Livingstonia synod wants govt to limit number of children per family

Advertisement
Malawi’s population remains high. (Image credit: Dawin Meckel)

The Church of Central African Presbyterian (CCAP) Synod of Livingstonia has expressed the need for government to limit the number of children a family can have.

The synod said government should develop a population policy as a measure of controlling the country’s ever growing population.

This is according to the Moderator for the Synod, Reverend John Gondwe, who was speaking with the local media.

Reverend Gondwe said the policy would guide people in the country as to how many children they need to have in a family.

The moderator said because of lacking this policy, people in the country are having as many children as they want.

He said the situation of having many children is putting people as well as the government under pressure when it comes to resources.

Currently people in the country are free to have as many children as they want a situation which puts pressure on the country’s resources.

Advertisement

381 Comments

  1. I wish the other churches were able to talk the sense as the synod has done. I 100%+ agree with the Livingtonia Synod. We really need responsible parents who are able, not only to feed, dress or shelter their children on daily basis but also to have a long term plan with high possibility of implementation. We need not only to quench our daily sexual desires, thereby reproducing unnecessarily, but we need to love our children, even before they are born, through proper family planning. The teachings against population control have always worked against us people. Malawi needs responsible citizens.

  2. MULUNGU ADATI CHULUKANANI NGATI MCHENGA NDIYE TIYENELA KUIGWIRA NTCHITO NGATI AKULU AKULU ALIVINGSTONIA MWAKHWIMA ZISIYENI AKULU AKULU ADATI UKAPANDA MANO USAMASWA PHALE IWEYO ULI NDI ANA 15 NDIYE ULETSE ANZAKO? IWEYO PAMODZI NDI BOMA LAKOLO NDINU ZITSIRU!!!

  3. That is totally stupit,what does the Bible says pankhani yobelekana ?.M’malo momalimbana mdikupemphera mwayamba kuwauza anthu zachambazo bwanji ?,anthuwo amadya m’makwanu ?,makolo anu akanaletsedwa kut asabelekeso bwenzi mutabadwa inuyo kapena mutero pot inu munabeleka kale eti ?,fotsekiiiiii tiyeni uko ndi nkhani yopusayo.

  4. I agree da synod cz due to high increase in population people hv started cutting down da forest’s for settlement its high high tym da govt consider dat

  5. Kakakakakka ose amene amagwilizana za nkhani
    imeneyi mbuzi
    amene akuvomeleza mbuzi
    atsogoleli aphingo umenewu
    ose mbuzi
    mulungu adamuwuza abulahamu
    kuti ana ake adzachuluka
    ngati nyenyezi zakumwamba
    kodi tachulukana kuposa nyenyezi
    zakumwamba?
    Komase adati tuchulukane ngati
    nchenga wakunyanja kodi
    tachulukana kuposa nchenga
    wakunyanja?
    Kodi inu muli ndidziko lanulanu
    kodi inu mungakwanitse kudyetsa
    munthu modzi kuchokwela
    pa zomwe mudazilanga pa nokha? Awa asaname ni atumiki
    asatanaotsutsuna ni mulugo

  6. Bible imati belekanani ngati mchenga. Lero church yodziwa mau a mulungu ikutsutsa kuti tichulukane ngati mmene ambuye adanenera. Pali chifukwa yapa ndiye chopitira Ku tchalitchiko?

    1. Pleasant Gondwe: bible imati musaonjezere or kuchotsera mau a Mulungu. The bible just says in general kuti ‘BELEKANANI NGATI MCHENGA.’ Tisiyeni ife amphavu tichite mau a Mulungu ngati inu mulibe.

  7. There z also need to limit how many kids foreigners can have in this country. Just imagin how the Burundi, amwenye, Congolese multiply faster than the locals? They get support frm UNHCR and yet they flock to our hospitals for free services

  8. I have seen here that all those are against it are male. Amuna omwe amangodziwa kufesa ana kulera sadziwa. Muwafunse a zimayi m’mene kumavutira ku lera ana akachuluka!

  9. Koma chopeleka no limit! Msiyenso kumadalitsa ukwati or auzeni achristu anu azikwatilana amuna kapena akazi okhaokha mukatelo musova. Musalole satana kukugwiriysani ntchito!

  10. Aaaaa ine ndine wa c .c.a.p kweni ivo mwayamba ndivyo yai munthu wakubaba yekha wakumanya icho wana wawapenge imwe chamusuzgani nivichi mukuwalerera wana wawo?munizgole apo inwe mwayowoya nkhani iyi pala chakuchita chamsowani nkhalani waka chete ndimweso mukunangiska charu kuti chiyende makola ndango ilo mu baiblo mulije nda ku china do u think the god will happy .no kuwelezgaso mazgu agho chaa mwavuka na mpingo lekani kutimbanizga wanthu wamwene yehova

  11. Be very carefull my beloved Malawi have this questions in you..where did they took this all complainments from, who send them I blv there is a souce somewhere atumidwa awa ali ncholinga awa plz!!

  12. Be very carefull my beloved Malawi have this questions in you..where did they took this all complainments from, who send them I blv there is a souce somewhere atumidwa awa ali ncholinga awa plz!!

  13. Come on ccap synod that is a gud idea, luk at malawi, the population is getting higher and higher while the country remains the same, as am talking now its, 17.1 million, while countries like botswana is biger than us, but there population is small, so why with us? Recall that our country is a land locked, i do support the idea.

  14. first lets talk of mind set change do not rush in imposing policy on people. look at chain one child policy they revoked. don’t make rashional decision.

  15. Hmmm bcause you have seen life so you dont want God to proced his work in the sense that others should also have access of life aaah leaeders of today God says the same like soil he knwz how to take care his child just be queit put the finger on your mouth one.

  16. Those who read the Bible and understand its prophecy can not wonder,the church want to unite with the state!!!!there is something dangerous that is coming out of this of which a lot of people who claim to be Christians are not aware of,history repit itself,how many Christians are aware of what happened in the Roman Empire when the church and state united,it was 320 to 321 AD,Constantine was the Emperor by then,those who understand the book of Daniel and Revelation know what I am saying!!!!!To my understanding I can not blame the livingstonia synod because it just gives me the the sign that time is getting closer to fulfill the prophecy?

