A Lazarus Chakwera ndi kutheka anagonja pa zisankho mu 2014, koma a chipani cholamula cha DPP sakugona nawo tulo.
Malinga ndi chikalata chimene chipani cholamula cha DPP chatulutsa, mtsogoleri wotsutsa bomayu ati ali pa kalikiliki ofuna kuchita chipongwe Boma la DPP.
Mlembi wamkulu wa chipani cha DPP, a Francis Mphepo, ati a Chakwera agwilizana ndi nyumba zina zoulutsa mawu mu dziko muno kuti azifalitsa nkhani zabodza ati cholinga anthu aukile Boma.
“Akufuna amemeze a Malawi kuti apite kumseu akayambe zipolowe,” alemba choncho a Mphepo.
A Mphepo ati a Chakwera ali pa kalikiliki olengeza nkhani yoti Boma la a Mutharika linachita katangale Pogula chimanga ku dziko la Zambia.
Ngakhale a chipani cha DPP akukana kuti sipanachitike katangale, ma report anasonyeza kuti kugula chimanga ku Zambia panayenda njomba.
Zinamveka kuti Boma linagula chimanga pa mtengo okwela kamba koti ndalama ina amafuna achite chosolola.
Pakadali pano, chimanga chikugulitsidwa pa mtengo wa K12,500 ku misika ya Admarc. Koma akuti chimanga bwenzi chikugulitsidwa pa mtengo wa K5000 kukanapanda kusololedwa.
Akuoneka o chakwera amaenda ndi mdidi,mpake ena tulo sakutiona ndi anyau omwe!!!!
These DPP guys r talking rubbish ,just accept that u have failed to change the lives of Malawians not always shifting the blame ,leave chakwera alone just carry on stealing our money but be ready to face the law after 2019
We’re looking for investors and first registered user who the whole Malawi will be under.
Call/Whatsapp: +2348063160229
Follow this link to join
http://ultimatecycler.com/refx/signup/joshkeys
YOU CAN ALSO JOIN OUR WHATSAPP GROUP NOW
https://chat.whatsapp.com/D52cJjnvESPAfco96XGjXq
Facebook Page
https://www.facebook.com/ultimatecyclermalawi/
Ultimate cycler has come to stay and make our life better
Register with MK10,000 and get MK40,000
How it works:
Get 4 people and be paid MK40,000 as soon as possible
Get 2 people and get paid MK40,000 in 1week
Get nobody and get paid MK40,000 after 2weeks..
(Computer automatically merges u with 4 people)
Ultimate cycler…… The Real Deal……..I was doubting it before but now I am a witness….
Don’t be left out in this move for the betterment of your life.
Register with MK10,000 today and stand a chance of being MK2,560,000 million richer in less than 4 months.
===========≈=============
You join free and pay $25 (MK10,000) to the person nominated in the matrix, normally your 2nd level up, and you will have a spot in their 2 X 2 matrix. That is the LEVEL 1.
Get your 2, and your 2 get their 2 and those 4 people that landed on your pay line, your green zone pay you $25 X 4=$100 (MK40,000). Out of your profit, re-enter and follow your sponsor in his new matrix and pay the person 2 levels above you. As that matrix fills again with 6 people under you, you cycle the $100 (MK40,000) again, and again without limit, giving you $75 (MK30,000) profit each time you cycle.
LEVEL 2
You upgrade with $50 (MK20,000) out of your profits.
It is also 2×2 matrix.
As your downlines follow you, together with spillovers from your uplines, you cycle $50 x 4= $200 (MK80,000). Re-enter as you did in the $25 matrix. You keep profiting with the cycle of $200 over and over without limit, giving you $150 each time you cycle, which is MK60,000 net profit over and over and over again without end.
LEVEL 3
It is also a 2×2 matrix.
In the same manner, you upgrade to this matrix with $100 (MK40,000).
At this level you earned $100 x4 = $400 (MK160,000), giving you a net profit of MK120,000 over and over without end.
LEVEL 4
It is also a 2×2 matrix.
In the same manner, you upgrade to this matrix with $200 (MWK80,000).
At this level you earned $200 x4 = $800 (MK320,000), giving you a net profit of MK240,000 over and over without limit.
LEVEL 5
It is also a 2×2 matrix.
In the same manner, you upgrade to this matrix with $400 (MK160,000).
At this level you earned $400 x4 = $1,600 (MK640,000), giving you a net profit of MK480,000 over and over again without end.
LEVEL 6
It is also a 2×2 matrix.
In the same manner, you upgrade to this matrix with $800 (MK320,000).
At this level you earned $800 x4 = $3,200 (MK1,280,000), giving you a net profit of MK960,000 over and over without end as you keep on cycling. It’s noteworthy that all these business centers operate independent of another.
LEVEL 7
It is also a 2×2 matrix.
In the same manner, you upgrade to this matrix with $1,600 (MK640,000).
At this level you earned $1,600 x4 = $6,400 (MK,2,560,000), giving you a net profit of MK1,920,000 over and over without end as you keep on cycling. It’s noteworthy that all these business centers operate independent of another.
EARNINGS SUMMARY:
========================
STAGE 1.
$100 (MK40,000)
STAGE 2
$200 (MK80,000)
STAGE 3
$400 (MK160,000)
STAGE 4
$800(MK320,000)
STAGE 5
$1,600 (MK640,000)
STAGE 6
$3,200 (MK1,280,000)
STAGE 7
$6,400 (MK2,560,000)
Payments Can be done with:
Bitcoin https://blockchain.info
Local Bank, PayPal, Payza, Hand-To-Hand.
Click to register
http://ultimatecycler.com/refx/signup/joshkeys
Chakwera angobwerera Ku kacisi akapitirize ubusa
Inu mukakwera bus ndipo driver nkumayendetsa molakwika,anthu amayankhula kumene koma akamyendetsa bwino, anthu omwewo amakhala phe.Tatiuzani inu a dpp mukufuna anthu asayankhule pomwe zinthu sizikuyenda bwino?
