Chipani chotsutsa cha Kongeresi chaonetsa mbonaona chipani cholamula cha Democratic Progressive mu zisankho za padera zimene zinachitika mu madera asanu a dziko lino.
Chimake cha zisankhozi chinali ku Mchinji kumene amasankha phundu wa nyumba ya malamulo.
Kumeneku phungu wakale wa chipani chotsutsa a Billy Kanjira anamwalira zimene zinapangitsa kuti kuchitike chisankho cha padera.
A chipani cholamula anachita misonkhano yamphamvu ndipo mtsogoleri wa dziko lino a Peter Mutharika anapita kumeneko kukawaopseza anthu a ku deralo kuti ngati asankhe phungu wa chipani chotsutsa, iwo sazaonanso chitukuko.
Koma kuopseza kwa a Mutharika kukuoneka sikunaphule kanthu.
Pa zisankho zimene zinachitika lachiwiri, anthuwo anavotelanso phungu wotsutsa wa chipani cha Kongeresi.
Kupambana kwa mpando wa phungu kwa chipani cha Kongeresi mu dera la ku Mchinji kunapitilila pamene chipanichi chinapambananso mpando wa Khansala mu dera lina ku Kasungu ndi lina ku Dedza.
Chipani cholamula cha DPP chinangokwanitsa kupata mipando iwiri basi ya Khansala, wina ku Kasungu ndi wina ku Zomba.
2019 boma DPP a aaaa paticia kaliat ndi ana ake Kondwani Nakhumwa ndi ana ake Geme kalilani ndi ana ake Henery musa ndi ana ake Godwel Ngondwe ndi family yake basi afisi amenewa ndi omwe azavote ine ndi ana ndizakhala ndili ku munda
MCP IKUYENELA KUZALAMULILASO, chifukwa aphuzila ndipo awona zomwe amalakwisa ndizomwe amachitabwino, A DPP mmmmm kaya,
You are happy with that?Expect to cry so loudly in 2019.Will the goaltender be the same one?I mean the believed to have fallen off God’s hands?Abale tidzamwanso wa mkaka mtheradi.
You are happy with that?Expect to cry so loudly in 2019.Will the goaltender be the same one?I mean the believed to have fallen off God’s hands?Abale tidzamwanso wa mkaka mtheradi.
Zako izo MCP more fireeeeee
Komabe MCP yo lkulamulidwa ndiboma la DPP
malawian by nationality
Where is Malawi Voice? Ana a njoka inu mwathandiza kugwesa DPP ndi ma propaganda anu. Ichi ndi chiyambi cha kulephera kwanu mu 2019. Paja ku mbali ya DPP mutsogoleri wokopa anthu ku MC anali ndani?
hahaha chipani chowina by election
*DON’T LAUGH ALONE, ABEG!!!!!!!*
A man woke up and shouted “Holy Ghooost Fire !!! ”
*Wife:* what is it, was lion chasing you?.
*Man:* that would have been better.
*Wife:* what is it then?
*Man:* I nearly voted Peter again in my dream OOooo.
*Wife:* Blood of Jesus! Honey, lets pray.
Kkkkkkkk kuthibula mpakana
zoona zake ndizimenezo kut mcp ndiyomwe anthu ambili amaifuna italamula koma mvuto ndilakuti DPP amabela kwambili koma anthu povota amafuna mcp italamula osat izi ayi
Mp anamwalirayo anali wa MCP ,atenganso mpando wao a MCP wa. Mukafuna mpikisano kapangeni kumpoto kopanda achewa kapena alhomwe
Zayenera
Iwe umafuna kuti nawo otsutsa asapeze mpando kkkk koma ndiye zikakhala choncho ndiye ndi democracy kapena ai,zakhala bwino koma dpp sikuopa kalikonse palibe nkhani apa
Nchiyambi chabe chimenechi
MCP 2019 BOMA a Chakwera kozani chipani cha makolo, si akavuluvuluwa
Adzipita basi kwao
To hell dpp …….that’s a sign,if you won’t change……..we don’t mind MCP back in government, but am only UDF fun#
Its also a sign yoti DPP idabela chisankho cha 2014
Koma nkhani uli APA ndiyakuti DPP yagwetsedwa basi kkkkk
MCP
misokho, kukwela kwa zithu kuba ndalama za boma magetsi tili mano gweeeeeee
kupanda kubela 2014 sibwezi muli otsutsa? tivomeleze opepela ndife amalawi.mcp akukangana akuyambitsa ndi a dpp musiyeni Chakwela sindine wa dpp or mcp
Bravo Malawi Queens, ndimakunyadani
Mcp bomaaa Mcp bomaaa Mcp bomaaa ngati wina zakunyasa pita ukakolope ocean koma ife tili nganga pa Dr Lazarus Chakwera! Dr Lazarus Chakwera and Richard Msowoya bomaaa
If DPP is managing to secure position in some parts of central region.Then mcp must be very careful. Because DPP capitalise on southern region. Not central. So its my advice to mcp to make sure u push harder to gain popularity in south. Otherwise DPP is very strong.
