MCP ithibula DPP mu zisankho zapadera

Advertisement
Lazarus Chakwera

Chipani chotsutsa cha Kongeresi chaonetsa mbonaona chipani cholamula cha Democratic Progressive mu zisankho za padera zimene zinachitika mu madera asanu a dziko lino.

Chimake cha zisankhozi chinali ku Mchinji kumene amasankha phundu wa nyumba ya malamulo.

Kumeneku phungu wakale wa chipani chotsutsa a Billy Kanjira anamwalira zimene zinapangitsa kuti kuchitike chisankho cha padera.

Peter Mutharika and Lazarus Chakwera
Mutharika (l) Chipani chawo chaposedwa ndi cha a Chakwera ). (File)

A chipani cholamula anachita misonkhano yamphamvu ndipo mtsogoleri wa dziko lino a Peter Mutharika anapita kumeneko kukawaopseza anthu a ku deralo kuti ngati asankhe phungu wa chipani chotsutsa, iwo sazaonanso chitukuko.

Koma kuopseza kwa a Mutharika kukuoneka sikunaphule kanthu.

Pa zisankho zimene zinachitika lachiwiri, anthuwo anavotelanso phungu wotsutsa wa chipani cha Kongeresi.

Kupambana kwa mpando wa phungu kwa chipani cha Kongeresi mu dera la ku Mchinji kunapitilila pamene chipanichi chinapambananso mpando wa Khansala mu dera lina ku Kasungu ndi lina ku Dedza.

Chipani cholamula cha DPP chinangokwanitsa kupata mipando iwiri basi ya Khansala, wina ku Kasungu ndi wina ku Zomba.

Advertisement

220 Comments

 1. 2019 boma DPP a aaaa paticia kaliat ndi ana ake Kondwani Nakhumwa ndi ana ake Geme kalilani ndi ana ake Henery musa ndi ana ake Godwel Ngondwe ndi family yake basi afisi amenewa ndi omwe azavote ine ndi ana ndizakhala ndili ku munda

 2. You are happy with that?Expect to cry so loudly in 2019.Will the goaltender be the same one?I mean the believed to have fallen off God’s hands?Abale tidzamwanso wa mkaka mtheradi.

 3. You are happy with that?Expect to cry so loudly in 2019.Will the goaltender be the same one?I mean the believed to have fallen off God’s hands?Abale tidzamwanso wa mkaka mtheradi.

 4. Where is Malawi Voice? Ana a njoka inu mwathandiza kugwesa DPP ndi ma propaganda anu. Ichi ndi chiyambi cha kulephera kwanu mu 2019. Paja ku mbali ya DPP mutsogoleri wokopa anthu ku MC anali ndani?

 5. *DON’T LAUGH ALONE, ABEG!!!!!!!*

  A man woke up and shouted “Holy Ghooost Fire !!! ”

  *Wife:* what is it, was lion chasing you?.
  *Man:* that would have been better.

  *Wife:* what is it then?
  *Man:* I nearly voted Peter again in my dream OOooo.
  *Wife:* Blood of Jesus! Honey, lets pray.

 6. Mp anamwalirayo anali wa MCP ,atenganso mpando wao a MCP wa. Mukafuna mpikisano kapangeni kumpoto kopanda achewa kapena alhomwe

 7. Iwe umafuna kuti nawo otsutsa asapeze mpando kkkk koma ndiye zikakhala choncho ndiye ndi democracy kapena ai,zakhala bwino koma dpp sikuopa kalikonse palibe nkhani apa

 8. kupanda kubela 2014 sibwezi muli otsutsa? tivomeleze opepela ndife amalawi.mcp akukangana akuyambitsa ndi a dpp musiyeni Chakwela sindine wa dpp or mcp

 9. If DPP is managing to secure position in some parts of central region.Then mcp must be very careful. Because DPP capitalise on southern region. Not central. So its my advice to mcp to make sure u push harder to gain popularity in south. Otherwise DPP is very strong.

 10. Mavuto aliko cozMCP ndiyachigawo chapakati ngati DPP yakwanitsa kutenga mKasungu zaonekeratu kuti DPP 2019 boma! ilipaliponse MCP ilipavuto ayilowera kuchipinda!