Kodi inu munthu akati adzudzule kuti mwaba ndalama za chimanga ku zambia mukuti akufuna kuti akulandeni boma kodi mukuwona kuti amalawi akusangalala ndi zauchitsiru mukuchitazi musiyeni chakwera amutuma ndi amalawi osawuka osati inuyo mbabvanu ayiii.
Niggar akapusa alandidwa kumene
U see ea true colors akakhala pabwino
Dzulo ladziwa chilungamo chafika…amayenda ndi ndidi ….anamufotokoza
kkkkkk mcp.moto.kut buuuuuuuu
Kkkkkk a great weapon in 2019…. Ndimasikando a maize gate akumuopa eeeeeeeeh..
Ayambira pati kulanda boma. Mukuyesa nğati banja eti.
Nonsense boma amalanda ngat mango wait 2019 alandadi
I love mr Ibu , full of no sense like his supporters dddddpppp
nothing is wrong here ngakhale ku america athu amakambirana nkhani Za ndale
Chakwera woye tilinawenawe oipa akuopa yekha ife tilikhale oipa athawa yekha kkkkkkkkk
Kodi paja Afcon iyamba liti….
Chakwera akufuna kulanda Boma – atelo a DPP By Mwayi Mkandawire January 13, 2017 19 People You Won’t Believe Actually Exist ? A Lazarus Chakwera ndi kutheka anagonja pa zisankho mu 2014, koma a chipani cholamula cha DPP sakugona nawo tulo.Malinga ndi chikalata chimene chipani cholamula cha DPP chatulutsa, mtsogoleri wotsutsa bomayu ati ali pa kalikiliki ofuna kuchita chipongwe Boma la DPP.Chakwera akuti akufuna kulanda boma malingana ndi chipani cha DPP.Mlembi wamkulu wa chipani cha DPP, a Francis Mphepo, ati a Chakwera agwilizana ndi nyumba zina zoulutsa mawu mu dziko muno kuti azifalitsa nkhani zabodza ati cholinga anthu aukile Boma. “Akufuna amemeze a Malawi kuti apite kumseu akayambe zipolowe,” alemba choncho a Mphepo.A Mphepo ati a Chakwera ali pa kalikiliki olengeza nkhani yoti Boma la a Mutharika linachita katangale Pogula chimanga ku dziko la Zambia.Ngakhale a chipani cha DPP akukana kuti sipanachitike katangale, ma report anasonyeza kuti kugula chimanga ku Zambia panayenda njomba.Zinamveka kuti Boma linagula chimanga pa mtengo okwela kamba koti ndalama ina amafuna achite chosolola.Pakadali pano, chimanga chikugulitsidwa pa mtengo wa K12,500 ku misika ya Admarc. Koma akuti chimanga bwenzi chikugulitsidwa pa mtengo wa K5000 kukanapanda kusololedwa.
kaboma kake kati kot munthu mkumafuna kulandako? kkkk
Mwana Otha Kubela Mclass Ndi Wamzeru, Koma Umamuvuta Umakhala Ulesi.
Bodza Dausi
Koma a dpp sure amasowa zochita bust kuloza dzala malo mot alongosole zachimanga basi chakwera mwanti mwanti…iiiii for once use ur brainz
aaaaaa koma inuso mwasowa nkhani bwanji ,chakwera akulandani boma bwanji anthu akuba inu ,mudzigulitsa nokha chifukwa chaumbava wanuwo
Ndikanakondwa ngatizitatheka achakwela kutenga dzikolo ndikuwasiyila bomalaolo dziko linawasankha Amutharika Amutharika anasankha anthu ndikupanga boma, ndikuma zumza dziko kuiwalakuti ndiosangidwa chomwe amakumbukila ndikusankha, osatikusankhidwa kwao anayila kuti ndiosankhidwa.
Hahaha hahaha ana achepa !!!!! DPP matha mudikile 2019 tidzalandadi kkkkkkkk
Mwayamba kare kunjenjemera.MCP bomaaaaaaaaa
Owina ndi chakwera akudziwa kale abuluziwa
Anaba ma voti uyu ndi mbava
zikuwonetsa kuti mcp ilibe mwayi owina 2019 Mumkachita Kukusa Anthu ngati mbuzi kuti apite misohano yanu
Chakwera akaopedwe ngati chilipo cha nzeru chomwe akunena iye? Ndale zophunzirazo palibe chilipo cha nzeru ndipo sangawine amene uja. Angobwerera azikalalika uko.
Mavuto alipo koma osadanda 2019 pp woeee jb osati enawa zakha zitatu olo cholozela munaona bwanji pp
Boma salanda ngati akulanda chimanga chootcha zautsilu baxi,, mwayima nawo kangati pazisankho? Munayamba mwawinapo? Obvious mr APM dziko lamulephera koma tikufuna tifatse posankha munthu woti angazayetsese kuthetsa mabvuto athu” tikati mabvuto we mean kuchepatsa njala (1) chachiwiri malipiro komanso ntchito, jst imagine chimanga thumba likugulisidwa Mk12,500 instead of Mk5,000 what z that? Sono ngati inuyo Achakwera mungazakwanitse dzinthu ndanenapazi it’s fine u ar welcom koma musabwere poyera kumanena kuti mukufuna kulanda boma coz mukazaluza pamawa anthu azakusekani..
A DPP akusakasaka njira zoti aperekere boma mmanja mwa a Chakwera iwo la wakanika. Masitha defecters mulimo m’Malawi muno? Mwanoti ziii.
Chakwela ali mmazi. Ife ma vote tizabela ufune usafune mpaka 2099 wooooo
N’ndima umadana ndi kuwala achakwera yatsani nyali anthu aone kuwala asie kugona
Bodza ilo alanda boma bwanji a Chakwera? Atakudzudzulani basi mwati afuna alande boma? Kuvomereza kuti mwalakwitsa ndi bwino. Sindilikukhulupirira kuti mutamachita bwino angamalankhuleso mwina zomwe zikukuphetekanizo, koma ngati simukukhoza akuyenera kulankhula. Ndiye nanga poti si a Chakwera okha alankhula, pali a mabungwe komaso a Malawi ambiri akulankhula, tinene kuti onsewa afuna kulanda boma? Ndiye ngati zilichoncho ndiye chokamoni n’bomamo kuti a Malawi eniake ayendetse dzikoli mwina chipani cha DPP ndi cha anthu akunja omwe sakudziwa kuti dzikoli lili ndi achiyeniake amene amalifunira zabwimo dzikoli. Osati kuponderedzana ngati zomwe tikuzionazi.