  17. Aaaa ixi NDE siza u mulungu izi a synod what’s wrong with u? Mukudandaula za kuchepa kwamalo Dziko munalilenga ndinu?, pene linayambira mpaka pomwe linathera mukupaziwa? Malamulo amenewo muzigwilitsa ntchito mumpingo wanu omwewo osamatiuza mbwerela zanuzo ife ayi, Go to hell straight mwatha mafilimu fokoff

  18. With a great respec, the synod is in my point. Just fancy, the country doen’t grow but population is growing rapidly. This influence presure on every assets

  19. Machende anu azimbusa nonse mukuikila ndemanga izi kodi ndalama zimene mukulandila kwamericazo zikukuzunguzani mitu yanuyo eti inu muli ndiana angati muli ndizibwezi zingati inu izi ndie sete ngati simukuziwa simukwezedwa malalipilo chaka chino. Halam mukuiyambayo kaya tikudulani mbolo zosavinidwa mwava inu agalu inu manyi awa ndie a president azisaina kungosaina izi panyapawo ndithu akhala nayeso mbuzi ya munthu paziko lose zapasi inu agalu chapter chanji chimene mulungu anati mubele mwalimiti machende anu mwava apusi inu if u want more about me go to my email .com

  20. They must go back to the bible and rub what was written ? God said go and multiply now the church wants to control????

  21. Nde chamba icho inu mukumvomeleza mumasamala munthu inu za ziiiiiii zopusa ngati mukukanika kutumikira osangokhala bwanji ndinu nomwe opemphela hahahaha mlaka maliro sananame eti kuti ndikulilira mbuzi zina kkkkkkkk aaaaaaaaa mbuzi kuti mbuzi

  22. This is rubbish what ccap proposal,what u must remember is that since independence up to now nothing is changing in malawi,only politicians they get rich and rich,now Christian stop this we take care our kids with small we have in the village,

  23. That is progressive thinking. We are even more populated compared to our resources. We are persistent food beggars. We can’t sustain the huge population.

  24. Is this a heading for the story or the main story. i think the reporter needs to answer why, how, when and where. give out the story plz.

  25. M’malo momawawuza anthu uthenga woti uwatengere kuchipulumutso mukulimba ndi zazii ngati zimenezi kodi inu ndimagulu amingo yomwe ikumagawa ma condom mu church aja eti

  26. Azisogoleri osaziwa mawu amulungu. Amangoziwa chopereka bas, malo mot muzilalikira kut anthu asiye zinyengo mungonena za ziiiii. Akuopa eti kkkkkk tanenanu nkhani ina kma ikhale yabwno.

  27. I strongly disagree. Its out of bounds, offtrack Iam telling you, church iyi satana adathana nayo kale.

    Ayamba kugawa makondom amenewa kkkkkk

  28. kkkkk ine sinzatheka bas ndasova kale zmenezo ndkwatira akaz two uku ana small mbali inayi pang^ononso apo ayi muziuze nkhosa zampingo wanuwo kt ztero km ine nde i luv babiez

  29. Ganizo labwino kwabasi; kungobereka ana ngat sasakawa kulepheranso kuwamveka;kuwaduetsa mkuwasamalira.awonjezereponso lamulo loti mwamuna akapereka mimba mwa mkazi mkuikana adzimangidwa kungofesa ana mmidzimu ngat bale panazale zopusa zikupititsa patsogolo uhule wa azimai zimenezi.kumpasa mimba mkumukana kumulepheletsanso sukulu ukuganiza zoti atayikwatilenso mtchembere yakoyo nda???

  30. who ever is behind this iddea is very foolish galatian. why dont you start by stoping members joining u.if u r apolitical club then ya.who has bewitched u

  31. many pple in da church = many offerings mumbale.few pple in da church few zopereka.Now,know dis,let u not shal say zopereka zachepa iwe pastor iwe take care otherwise kolalayo tizachosa.wamva uziti,eeeeeeeee!!!n

  32. 100% correct for the first time agree with Livingstonia synod

  33. Livingstonia Synod is led by a Lunatic & doubt if this Synod is any part of the CCAP we’ve always known in years. Wonder how a Church leader would make such a call when all others are against the same. Contraceptives or any such form would still amount to the same crime as abortions. Surely, this is typical of Rev Nyondo & certain that this would not be a shared idea with all other Churches inclusive of the Nkhoma & Blantyre Synods of the CCAP.

  34. Mmmm apa aonjeza kodi anao amatithandiza kulera or tomakapemphepesa ku church kwao ndine wa synod koma njila yake siimeneyoyi yolangizila anthu abusa mwalakwitsaaaaaaaaaa

  35. This is long for the church of God according to the bible,were did you get that your telling the Government that is long overdo for the church

  36. Yes agood proposal, Bible imatidi mubalane muchulukane osati ubalane uchulukane iyi nintchito yothandizana komnso the same God sangakondwe munthu kubeleka then ndikulephela responsibility yake yosunga anao imagine street kids mtown alimbweee thats why God blessed man with WISDOM kuti azitha kupanga control zinthu ngati izi . Under aged girls angobeleka ngati ali pa fashion show lets not abort but control wisely

  37. so now are trying to copy what’s happening in china. You ara Magogos and Madalas thus y you are saying lyk that. How many children do u hav? May b 13. So Now you become clever coz you can’t make Babies anymore. Aaaa! Shame

  38. Apologies but lemme say “FUCK ALL THIS HOLLY CRAP, I mean this is Shit that you get paid when you train “religious leaders ” pastors and schools from collages , fuck that!, I hope God calling minstering like a gift makes more sense…. stop brainswashing those poor souls in religious universities and giving the degrees that they have qualified qualifications to SERVE THE LIVING GOD, to hell with rusbish, to hell with those devilish ideas

  39. I thought the bible is all about “multiplying like the Sands of the ocean.”..
    I’d the church going against God’s word
    Or does this have a scriptural backing ?