Mavuto aliko cozMCP ndiyachigawo chapakati ngati DPP yakwanitsa kutenga mKasungu zaonekeratu kuti DPP 2019 boma! ilipaliponse MCP ilipavuto ayilowera kuchipinda!
Anthu sakukondwa ndi momwe dpp ikupangira ndondomeko zake.ziri ngati m’nyumba muli njala nde bambo m’malo moti agule chakudya iye akuuagula galimoto.kodi tinene kt bambo uyu akuganiza bwino?
As usual I have been saying that MCP can’t win a national elections because it is a region party. What a type of a party is MCP just based on central region. Mr MCP come and penetrate here at Southern region if you want to win 2019 because it’s where the majority of people are.
Congratulations MCP…….. when the opposition party does so……it tells people needs change………mo fire…….buuuh.
m c p woyeeee
kd zisakho zimenezi zimachitikira kt a MCP aonesa kusagonjera DPP kakhani kokoma kwambiri eeeeee! kodi heeeeee!
iii bola ku egypt (mCP)
Kuchedwa kulimbana ndi ndare lero ,ndare zinatha kare
Ifenso kuno kuteba tikufuna mcp ibwerere ilamulire zaka 30
UDF kudalibe?
Kkkk koma iwe Admin mtopola wake mmmm
Viva!!!
beating mighty DPP is not as simple as you think.
Tikufuna magetsi ife
we love chipani cholamula chifukwa zinazo za chimozimozi olo chitaaaaaaaaaaaaaaaaa
A DPP awanyenya
A DPP awakudzula
A DPP awa fwafwantha
A DPP awachotsa chimbenene
A DPP awatsukuluza
Kodi akanyimbi inu mukukangana chiyani? apa MCP itenga boma 2019 osati president wotha mano central ndi ya Chakwela Kwacha Idzuke Malawi Ndimkale Idayambila Kugona Nthawi Yakwana Yoti Amalawi Azindikile Chabwino Poti Choyipa Tachiwona Kuchokela Ku DPP, PP $ UDF vipani vowononga dziko muli kudzikonda,umbava,njala, Cashget komanso umbuli mamphunziro alowa pansi ndiye akanyimbi mukukamba zopusa poti mbava ndi inunomwe panyapanu kkkkkkkk
Kodi akanyimbi inu mukukangana chiyani? apa MCP itenga boma 2019 osati president wotha mano central ndi ya Chakwela Kwacha Idzuke Malawi Ndimkale Idayambila Kugona Nthawi Yakwana Yoti Amalawi Azindikile Chabwino Poti Choyipa Tachiwona Kuchokela Ku DPP, PP $ UDF vipani vowononga dziko muli kudzikonda,umbava,njala, Cashget komanso umbuli mamphunziro alowa pansi ndiye akanyimbi mukukamba zopusa poti mbava ndi inunomwe panyapanu kkkkkkkk
Boma I’ll 2019
M c p 2019 ndi chakwera boma.
2019 chipani cha MCP chidzasesa mipando ya phungu ambiri! zaonetseratu apa! kkk!
Dpp must fall
tambala wa dya chimanga
Ayithidzimula,aiphwasamula,aiting’inda,aikong’ontha,aibwanyula,aiswa,aiwonetsa mbonaona.Viva MCP
Eeeeeeeeee! Comment koma iyi adha
Central region is always been MCP strong hold,thinking DPP wud win there, is asking too much,besides that the ruling party has been making head lines for wrong reasons together with all miceries the pple facing, I don’t think thy cud make in rods in those areas.