Zitsiru zosowa fundo za kumwera zili busy zimvekere chakwera analephera kuyendetsa mpingo, komaso anaba za mpingo mulindiumboni? ati kufuna kumpezera zifukwa chakwera zazii, bibulo lake liti limeneli ?baibulo limati musawereluze ena, chiwerezo chili ndimwini wake mulungu.inu chakwera sioyamba kujoina ndale mwava? John chilembwe, Desmond Tutu wa Ku South Africa komaso papa tsogoleri wa roman Catholic amalowerera ndale.inuyo machimo alithoo koma busy kuwereza azanu .pathako pano nonse akumwera .
Chakwera hoooyeee peter is a stupid one he take the Government like for his family is idiot President in Africa
#Hanna tawauze manyasawo kunyasalako chakwela ndiwadyela kumene why anasiya ubusa kupita kundale samalani amalawi
Hahahaha
mmmmmmmmm abodza amenewo zoona munthu angaope chomuopa?
Zilibwino chakwera go forward usagonje ungolanda Boma chifukwa mbuzi ilipoyi singatinthandize more fire chakwela
Olo atalanda palibe chiona ine Dpp mbamva Za anthu
Chakwera malo mopanga za ubusa ukupanga zandale never kuwina baba bwererani ku Church and MCP is for John Tembo.
U must always remember cash gate err that blave woman robbed money. When Mlomwe and his cabinet entered DPP anapeza mulibe ndalama.Olo mutachenjera maka simungasinthe zinthu.5years ngati mulibe capital, zimapepuka zikakhala kwanzako DPP boma.
ZAWA LEPHERA A DPP
MCP Boma!!
Don’t stop giving them pressure, 2019 election you will be President. See how they are losing by-elections. It will be in the same way.
Chakwela uphawi wamukwana or atatokota sangazawinebe ata or pang’ono pomwe.
Uyu nde wanyamula vote yanga
Wandale Aliyense Ndiwakuba Ngakhale Chakwela Akadzalowa boma
Azaba Kwambiri Kuposa Peter Osakhulupilila Anthu Andale Ndipo Katangale Sadzatha Zapadziko Izi
Wandale Aliyense Ndiwakuba Ngakhale Chakwela Akadzalowa boma
Azaba Kwambiri Kuposa Peter Osakhulupilila Anthu Andale Ndipo Katangale Sadzatha Zapadziko Izi
Amalawi ndichan? mungotukwanizan azanu akupindurapo zopuxa
Zisandikhuze
Atayi inu awa
I have never seen boma la mantha like this one.Chakwera asatsokomole AAA iai afuna alande boma,asapite Ku maliro ayi wayamba kampeni iiiiii kma
Propaganda at its best
Kulanda kapena kutenga?
…feudalism is the only answer….POP-CORNiyo aziwabera akumwela omwewo, ife AYI!!!!
Kkkk, kodi anthu mukuchedwabe ndi andale heee mufuse nkasa, adanena kale kuti ndale mkanyama koipa
Osat Kulanda Ayi,, Koma He Is Taking What Is His,,,,, MCP Woyeeeee!!!!!!!
Osat Kulanda Ayi,, Koma He Is Taking What Is His,,,,, MCP Woyeeeee!!!!!!!
Chakwera ngati chipani chake chidamkana,….mukuganiza angalamule ndani?
we dot want x 2 b presdnt but we nid changes so that we live haply.we dot hate apm nor dpp bt the way economy is.unless u tel us that things are ok,u cant tolerate it.may b problems rocking the country do not affect ppo who r strong dpp sapotaz.
A MCP , mulipo ? Kkkkkkkkk
Guys chiyambireni cholemba nkhani zonyoza atsogoleri azipani mchiyani chinasinthako panganizanu ndimabanja anu or mutakhala inuyo
Boma Lake liti? A Chakwera ali anthu oti nkulanda Boma?
Nthawi zambiri anthu amasokonezeka pankhani zandale chifukwa cha News paper ngati panopa malawi24 ikuonjeza bodza musinthe
Bola Alande Dziko; Osati Bomalo
what I observed is that politicians are lyk football clubs officials,they only being angels on opposing once gven a chance of ruling nzeru zonsezija ng’ooo.
mwayamba kunjenjemela? 2019 paulendo
Chakwera ndiye mbava yeniyeni.lnu anaona kuti chopereka Chimachepa ali koma ndikawone kundale.guy osachita mistake .Osaiwala anagwa MMANJA mwamulungu ndi jabulosi uyu mph wake wauja anaismpusisa Hava uja.
Koma a DPP akudziwona uchisiru wawo, ayamba mantha tsopano akudziwa kuti Chakwera atenga boma pavute pasavute. Musanati DPP ndiya zisiru zokha zokha.
Ka amalawi
Munasiya Ma Bible Ukooooo!!! Nde Lero Mwat Mupange Ndale!? Komwe Uliko Chakwera Umve Kut Mulungu Wakwiya Nawe Ndpo Boma Lino Sudzalamulira,pomaliza Mutu Wako
If you didn’t vote for dpp you must just kip quite mkut dpp inabela mavotes pomwe ineyo ndnavotela dpp ife ambritu tinaivotela but the problem comes when you see that agalantia sanawine aliyese anavotela chakwera analuza sungamat ndewu ija sinaluze komano ndmangofuna mtendere that’s why ndavomeleza kuluza don’t lie to ppl when you luz u luz don’t expect to win when you gatta pikinin supporters DPP ND BOMA
Mukuti chani kodi inu
Iwe wamva chan?
