Mkwati wina m’dera la mfumu Musisita m’boma la Nkhotakota walira ching’ang’adzi mkazi yemwe adakwatira naye atathawa ndi ndalama zomwe adapeza patsiku la ukwati wawo.
Malingana ndi mfumu Masisita, Bamboyu adakwatirana ndi mayiyu mulungu wathawu koma bamboyu adazizwa ataona kuti mayiyu pamodzi ndi ndalama zomwe adapeza patsiku la ukwati wawo sizikuoneka.
“Padali patangotha masiku awili pomwe mkuluyi adadziwa kuti mkazi wake wamuyenda njomba pozembetsa ndalama nkuthawa nazo,” Mfumu Musisita Wauza Malawi24.
“Bamboyo adayesa kufufuza komwe kuli mkazi wakeyu koma mpaka pano sakukupeza,” adaonjezela mfumu Musisita.
Mkwati ndi Mkwatibwiyu onse ndi a m’mudzi mwa mfumu Musisita, Mfumu yayikulu Kanyenda m’boma la Nkhotakota.
M’mudzi omwewu wa mfumu Musisita, M’busa wina wasiya ubusa kamba kosankha kukhala ndi mkazi wachiwiri.
Malawi24 yapeza kuti m’busayi yemwe ndi wa mpingo wina m’dera lamfumu Musisita m’boma la Nkhotakota adakwatira mkazi wachiwiri zomwe zidali zotsutsana ndi malamulo a mpingo wake.
Malipotiwa akusonyezaso kuti izi sizidasangalatse akuluakulu ampingowo omwe adamufunsa m’busayi kuti asankhepo chimodzi pakati pomusiya mkazi wachiwiriyo ndikupitiliza ubusa kapena kusankha mkaziyo ndikusiya ubusa.
Akuluakulu ampingowa adazizwa ataona kuti m’busayi wasankha kusiya ubusa ndikukhalabe ndi mkazi wachiwiriyu.
Pakadali pano m’busayu wanenetsa kuti sangamusiye mkaziyu wake wachiwiriyu.
Kkkkkkkkk Chikondi cha bodza
Adachita bwino
kkkkkkkk…khani za ku malawi guys..
Za ulendo uno
Zam’maboma
Wangolakwitsa Kuthawanazo Ndalamazo Chifukwa Ndizake Zomwe .
Mkazi uyu ndi shasha bad. Respect. Apa wapeza mpamba wa gain. No mulandu apa the wedding was for both of them
kkkkkkk mkaziyu mwina amawonerera kwambiri Nigerian movies, ndiye imeneyi ndi real action.Mwina akukawengera kaye kutchire kuwopa akuba abwera nazo madzulo ano !!!!kkkkkk
makwatiwa kwatiwa achimwene mwakwatira nazo nkhalamo, mbava
Yoweta sagula pansika,ndikukhulupilila kuti wakupasa phunziro.
kodi #Hule amenei anathawisa dolazo afta #Wedding #Night or before?…koz ngat anathawisa ndalama-zo before wedding night,,,adhaa awa #Aluza kuwiri….
werenganso post yo den u’ll get an answer
Ndaiwerenga kale….ndeee anzathu omva zizungu tiuzeni
kkkk wakupas phunzilo ameney uziziw kt azikanz amasiku ano ali a4 dollar usoveg iwe kkkk wakula watha uziona iwe better life nyatwa.
Amemeyo Sinali Nthiti yanu wachitabwino wawonetsa chikhalidwe chake chifukwa ameneyo akadakupha.
Wanga Ine Ndi Mutumbuka, Osati Mahule Apa Fb
Jonalaaaaa
Aaaa azibambo muziwona osamangoti chikomekome chamkuyu, mkati mumakhala nyelere eeeee mwazionatu
Mwatiwonje apa admin zoona anthu akuno kuno ku nkhotakota angapange zimenezi
tisabuleme mkaziyo mwina vuto analinso mwamuna
Wacita bwino ameneyo akapeze poyambira,azibambo wanyanya kumagula nkhuku zapamtsika.
