Nyasa Big Bullets star has sealed a move to a South African Premier Soccer League side after week long trials.
Chiukepo Msowoya has signed a six month deal with Golden Arrows, Malawi24 has learnt.
This was after Arrows released Nkosinathi Zitha and Namibia international Chris Katjiukua.
According to the Kickoff, the two defenders have only played once in the league this season as coach Clinton Larsen has preferred Nkanyiso Mngwengwe and Limbikani Mzava at the back since the latter’s signing from Mpumalanga Black Aces.
They had earlier on bid farewell to Quincy Ngcobo, Sandile Dlamini, Clifton Miheso and Mauricio Barrios.
Bullets will have to make proper replacement for Msowoya who has been their top forward in the recent seasons.
He was on fire in the TNM Super league finishing second on top goal scorers list with 16 goals, three behind Mafco’s Richard Mbulu.
In the 2015-2017 season he was joint top goal scorer with Red Lions’ Innocent Bokosi as they scored 14 goals and shared the top prize.
Tamabwelani basi six ndiyechiyani
Gyz ndiye mwati timu take ndiye iti kumene akukamusunga kwa sixi month ko
Mmm season yatsala miyezi 6 kuti ithe ndiye anena kuti it will depends mmene apangire perform aza sign contract ya 2yrs, muzivetsa Kaye b4 commenting
Much beta
Mwati 6moths or 6years?kiiiii kiiiii kiiiii mpaka ndalama zake osazitchula Maaaa Maaaa kungothawa mavuto ali kumalawiwa basi
Guys etindizoona kuti achina kamwendo kuJapan amaauza kuti azigulitsa freezes wamalambe mustreet emwe maJapaneese ena anamusilla atabwera kuno kuMalawi powanamiza kuti akukasewera mpira?
Guys etindizoona kuti achina kamwendo kuJapan amaauza kuti azigulitsa freezes wamalambe mustreet emwe maJapaneese ena anamusilla atabwera kuno kuMalawi powanamiza kuti akukasewera mpira?
Tiuzen inuyo man ife palibe chomwe tikudziwatu
Fack you and fack you thoo peter
6 months? ?? better stay there,
6 month deal basi akuwumila bwanji
Bola ameneyo koma achina kamwendo anarandira yasix days
Bola ameneyo koma achina kamwendo anarandira yasix days
Zikhala ngati za Sulumba zija
SAfrica!Safrica!basi!amalawi chimwemwe ukooo!sitingaveko kuti player wapita ulaya!mpira wapanyasaland zachisoni!
Eeeee shiiiiii
Ndinkhani yomveka komano man mmmmm nkani mulungu ana ika anthu ofanana koma mitima kukhala yosiyana ndipovuta kutero iyeyo mwina tsoka kwa ife amphwi kaya.
Congrats..!
Bola pamenepo…………
kkkkkk 6months olo dzimayi ya pamkatiyo
As big tim
Ulibho mkulu.ukamuuza kokwana kawiri avetsetsa
Kkkkkk 6 month ndiye chibwerekeratu
kkkkkk lol 6 month contract!! shame.
Kkkkkkkk miyezi 6 zikukaikitsa et
ndani ameneyi guys
Angakhaleso ndan mr penalty(chiukepo)
Abdul uliboo wamuunikila big man
Big up!!!!
nde bullets imeneyo,simatumiza ma player ku japan kuti azikazunzika iyayi!!!!ku vaya kayesa mwayi pa jon nku signer contract,siii izi za pink zi!!!!
Iwe contract imakhala ya miyezi six?teamuyo yowona chan bolaniso akanapita ku mizimbe kujatu
Gabeya zikumuvutayo ndi wa Noma??
mukuziwa ndinu kuti zamuvuta!!