  40. Just continue kuuza anthu za ufumu wa kamwamba, rather than interfering pa Program yanga nda akazi anga, kubereka ana ambiri m’banja langa is non of yo bzness, eniakefe nde tingaione mita, ndipo mkadadakhala anzeru you would be happy for overpopulation, since overpopulation = over CHOPEREKA ku church

  41. Good destination koma
    Popeza anawa akumabadwilaso ngakhale kwanthu opanda ma banja ndezidzikhalabwanji?kodi opanda banja wa muwapatsa malamulo otani?akapezeka ndimimba kapena mwana opanda bambo(okanidwa)mudziwatani?

  42. ndine wa LIVINGSTONIA kwee mmmm mwayamba kusopa ndalama izo tuma wupu tukumupani,imwe ndimwe mukalenga charu? mwenecho Chiuta ndiyo wakusamala umoyo wa munthu,kenako mutiphalirenge kuti kufumumiska zinthumbo nkhwakuzomelezgeka

  43. Uku nde timati mpingo wapenga misala. Ngati akhristu amene akutsogolera anthu pa maganizo ombwambwana ngati amenewa, ndekuti osapemphera anena chani?
    Mulungu tu ponena kuti anthu abelekane anadziwa kale, kuti zonse mukunenazo zidzakhalapo.
    Kwa ine Ndikuona kuti ganizo limeneri, ndilotsutsana Ndi bible.
    Ndipo mulungu siopusa ponena kuti tibelekane ndipo tichulukane.
    Msiyeni mulungu akhale mulungu basi.
    Iye Ndiye mwini chilengedwe chonse ndipo salakwitsa.
    Ngati mwatopa Ndi ubusa tangolowani Ku unduna wa Za umoyo basi. Mukhale alangizi otengera kulera khomo Ndi khomo. Ntchito ya chauta yakukanikani.

  44. Zamisala basi. Bwanji osakamiza kuchotsa nduna zakubazi kuti muteteze chuma chomwe chikuonongekachi? Lolani anthu aswane mchenga-mchenga

  45. I wonder how churches are busy trying to commit sins against god these days than preaching the message of love and kindness !church people are trying to convince pagans to practice evilness

  46. Inu aSynod simumatidyetsela mabanja athu mwamva!!! Olo boma mutaliuza nde lithandiza chani heeee? Osaliuza boma fundo zanzeru bwa? Anthu tikuvutika chifukwa cha ulamuliro woyipa ulipowu

    1. Man mulibe nzeru ndipo simumaganiza olo pang’ono. There is sense in what the synod is saying, use your brain think about it and come back later to comment. Just to brush your brain pang’ono, overpopulation imabweretsa zinthu ngati kuwonongeka kwa chilengedwe komwe kumabweletsa mavuto ambiri ku dziko. Think about it in a positive way you will finde some sense.

    2. Mmalawi ndi ovuta kumumvetsa that’s why andale amangotibera. The truth is those who have big families ndi anthu ovutika on average unlike those with manageable families. Yes you can have 8 children but I bet they scramble for better clothing,healthcare and education e.t.c. Anthu ochuluka koma osauka amafuna mankhwala aulere,feteleza waulere, sukulu yaulere,chimanga chaulere. Majority of families with large population ndi osauka. Thats the fact.

  47. As if defying God’s order that says ” multiply and reprenish the earth like sand” ni baibolo njini ilo mukuwerenga imwe anthu achiuta?

  48. Am a CCAP member but this proposal is not good idea coz even in the bible there’s no chapter and verse which states this stupid idea

    1. Are you More intelligent than God chiku chibwana? Read Genesis 1:28, and you should give me the verse from the bible which says you must not be fruitful and multiply

    2. amapereka ana ndi mulungu boma silipereka ana, ngati mulungu wapereka ndiye tiziwapha chifukwa dziko lafuna? Kulera ndi tchimo, so mukufuna mulimbikitse mchitidwe otaya mimba? Shame on u a livingstonia synod. Mmalo mowalalikira anthu uthenga wachipulumutso mwayamba kularika zimenezi ? Go to hell.

    3. Watson I understand you angle from Bible side, but we can’t be so blind with Stupidity that we can’t face reality. wrong is wrong, no matter who does it or says it. Do you (suqqort overqoqulation?) think B4 you wrt anything.

    4. @ Omega you are not the one who support your family but God through you, and God can’t be stupid to say you must multiply, He knows every thing

  49. We make alimited number of children depending on our resources. And this is not the government’s business bt family issues.

  50. Let the church tell its congregates a child limit policy.See how they respond,and then propose it for the general public.its a welcome move,except from the wrong corner!as a church,the scripture will it follows as source of their doctrine will not support the ideology.

  51. Dont 4rget tht we v NAPUSE NAPUSE MULUNGU AFUNA ANA CHURCH. AND THE BIBLE IT SELF SAYS BELEKANANI NGATI NCHENGA, ZONSEZO SIMUKUZIDZIWA ? THTS NOT FAIR COMRADES, YOUR POINT IS OUT OF ORDER KIKKKKK,

  52. mukutsusa inu ndi amene mumakhala patsogolo kulira ma coupon kuti mugule feteleza,,,nanga dzikolo amati mulidzaze nokha?? ,,

  53. I strongly agree with what the synod is proposing. Population is one of the major obstacle that hinders our nation from progressing in all dimensions of development. Any student of economics, development or sociology eventually comes across the name Thomas Robert Malthus, a cambridge professor. He noted that country ‘ Population tends to grow faster than the means of sustaining it. In ordinary Language, we would say Population grows at a faster rate than food production. When the Population grows much faster, it is checked by diseases, pestilences, was and famines. We people of Africa envy the people of Asia, Singapore, China and South Korea for their economic growth but seldom envy them for achieving very low Population growth rates. While in Africa, Population grew on average of three percent annually, in Asia it grew at 1.8 percent, in europe at 0.2 percent while in north America it grew at 0.8 percent. Although we cannot conclude that Population growth is not the only factor that hinders development but it contributes largely hence i second the synod we need that Policy at all cost

    1. Zaziiiiii eg SA kuli anthu ambiri why zitukuko akupanga daily ??? Osanena zakuba bwanji ndiye vuto loti malawi sakutukuka

    2. A Mateyu read my comment again, i have said Malawi as a Nation we have several problems that impinge our development, there are numerous to mention,, Bad governance which is followed by Corruption, week institutions, population growth jus to mention a few. I didnt say population growth is the only obstacle but rather its one of obstacle,, please re-read the comment before attackin me again