That is really true Harold. You can just worst your time and drop down yourself; just focus on how you can achieve yourself on daily basis. These days politics is abusiness game “Amacoka atalemera, kwambiri antuwa ndicifukwa or materm (2) onse walamulira kale muzaona akufuna azipitilirabe kulamulira, why??? it’s simply bcz zima alemeretsa.Muligeni misonko yonse imapita m’mathumba mwao osati kwaantu wamba, Ndiye my point is that: we have frustrated to believe in those governments now!!
Mcp ndichipani chosusa basi. Kulamulira ziko liti?
Muzingozinamiza palbe azabwere nkut azakusangalasen muchedwa
MCP singalamulire man galu amayerekedwa kwawo
Dpp criminals baba!
kulimbana ndidzandale mudzingotaya nthwiyanu asogoleri onse ndi atambwali amangofuna kukhutisa mimbazaobasi ndiyetisanamizane kuti adzabwerawina ndikudzasinthazinthu chachikulu amalawi anzanga tigwire ntchito zotukula mabanja athu kulimbana ndindale tingotaya nthawi anthuwa amadziwana
ana obadwa nthawi ya chair ndiomwe angakonde mcp ngati akazitape a mw 24 kma ife amvula zakale 1949 sitingalole
2019 DPP bomaaaaa
Just as I believe would have been the case had it been that the by-elections were held in the Lhomwe belt, the DPP was obviously going to conquer as the MCP has just done in Mchinji and other areas. Typical of ndale zapa Nyasalande. Wake up mother Malawi
Ndiye ukutiuza ife,chikutikhuza ndichyn?ife sitimadya ndale aise
Ndaona vision ku Mpoto pakati onse ndi MCP ,,mutchona ndiku mwera,,,Chakwera anasiya Ubusa anatumidwa ndi Mulungu kut ziko la Malawi ali phule pa Moto Amen 2019 kuwina kwa Bwino
mcp idzalamulira kamuzu akadzakhala ndi mwana
Foolish point …..hu r u nonsense
CHAWAMA TAWINA WE HAPPY ALL MALAWIANS WITH GOOD “
Dpp 2019 bomaaaaaa !!! Kkkkkkkkkk .
Kod mukut dpp 2019 bomanu ufiti, usavage, kukhwima chan? Anthu oipa inu
Siyani zoyendera kuti ndiwakwathu tamakulani mdimokalase plz, amalawi. Sankani msogoleri okonda ziko lakwao oti alindiukadaulo oti atha kuisintadi Malawi ndikukhala okoma mzonse, abweretse zitukuko ponseponse osati kusanka zigawo ayi, (osati zimene mukunenazo wakumwera, wapakati, kapena wakumpoto. Zimenezo sizingathandize ayi kulani mu Democracy imveseseni tantauzo lake)
Mwamuona munthu akanawima mukananena kuti abela koma munthu sazatheka
Asowe basi
Anthu DPP sanatope nayo komano ndale za MW zimatengera mtundu ndi komwe akucokera munthu.
SHAME!
Achita bwino eyaa
Mcp, dpp, udf, pp ntchito zawo nkunamiza amalawi ncholinga chowadyera masuku pamutu. Chofunika apa ndikukozanso constitution kuti mtsogoleri asamakhale ndi mphamvu zambiri
foolish ideas.koma mmaidziwa bwino DPP inu?
Malawi kwachaaaaaaaaaaaaaaaa
Unless anthu akummwera atatengedwa ndi Napoli then MCP can win ! Otherwys idn’t see them winning elections in 2019
Mmmhhh MCP ndi central region only, if DPP is getting some votes in central region then 2019 izalowanso m’boma opanda kupikisana nae. MCP singadzawinenso chisankho cha president koma idzingokhalira kutsutsa basi in the parliament anzao akulamulira
Malipota M C P Ndi A Zbs, Ndamoz Onse Ndo Chewa, 2019 Muzaptanso Ku Khot Cauz Muzafaso, Mot Muone Kt Mwasyana Bwa Kmas Ndi Kwa Mcp, Musamalet Inu Ndamene Mumaymbitsa Chisokonezo
With little resouces
Akanawina phalombe bola
Tikudikila 2019 atibulidwadi zenizeni
kkkkkkkkkklk
Zamkutu
Realy? glad to hear this. mwano siundula ANC ukulira pano chifukwa cha mwano. don’t think people are fools they know they hear they see. inu mukuti 2019 DPP boma m’phunzire poti chipani chanu ndi akaswiri obera mavoti tizawona koma simungabere kawiri tikungoyang’ana
Once beaten second shy!
