Malawians have been made proud by 24 year-old Lusekero Mwenifumbo who has graduated as a pilot.
According to authorities from Malawi Airlines, Lusekero completed her aviation training in Addis Ababa, Ethiopia.
She joins Captain Yolanda Kaunda, another female pilot who went through the same path years ago.
“Women can fly Malawi Airlines together let’s promote our women and girls,” reads part of the statement made available to Malawi24.
So proud
Remembering our own Felistus Matengo the daughter of my Headmaster at Mchinji Sec. School now Magawa.
proud of u Lusekelo, ngakhale ulamulilo umapita kum’mwera ndipakati, koma aaaaa!!! tikuyesesa mbali yathu pa nkhani yamaphunzilo, nafeso tikutukula ziko, keep it up Lusekelo mwatifyulako soni.
So proud of her
Ok gd move bt ndi zakumpoto
Keep it up girl…
Haaaaa everybody be like my sister
But some of you belittled her dreams dont forget that
Cpngrats
koma mesa tili ndi ndege imodzi kkkkk anyaway thats grt
woooow that incredible
Nc 1… Proud of u mwana wakwithu…
I fly an Emirate Airbus 380 but from south none ov say nothing mmm Malawi
That’s great.
Even alimfana wayendetsa ndege zaufiti nthawi yayitali,sindikuonapo chachilendo… Congrats mama
Congratulations!
Proud of you
The first was Felie Matengo Mkandawire, second Yolanda Kaunda, this one is third!
Actually first was Veronica
Veronica who?
Foy
That name surely can’t be Malawian. Tukunena anthu osati azungu lol
Congrats..!
Yolanda Kaunda si mtumbuka
ku Malawi ndege ndiye Anagulitsa kikiki
Congrats. Is it about regionalism. Akanati zonse apangira kumpotoku bwenzi pano ali kuti. I can only see her akugulitsa mtedza pa jenda.#stopthisaboutnorthenersweareone
Do we still aeroplanes there or abwera azasake ntchito kunja kuno
Mmmm kaya zake zimenezo koma sangayendetse Galimoto coz ndege ilibe revers
Malawi is proud of u sister u have done well for urself and the whole country congratulations
Congratulation dear all the best
Ok,poti ku Malawi Ndege ndi imodzi.Kaya sanaigulitse
Ahe bane am so proud of your little girl may the lord keep blessing her you have done well
Congrats first dayz udza fly mu M1 nsanje 2 chitipa
Is she a Tanzanian , coz her name sounds like a Nyakyusa from kyela , Tz
Nop…..our own Malawian…Daughter wa Hon Frank Tumpale Mwenifumbo uyu…..Karonga’s finest
Thanx my brother to let me know that
Nic job
Ndaonera nkhope ndi mtumbukadi munthuyu kkkkk
Kulima fodya basi chitumbuka mpaka kukwera nacho basi mpaka pretoria
Tione ngati akayamba ntchito azikhala kumpoto kwanu kuthengoko.ntchito kupanga zitukuko mzigawo zaeni.musova ndi kutchire kwanuki
Atumbuka ndiye zisilu zonyngedwa wamba apa matama ngati wanthu eni eni
Atumbukatu apa mwagundika ma nonsense vuto ndi chani kodi??????
All we are Malawian
All the best !!
Conguratulatio Ccta proud of u mwaaa
Congrats kalonga lady
Kodi enanu ma comments anu ndi otani pilot sanyengedwa kape iwenso eti
Nzolembalemba
Congrats young lady.
Gud vuto la amalawi jealousy timva walodzedwa
Ngozi ya banoi eeeeeesh imandiopsa kkkkkkkkkk
Weldone Karonga girl
Happy for u ccta,,, God bless u!!
I smell,cashgate and maizegate here,eishh my Nyasaland.Nkhalambazi koma kuba ambuye tawatengeni musachedwe atiwonongera Malawi
Malawian north woman will fly us even though we dont an airport in the north. Proud of you!
ZAZIIII NORTHENERS NDE KUTI CHANI
Mmalawi, muli anthu ambiri ophunzira, koma agalu ofuna kumangoponderezanawa ndi amene amantchukitsa kuti dziko LA malawi ndilosauka. Osati muchite nsanje apa. Mwana watichosa manyazi uyu.conglats dear sis
thats nice
wow!! that’s wonderful, your achievement has put malawi on the map, that we can do the same as they do
north nd dhiluuu mwenefumbo mul nd funso its time to make our own govt we don’t suffer hunger we do business we got fuel so what mzingomba chimanga nkhanga izo pluuuuuu
Mtumbuka opusa iwe machende ako
kkkkkkkkkkkk koma amwene #phoya
Atumbuka pena mumaziyamba dalatu
ka atony kakungotukwana after kugona nd njala uyambeso kuyamwa Bere lamai Ako happy northerner educated ppl and cool nkhanga izoooooooooooo
Proud of you…..Wukani school has done a great job
Wakhwana iweyo
GOD BLESS YOU .MY .DAUGTHER .. GOOD ..JOB
All the best dear let us show that also women can do better than men
Congratulations to her, proud of you dear.