Kape Iwe
Iwe nde mbuzi ya munthu
Hahahaja♡♡♡♡ is unique baba u cannot say mbuz ya mnthu pomwe sukuziwa kut amene Ali ofuntha ndamene amayankhula Anthu abwino kut”””” awaso ndopenga
Looks like you’ve got shit for brains
Looks like you’ve got shit for brains
Looks like you’ve got shit for brains
Mukumuopa Chakwera,Abusa sangalande boma,koma inu a Dpp zangokuvutani basi.osati mumupedzere zifukwa zoti mudzimumanga munthu wa a Mbuyeyi ayi.Musamusokonedze musiyeni munthuyi..
Awa achakwera sangakhare papando komanso ndikaona mavuto akulu ndiakuti unsongoleli wakakamira kumwera dzikumanyasa chifukwa pa dzatenga nthawi kt udzafike Ku chingawo chapakati.kuti udzafike chingawo chapakaki ayembekedzere dzaka 27.kunsongoroku osati pano mukalambira popo achakwera pa otsawoo ndiye pando wanu.achakwera osati oramura dziko never.
We r the MCP’s pambuyo pa Achakwera nganganga mulira Xeni-zen
chakwela wafika ponyada! ganizo lake ndilofunadi kulamulira boma! koma ndikanakhala peter sindikadalora wotsutsa azinditcha “patient/,olephera/mbuli yophuzira’ ndithudi akadandiva!! kwa ine chakwela mchitsiru,galu wa munthu,bwanji safuna kuthandizapo ndi zelu zofuna kuthana ndi mavuto we’re facing,bwanji sathandizapo odwala azipatala,koma kunyoza basi! zauchitsiru basi!! nanuso amalawi24 simulemba nkhani yoyamikira munthu,koma zomwe wina wanyoza boma basi! why? even mundi blocky vuto mayazi koma nanuso mumachita zauchitsiru! ndikadakonda nanuso mutakhala gulu lotsekedwalo.ndamaliza!!
Kapeni inantha kale inu achakwera cholinga chanu mukufuna mutinthamangisire anthu amene akutinthandidza osati kuwaunikira amalawi.mukudziwa kale tengo umene boma limangulira chimanga.ubuli achakwera nanu munali mutaba kale dzapingo.2019. Munsowa dzopangira kapeni ndalama.
Cardiac arrest redeemed us from dictatorial evil Bingu, another cardiac arrest is very soon going to redeem us from these evil walking dpp leaders, God is not Peter Mutharika or Chaponda. Just wait, cardiac arrest is looming
chakwera ndi ntondo angozo enieni
Ine ndikuonanso KT chakwela ndiye mbava yeniyeni inu taganizani mozama komanso yamban kupenya patali munthu kusiya kutumikila mulungu,kusiya nkhosa zamulungu ndikujoyina ndale ndiye mukuona kt ndichanzelu? Amalawi azanga mwatan?bola mbava zomwezi
Ameneyo ,chisiru mbuli yachabechabe, kulanda boma aona ngati kulanda munda eti ,CHAKWELA chisiru kwa baasi.
Ameneyo ,chisiru mbuli yachabechabe, kulanda boma aona ngati kulanda munda eti ,CHAKWELA chisiru kwa baasi.
Savage
U who is savage, savage ndi iwe ndi chakwera wakoyo ,akanakhala ozindikira akanapanga mapulani oti azawine 2019 osati kulanda boma, mphwanga ukalimbana ndine ,uyithawa MALAWI.
ayamba kale kunjenjemera…sakufuna kulanda boma timvetsetsane koma Ibu akufuna kulanditsa yekha boma..kwacha
Kkkkllllkkmmkkk ndakomoka
Mwayamba Kale kunjenjemera? Kkkkkkkkkkk
Matenda avutawa adafalisidwa ndi #MCP amene amaumiliza kugonana ndi aliyense pogwirisa mphamvu za chipani komanso #Chakwera analephela kusogolera mpingo ndi azasogolera dziko lake liti?
Matenda avutawa adafalisidwa ndi #MCP amene amaumiliza kugonana ndi aliyense pogwirisa mphamvu za chipani komanso #Chakwera analephela kusogolera mpingo ndi azasogolera dziko lake liti?
Matenda avutawa adafalisidwa ndi #MCP amene amaumiliza kugonana ndi aliyense pogwirisa mphamvu za chipani komanso #Chakwera analephela kusogolera mpingo ndi azasogolera dziko lake liti?
Ok we are watching
Peter mutharika ndi proffesor wa mkalasi osati ku ndale,utsogoleri ndi mphatso yochoka kwa ambuye osati kungogwera ayi,munalowera pawindo lero mutulukiranso pa windo
hahahahaha mwaba nokha chimangacho. Zangokubvutani. Musiyeni Chakwera. Sanakutumeni kukaba chimanga cha amalawi.
muziti chifukwa chosaziwa ntchito a DPP akufuna ku zisiya okha!!
guys do your politics am never voting again,, to hell with malawian politics you make the country look stupid but God is watching you.
Its better the devil we had(MCP)than these so called saints we don’t know!
Chakwera is a failure.who can put him on presidency. He failed to lead 200 people in his Church. No wonder he is failing to lead MCP .Lo a country; Malawi; with central region only. Forget .stop dreaming in vacuum.DPP woyee 2019 motomoto.
you are a big failure too,more than wina aliyense,you a real blind bat,ndiwe cadet wa dpp eti,party full of madeya,zigawenga,mbava,mahule including u
Nyote wajinga2 hamjuwi mnachokifanya pumbav zenu
we are behind opposition, mbavazi tikumana nazo 2019 ndipamene azaone kufunika kwathu
Fwetseke…vitsiru va diphi phi…vidempete vachabechabe…anthu oduka mitu
Some tyms a malawi 24 amalemba zinthu zopanda meaning,what they tryng to tell the ppl of malawi????
Kkkkkk kayatu pamenepa bwiyache che Mangani tafuseni ndinu
Dr. Chakwera Bomaaaaaaaaaa!!