Palibiretu zowina a DPP, kwao kwatha, akapune mumtendere Ku Ndata
kkkkkk mwandisekesa ada Longwe kundako alutengi amoyu? kkkkkkk sonu nditumupenjani ubwezi wapa FB kkkkkkk
Mcp the next government come 2019
kkkkkkkk amalawi mundisekesa kwabasi or zitavuta maka central singachoke pa MCP muziwe DPP ndiya kumwela ndiye mavote anachitikila kuti mupeza malo ambiri ndi ku central tipite kumangochi UDF kkkkkk
COLLECTION:timati i Tibula (kuyinyenyanyenya DPP) osati MCP i thibula(kubenthula)
U guyz dont blame any party but congratuation 2 de wnner
Azalamure yani a mcp
am not sure ngati mcp idzalamulire M’badwo wa mcp unatha, kodi ngati munthu anathawa anthu ku church mukuona kuti azakuthandidzani? (Schilama boma 2019) ufune usafune
Izithibula ndithu mpaka anyani amenewa tiwatulutsamo mmenemo MCP go go go
Umboni onena kuti dpp ilibe tsogoro ndiuwu.
Peter,chakwera Ndi Atupere Alephera.Koma Ndikufuna Mcp Itawinako Mu 2019.Kuno Kumwera Ndayamba Kale Kutchola Mano Ofuna Kundithandiza Tilumikizane.
Momwe ndikuwonera M C P ikhoza kuzachita bwino 2019 ngat atakhala president wina osati chakwera,koma othawa mulungu mcp sizachita bwino ayi mwina ku mp komweko zizakhala better komanso ulamulira wabwanawa aaaah ukuvutirapo
mavuto alipobe dziko muno
Thus what we call, civilization. .only fools go to pouring station but to vote for failures! A chair said., no body eat politics but development indeed. ….
Atupele wapha yekha udf chimozi modzi pp kukhalitsa kwa Amayi kunja sizikuyenda kuno
Amatelo koma pama peto ake amalilanso nkumapita ku court
Mwacisanzo cabe Kuno Zuma akugwa pakalipano cifukwa Cosasatila zimene antu akufuna akumidziko kuma branch ndiye kaya tizamvera momwe zizayendera pazisanko zazikulu 2019 kumeneko koma na maripotio enewo zayamba kuavuta ngatisasinta magiya azagwa mu 2019.
That’s what happens when the ruling party does not lessen to people on the ground and when the leader is selfish
Pepani ndiyerekezera, Mpamvu zachipani zili kumabranch Enafe tinasiya kusapota zipani cifukwa ndinazindikira mocedwa kuti ndikungotaya ntawi yanga m’malo motukula pakhomo ndimakhalira kuyendayenda kumapanga ma campaign, Ndinali mlembi okonza zamisonkano like District organising Secretary, So ndimaziwa kumene kulimpamvu za Cipani.
Hahaaaaa munthu kuwina nkhondo pakwao muziti amatha??? Musamale 2019.galu amanyada pakwao…..
Zili bwino kobasi, panopa dziko lili m’manja mwa amnchona amene adakhala zaka 40 ali mujango
Even one amanyamula world cup! MCP you beat goverment and oposion UDF! He use goverment resouces, like car, radio, mike phones, and time for goverment, water, ndikuluzanso, Haaaaaaa
ine ndikufuna kuziwa kuti maderawa onse anali achipani chanji? chifukwa apa mukunena ngati kuti onse anali adpp ndiye mcp yalanda Dpp isalamulabe paka kale
The point is that if the ruling part doesn’t gain ground and the opposition maintains its stronghold there is nothing to lose to their part but in the other way i can say that the Dpp government has nothing to offer it will packing bags come next election.