Eeish koma nthawi zina zimene umapanga mwayi! Kubwera atakalamba!!
komandiye mwatikanda pa cetara mukufuna BB inthe basi.
pepani potumiza apa uthengau koma mutimvetsebe kwa omwe ali ndi kuthekela akafikitse kwa anuwake MALAWI. Uthengau ukupita kwa Mtsogoleri wa dziko la Malawi. Olemekezeka Bwana Prasident komwe muliko. Imvani mtundu wa malawi kulira. Bwana ife ndi anthu omweaja tinakuvotelani tilibe nanu mangawa koma lathu ndi pempho chabe. Malonjezo anu sitinaiwale maka munati muzapitiliza bwino pomwe akulu anu anasiyira. Ife amalawi sitifuna zambiri bwana monga mukudziwa ife ndi anthu olimbikira muzintchito ndipo sitidalira kuti muzitipatsa ndalama pa mwedzi kapena mudzitimangila manyumba ayi. Koma nkhani ndadza nayo pano ndiyoti Ife amalawi tili ndi umphawi wadzaoneni pamene ndi anthu omwe anakuvotelani. Mwina mungathe kufunsa kuti simukufuna ndalama ndi manyumba awulere ndiye ndikuchitileni chanu? Bwana ife tili pano tikufuna mutichepetsele njala momwe akulu anu anachitila koma zimafunika inu mupitilire pamenepaja, mfundo zathu ndizotere pa nkhaniyi: Ndalama zomwe mukanatengera anduna anu kupita ku America kukanjoya. Mukagule Feteleza m’maiko ena ndikuika m’ma admac ndi m’ma dillers onse m’malawi ndikuika mtengo otchipa monga K5 000 thumba limodzi kuti amphawi ndi onse ochita bwino adzigula mofanana. Feteleza asamasowe m’malo tawatchulawa ndipo pasapezeke munthu akugulitsa feteleza mopitirila mtengo wa boma akapezeka oteroyo adzimangidwa komanso kutseka business yakeyo. Chimanga chikakololedwa chidzigulidwa ndi aboma pa mtengo umodzi ndipo anthu onse amalonda ya chimanga asagule chimanga pa mtengo opitilila wa boma oteroyo amangidwe ndipo business yake itsekedwe. Anthu adzikhala ndi ufulu okagulitsa mbeu zina kupatula chimanga’ mwachisanzo Fodya, thonje, ndizina zambiri kungopatula chimanga. Kupanga zimenezi kwa zaka 3-5 muzapeza kuti Malawi tidzasala ndi umphawi koma njala idzatha kotero anthu akadzakahala ndi chokudya chokwana adzagwira ntchito zachitukuko cha dziko molimbika. Or mutamanena kuti munthu afuna kupita maiko akunja ayenera kumapezeka ndi account bank ndipo mudzikhala ndalama zokwana K500 000 amalawi adzakhala omvetsetsa or mudzidzati passport ndi K100 000 anthu adzalipila chifukwa opita kujon or ku UK adzadziwa kuti pakhomo akusiya pali chakudya. Pomaliza muzaganizile nkhalamba, ana amasiye, olumala ndi odwalika nthenda zikuluzikulu onse adzilandila K12 000 pamwezi ndiye kuti ndalama imeneija anthu aja azidzigwilitsila ntchito kukagula zosowa zao kuti misonkho mumatidula ija idzithandizanso anthu osati boma lokha. Guys kwinako pitilizani. Zikomooo!
Mfundo ya bwino kwambiri,koma vuto atsogoleri anthuwa kudzikonda ,dyers too much. Amangoganiza za Iwo okha ovota amawatenga ngati akapolo.
Man mulibho and mukufunika mutakhala mulangidzi wa president
zambiri wakamba zosatheka kmanso dont expect kut uthengawu ukafika kwa big man
yababa kaswiri:kumeneko ndiye timati kubwezerana mmbuyo,palibe yemwe amadziwa kucha kwamawa,uthengawu ukafika ndithu,ngakhale kuti ufika mochedwelapo,ndi ochuluka omwe awelenge comment imeneyi,tsikulina uthengawu udzawafikira ayeniakewo bwana#pitala
Well said,I hope this message will reach my president.
Project ya fertilizer subsidy imakhala ya kanthawi kochepa osati moyo wanu onse.
Am gonna make plan mpaka bwana mkubwa amve kuliraku
Bwana akawelenge zoputsa ngati zimenezi?
Za ziiiiiii
ndakumvani mr nkhoma zitatero zingayende kuliraku kwagwera tonse
congrats m’bale…Wasyana nd mavutowa iii
Save My Click.
Chiukepo Msowoya
Timu yanji man?
Ok. Well Done To Him.
golden arrows
Hailand park
za mpira
viva