Osanama Boma Ili Latikwana Heve Angakhale Boma Ili Likudziwa Kuti 2019 Lili M’madzi Amalawi Onse Amadziwa Kuti Boma La Malawi Lidagula Chimanga Ku zambia Mwakuba Kusonyeza Kuti Chimanga Chomwe Chidabwela Kuchokela Ku Zambia Ndindalama Zomwe Boma Lamalawi Limanena Kuti Lidagwilitsa Tchito Sizimayenelana Ndalamazo Zimachuluka Pomwe Chimanga Ndi Chochepa A Cham’kwelawo Sakunama Boma Ili Linabadi Ndalama Za Mondokwa.
Chakwera is the most stupid person in Malawi coz he failed to take the government through ballot paper. i Dont think he can take the government through any means. He must be kissing his anus……
kwacha?
dpp woyeee!
Anold kachimanga don’t behave like a savage insulting pipo and using obscene language
You are the most stupid and foul mouthed mbuzi on this page. Yea, like all dpp supporters. Always clapping hands for mediocrity
mr jumbe u are also very stupid including your mother and father. i have believed that writing words like this is not good but this is being promoted by mcp supporters who are fond of insulting the leader of this country by doing this. lero tikamabweza muzikamba zambiri. Go and read what mcp supporters have written on this page. Tonsefe sife a mcp and mudziwe zimenezi. Inu a mcp mukatukwana ntsogoleri wathu wa dpp ifenso wanuyo tizimutukwana agalu inu.
mr .lockshana, thanks for that am not like that. mcp supporters should behave well inorder to avoid this.
Ndimamva chisoni kuona anthu mukukangana nkhani zokhuza agalu andalewa taganiza ndi mtsogoleli uti yemwe analowa m’boma ali osauka ndikutulukamonso osauka? Ndiye muzifunse why, kapena chikuna ninji aphungu athu sanayambepo akana kuti musationjezere malipiro nthawi iwo tiyambe takonza za mavuto ali mdzikowa?
Kho kho kho mau Mfumu yanga mwayankhula.
koma ndiye
Dats de fact,timangotaya nthawi yathu ndi za ziii
Munthu wamkulu,ena angotekeseka naye kkkkkkk
Its a time for DPP to rule this country ngat muli ndi milandu khani ndi pa 2019 election bas ngat azalowe enawo tizaone ngat azathetse mavuto M’Malawi.
You are a real blind bat,very very blind so that you cnt see beyond ur nose
Its a time for DPP to rule this country ngat muli ndi milandu khani ndi pa 2019 election bas ngat azalowe enawo tizaone ngat azathetse mavuto M’Malawi.
Choka cadet iwe kasute chamba
Nkhani ya chakwera wanuo imandinyasa kwambiri anakanika kutumikira nkhosa zamulungu kuli bwanji kutumira dziko? Chimu2 chadyera ngati chimenechi ndipo akungovutika ndikubwebweta sangawine ataa!!
Chizimai chidzimawere zikuluzikulu kumakamba zopanda zeru, iwe ndiwe ulungama?
kkkkkk this is funny
O Ooooo Zamwe Mungandiuze Nthuni Inu Tsanotu M’mepa Nzongoonetselatu Kuti Ochakwela Oludzatenga Boma 2019 Komasotu Odara Ochakwela Sodaname Boma Iri Its Verry Hurd Kuba Odala Olutibela Olukapondeleza Kadziko Koomalawi Tsanotu M’mepa Okadapanda Kukhalako Mavenda M’mewa Dalatu Oma Admarc Om’mewa Okadati Gwirililatu Tikadasowa Kothawila Koma Oma Admarc Om’mewa Okhaula Ochimina Odziwaso Anya Awona.
Chakwelayo kulanda boma, alimkanthu monga
Ndiwe cadet eti,pitani mukatenge zikwanje
baaaaaaaaaaad
Bodza ili, Chakwara can not descend so low kufika polanda boma mwangosowa chonena inu.
Malawi poorest country in the world
Zilibwino kwambiri
kawirikawiri munthu amadana ndi chilungamo. Aboma mulikuba koma musatiopseze ai. makamaka chaponda mbava aDPP nose shem. chakwela sakulakwa vuto ndinu. Zodiac sidalakwe akukamba zoona, boma lakuba shem!!
Dpp mmmm failures
Face him, why fearing him?
Tangowapasani achakwerawo ayendese dzikoli palibe zikulongosoka pa mw pano bola nthawi ya masten ija zikaonesa
Palibe kanthu ndipo zikhala bwino kwambiri
Dziwani izi amalawi anzanga mungovutika ndikubwebweta za Galatiya uyu mukuti chakwerayu ameneyu oro zitavuta mpaka sangatenge boma la Malawi ndipo sadzalamulako mpaka kalekale ufuse John tembo bwino bwino .Amene adzalamule dziko Lima Ali pheeee inu simukudziwa munya muona tamangosililani ulamulilo wamzanuo ng,ooo
uli mgulu loti people from other regions will not rule this country just wait and see how thing are turning out to be its not about comming from densely populated region but what you achieve for the majority remember what David did to Goliath
sine mmodzi mwa io ndati mungiti phee muone
Iwe Frazer David anali wosankhidwa wamulungu pomwe cakwera wakoyo anali wokuba zamulunguzo
kwacha??
kodi iwe freza mutu wako umayenda bwino despite it has no legs upite kumento ndakuuza kale chakwera ndi Galatia anayamba zabwino akutsilizila ndizoipa waba iba za mumpingo pano akufuna kudzabaso za boma la malawi komatu ayaluka
thats de point man,idont think mcp will rull dis country again,zowona ndithu agalu a mcp kuthamangitsa azungu kenaka mkumawapemphaso,bwezipano malawi alipati
BINGU AMENE MUMAMUTI WANZERU ANATHAMANGITSANSO MZUNGU .
kodi dzikolo likuywndetsedwa ndi Bingu kodi
Comment Yausilu Mwachitayo , Kodi JOHN CHILEMBWE sanali m’busa?
unamuona kapena unangova history
bola Atalanda chakwerayo basi nanga pali chime chikuchitika apa?