    3. Am with you in this. the way we are multiplying mmmmm it is very dangerous and we are putting alot of pressure on countrys resources

    4. Mfundo ndiyabho koma sizingatheke ampingo inu,,,,,tathokoza potikumbutsa koma ai sizingatheke nkomwe….abusawo ali ndi ana 4 pa banja lawo koma akhala akusiya zimimba kwa tiatsikana totsatira ku mpingo kwawo moti kuphatikiza yapo nditha kunena kuti ali ndi ana 14……which is already populated

  54. Only those CCAP Members will do that but don’t expect every Malawian to do that stupid things coz even if I get the team in my house it won’t affect u, will you feed my family if I follow your opinions? Keep quiet then if you no nothing about God

    1. atambala amenewa asowa zonena iwo mmakomo mwawo ali ndi ana makumi makumi tisawuzanepo zochita apa aliyense amadziwa mulingo wa ana wowakwanitsa kuwasamala.Bwanji ma verse atha m’baibulo otilalikira?.pangansoni fundo zanu malawi sakusawuka chifukwa cha fundo yanuyi..muwonetsetsenso bwino bwino..

    2. Ana 12 amunthu mmodzi onsewo azapeze ntchito pamalawipano? ena siomwe mukumaona akupemphetsa mtaunimu,mukuona ngati ndionse omwe ali amasiye? mpake madona azikatilererako enawa, amalawi tanyanya,

    3. Guys ntchito ya ubongo ndikuganizila, osamangobwebweta apa mukamabeleka ana ambiri population imakula kupangitsa anthu tizikanganilana zinthu(pressure on resourses) just imagine m’mene chilengedwe chikuwonongekela chifukwa chakuchulukana, Malo olima akusowa, madzi akuvuta anthu tachulukana supply ikuchepa chimodzimodzi magetsi. Inu PA umunthu wanu mukuganiza kuti munthu akuotcha makala(akuononga kale chilengedwe pamenepo) nde akuzabelekanso ana 8 pali nzeru pamenepo? Nkhani siyoti ukutha kuwadyetsa ayi koma let’s think how it affects our nation. The problem is you reason using your legs instead of your brain. Ndakwiya nanu……

    4. Aah! Zeru ya mclass sizelu mkomwe ngakhale utakhala kaya ndani! Mulungu ali ndi njira zake. Ndani angamuthandire?

      Lero ndiyawa ma China akukhala nawo kuno. Tianthu tanzeru!

      Dziwani kuti choipa chokwiriritsa chaima pa malo opatulika- mpingo. Anthu adzatha psyiti!

    5. Berekani anawo 20 munthu m’modzi. Musazadandaulenso za magetsi, mankhwala mu zipatala, madzi abwino ndi malo olima ndi okhala. Zonsezi udziza peza mu nyumba yakoyo.

      Komanso anthu ngati inu mumangodziwa kupereka mimba kusamala ana mumasiyira akazi anu ndi adzilongo ake ankaziyo. Sikuganiza mo pepera kumeneko.
      Anakuyika iwe factory yopanga ana kuti adzikulelera ena.
      Malemba oyera amanena kuti mwamuna wokanika kusamala banja lake amakhala oyipa pamaso pa mulungu kuposa munthu osapemphera.
      Apa ndizachidziwikire kuti udzikhala ndi size ya banja lomwe ungalithandize. Ndipo olo utamwalira sizingazakhale chiphinjo kwa osalawo

    6. Very soon government will introduce fees in primary education due to financial crisis. If govt hv introduced a fee of K 5000.
      Consider a family of 12 children. If 5 children are in primary a family will pay K 25000 each term. If 4 are in secondary (cdss), a family will pay 8000 x 4 which is K 32000 per term. In total its K57000. In three terms K 171000.

      If one child has been selected to polytechnic (unima) fees is K400 000 plus K200 000 for meal and accommodation the total is K 600 000.
      Therefore if we add a fees a family need to pay a year, it will be 600 0000 plus 171 000 is 771 000.

  55. Inuyo teloni only God can limit not u & me mwazitenga kuti izi ?kodi mu holy bible muli mgwilizano wina uli wonse ndi boma?and we know some of you sold your soul to devil and nick named it called bone again yet ua under (Illuminate)God is watching

    1. You are right frank….akungofuna mtundu uchepe since gay/lesbian marriage siikulongosoka mmalawi muno.amalela ndi Mulungu tu ngati sadziwa.kodi atasiya kubala amalawi muzatipasa ma hummer familly iliyonse?mavuto azachepa?kapena tinene kuti boma/satana wadzela mwa inu ampingo wa pansi?ccap ndimavuto kwabasi.thangani mwafuna ufumu wa Mulungu ndipo zonse zizakutsatani.ana ambiti sabadwa mmabanjatu akubadwa kuuhule.mwakanika inu simungapange control dziko let GOD who made it step in before ts too late

    2. You are right frank….akungofuna mtundu uchepe since gay/lesbian marriage siikulongosoka mmalawi muno.amalela ndi Mulungu tu ngati sadziwa.kodi atasiya kubala amalawi muzatipasa ma hummer familly iliyonse?mavuto azachepa?kapena tinene kuti boma/satana wadzela mwa inu ampingo wa pansi?ccap ndimavuto kwabasi.thangani mwafuna ufumu wa Mulungu ndipo zonse zizakutsatani.ana ambiti sabadwa mmabanjatu akubadwa kuuhule.mwakanika inu simungapange control dziko let GOD who made it step in before ts too late

    3. You are right frank….akungofuna mtundu uchepe since gay/lesbian marriage siikulongosoka mmalawi muno.amalela ndi Mulungu tu ngati sadziwa.kodi atasiya kubala amalawi muzatipasa ma hummer familly iliyonse?mavuto azachepa?kapena tinene kuti boma/satana wadzela mwa inu ampingo wa pansi?ccap ndimavuto kwabasi.thangani mwafuna ufumu wa Mulungu ndipo zonse zizakutsatani.ana ambiti sabadwa mmabanjatu akubadwa kuuhule.mwakanika inu simungapange control dziko let GOD who made it step in before ts too late