Timaona ngati muzinena kuti 3-0
Central region ndi pa home ya Mcp kotero DPP yayesetsa
Nde ife titani? Mufune musafune DPP 2019 ikutengaxo boma…..Dpp woyeeee!!!
BODZA LOOFIIRA, KULIBENSO KATANGALE WAMABALLOTI PAKOMPYUTA MU 2019.
Mwauponda a fisi inu!
Ngati MCP yazatenga boma 2019 muzandidule khosi langali
Kodi a NTABA angatsutse bwanji apa “TATI TITSUTSE KUTI…………………………………………hahaha
Congratulations to all the players, on the free, fair and credible bi-elections conducted over some parts of the country on 1st November, 2016, It is not easy for the opposition to win, if a playing field was not leveled fairely. Bravo the ruling party for showing maturity, honesty, progressive democracy and rule of law.
come 2019 mcp boma
Mwalemba bwinoo 2019 tiyithibulanso anthu abodza ngati awa osekelera kuba safunika mboma
Yagaganda
Its a good development for DPP
Dpp pempho langa ndiloti 3:2 ndipafupi mutha kubweza mukapita ku dressing room mukakoze molakwikamo poti kubweza kumawawa kusiyana ndi kuyamba mukapanda kusamala 2019 akukwapulani osati masewera amalawi anachenjera
Ayi zawonetsa kuti anthu akuona mmene olamula akumapangila zinthu ngati ali wokha kale kukhala chibwelezs chotchi ndie kuti kaya kunaloi otsutsa olamula amatenga basi koma apa mwina olamulawo nimwai kuti awone bwino mngakhale akuti sanatenge wawo komabe ndie kuti anthu ali ni chikhulupoililobe ni otsutsawo
mukati mcp idakalamba ndiye mukunama zd,komaso atso ambiri kuchipanichi ndi anyamata ngati chakwera ndi ena,kuika munthu okalamba kale pampando ndikulakwa zd ndizmene tikuziwona lerf kusowa mfundo yoti ugwirepo ana ndiye apanga bwanji?kumangowombana mizu palibe chanzeru amapanga chomwe walota usiku osati kuganiza.Olamula amafunika azitsogola osati kubwelera mmbuyo ayi chipanichi chapendekera.
Ndale za pa Malawi ndizazigawo. Ku mmwera zipini zinazi kulibe only Mayb 2/100
Let’s wait 4 the second half. Mwina idzathera m’mapenalty 2019. This was just the first half.
More Fire MCP
Usamati kuthibula akulandaso ka layisesikotu iwe udziti angoluza wezi
MCP Boma 2019
DPP nka chan akagwere kuntaya nd pressident wao kkk
Zamziiii zopanda ndi mchere omwe Koma anapanjala inu ! Kkkkkkkkk ndinu osekesa kobasi , anapazakande inu !
Dpp woyeee
kkkkkkkkkkkkkkkk koma inu muvutikiranji mu Ntima koma zowona inu mukamakhala mukuganiza kut Dpp muzaigonjesa???? Inu inu musamasausike mu ntima plz.kkkkkkk a mcp mukundisangalasa mwamva. Phuma lake limeneli muzawine inu?? Nanga kachisankho kake kameneka koma kukhala ngati wawina ndi chakwera??? ndie ngati ali chakwera ndie amulumbirisa Liti?? Kaakakakakakakakakakaka kkkkkkkkkkkkkkkkkk zomvesa chisoni. Koma zoti muzimvere chisoni chifukwa choti dpp ikulowa ku chipinda cha mcp simukuona??? Ai ndithu. Isamaleni dpp ndithu izakulizani musakaike
Malawi Queenz yabwelako number chan ku fast5 competition adala inu? Bwanji mmene dziko lasangalila wait and see wat wil going to happen in 2019.