Wabwino ndani kudziko kuno?
JUST CHANGE UR STYLE OF LEADERSHIP,STOP OPPRESING THE POOR, DO WHAT IS RIGHT PALIBE AKUFUNA KULANDA BOMA APA PPLE WANTs JUSTICE TO PREVAIL WHY R YOU STIL KEEPING THAT TWO FINGER CHAPONDA?
a Malawi panopa azindikira sazaperekanso zaka 10 kwa President kuti alamulire dzikoli,,,,ndi Bakiri yekha yemwe anakwanitsa zaka ten,,,Bingu zaka 8,,,anamuchotsa ndi Mulungu pa mpando a Malawi atakwiya ndi ulamuliro wake mu term yachiwiri,,,Joyce Banda zaka ziwiri nayenso atangotsegura loko anthu kunali kuba ndarama ku likulu la boma,,,anthu anakwiya naye ndipo sanamuvotere amene anajijilika kumuvotera ndi omutsatira akewo,,,ndye awanso a Petulowa mukumva kuti zachitika,,,,koma 2019 sadutsa
Kodi munthu kuzuzula ndikulanda boma..
i hate politics . had to say it
Zoopsezana zidatha nthawi ya chipani chimodzi. What is wrong with the leader of opposition when he opposes? If ordinary citizens are opposing, what do you expect the “leader” of opposition to do? Do not think you will be there forever. TIME WILL TELL. Dphwiphwiii chipani cha mbava, zigawenga, the failures.
Haha #Chakwela amphawi wamukwana bola dpp kaya mukut ndiakuba bola tizitukuko tao taziona olo atati achoke lero titha kuzilodza nanga Chakwela olo atati wafa lero muzaloza kut wakupangilani chan agalu inu? Mcp ndmaipasa ulemu ndkamamva za #Kamuzu osat ana onyela nyelawa aka #Chakwela zazi dikilan muonenso dpp ikuwinanso kachikena cz #pp inatha #udf inatha #Mcp akungokanganamo okha okha mpaka kuotchelana ma galimoto bcz of Chakwela ndye mukuona ngat Mcp ingalamulire dziko lino Kkkkk mudakalirabe pepan
u should be talking of DPP vs MCP not Chakwera vs DPP rather pitala vs Chakwera, pitala wapanga chani choti tizamukumbukire?
Dpp ili under ndani? Dpp ikamalakwitsa anthu amalodza chala ndani?
Pitala Wapanga Chitukuko Chokweza Chimanga Ndi Kuba Chimanga Cha Zambia Ndikubisa Chaponda Nanga Magetsi
Tatchula zomwe wapanga mdala wako wopanda manoyu ali mboma tiloza bwanji za chakwera ngt analamulilapo, umbuli osamachita kudzitsatsa osamangokhala osapanga cmnt bwa,kkkkkk km enanu kuvetsa chson
Pitala pazaka zitutu wapangapo chana kumangobela anthu ovutika basi
galu wamkulu ndiiweyo..Chakwera analamulira dziko lino liti kuti tikaloze chitukuko chake..Ibu wakoyo nde palibe 0 weniweni akungotisaukitsa ali pheee galu nzakoyo nonse ofunika chain
Chakwera citsilu camunthu azawina kwawo komko but never in the south !! Mcp inatizunza kwambili kumwera
takulani a malawi,mcp ya kale ija inatha,alipowa ndi anthu anzeru zawo ndipo sangabwerezenso zakale zija.
Komaso bola nthawi ya MCP yo timazuzika mukutero koma cilicose pamoyo Wa munthu cinali bwino talk of cakudya ,maphuziro, umoyo, magetsi in short zonse zinkayenda nanga pano
Haha ndzakupasan ulemu nonse amene mukunyoza dpp mukazafa ndiamene ndtazaziwe kut mdziko munodi mulinjara nanga munayambila kudandaula muja simukufa bwanj mpaka pano mulindizizukulu zanu enanu mpaka mwakula opanda chilema ndye mavuto ake ati mukuwanenawo zaulesi basi muzipanga maganju ngat ntchto zikusowa or mumuuze #Chakwela wanuyo akulemben ntchto yosesa zitosi za #tambala wakuda mumvekere kwacha ! Kwacha ! Ndye mukudandaulanji mesa kumalawi kwacha kod Kkk bravo mr #Peter #Muthalika ziko lilibwino kale ili but akufuna kusokoneza ndi awa a #Chakwela anathawa ku lalikila mu church pano akutukwana presidnt aneneri onyenga mumakwana mr ka Chakwela go to hello wif yo fuckn cheap pussy party well knwn as #mcp
Kkkkkkkkkkk koma mantha ake
Zanu izo ine ndiri bzy kugwira ganyo
Mmmmmmmmmmm pezani zina zokamba kkkkkk
Kape,mchewa ngati ameneyo tinamukana kalekale mu 2014 muja alibe ntchito akulira ndi mtima,Boma ndi lathu ili tizingosinthana ku south konkuno.
Ndiye osamatibera misonkho. Tisiyeni a Chewafe tizidzilamulira tokha. STUPID!! ukungoyankhula ngati ukunyera.
Iwe ndi mtundu wanji wa munthu,ukunyoza mchewa, kamuzu anali ndani,iweyo kuda kumeneko uli ndi mtundu iwe
Patrick wanena zowona ase no mcewa kulamulira Malawi again . Tizingosinthanadi
Pathako pako tachionani kunyasa ngati pitala
Chilungamo mchimenecho ngakhale mudane nacho,palibenso mchewa kulamulira dziko lino come 2019 Chakwera wanuyo tizamunyenyanyenyanso.
Chokanipo makape inu a DPP zisiru za anthu tatopa nanu bwanji mngosazika ngati zakulepherani ndi Nyapapi wanuyo
Dzna lot ibu or bwampn, limandmvetsa kukoma. Kutengela nd mmene mwn dznalo akuonekela.