    4. You are right frank….akungofuna mtundu uchepe since gay/lesbian marriage siikulongosoka mmalawi muno.amalela ndi Mulungu tu ngati sadziwa.kodi atasiya kubala amalawi muzatipasa ma hummer familly iliyonse?mavuto azachepa?kapena tinene kuti boma/satana wadzela mwa inu ampingo wa pansi?ccap ndimavuto kwabasi.thangani mwafuna ufumu wa Mulungu ndipo zonse zizakutsatani.ana ambiti sabadwa mmabanjatu akubadwa kuuhule.mwakanika inu simungapange control dziko let GOD who made it step in before ts too late

    5. You are right frank….akungofuna mtundu uchepe since gay/lesbian marriage siikulongosoka mmalawi muno.amalela ndi Mulungu tu ngati sadziwa.kodi atasiya kubala amalawi muzatipasa ma hummer familly iliyonse?mavuto azachepa?kapena tinene kuti boma/satana wadzela mwa inu ampingo wa pansi?ccap ndimavuto kwabasi.thangani mwafuna ufumu wa Mulungu ndipo zonse zizakutsatani.ana ambiti sabadwa mmabanjatu akubadwa kuuhule.mwakanika inu simungapange control dziko let GOD who made it step in before ts too late

    6. You are right frank….akungofuna mtundu uchepe since gay/lesbian marriage siikulongosoka mmalawi muno.amalela ndi Mulungu tu ngati sadziwa.kodi atasiya kubala amalawi muzatipasa ma hummer familly iliyonse?mavuto azachepa?kapena tinene kuti boma/satana wadzela mwa inu ampingo wa pansi?ccap ndimavuto kwabasi.thangani mwafuna ufumu wa Mulungu ndipo zonse zizakutsatani.ana ambiti sabadwa mmabanjatu akubadwa kuuhule.mwakanika inu simungapange control dziko let GOD who made it step in before ts too late

    7. You are right frank….akungofuna mtundu uchepe since gay/lesbian marriage siikulongosoka mmalawi muno.amalela ndi Mulungu tu ngati sadziwa.kodi atasiya kubala amalawi muzatipasa ma hummer familly iliyonse?mavuto azachepa?kapena tinene kuti boma/satana wadzela mwa inu ampingo wa pansi?ccap ndimavuto kwabasi.thangani mwafuna ufumu wa Mulungu ndipo zonse zizakutsatani.ana ambiti sabadwa mmabanjatu akubadwa kuuhule.mwakanika inu simungapange control dziko let GOD who made it step in before ts too late

    8. You are right frank….akungofuna mtundu uchepe since gay/lesbian marriage siikulongosoka mmalawi muno.amalela ndi Mulungu tu ngati sadziwa.kodi atasiya kubala amalawi muzatipasa ma hummer familly iliyonse?mavuto azachepa?kapena tinene kuti boma/satana wadzela mwa inu ampingo wa pansi?ccap ndimavuto kwabasi.thangani mwafuna ufumu wa Mulungu ndipo zonse zizakutsatani.ana ambiti sabadwa mmabanjatu akubadwa kuuhule.mwakanika inu simungapange control dziko let GOD who made it step in before ts too late

    9. You are right frank….akungofuna mtundu uchepe since gay/lesbian marriage siikulongosoka mmalawi muno.amalela ndi Mulungu tu ngati sadziwa.kodi atasiya kubala amalawi muzatipasa ma hummer familly iliyonse?mavuto azachepa?kapena tinene kuti boma/satana wadzela mwa inu ampingo wa pansi?ccap ndimavuto kwabasi.thangani mwafuna ufumu wa Mulungu ndipo zonse zizakutsatani.ana ambiti sabadwa mmabanjatu akubadwa kuuhule.mwakanika inu simungapange control dziko let GOD who made it step in before ts too late

    10. You are right frank….akungofuna mtundu uchepe since gay/lesbian marriage siikulongosoka mmalawi muno.amalela ndi Mulungu tu ngati sadziwa.kodi atasiya kubala amalawi muzatipasa ma hummer familly iliyonse?mavuto azachepa?kapena tinene kuti boma/satana wadzela mwa inu ampingo wa pansi?ccap ndimavuto kwabasi.thangani mwafuna ufumu wa Mulungu ndipo zonse zizakutsatani.ana ambiti sabadwa mmabanjatu akubadwa kuuhule.mwakanika inu simungapange control dziko let GOD who made it step in before ts too late

    11. You are right frank….akungofuna mtundu uchepe since gay/lesbian marriage siikulongosoka mmalawi muno.amalela ndi Mulungu tu ngati sadziwa.kodi atasiya kubala amalawi muzatipasa ma hummer familly iliyonse?mavuto azachepa?kapena tinene kuti boma/satana wadzela mwa inu ampingo wa pansi?ccap ndimavuto kwabasi.thangani mwafuna ufumu wa Mulungu ndipo zonse zizakutsatani.ana ambiti sabadwa mmabanjatu akubadwa kuuhule.mwakanika inu simungapange control dziko let GOD who made it step in before ts too late

    12. You are right frank….akungofuna mtundu uchepe since gay/lesbian marriage siikulongosoka mmalawi muno.amalela ndi Mulungu tu ngati sadziwa.kodi atasiya kubala amalawi muzatipasa ma hummer familly iliyonse?mavuto azachepa?kapena tinene kuti boma/satana wadzela mwa inu ampingo wa pansi?ccap ndimavuto kwabasi.thangani mwafuna ufumu wa Mulungu ndipo zonse zizakutsatani.ana ambiti sabadwa mmabanjatu akubadwa kuuhule.mwakanika inu simungapange control dziko let GOD who made it step in before ts too late

    13. You are right frank….akungofuna mtundu uchepe since gay/lesbian marriage siikulongosoka mmalawi muno.amalela ndi Mulungu tu ngati sadziwa.kodi atasiya kubala amalawi muzatipasa ma hummer familly iliyonse?mavuto azachepa?kapena tinene kuti boma/satana wadzela mwa inu ampingo wa pansi?ccap ndimavuto kwabasi.thangani mwafuna ufumu wa Mulungu ndipo zonse zizakutsatani.ana ambiti sabadwa mmabanjatu akubadwa kuuhule.mwakanika inu simungapange control dziko let GOD who made it step in before ts too late