Akabwela kudzapepesa umukhululukire poti ndi mthiti yako. Chifukwatu abusa adalitsa kale kummawaku
Man Mutani Pamenepa? Zadziwika Kuti Mudagula Pamsika Nkhuku Imeneyi Yakuthani Man
Koma ameneyo kungompeza
changu pa malo kkkkkk
Sazaupezaso mwayi ameneyo
Hahaha KomA abale kusiya mamuna kuyiwala kuti ndalamazo zikatha huh?kkkk Akazi tizikhala serious
Kkkkkk.. Moyo pampanje..
Hahahahahaha
How?for how long have u been in a relationship kuti musadziwane mitima?thats not fair.
kkkkkkkkkkkkkkk koma anthuwo analidi pa chibwez or anangofikkira kupanga ukwat……………… zabodza izi
it signifies one thing GOD’S kingdom is come people will be lovers of money in the last days
Zachamba eti ife tili mmudzi momwe muno tisadziwe za ukwatiwo fokolo
Kkkkkk drama watenga gawo lake
Its part of life
Akazi mumaganiza bwanji?kupeza banja masikuano sikophweka. Ulinditsoka
KKKKKKKKK
kkkk akotakota kuba shaaa
Uyo asandu hule
NKhuku yoweta sagula pamsika,anapezana bwanji?anapezana kumowa? Life ya adonawo inali yotani?
Thank u sis.
Zabodza Ine Ndimakhala Konkuno Mwina Akanati Mwezi Watha Komaso Nkaziyo Anabwelela Kale Et Anapita Kwamake
Hahahaha kkkklkkkk
lol akapezeka aphedwe…..
kkkkkkkkkkkkk kaya asova.
Eee mbola!!
Aah para vwandigongoowesa bt anakazi alero uuh ali makola cha,iwo akupenja makopara real nthengwa ikuwatonda asshh!!!!
Chilipo chipongwe wakhala akuchita mamunayo kumpangira nkadziyo ndeiye anangoganiza zobwedza njira imeneyo
Watenga dzalobola wapita kukadya dzikatha abwela
Vuto lakazi acilomwe ndilimeneri pandalama saphenira.
kkkk kma yaaa
Koma ndie-koma ndie njila zopezera ndalama atsikana mukuziponya patalitu!
Yimwi Kaka Koma Mdamujiwisisadi Dada Uyu Kapina Mdagula Pa Msika? Nimu Vikhalira Mkatola Nakudya Mfulumira But Its Ok Life Goes On Chafukwa Simwi Woyamba Wambiri Wadakumana Nazu, So U Better Pause And Ask 4 D Time Inangu S O R R Y !!!!
If interested all cute ladies available in this group who needs a guy to give them good sex and this includes all sugar mummies or just older ladies but should be smart and ready to spoil with money inbox or call on 0882926882 same line hit me on whatsapp, love you
Kkkkk koma zoona
KKKKKK CLEVER GIRL
Sanabe mesa unali ukwati wake? Haha lol
Kkkkkkkk waziona kumachenjerako pena
Koma zina ukamva!!!!!!! Kamba anga ujeni ndithu
I am here to give my testimony about a doctor who help me in my life. I was infected with HIV virus in the 2010,i went to many hospitals,churches for cure but there was no solution out, so I was thinking how can I get a solution out so that i cannot loose my life, I lost everything I have my husband run away from me and also took my children along because of my sickness. One day I was in the river side thinking the next step to take if it is to jump into the river so that I can loose my life totally or just think where I can go to get solution. so a lady walk to me telling me why am I so sad and i open up all to him telling her my stories, she told me that she can help me out that’s the reason she normally come here to help people so that thy can be cured because she was into this problem before, she introduce me to a doctor who cast spells on people and gave me he number and email so i called him and also email him. He told me all the things I need to provide and also give me instructions to take, which I followed properly. Before I knew what is happening he called me and told me that i should go for test which i did to my greatest suprise the result came out nagetive, am so happy right thats why i decided to share these with my brother and sisters that is passing through pains contactthese great man he will help you through whatsaap +2348162447651
Kkkk kkkkk oho
amafuna ndalamazo osati mamuna.
A kotakota sadzatheka basi. Dada mpaka kuba za paukwati?
akazi amasiku ano mtima pandalama basi zabanja ndinyambo chabe,safuna tsiku kulowa osamwa tiyi amayesetsa kaya ndiwa chimanga chokazinga bora ziyende zikapanda kutero mapeto ake akuthawa
Ukwati Matsiku Ano Ndi Bisiness,AKWAWO KWA MKAZI ATI BWANJI?ONSE NDI AMAVUTO.