Kkkkkkkkkkk
DPP SIKULABADA ZA ANTHU
Driver akamyendesa basis mwausilu atha kuphetsa anthu,alandidwe stealing ena ayendetse anthu akhale moyo. Ah sinaone bama lonseli kukaopa munthu mmodzi. Nanga akazayamba ntchito limodzi ndi manganya si ma bp,ena kubibidwa ngati nthawi ya treason case ija.aaaa. mwinadi mavoti zisakho zapita zija kalipokalipo kanachitika kwa chakwera.nanga mantha amenewa bwanji anthu asyankhule basi mayooo mayooo.
A malawi24 ndinu abodza munatinamiza kuti the president is going to conduct a rally in nsanje on wednesday apa mwanamanso i can see politicians driving u. Paja munthu akakutsutsani u brock him ngati afriem brock me.
as we draw closer to 2019!
mantha boma, kkkkkk. maulemu kwa Chakwera, man akuchokitsani, keep on fighting for us
Ayerekeze Awone.
c
U are failing to get inner peace because of the maize u steal. For show you will lose come 2019.this is multiparty democratic nation. Why u always want to silence a potential party. We are sick of your games. Kachipani kaanthu akuba
Nawo adpp ndi manyaka bwanji !! Wy kumalimbana ndimunthu oti he wont b president az long az our voting system will still b based on majority rule ? Kodi mesa dpp comes from komwe kuli ambiliko ?? Mlekeni azawine kumpoto ndi central kwakeko !! Kwawo kwa mcp dpp izizapeza mavoti koma iwowo kuno ndi zero chitsanzo ndizisankho zinacitika zama by election Ku mcinji zomba kasungu pomwe dpp yapeza kukasungu pomwe kuzomba mcp zero . The same with mayor elections !!
this time no chance for ur DPP
Adzakhumudwa a DPP 2019
Tizakhumudwa Ku central region kwanuko !! More over Ife adpp sitikhumudwa but u & u always cry kuti mwabeledwa . Do u think kuti southern will overwhelmengly vote for mcp ?? Kodi chisankho ca by-election simunaciwone mene cayendera ? Ku zomba mcp yapezakotu zero then look at kasungu the home of mcp dpp yabwelakotu ndi khansala !!
DDP is full of bunch of fools
dpp Boma
dpp chilungamo
dpp chitetexo
galu mukamamuyamba alipachean musamaone ngati saluma,muchenjere kuti akangodura pacheani muchotsedwa akatumba samalani a APM mwakhala pang’ono ndondocha zanuzo ziuzeni tatopa ndikutibera misonkho yathu agalu inu
Sanagonje Ibu wanuyo anaba ma vote open your eyes my fellow Malawians some people are not born leaders but you force them to be a leader Ibu has failed malawi is seing a danger warning signs
Mawu kachingwe ?
Mbuzi
A Kachingwe mwayankhula zeni zeni. Ati inu Mbuzi, pamene iyeyo ndiye Mbuzi ngakhale Standard 8 sanayione….The most Stupid dpp Kadeti boy! Kusapota zimbaza zi Amalume ake kkkkkkk
Agwape inu munya muona 2019 boma Dpp woyeeee mukudza liwende chaka chake chino
Hahahaha God bless you
Also u be blessed mmene amkabera iye analikt ndiye tuloto timeneto ndale sitipanga tulo tili phaaaa ngati ukulandira chachikhumi
koma aMalawi amvekere munya 2019 DDP Boma woteroyo ngakhale K500 ku account yake kulibe kuli zero zero, mind your business ngakhale ku mwalira lero aDPP wo saziwaso kt m’modzi waife no more
Ibu the president doesn’t know anything zomwe amalawi akufuna a big puta president
Kkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkk
Frasher Kachingwe I think were a baby when people voted in 2014 thats why u don’t know who won the elections and don’t allow the politicians to misuse u just work hard to earn a living FULL STOP
Welcome to africa the darkest continent of earth shaped like a question mark
Welcome to africa the darkest continent of earth shaped like a question mark
Odyazake Alibe Mlandu, Mchifukwa Chan A #dpp Mukunjenjema?
Peter apite basi 2019,iwe ukoona ngati ndi kutali. Uwona!
Achita bwino
Mulira DPP tizawinaso 2019
Are you still blind
2019 Dpp boma
Uli blind ndweyo,Chakwera anatukwana Mulungu sagawineso
Koma mbava za DPP osanama zafika pakuba mwa uchisiru ndikwabwino kusiya kut ena atenge ayendese dzikoli. Ndikunena pano Britain yapereka 193 million pounds yot achepesere umphawi muziko muno koma ayi ndithu akuluakulu athoyolera ndalamazi mmatumba awo kutisiya anthufe tikuvutika.
Nsanene nkhan ya ndalama zomwe chaponda akubazi linaperereka ndi dziko America kut agule chakudya ku Dziko lino koma Zachisoni ndithu waba ndalamazi . Anthu kut alembe a nkhaniyi mukusekanso pakamwa choona chisaziwike shame Peter Ndi Anzakowo bg up Times news
Umakwana Chakwera
Ndikwambwino chakwera atenge upulezideti chifukwa ntchito za mtsongoleri wa a peter sidzioneka katangale basi
Azafa osadwala asamale
Iwe unafa utadwala?kkkk anakuyika kuti
Akufuna athawise nkhani ya chimanga anthu azikamba imenei nde munyeratu!!!!!
I think this handsome man gives sleepless night to Dpp
akapusa alandidwa adpp chifukwa adpp achulusa zibwana zakuba
Anthu ochita zamdziko ndichoncho basi kukanganilana zapadziko cholinga choti alemere nd misonkho yamphawi kma anzelu akulimbirana ufumu wakumwamba ndipo ochita chamuna akuwupeza ufumuwo
I thout uyikapo ka verse…inunso
Boma2 simasewera! tangoyimanipoyera muwuzemtunduwa a Malawi kutimwalephera,anzanu akuthandizeni,basi!