Mutayeni kape uyo man!ukamalimbana ndichitsilu oona sasiyanitsa,mavuto onse abwela chifukwa cha dpp wa alipo yemwe sakuwaonayi?i
Which dpp?mukamakhala ndiganizo loti tikusankha chipani ichi kt chitithetsere mavuto,mudzafa muli amphawi ndithu,pemphani Mulungu akukonxereni mavutowo anenena Yekha kt pempheni ndipo kudzapatsidwa kwainu,ndiye mutukwana zipani zingati popeza boma linalililonse lilindimavuto ake,tidzisankha boma poti ndimwalamulo osati chidwi chathu chonse kwaboma tidzingolira mpaka kale,palibe boma lidzabwere mkudzathetsa mavuto alidziko muno never and never,lets work hard at our level and seek the glory of GOD to guide us,kma kumapanda kutero ndimayo ine mayo ine mpaka kale,zomwe akwanitse akwanitse kma osati boma ili lokha lichepetsa mavuto forget about that my dear friends,akamalowa boma amachita kt eeeya nthawi yakwana yotha mavuto athu,wakuva wava osava akhale thamks
Kunalibe DPP ,idalowela pawindo Ufuse aUDF amkati siidzachoka ilikuti pano usamathe mau tiyembekeze 90 mins
Ndale za Democracy ndi choncho apopo zikusonyezerathu kuti antu akufuna MCP Ibwererenso mboma ndekuti, DPP atopa nayo. Bcz if the ruling party is coming behind it shows exactly that more majority needs MCP to take a rule now. Also we says; you can’t allow to be beaten inside your own house with a strange person. Only he can manage to beat you if you’ve lost power. So in these reports it shows exactly that APM is losing power as of now%#
kkkkk osati MCP ibwelerenso chifukwa MCP siinalamulilepo mundale zamatipate 2019 kungankhale nkoyamba kulowa m’boma kkkkkkk
Tamuphunzise ameneyu
national election is complicated Owen. MPs and Counselors are voted by relations that know them within those area but a president is voted for the whole nation
national election is complicated Owen. MPs and Counselors are voted by relations that know them within those area but a president is voted for the whole nation. Ask Tembo. He had a majority of Mps but lost presidency.
kkkkk MCP in multiparty has never ruled. DPP won in Kasungu which can never happen with MCP in South
if the elections were in south the results would have been opposite.
Zakuti mcp singawine kumwera maganizo ameneo ndi omwe adzakomoketse Dpp 2019 becoz it will be caught by surprise. Pple are now getting matured in democracy, are now tired of ushering crooks into power though own relations. They want trustworthy leaders who will do their best to bail out Malawi from this untalkable poverty for betterment of the future of their children.
Ndale zazigawi, izotu ndfizimene zaika Malawi pangizi, kukavotera Mtshona wakalekale Ku a America, wakwathu wakwithu, wakwidu, sidzidzapindula a Malawi.
Southern, Central, Eastern and Northern make Malawi not South yekhayo angathane nazo zovuta,
Izotu zaskukanikani.
Wakwathu poti ndi professor wa zamaphunziro, zamkanikatu,
Dikirani, pa2019 May abwereranso Ku America ameneyo
Kma amalawi simupenya maso olo mulinawo,zosankho zachitika chigawo chapakati kudakakhala kt ndikumwera kpna kumpoto mcp idakagwa kwambiri muone masiyanidwe ake.
mcp idzalamulira Tembo akazabwerela pa mpando wake apo biiiii ng’Ooooo mwalemba mmadzi
Ndale zamasiku ano sizotembelera ngati zakale koma zatsala ndizowelengera. apapa mukawelengera statistics DPP is still a threat in central region.
mcp siingalamulexo malawi! muzngovutka ndntima kumavotera zoluza ha!
Anthu ake ati atopawo kodi? A ku Dedza. Mchinji Kaliyeka basi. A ku Kasungu avotera DPP kwawo kwa Kamuzu oamati anthu utatopa iweyo. Kodi anthu unenawo apanga represent what fraction of Malawi? Samalani2w019 ndi mma region as usual. Afe wa ku Thyolo tione ngati Mcp ikapeza mavote
Apa zakhala bwino yawina MCP, tsopano ndi nthawi yoti DPP ikonze molakwika. Ndiye usanyadire lero kuti yawina, chifukwa anzakowono sukudziwa kuti aganizano zotani. Pamenepo, yaperekano mangolomera anaona a Chair ndiye uwone zichitike tsopano.