Mmmm bhoza ayi
Ndalama Yakuba Chonchi Simapindulitsa.Adzayamba Kulingalilanso Zikadzatha.
Za m’makwalala .
Napepe angoyang’ana kwa mulungu ampatsa madalitso nkaziyo ngotembeleledwa moyo wake wose.
koma zimenezi zoona? ndeufiti uwu ndithu, iyi ndi murder ndithu
kumachenjela pa town n’dala,nkazi osamamukhulupilira ngati FMB pa nkhani ya ndalama apa ngongole ubweza bwanji ?
Hahahaha a Malawi24 mwayamba nkhani zam’maboma
Kkkkk
wakasegula chorp kupotho
She just got her share,
Haaa dzoona wathathawirsadi. Ndalama zija.. Haa wandililirsa ku usi zedi. Haa ine kumati ndapeza. Yanga njole yondipukuta. Minsonzi pathawi yamavuto. Haa wandionjera. Minsonzi yakhani khani masaya anga. Haa kodi ndilowera kuti. Haa wapitadi wachikondi chabodza uja. Haa uyu yekha waswa mtima wanga. Haa kundipyopyona konse kuja inali plan. Haa zoonadi iwe wekha wawina..Haa sindibweza choipa. Koma tizaonana pa siku la chibaluwa
kkkkkkkk…koma adaah…
Bwanji man kkkkk
aaaah waitha comment yako….waponda onseo pamenepo
aaaah waitha comment yako….waponda onseo pamenepo
mpaka ndakatulo pompa kkkkkk koma adha
Yah umaziwa kuidoloma. Ali yense apange ka comment kosiyana nd mzake, kkkkkkkk
Umakwan
Vuto akazi zelu alibe pandalama,azingogulila mesh,kamba,jigisi zikatha azifunaso banj
Alibi uthawa……wabishala chaje kkk
Chiyambi chosauka icho akhale nazo
kkkkk vuto lotengana ku bar ndilimenero akukadya ndimamuna wina zimenezo basi
A good wife who can find? she is far more precious than silver and gold; her husband trusts her. she does him good, but not bad all the days of her life.
Wachita bwino ameneyo kuthawa ndi cash, better ulimoyo anali woipa ameyo eee unakaluza moyo man.
Kodi ndalamazo ndizingati ndipo mumapanga musanaziwane mitima akuwona ngati wachenjera
Muzitchula ma boma ena nkhan za mabodzazo .ife akotakota tingokutoperan tikakhwema
Too much movies …..She got skills
Am sure kt nkaziyo mu nkk ndiwobwera..achina dada sangapange vipengeya vateyapa yaye..
mamakhala busy kuseka maswazi koma inu mukuphula njerwa mmabanja kkkkkk uisova
Vuto si iyeyo, but Umphawi uli kuMalawi
Wapangitsa passport wabwera kuno ku Jonz dzana kkkkkkkkk, manyaka enieni
Odya zake alibe mlandu
Mmmmm ine no comment
kkkkkk watsukidwa mmutu ameneyo amuna munyanya kuchenjera nkaziyo sanalakwe
zochita kugwirizana zimenezo cholinga asabweze ngongole yomwe anaiputa pokonzekera ukwat wawo kkkkkkkkkkkkk
Makwatirakwatira
MAKWATIRA KWATIRA MUZAKWATIRA #MBAVA
Kkkkkkkkkk
hahahahahahahahga xogwirizana!
Kkkkkkk she was a gold digger not marriage material sorry bro
Nkhani zamumaboma izi, how? ??….
Kkkkkk eish umphawi ndiwomwe watipha pa Nyasaland nothing else
Ine ndingoti mwina ndi mwai wako….??
vuto la mkazi ochitakukupezela.sorryman keep on searching u’r self now.
Koma akazi alowa chiwewe pa malawi
:v :v :v kuliza namkwichi’popopo!!! :v
People must understand that love exist no more. But some fools are still getting married.
nkhani iyi ndiyongopeka sizoona izi. unali ukwati wa mpingo wanji umeneu? mkazi wachiwiri mpaka ukwati lol mbusa wa church yanji osanena apa?