    14. You are right frank….akungofuna mtundu uchepe since gay/lesbian marriage siikulongosoka mmalawi muno.amalela ndi Mulungu tu ngati sadziwa.kodi atasiya kubala amalawi muzatipasa ma hummer familly iliyonse?mavuto azachepa?kapena tinene kuti boma/satana wadzela mwa inu ampingo wa pansi?ccap ndimavuto kwabasi.thangani mwafuna ufumu wa Mulungu ndipo zonse zizakutsatani.ana ambiti sabadwa mmabanjatu akubadwa kuuhule.mwakanika inu simungapange control dziko let GOD who made it step in before ts too late

    15. You are right frank….akungofuna mtundu uchepe since gay/lesbian marriage siikulongosoka mmalawi muno.amalela ndi Mulungu tu ngati sadziwa.kodi atasiya kubala amalawi muzatipasa ma hummer familly iliyonse?mavuto azachepa?kapena tinene kuti boma/satana wadzela mwa inu ampingo wa pansi?ccap ndimavuto kwabasi.thangani mwafuna ufumu wa Mulungu ndipo zonse zizakutsatani.ana ambiti sabadwa mmabanjatu akubadwa kuuhule.mwakanika inu simungapange control dziko let GOD who made it step in before ts too late

    16. You are right frank….akungofuna mtundu uchepe since gay/lesbian marriage siikulongosoka mmalawi muno.amalela ndi Mulungu tu ngati sadziwa.kodi atasiya kubala amalawi muzatipasa ma hummer familly iliyonse?mavuto azachepa?kapena tinene kuti boma/satana wadzela mwa inu ampingo wa pansi?ccap ndimavuto kwabasi.thangani mwafuna ufumu wa Mulungu ndipo zonse zizakutsatani.ana ambiti sabadwa mmabanjatu akubadwa kuuhule.mwakanika inu simungapange control dziko let GOD who made it step in before ts too late

    17. You are right frank….akungofuna mtundu uchepe since gay/lesbian marriage siikulongosoka mmalawi muno.amalela ndi Mulungu tu ngati sadziwa.kodi atasiya kubala amalawi muzatipasa ma hummer familly iliyonse?mavuto azachepa?kapena tinene kuti boma/satana wadzela mwa inu ampingo wa pansi?ccap ndimavuto kwabasi.thangani mwafuna ufumu wa Mulungu ndipo zonse zizakutsatani.ana ambiti sabadwa mmabanjatu akubadwa kuuhule.mwakanika inu simungapange control dziko let GOD who made it step in before ts too late

    18. You are right frank….akungofuna mtundu uchepe since gay/lesbian marriage siikulongosoka mmalawi muno.amalela ndi Mulungu tu ngati sadziwa.kodi atasiya kubala amalawi muzatipasa ma hummer familly iliyonse?mavuto azachepa?kapena tinene kuti boma/satana wadzela mwa inu ampingo wa pansi?ccap ndimavuto kwabasi.thangani mwafuna ufumu wa Mulungu ndipo zonse zizakutsatani.ana ambiti sabadwa mmabanjatu akubadwa kuuhule.mwakanika inu simungapange control dziko let GOD who made it step in before ts too late

    19. You are right frank….akungofuna mtundu uchepe since gay/lesbian marriage siikulongosoka mmalawi muno.amalela ndi Mulungu tu ngati sadziwa.kodi atasiya kubala amalawi muzatipasa ma hummer familly iliyonse?mavuto azachepa?kapena tinene kuti boma/satana wadzela mwa inu ampingo wa pansi?ccap ndimavuto kwabasi.thangani mwafuna ufumu wa Mulungu ndipo zonse zizakutsatani.ana ambiti sabadwa mmabanjatu akubadwa kuuhule.mwakanika inu simungapange control dziko let GOD who made it step in before ts too late

    20. You are right frank….akungofuna mtundu uchepe since gay/lesbian marriage siikulongosoka mmalawi muno.amalela ndi Mulungu tu ngati sadziwa.kodi atasiya kubala amalawi muzatipasa ma hummer familly iliyonse?mavuto azachepa?kapena tinene kuti boma/satana wadzela mwa inu ampingo wa pansi?ccap ndimavuto kwabasi.thangani mwafuna ufumu wa Mulungu ndipo zonse zizakutsatani.ana ambiti sabadwa mmabanjatu akubadwa kuuhule.mwakanika inu simungapange control dziko let GOD who made it step in before ts too late

    21. You are right frank….akungofuna mtundu uchepe since gay/lesbian marriage siikulongosoka mmalawi muno.amalela ndi Mulungu tu ngati sadziwa.kodi atasiya kubala amalawi muzatipasa ma hummer familly iliyonse?mavuto azachepa?kapena tinene kuti boma/satana wadzela mwa inu ampingo wa pansi?ccap ndimavuto kwabasi.thangani mwafuna ufumu wa Mulungu ndipo zonse zizakutsatani.ana ambiti sabadwa mmabanjatu akubadwa kuuhule.mwakanika inu simungapange control dziko let GOD who made it step in before ts too late

    22. You are right frank….akungofuna mtundu uchepe since gay/lesbian marriage siikulongosoka mmalawi muno.amalela ndi Mulungu tu ngati sadziwa.kodi atasiya kubala amalawi muzatipasa ma hummer familly iliyonse?mavuto azachepa?kapena tinene kuti boma/satana wadzela mwa inu ampingo wa pansi?ccap ndimavuto kwabasi.thangani mwafuna ufumu wa Mulungu ndipo zonse zizakutsatani.ana ambiti sabadwa mmabanjatu akubadwa kuuhule.mwakanika inu simungapange control dziko let GOD who made it step in before ts too late