True
Kkkkkkkkkkkk Chathibula Koma MCP
Tikufunatitapangazakwathu koma DPP ikutitchinga….out DPP!
kkkkkk lindani madzi apite kaye a kongeresi pakuti dpp yatsikiranso komweko
Kuzima zima kwa magetsi kwatikwana plus njala kuba ndalama zaboma eeish tionepo zina
kkkkkk muonepo china chatsopano chani ?khansalayo kapena muona ngati mwatsintha president?moya akulamulirani mpaka 2024 woooo!
Eeeeee ndiye mbonaona mbonaona heeey!!! Kkkk
bola kongelesi must come back
Mcp ikawina ineso nd kubwerera kumalawi pompopompo nd zapitirize my business
Tikufuna ufulu ife osat ukalakhura next page akunga iya
guyz ngakhale MCP ikutsogola u must know that inakalamba izatilamulira ndi ma plan akale opanda magets
Atolankhani akumalawi amenewo,mwatiuza kuti chipani chosusa chapeza ingati nanga cholamula ingati?ndiye mbonaona ilipati pamenepa?apapa zangoonesatu kuti nanu ndi a MCP tu
inu anthu akumwera othawa nkhondo kumozambiki “mukati chosusa ndiye kuti chiyani?ndichichewa chake chiti mumayankhula inu?,
kaya ufuna kaya sufuna MCP ikulowanso 2019,apo bii ,ndiyekuti mudzabelenso ngati nthawi ija,
Nkhani ili apa siyolowa m,boma nkhani ili apa ndiya atolankhani opanda nzeru,komanso olo Mcp yanuyo italowa m,boma palibe chingasinthe chifukwa Malawi ndi Dziko loyima palokha koma lilibe ma resources okwanira kuti lingathe kuyima palokha,even banja lodalira makolo kumakuthandiza akasiya kukuthandiza limathapo.Tikati uyu ndi osusa timatanthauza kuti wa opposition popeza chichewa simumamva ndiye mwina kachizunguka mumvako
MCP Bomaaaaaaaa
Kwaaaaaaaaachaa
Akadayeneleka kutenga mipando yonse poti nkwao a MCP WO! Apo bii 2019 alira ndthu coz kummwera kuno sangapeze olo mpando,
Kodi chilipo chipami chomwe chalandidwa mpando? I mean ngati wakaleyo anali wa MCP ndiye watsopanoyi ndi wa DPP and vesa vesa? Anali ndi ma gap (ward and constituencies) ambiri ndani between MCP and DPP. This is well celebrated and the media is so stylish in writing the victory of MCP. Had it been that DPP has won, it could be labeled the rigged elections as we all started hearing of headlines that DPP is rigging elections in mchinji and kasungu. Ndale za masiku anotu ndizowelengera (statistics) osati zotembelera ngati kale.
Eya akulu talanda Kaliyeka inali ya DPP
Congratulations Moyowina
Come 2019. Dont change the muzik. Must be the same way it is now. Keep APM to help other parties gain vote. Dpp stands for Dictatorship poverty movement kikik. No hard feelings its part of the game. These are just symtoms of kamwadzi.
Mkandawire, every competition has preparations and priority plus winning formula. Let’s draw a small lesson from soccer. When a team is playing for a cup game shifts an objective towards the cup no matter what it takes for them to win as compared to a league game.
Man ine 2019 ndikudzaponya tambala wakuda m’bwalo
Malota, we don’t know how many will vote for open lock or maize cobs.
Kaliyeka councillor anali wa DPP-meaning kuti DPP won back two seats out of three they held namely-kasungu , zomba and lilongwe.while MCP retained 2 of their seats ( mchinji and dedza)and snatched one from DPP.
That’s democracy and it is a good development
No dpp mp n kaliyeka ndani amakunamizaniyo. mumazisata bwinobwino koma kapena mumangomvela kwa ena ?
Tikuti kwachaaaaaaaaa !! Eeeeeeee!! Dzukani a Malawi azanga . Osamaguti woooooo ayi kupenga eti !.
Sanayithibule coz kunali kwawo kwa mcp koma mukanawina kumwera nduye tikanayamika.
koma iweeeee!! 2019 size yomweyi.
Come back mighty MCP with new vision approach, you can’t miss this opportunity out.