Uuu uyu dziko lamuziwa kuti awawidwa …..but story makwatirakwatira anuwa mwakwatisa mbava achimweneeee mumalo moganizira honey murn ayamba ndlama kut zapitaaaa
Zinakhala bwanji kuti mpaka kuthawitsa ndalama
She wasn’t serious with the marriage, finally she get what she wanted, she wanted that money most not that man, she was after money, thats what happens when you are forcing a prostitute to be your wife!
Money GO! Love GO!
zomvetsa chinsoni akazi alero basitu bola wosakwatila
Kkkkkkkk anangopangapo business adhaa wautali kkkkk
Nkhani ya bodza iyi,
Gold digger ameneyo
lucky you are, she could hv store you too
Azimayi iiiii kutengeka wina akuwona kuti uyu ndi m’busa ndipo ali ndi banja lake koma nonoloo pomweposo kodi bwanji kusaugwila ntimawu?
Kkkkkkkkkk anakwatira chiphona bola chatenga cash kusiyana anakalowa banja coz akanazakupha ndiwachabe
Kkkkkkkkkk banja lalepheleka bas
Maukwati ofunsirana m’mawa madzulo ndi Banja ndichoncho,kumangopusitsana basi.
kuthawa ndi chikwama??
Makwatilakwatila mukumana nazo azibambo simunati kkk musovenge
Komabe waitha zofunazake zakwanilisidwa
Theft by wedding.koma mkazi ameneyo ndioiwerenga
Yooooooooo
Mmmm fwit imeneyo
Azimayi ambili akutenga banja ngati bizinesi, chikondi chinatha kale, angofuna kuzikundikila chuma basi kumangomupusisa man …….
Wale Adenuga production, ths is a super story…..kkkkkkkkkkkk Malawi eishhh evryday tikumamva nkhani zonga zabodza bt zili zenizeni eishhh
inu mwazijambura bwanj atathawa nazo??? ndye kt komwe ali mukukuziwa
Zomathamangila kumangitsa ukwati musanainetsetse…. uli ndi mwayi kuti waziona kumayambiliro.
Nde zamaboma sanalengeze coz iyi ndinkhani yosekesa kwabasi
amzawo akugona mmapiri kupempha banja kwa ambuye,adzalifuna ndarama sichikondi ayi.
Aa pali zolira apa atokhala umafupa ndiwe mesa anthu ndi omwe afupa? Mbuzi ya mamuna iwe eti..?
Azichenjera
kkkkkkkkkkkkkkkkkkkkk watani
Et mkazi wathawitsa ndalama zomwe anawasuper pa ukwat
Akuti wagogoma ndi money kuyiwelengatu kkkk!
Kaka namwe vibwataka mwapanga ivi vitinyozetsa kwambire,akaze amasiwano safunika kuroromwa yaye zotchatila zake mvinevi.mpiti kwawo mukayabwi akabwezi mteleshede osewo kuphatikizaso nkhuko yakamoongo akapheleki
Kkkkkkk mukambitchadi kaka…watinyozetchera kumuje mkazi mneyo,kkkkk
Asova
Kmansotu Nkhotakota penapaketu……
Langa ndi fuso munadziwana bwanji? Nanga mwakhala limodzi kwa nthawi yaitali bwanji?
Ndizelube ali bho!
kkkkkkkkkkkk amuyeresa mmaso
Ine langa ndifuso kut Kod amenewa Anapezana bwanji Nanga akhala nthawi yayitali bwanji ali pa ubwez
Owooh
akwatile wina akatelo afupa zina zombo zapita
pavutadi mpaka inu kulemba chibwibwi? ‘pa pa ukwati’ kkkkk ndatha kuona nanu zakudodometsani
Kkkkkkkk
hahahahahaa kooma mark kkkkk
hahahahahaa kooma mark kkkkk
Eya zamunaso kuyelekedwa tizibwezela choncho kkkkkk
yoweta sagula pamsika!mwinatu nkutheka anamutenga kubala!mamuna pamafunika upange kaye chibwezi, kumufufuza mkazi kwao makhalidwe ake then ukwati.mani munadya mfulumira.
vuto lotenga mahule mwawonatu mani?
Tiyeni tikomente Chichewa guys Chifukwa nkhaniyi ndi ya Chichewa kkkkkkkk Sitikufuna kuwelenga zizungu zanu zozungulira mutuzi kkkkkkkkkk Iya nanga tiname hahahaha , Chizungu chinechi atakumvani eniwake azungu akumangani Sure !
