame on you.
sodomising
shame
Akamapanga zimenezo azimphwanga ndikanapha ndekha ameneyo,pantumbo pake
Zokhumudwitsa
There is no rape law in Malawi when in involves 2 men or boys. There should be and applied as it is for a women or a girl defiled.
The convict should have received 13 years,
Wake up Government and change the sodemy laws to include the definition of rape when it applies to boys and men,
So many outdated laws Parliament should be updating but members just sit around get to workband solve the nstions problems not your own. Work harder.
Chaponda gets reinstated Why, that’s right No Law,
Koma amuna enawa bwanji? Zinyero nyero zati bwee izi nkuma kasilira mamuna nzako eeh,zina ukamva ngati bodza.
Apazikutsimikizika kuti mitundu yoteleyi ilipodi komaimangofunika kuphayose itheletu
5years kumuopa?? Anakakhara mwanawao wapangidwa mathanyurao anakampatsa how many years??? Shit
Rape?. No, but anywhere let’s findout from the Masters of this art, Trapence & Mtambo what this is called.
Nde 5 years yachepatu bcoz ali ndi milandu iwiri, wogwiririra ndi mchitidwe wa amuna okhaokha.Akanapatsidwa 30 years chifukwa wanyatsitsa mtundu wa Malawi
izi ndiye zachamba.2 boys kupangidwa rape ndiye opanga rapeyo zaka 5 ndimiyezi 5 kundende?anayenera kuphedwa basi.ngati wagwilira anyamata 2 akapita kundendeko ndiye azikakwera amnzake kangati patsiku?lamulo limati mkaidi samalakwa ndiye kumeneko azikangokwera mwaufulu which is very bad.
Judge ameneyo ngwa chucheee!
Mchiyan Kodi Amalawi,, Nanga Zikoli Likupita Kuti???
Aaaaaaaaa
he raped two boyz?i hope they are not pregnant!!!
How? Idiots
it simply shows the end of life mpaka nyamata nzako eish!! foolish
this is a testimony of how i got cure from HIV/AIDS, i have being suffering from hiv/aids for the past 8 years without the expectation of being cure, i was on ARV, despite the ARV i was not comfortable and there was nothing i could do because i knew and i was told by my doctor that there is no cure for HIV/AIDS, my dream of getting cured came to past the day i came across a testimony like this on a facebook page of how someone was cured through the help of dr abumen herbal medicine, i was advice its not real that there is no cure but something keep telling me to contact him, of which i later did and the cure was sent to me with an instruction on how to use it which i did accordingly and went for a test, to my greatest suprice the result was negative i could not hold back the tears of joy running down my chick my doctor was shocked, i thank God that am finanly cured from hiv/aids, DR Abumen is an herbal specialist that can cure hiv/aids, you can contact him through his email which is [email protected] or whatsapp his mobile number is +2347085071418, am sharing to save lives, PLEASE SHARE TO SAVE SOME LIVES.
Nkadzakhala president milandu yamtunduu Chilango chake ndikupha basi
Idiot
mwazionatu inu akaz mukamakaniza katundu wanuyo zomwe zimachitika azibambo amangolowetsana kotulukila mgaiwa …
Kkkkkkk komandekulankhula eish
umenewu ufiti kapena chani?
Where
mamuna zako bola hule ukanaupeza
Man raping boys?? Hahahahahah ziwanda zake zodabwitsa
Hahaha…! madest ting
why nat life in prison???