Malawians are lost with no vision and no future.
Kwaaaaaaacha!
No doubts mighty MCP will bounce back again, believe it or die.
Come 2019, no any dubious fraud of electoral data capturing tricks, we are awaiting.
No more burning election storage.
My vote awaits for a prosperous Malawi.
MCP mukane muvomereze nokha adzawina chisankho chapa 2019, pali anthu odzindikira zinthu bwino mu dzikoli, osati kutengeka ndi mkuntho wa Ku America ayi,
Malawi Ali pangozi, pamavuto oti mwina ngati sipapedzeka mtsogoleri waphindu woganizira zabwino za dziko kuposa zache, basi tiiwale za ufulu womwe tinaupezera mokhetsa mwazi mu1964, ndipa 1994, kusintha kwa zinthu pa ndale mu Malawi.
We want change not Mtalika brothers.
Zosadabwitsa,central region ndi mmene zimakhalira
Chipani chafuko lose la Malawi!D P P !!!Tilowaso 2019 Nde Muone NU Mmene DPP imanyamulila Mipando Kumangoni! kkkkkk Tiona 2019 Yomweyo! Atcheya APM 2019 Bom kkkkkk !!!
Kwanu konkotu
Man mudzidyeratu za Dpp zo coz tambala wakuda akangolowa yese wakumba ndalama za Bom ndi nyakula,kukamuwerengera ma step akamakalowa mumchitokosi and ija ya Red ija idzabwereranso kkkk plus achinyamata akuvutikawa onse akalowa ku Young Pioneer,zonse zidzabwerera,koma.kuweta ng’ona kokha ayi kkkkkk
ndimmene zidzakhalire 2019 mcp woye
Woyeeee
Kuwina ndi kuwina basi olo utawinira penalty chifukwa DPP ndiyolamula apa ikuyenera yokha izifunse kuti tikulepheta pati ? Otherwise mmmmmmm
Had dpp score hatrick as has done mcp, mbc radio and tv adakayambitsa maprogram onyoza mcp that would have their bootlicker boy PB as the anchor. I feel very sory for this boy!
Iye Ujadi Bwanj? Amandbwadwtsa Heavy Mm
bwana Phillip Business kunyambita masokosi a Nyapapi
Mpira umenewu uliponso 2019 uwu unali Friendly chabe koma 2019 ndkulimbirana chikho pakadali pano chikho ikusunga ndi Mighty DPP,,,,pempho langa kwa MCP musatope ndikutrainer poti mwagonjetsa DPP 3-2
Kongeresi ndi yanthu osazindikira mbuzi
iweyo ndiye mbuzi monga sikudziwa MCP for life
Dpp ndi ya anthu akuba mbuzi za mano kusi
Zaonetseratu kuti mcp siingalamuledi pa malawi pano.Sindikuona chomwe mukusangalalira apa cos alibe chomwe chasinthapo apa come 2019 DPP idzawinabe basi.
Pakamwa palibe amayembekexa ndi momwe MBC imakokomezera zoyambana kwa mu MCP
Iwe Kalieka ward kunali councillor wa DPP lero kuli councillor wa MCP that means MCP is a mighty party to defeat the ruling party
olo ndikuuzeni kuti musove,simuthanso vuto lake.kkkkkkkkk
Koma pali mbonawona pamenepo mcp 3 DPP 2?? amtolankhani apa malawi kkk DPP apapa ndiyo yalowa mkati mwa mcp ndikuwina kk
Apa kwa away zayenda bwino mcp izasamale ikadzabwera pa home ya dpp
What next ? kkkkkk
2019 MCP Boma
Aiziwe line…
2019 MCP Boma
Devils People s Party woyeeee (dpp)
This is just the beginning of thunder storms, the rain is coming 2019!
Kusowa Nkhani
ingoyenela kuthibulidwa tatopa nalo bomali
Eti kumakopa anthu ndi mpunga kkkkkkk
Mcp3 dpp 2.waziziwA.
Kkkkk Koma Kumeneko!
Imeneyo Ndiye Mcp Simanyengelera. Kwachaaa!
Koma ndiye kui chemelela mcp kkkkkk mpaka ithibula Dpp kkkkkk..
kunyambitana ndikosayamba