All the best.
Congrats, pamene asikana ena akulimbana ndi nkabudula mwa Azibambo Iwe watichosa mayazi..
Prophets that can serve southerners for life in terms of miracles n
woow!! gd nws all de bst
Congrats lady. Mwayi kuti ndi kunja, kukakhala ku Malawi, anthu akanakupondeleza ndipo sikanafikapo apa. Praise God.
Atumbuka ambiri ndi azilonda my mzuzumu
keep it up my sister
Congratulations Alongosi as u hve entered in the chat of roll models. Encourage others to forsuit.
Which family is she coming from ,?
Daughter of Hon frank mwenefumbo
Iknew sangakhale osauka kkkkk , iadmire educated people from poor families coz they really struggle osati zinazi
Why always us? even our national netball team ndife basi inanu nkhonya , ndikuyendesa chimpopa manyi basi am very very triple proud for you mwana wakwithu
Foolish comment,
Sukudziwa kuti ndi angati apanga contribute to her success, it may b that many of them si atumbukaso
Watch wat u say
congrats babie girl ….mwaaàah
Zachinyengo izi ameneyu amanyengana ndi akuluakulu akumeneko
nsanje siyabwino ndipo sizakuthandizani moyo wanu onse …inu background yake mukuidziwa ??
kodi ndi atumbukaokha ,zigawo zinazi anthu sangakwanitse kuyenda mumpweya?,zachinyengo izi
Congratuation she set a good example in malawi not only nothern
Congrats girl may the good Lord continue to protect and guide you dear
bola ameneyo si atsikana enawa ayi koma u pilot wa zidyamakanda
congrats gal ,,,,wina he is busy talkin nonsese instead of kupanga zako
Takunyadirani adona zabwino zonse
Ine sinaonepo mwana wamunthu olemela ozichepesa komaso wakhalidwe ngati u, ndipake akupanga zabwino, wish u all the best
nanga akanakhala ngati kuzimbabwe pilot kuyamb ndi 18 years mukadalankhura bwa?
Mwanau ndi odalisidwa
Congrants
Proudful
NORTHERN region Motomoto.
All the best my dear
You make us proud.. Congrats!
Any wherebouts of the malawi made plane guarded by the police?
Kukhala wakumpoto ndi more fire osati za ufisi ndi nyau basi
congrats my ccta
Wish her all de bst
Great
We have done it again the notherleners
kulimbikira pays
Komano khan ndiyot iyeyu wakoza tsogolo lake winawe uli busy kut kumpoto iweyo ulibe olo school report manyaz ulibe
Komano khan ndiyot iyeyu wakoza tsogolo lake winawe uli busy kut kumpoto iweyo ulibe olo school report manyaz ulibe
thus great…..koma university yopanga zimenezi imapezeka kuti and imafunaka wt subjects….kkkkkk …despite kumalawi tilibe ndege…..???
Nkhani ya u pilot yomweyi mpaka zalowa xenophobia.atumbuka mozingothera momwemo koma zolamula muiwale
Nanga malawi nde alipati? Dziko lawonongeka palibe chanzeru
You are very right. Only God knows where we are heading to.
Kkkkk zalowa zenophobia malawi siidzamva
God is at work
Proud of u gal
Congrats!Uzipemphera Cz Mulungu Wakupasa Ntchito Yayikulu Apa
Fly high my sister
May The Good Lord Bless U!
Joyce Mvula wapita ku Manchester Thunder then uyunso pilot ??? northerners are blessed
Mwayi Kumwenda
Muvukenge Nakuwerenga Lekani Waka,Mbachokoyayi.Tasokwa Tawakukwithu Uku.Kkkkkkkk!
kenako nonse a ku no mukalowa kumwamba, zinangovuta kuti muli ku malawi kuno inuyo munakakhara angero.
she joins the other Pilot at Malawi airline Kaunda kkk making it 2-0
north north always mpaka Kenneth kaunda adakalamula dziko la Zambia more than 30 years from northern ya Malawi
Mmmmm kuganiza mopelewela,komatu
the north again
kkkkkkkk nde muziti akumpoto ngosatha komaso ngosazindikira , why not sthrn n centrl ngat mumazitcha madolo amugheto?
Iweyo ulibe or school report why
Iweyo ulibe or school report why
Kkkkkk
kuyendetsa ndege sikovuta man, kungotiba mbali imeneyi anthu ambiri alibe nayo chidwi.