    23. You are right frank….akungofuna mtundu uchepe since gay/lesbian marriage siikulongosoka mmalawi muno.amalela ndi Mulungu tu ngati sadziwa.kodi atasiya kubala amalawi muzatipasa ma hummer familly iliyonse?mavuto azachepa?kapena tinene kuti boma/satana wadzela mwa inu ampingo wa pansi?ccap ndimavuto kwabasi.thangani mwafuna ufumu wa Mulungu ndipo zonse zizakutsatani.ana ambiti sabadwa mmabanjatu akubadwa kuuhule.mwakanika inu simungapange control dziko let GOD who made it step in before ts too late

    24. Atisiye Mulungu atitsogolele osati owowo,coz days are numbered zonse analosela aneneli akale zikukwanilitsidwa

    25. So true….the devil is aliar….but they cannot compete with GOD for HE is not man.they have try everything from hiv,family planning methods,gay,lesbian,fatherhood,abortions just to end human race koma sizikutheka..mukamaliza mtunduwu mukhalamo ndinu mu dziko la Mulunguli?anakuuzani kuti malo atha ndani?kuamerica mwinatu koma kuno tchire mbwe kunkholongo uku chikangawa konse uku mukukhalako ndinu?ndalama zolelela anthu mukuba.tibalanadi sitinati zinaxo nzanu

  56. mwasowa chochita mpingo wanu eti? mubwinj mutanenako nkhan zothandiza mudziko muli mavuto mbweeee. njala. kusowa kwandalama ndizina zambili nde mukanene za ana kut atani pano aliyese ndimmene zafika zithuzi akuziwakale kut kubeleka ndibeleke motele ndimene ndikupezele kodi kwanuko kunayamba kwabwela makolo wozapepha kut alindiana ambili ndiye ena asungiseko kwanu? mbuzi za anthu ndinu osamapangaso zopusazo efe tilinawo ana 10 koma ndimakwanisa kusamala ndichifukwa ndinasiya kukupasani chopeleka ndichakhumi ndalama ndimasamalila banja langa osat zoti muzidya inu. pezani podyela. kuchipatala kulinjila zolela kut tichepese kuchulukana nde ngat mpingowanuwo umatswwana ngat makotswe nde musovatu ine anga awili ndilinawo koma sizot anachita kundiuza ampingo kut ndisiye koma kuona ndimene zithu zikuyendela. muuzane asinod kut mulibe zeru. my # is 000000000000 cali me now

  57. Zasiyana pati ndi abortion..kutsekesa etc… actually u r the same people who marched for a pro life campaign and today u r saying the opposite….hypocrites

    1. Sizokakamiza. If you feel like it’s a sin you are free to make a choice. Otherwise sibwino kumabeleka ana ambirimbiri nkumalepheranso kuwasamala. I think kulephera kudyetsa ana omwe unabeleka wekha ndi tchimonso

  58. Anthu omwe mukuti bible limati tibalane ngati mchenga,nthawi imeneyi Mulungu ankalankhula zimenezi chifukwa padziko pano panali anthu awiri okha Adam nd Eve.Tsono pano anthuwa anachulukanadi ngati mchenga tachulukamo chiwerengelo chachuluka akuti rizilera mukuti ay……bible lija osamalimva mogupulira

  59. That’s Briiiant Decission,gvt Shud take an action otherwise in yrs to come we wil exert much pressure on resources,which z not gud.

    1. kkkkkkkkkkkkkk. No becoz he was looking for somebody to give him his name, he could have stopped at me and that could have been a disaster for some of you guys.

  60. U r a stupid man that is not a main issue. Tell the gvt that they must reduce the price of maize n corruption not to have a limit of children is anybody came by ur house n ask 4 food? Ur a big puss

  61. Mmaganizo anga: Zinalibwino A Luvingstonia Synod akumat…. Tawuza ma members awo kut ayambe njira za kulera…. not kuuza boma, cos iwowo ali ndi ntchito yaikulu ku mbali ya mpingo wawo. Chifukwa awona kut satha kukwanitsa kuyendetsa mpingo wawo chifukwa chot anthu achuluka….. Leave the Govt alone now lol

    1. kadi iwowo akamati boma akutanthauza chani.? Mesa boma ndi anthu mnga iwowo, ndeosa panga zoti aziwauza anthuwo mumipingomu bwanji, amene akuyenera kuyambisa ndi iwowo.

    2. Ndiye abweletsa njira ya tsopano ya kulela ?kapena mabanja samakhalapo azikhala okwatilana amuna okhaokha kut kusamabadwe ana? Coz njira ya ku lera iliyonse ikumabwetsa mavuto kwa azimai.more over boma lili bizy kufuna kuthetsa khansa ya nchibelekelo ayiwala kut zimamkhwala zawozo ndi zomwe zikuononga anthu.so which is which? Devil akuyenda mmipingo tsopano

    3. Sometimes Devil amazungulira Munthu yemwe akupanga za U Mulungu cholinga Asiye kutumikira Mulungu yo… This is a real Example

  62. ha ha malo padziko ambirimbiri, Jacob anabeleka ana 12 amuna nanga akazi anali angat? iwe uvekele tichepetse ana kodi mumangopepha boma kut lizikuchitilani zinthu inu panokha simangapanga lamulo limenelo ukapange kwanu.

  63. You said family planning no, abortion no, then the same church is coming with limiting number of children per family. The church cant you see that you are contraditing yourself? I do not support abortion but in my opinion I think the men in the white collar are misleading us. Then we end up being confused kuti which is which????

  64. Komatu musamale mkwiyo wa Mulungu uli painu,kodi simunawelenge mau?mwayambapo kodi mukuwadyesa ndi inu muli ndi dziko kodi inu,mukufuna chani kwenikweni soka kwaiye okwanilisa lemba,kodi inu mukutumikila Mulungu wake uti?

  65. Tanva, ndipo tivomwereaza, km mutiuze njira zomwe tingamatsate kt tisamakhale ndi ana ambiri kmanxo muonetxetxe kt tisacimwile mulungu, coz ife timatsata mau a Mulungu ndipo timalambila iye nt mpingo kapena Boma ayi

  66. Per Woman Is Fairer Though It Is Expected Of The Church To Only Think Of Family ( Let’s Avoid Politics On This Matter And Support The Idea Or Perish As A Nation)!!! I Suggest 3/ Woman!!!

  67. Thus true infact that many parents know only giving birth than care of children.We have a lot of kids on street just begging while the parent is not dead.Have few with good managent.Children are suffering in our deverloping country.Multiplication is not for one person understand the civic Education.