, so para ise talemba chakwithu”chitumbuka” imwe achewa mutikakenge namwe.
munyanya mwezi umodzi kukumana mpaka ukwati hehehehee zoti anasanzika mamuna wake kuti akupita ku business inu osadziwa koma yandiwaza mmmm
syz ya mtown
Hahahahahaha Si ku Ngala kodi. Za Chitonga ndi zomwezotu. Tulo mumaso ngweee Koma tsopano aziti ife a Tonga ndi ochenjera. Kuchenjera kwake kuli kuti tsopano apa? Kuchenjera powedza nsomba basi pokwatira ndikusunga ndalama zaukwati tulo.
Zakuba zilibe zilibe tsogolo ,,if u take from universe no matter how long it might take the universe will take it back from u,,
That’s what we call professional in business. Sorry brother its part of life keep on searching
Koma nde kulawiriratu maplan akantema wa thadzi kkkkkkkkkkkkkkkkkkk
sadalakwitse mkaziyo pajatu nthawi zambiri maukwatiwa amaluza ndi akuchikazi.
Kkk
kkkkjkkkkkkjjkkk asovatu ameneyo
Siwa Chikondi Ameneyo Chikondi Sichocho Nijuleli Menelo Achinyamata Tiyeni Titengepo Phuzilo Mawa Ndife Chenjelani Achinyamata
Azichangamuka
Hahahahaha koma ndatseka …..
Many ways of getting rich, but dis is rediculas, mwanyozetsa boma langa. Man muziona mkazi omukwatira….mukayamba chibwezi mukanamudziwa koma madulira ndio akupwetekani bro. Sorry.
lif is nt simpl
Iyi amayesa ngati Ku thiwi wakumana Nayo mzaliwa
mwina anali ndipassport imamusowa transport fee ndekuti basi ameneyo wadusa ali kuno ku SA…paja ku Nkhotakota safupa zambiri zonse zathela munjira…chongofunika abeleso ena pano pafumbi labwana Zuma.
Amumeta
Tilitonse kkk
ala kumene akayambe moyo wanyuwani ndi chibwezi chake chakale
malawi @ 51
Wathawila Ku theba ameneyo
Kkkkkk anapita ku kawuni, ndiye waphako apa
Nkazi wanzeru, anali pa business alibe maganizo abanja.
Akulila ngati ndalamazo ndi zake oyenela kulila ndi amene amasupa ndalamazo zilingati kumuwuza mkazi kuti choka pa nyumba panga pano chonsecho ndi pa rent
No love btwn them
Ha ha ha. Asaaaa. Anasunga ndani
So wedding is business nowadayz!!
Eeee amuyeresta mmaso!waona pole..siyense wovala sket tkuyenera kukwatla”UZAONA POLEKEZERA”
Vakaz ivi vilibusy looking 4 money not chikondi yayi,vikondi walije awa,sono uyo wathawitsa dinyero zilinga?
Uli Mushe
Kkkkkkkk! Dinyero kodi? Chiyankhulo chanji chimenechi?
Kkkkkkk are you fucken amigo…de patarau?
Adzichenjela
Ndye akazi amatsiku ano maso pandalama basi amacita kufusa umapanga cani ngati iyeyo akupanga alilova
Kkkkkkkkkkk munatola kuti kkkkkkkkkkkk usova kkkkkkkkk
Its Part Of Lyf! By Dan Lu! Tititititi
funy
kkkk
Eeeetu Azikazi amasiku anotu maso Ali pandalama osati chikondi chenicheni ayi, Ngati ndalama yavuta uzaona behaviour ya mzimayi yayamba kusinta mbanja. Sono apopo zaonetserathu kuti sanali mkazi ofuna ukwati ayi koma ndalama. And wazipeza.
makwatirakwatira okwatira ndiviphona kkkkkk
Kkkkkkkkkk tikuseka ngati ndizabwinotu et
Nkhaniyi amene walemba akanayilembaso. Sindikumvapo kanthu . Pali nkhani ziwili zosagwrizana.
kkkk-eeee-love-is-not-game
love is a game
kkkkkkkkkkkkkkk sunali ukwati koma masanje
kkkkkkkkkkkkkkk sunali ukwati koma masanje
zosadabwisa chifukwa masiku ano maukwati ake nd business
mmm mkwatibwi ameneyo ndi wakuba