#abinwell ine ndili bettr than wina amene amangoba za anthu osauka pomwe ine ndimalimbikira pandekha , koma simazitama ai kut ndili ndi chani or kwanthu kwatundu wanji koma ndine olimbikira , chimodzi chomwe ndinachiona kut pa moyo wanga kugwadira munthu kut andithandize kuona sipanga dpnd pa munthu oti ali ndi chuma koz amakuona uchitsiru dairy , nde mukanena za kusukulu timapepara tokha ndili nato toti tapita pa cmpny sangandikane koma ndinachiona cha nzeru kuziimira pa ndekha dan ndikakhale lvr wa boma , bt am the best than u
Nice one congrants
Nkhani yabwino
Congrats girl
beware of hijackers ‘sister
She is only 24 and that’s a great achievement… congrats
Bravo
All the best my sister hard work pays keep it up to make changes in society where by people think only men can do better l’m proud of you RSA
Congrats!! Koma snanga vuto ndilot amalawi we believe kut ndege amaendetsa ndi Mzungu… Nde kaya amulemba vepi ndan kaya…
chilibe molaro,bora moto car.
Congrant Gal!
Why always northerners?? Bcoz all the team of Malawi is from northern, Pilots, Minsters, Drivers,Prophet Kkkkkkk Southern musova
kkkkk haha i ddnt expect tht…ndasekaa
Northern is the only place of educated pple. Watch the space. Even democracy came from northern with Chihana. Kkk
koma upuzidenti umakuvutani bwannji inu anthu omwa ink kkkk
Kkkkkkk
Kkkkk northeners ndi dhilu
Kkk some are popular with people thru foolish ways like ‘cashgate ,maizegate n hyenas alas !Southern region mxaah!
Kkkkkk nkhani zili apa ndizomwe mukukamba zosagwiridzana ,nosense!
Komano why iweyo u dont have any qualification
We can’t develop Malawi like this shit behavior, we together us Malawians, stop being a dick head,
And why is it that the northen region is the least developed amongst the 3 regions? have you ever attempted to answer that simple question?
God loves us there
Proud ov u ppl
We hv more educated people in South and we don’t dance like u northerners when we achieved things…..with that mindeset we cant develope our Malawi …don’t divide people we are one after all.
Lets congratulate this young girl….she set a good example to others. ..
The northern region is the least developed coz most of its people are busy developing other regions or they have permanently relocated to other regions I personally blame them.most of the beautiful apartment u see in BT or LL belong to northerners yet they cry of lack of development in their region.most govt department are run by northerners.we have ourselves to blame for lack of development in our region unless we wake up we will remain like that
Tell them my Bru kkkkkkkk. #EDUCATION
The fact is that development goes with population too and its politically motivated
Am wishing her all the best while am remaining with few months to graduate as a pilot as well here in east london, south africa and ndine waku southern so wat i cn say is Malawi woyeee
I will be the first malawian to go to the moon / space!
The myth that northerners are the only educated people was debunked years back, if you are the educated ones why is the northern part of Malawi still looking like a desert?
southern ndi ya ma president .North ndi ya ma office boy .Ndiye ophunzira ndi ndani?
Hihihi the only place ov educated pipo my foot dats y dat place stil luks lik desert not city hihihi southern en cetral region woyeeee asafuna azikande kusana weather educated or no we r stl the best dan u
Ophuzira koma chigao chakwao choowoneka ngati kuthengo.
Ati apita kutown ndie BT L city das y amalimbikira xool kuti akaone town
Congratulations and all the best Lusekelo
Munatiuxa kale
Well done girl
while other young ladies are busy opening their legs for men kkkkkk
hahaha that’s what they can afford you don’t pay fees for it. Even this one has opened legs for men maybe several times we never know.
Including your wife
Baloyi nkosi, your wife too
Zilibwino chemwa zosalana mitundu ndidzausiru
Congrats! Koma ndege zache zilikwaniko abale pa malawi kapena za Bushiri?
Congrants all the best in your career as a female pilot!
CONGURATURATIONS
Conglatulations. Proud she has made us may she inspire more other females out there
Wow great .
Congrats
kumutelo mtumbuka sangaganizeso zakukaya
sizikugwirizana.
Fodyayutu bwino naye
Fodyayutu bwino naye
Mbuli iwe
akanangosiya kupanga coment!
Moyo wako oipawu unatengera ndani? Osafuna kuyamikira wina akachitabwino
come on @Friday
Maybe its a sense of humour. Atumbukafe tinangofika pozolowela
Kumakhalako ndi nzeru za umunthu pena.
Jealous sipindindura
Akufuna kutchuka
Vuto siiwe ,koma MAKOLO ako. Wamvaaaaa?
Wasowa zolemba kapena sumatha kuyamikir nzako , tonse ndi amalawi
kagwere uko
simwenye munthuyu ali dziko lake ndipo akazati dziko wanu ndalama wathu pamenepo tizadabwapo
Good
aaah zachani? zikaulukanitu, ife muzitipeza pansi pompano
Hahaha boss
Kkkkkk,kma guyz!
Thats Grt