  68. The church can start by putting up a church policy limiting number of children by their members. If de church takes de leading role it will b so fast and infective. Lets take it as a church thing with de gvt it will take too long.

    1. man, it z de govt dat influences policy decision making, hav u not heard of china? was the 2 children policy initiated by clergy?

    2. It is de church which has started it. Many in Malawi r Christians. Lets give it 2 de church through PAC 2 take de leading role.

    3. Which verse from the Bible should the church start family planning.
      When presenting this issue to Church members, as a church u have to quote scriptures

  69. Tikuyenera kuligonjetsa dziko lino lapansi kufikila aliyense adzangoimilira.chonde a Malawi tiyeni tipitilize kubelekana komanso kuyamwitsa mwakathithi.

  70. Amipingo chonde tatilalikire za mulungu apatu mukusocheresa anthu kodi muli mbali iti zimenezo muziwauza anthu mu mpingo mwanumo bs

  71. Dzikoli ndilanu kapena la Mulungu? Relax GOD is in cotrol, inu amipingo chikukhuzani chani za UMULUNGU? ndinu openga inu anjilu kufuna anzanu azalione dzikoli

  72. Ndezopusa zimenezo zakukanikani munavomereza kukwatilitsa amuna okha okha pano mukutiuza zopusazo ndalama zimenezo mukabwezatu mulungu simunthu

    1. poor line of thought, if u die who will take care of your mangy kids? do u know dat there r orphans out there? and who z burdened with these orphans? is it u?

    2. man, b wise enough, GOD uses his pipo, so u cant go 2 heaven to ask 4 nsima or loan, u need somebody and if that somebody z nt ready 2 assist, pipo commit suicide, havnt u heard of this and all those prostitutes out there?, find out y they r there

  73. Heeeee! Heeee! Kodi Iye Wanenayo Kwawo Kuli Ana Angati? Iyeyo Muchurch Mwake Safuna Anthu Ambiri?Apeleke Kulera Muchrch Mwakemo Ife Takana Mpongo Wanthu Umakana Chulukanani Ngati Mchenga

  74. Chigololo chimakoma ana palibe. mukatha inu nomweso muzatembenuke muzizati Akususana ndi mulungu mbuzi ya mpingo.

  75. Church timaidziwa awa amangobisalira mmalomolalikira za ufumu wakumwamba koma ndale zilitho church siingakhale yotsogoleledwa nda china Zenasi Ungapake ai a! Church imodzi mpaka kugawana magawo atatu osangokambira ndi Bushiri simukusiyanatu apa kkkk

  76. Influencing policy formulation. That is a welcome development. Malawi is too small for a population explosion greater than the 16 million people.

    1. My friend, you thinks like those old creatures in Stone Age who had everything on their noses though their thinking capacity was very limited.

    2. I really don’t understand how people think that using insults will make them look wise. Assuming you are Christian and you read that verse ‘ Muchulukane ngati mchenga”. God vs humans great thinkers! Let’s see who win!

  77. Ndizoona koma nanga chifuniro cha mulungu polenga munthu anati tiberekane ngati mchenga nanga apa tingati Bible limanama? Tikuyenera kumupempha mulungu kuti atipatse nzeru apa iiiiiii zitsutsana penapake

  78. Which Bible this church reading? Bible says mubalane muchulukane ngati mchenga muzaze dziko lapasi, komaso ziwani kuti kugwirisa ntchto njira zakulera zamankhwala ndi tchimo(ndikupha) kumeneko kapena muli ndi njira Zina, ndiye inu a CCAP lemba limenero mwalitenga kuti kapena satana ndi amene akukutumani?

    1. iwe kukhara ndi ana ambiri kukanika kuwasamalira bible limat ndi ntchimo mwana ndi mdalitso ndye ngat ndi mdalitso uzioneka monyozeka ndizomwe ukufuna..??

    2. amwene tangopelekani lemba losonyeza kuti kulela pogwilisa tchito mankhwala nditchimo.poti inuyo mwafusa azanu kuti lemba liti….which means mumazisata nde inu tatiuzani ndilemba liti?basiii

    3. Kkkkkkkk… how can someone to support kuti adzikhala ndi ana ambili.many r failing to progress bcoz alipo Ana ambili mnyumba mwao.
      Azibambo akapanga retire form their job nde udindo amauponyela ana omwe akuzisaka kuti asamale anzao.

    4. Malawi ikusungila zitsiru zambiri, inu church ili ndi udindo wokambapo PA nkhani zokhudza dziko. overpopulation imabweletsa mavuto ambiri mdziko even iweyo ukususawe utabeleka ana 20 uvutika wekha kulera komanso zipanga affect tonsefe. Kuchulukana kwabweletsa mavuto ambiri padziko pano monga siukuona iyayi? Your brain need to be brushed

  79. palibe choveka pamenepo ndiye enawo azikapemphera kuti poti amai ndi bambo awo ndi a mpingu umenewo mulungu sawelengera kuchulukana kwawanthu mu church ai koma faith ndi zintchito zako kurakwa2 kumeneko, mpingo ya chine imeneyo

    1. palibe angathe kutanthauzira mawu a bible koma kuchita zomwe maremba akunena basi.#Rechard izi za mpingo izi si za maganizo akowo RIP

    2. Mtengo tikadula amati tidzalepo wina, anthu akutha awa and we need to replace them immedeately, malo akatha basi anawo azidzamanga pamwamba pamadenga anyumba zilipozi, ndiye kuti pamwamba pamadengapa tizidzagulitsaso ngati malo, hooo! tipha makwachatu mtsogolomuno

  80. Zibwana zimenezo they can have children as many as they want bcos its your CCAP or your synod that wil feed them so ngat ukufuna potchukira sakani njira zina not that hahahahah

  81. I don’t think the idea is Biblical.
    Nowhere in the Bible did God limit his population.
    Mwataninso nanga abusa? What actually do you want to score here. Kapenatu you are in support of abortion law, if so, sorry because Donald Trump is not going to fund your agendas.
    Teach the world the truth from the Bible, not your business and political philosophies.

Comments are closed.