That’s a welcome news to us chakwera better do it fast
DPP ikuthawa chithunzithunzi chake chomwe , 2016 inayenda moyera , yapondereza a Malawi , yapha a Malawi ndi njala , yapha mabizinesi a Malawi. 2017 ino iyembekezere zokhoma bwana weniweni aoneka kuti kuti , kodi ndi iwowo kapena ife timkapita kukawasankha pa mavoti . Chakwera asadane naye chifukwa akulankhula zofuna a Malawi .
Kulanda boma losauka ngati ili ndimavuto ndithu
Dpp Ali nje nje nje cz of chakwera especially cz they known kuti Ali pampando wokuba from chakwera yemweyo so sangagone naye tulo.dpp mwayaluka
Dpp Ali nje nje nje cz of chakwera especially cz they known kuti Ali pampando wokuba from chakwera yemweyo so sangagone naye tulo.dpp mwayaluka
Anamubela cakwera ? North vote for amayi central vote for mcp & south vote for dpp . Therefore the region with high population z south so hw cakwera who come from minor region b the winner ? If dpp comes from north ur comment would hv make sense
Anabera y mbendera amalira?y amakana kuwerenganso votes and all computer systems hacked thru chilima.u u dont know??? Why akumusemera stoty yoopsa they want ti do treason like they did with casm chilumpha???? Evil pitala and all dpp followers,cashgaters.admarc maize gaters.shame
All those illegularities anganene ndani kuti dpp inawina? Whre in the world munthu amawina ndi 36percent meaning 64persent sinamuvotere.ask pitala will tell you kuti anabera
Eeeeeeh kkkk a boma akudera nkhawa ndi munthu wa opposition kkkk
nde sanatitu
Kulanda boma lake liti?
Mwina kapena ku Malawi mkukhala nawo mbili zolandana boma.But i wil wonder if that happens,MCP has a lust for power since it has been in opposition for 20 yrs now
ASANGOFUNA KOMA ALANDILETU ZIKHALABWINO.
Bvuto ndilakuti olamula amene alopowa akumuopa chakwela, sizoti azinena zomuyipisa apa n for the way i c its btr one party system timadula makadi ndipo ndalamayo imagwila ntchito zotukula boma than this pipo who are full of corrupted. Pa umoyo nthawi yomwe ndimakula ndinalibe maganizo ozagwila ntchito mayiko akunja koma the way things are it made me left my blvd country. Koma ndimene kwacha ilili panopa olo Mwana wokwawa akuuza zopinda kunja shame on u bingu leave chakwela alone
Kkkk man mwalalatatu kkkk shaaa
Ndili ndi history kwambili when it comes to my blvd malawi, that’s i get pissd off when i read what is happening. I was supposed to b back last year already from this underground of mine bt i always get dissatisfied with DPP
wakamba zoona man mbava izi zikuonjeza
Ofunika kwauza ndipo zomwe amati tisiye kulankhula pa social Media pokhuzana ndi president aaaaa chilima what ever u call yrself we are not stupid this where our voice will be heard. Let’s 2lk guys wat we want thru media
mfundo
Kkkkkkkkkk Kamuzu ndiye akanaletsa Multiparty.kuti isalowe ngati analidi ndi mphamvu.Tsoka mphamvu zinatha ndi Mabishopunso aaaaaaaaa sakanachitira mwina koma kuviomereza.Ngakhale mbali ina amakana komabe zinali zosatheka Malawi waipa basi even akubwera kusogorowo mbava zokha zokha yayipa dziko basi.Ife bola kuno ku SA tikuchita ngatiko ndi Randyi tikatumiza R2,500 ayi ndithu K120,000
Frazer wakamba zanzelu komano ndiangati amene atakwanitse kuti abwele kumayiko amene enanu mukukhalawo, ndalama ya passport yokha panopa ndi plot yonse yamakolo ako kuyigulisa nanga transport kokafikila ndim’bale yemwe alibe life is hard brother. Ingochoka DPP tione zina basi
Go deeper mafrnds
Fact
gk unt0ta dmtktha wn tjadm, aadtw
Sukunama sizapafupi munthu kupeza passport ku Malawi
Analikuti nthawi yonseyi? ndikuona ngati chatsitsa dzaye kt njomvu itchoke nyanga ndi kuba kwa ndalama zomwe a chaponda aba za maize gate. boma liri ndimanyazi kt liyaluka zangoyambika chabe zazikulu zikubwela bingu unatisiyila mamvuto nane ndidzafa kma boma iri lanyanya kuba…
dzikoli ACHAKWELA akuitenga ngt ndikumozambiq et??? zakunyelo basi Ndale zkusokoneza kwambili ndichfkwa chake mwatulusa k2.000 ya solid kupusa basi…
Kulamulilidwa ndi agwape ndi vuto, kodi amakagula chimanga ku zambia ndi chakwera……
Zinthu zakusokonekelani mukufuna muone ponamila.
Boma lake liti? Palinso zoti pali boma apa.
Zayenera kutero ndipo tikuthandiza chakwera kulanda boma
Mapadzi angangako kapolo iwe
Mwana wa hule Raphael usalimbani ndiine oshosha yolakwika
Zaziiiiiii
Kkkkk
Koma apa dpp mantha basi alibe zida uyu koma Chauta akunva kulira kwa malawi
Can someone shut up here
Mmmmmmm thats nonses
Atalanda bolani, boma ili liri mmanja mwa chitsiru
Mmmmm
Nyapala inu mukuwona ngati tizakuvoterani Ife aku south ? Majority will rule Malawi forever and we the southerners we r in majority
Sitsiru zimadziwana zochita iweso ndiwe mmodzi mwa iwo
DPP has always had insecurity issues.
Fuck Malawi24 ur backing up this Gvnment so much I’ve never seen u publishing good stories concerning Opositions
Kkkk koma Ndale yavuta apa 2019 kuchedwa ine
Boma lake liti? Boma lomweri la Chiradzulu lomvetsa chisoniri
Yes if u continue to stl our money u wll s in 2019.Chaponda stl alot of money 4us and people nw dying bcz of him.Wat kind of leaders is this?.
CHAKWERA NDI MKANGO WA MALAWI ALANDE BASI