 11. Anthu sakukondwa ndi momwe dpp ikupangira ndondomeko zake.ziri ngati m’nyumba muli njala nde bambo m’malo moti agule chakudya iye akuuagula galimoto.kodi tinene kt bambo uyu akuganiza bwino?

 12. As usual I have been saying that MCP can’t win a national elections because it is a region party. What a type of a party is MCP just based on central region. Mr MCP come and penetrate here at Southern region if you want to win 2019 because it’s where the majority of people are.

 13. Congratulations MCP…….. when the opposition party does so……it tells people needs change………mo fire…….buuuh.

 14. Kodi akanyimbi inu mukukangana chiyani? apa MCP itenga boma 2019 osati president wotha mano central ndi ya Chakwela Kwacha Idzuke Malawi Ndimkale Idayambila Kugona Nthawi Yakwana Yoti Amalawi Azindikile Chabwino Poti Choyipa Tachiwona Kuchokela Ku DPP, PP $ UDF vipani vowononga dziko muli kudzikonda,umbava,njala, Cashget komanso umbuli mamphunziro alowa pansi ndiye akanyimbi mukukamba zopusa poti mbava ndi inunomwe panyapanu kkkkkkkk

 15. Kodi akanyimbi inu mukukangana chiyani? apa MCP itenga boma 2019 osati president wotha mano central ndi ya Chakwela Kwacha Idzuke Malawi Ndimkale Idayambila Kugona Nthawi Yakwana Yoti Amalawi Azindikile Chabwino Poti Choyipa Tachiwona Kuchokela Ku DPP, PP $ UDF vipani vowononga dziko muli kudzikonda,umbava,njala, Cashget komanso umbuli mamphunziro alowa pansi ndiye akanyimbi mukukamba zopusa poti mbava ndi inunomwe panyapanu kkkkkkkk

 16. Central region is always been MCP strong hold,thinking DPP wud win there, is asking too much,besides that the ruling party has been making head lines for wrong reasons together with all miceries the pple facing, I don’t think thy cud make in rods in those areas.

 17. That is really true Harold. You can just worst your time and drop down yourself; just focus on how you can achieve yourself on daily basis. These days politics is abusiness game “Amacoka atalemera, kwambiri antuwa ndicifukwa or materm (2) onse walamulira kale muzaona akufuna azipitilirabe kulamulira, why??? it’s simply bcz zima alemeretsa.Muligeni misonko yonse imapita m’mathumba mwao osati kwaantu wamba, Ndiye my point is that: we have frustrated to believe in those governments now!!

 18. kulimbana ndidzandale mudzingotaya nthwiyanu asogoleri onse ndi atambwali amangofuna kukhutisa mimbazaobasi ndiyetisanamizane kuti adzabwerawina ndikudzasinthazinthu chachikulu amalawi anzanga tigwire ntchito zotukula mabanja athu kulimbana ndindale tingotaya nthawi anthuwa amadziwana

 19. Just as I believe would have been the case had it been that the by-elections were held in the Lhomwe belt, the DPP was obviously going to conquer as the MCP has just done in Mchinji and other areas. Typical of ndale zapa Nyasalande. Wake up mother Malawi

 20. Ndaona vision ku Mpoto pakati onse ndi MCP ,,mutchona ndiku mwera,,,Chakwera anasiya Ubusa anatumidwa ndi Mulungu kut ziko la Malawi ali phule pa Moto Amen 2019 kuwina kwa Bwino

  1. Kod mukut dpp 2019 bomanu ufiti, usavage, kukhwima chan? Anthu oipa inu

 21. Siyani zoyendera kuti ndiwakwathu tamakulani mdimokalase plz, amalawi. Sankani msogoleri okonda ziko lakwao oti alindiukadaulo oti atha kuisintadi Malawi ndikukhala okoma mzonse, abweretse zitukuko ponseponse osati kusanka zigawo ayi, (osati zimene mukunenazo wakumwera, wapakati, kapena wakumpoto. Zimenezo sizingathandize ayi kulani mu Democracy imveseseni tantauzo lake)

 22. Mcp, dpp, udf, pp ntchito zawo nkunamiza amalawi ncholinga chowadyera masuku pamutu. Chofunika apa ndikukozanso constitution kuti mtsogoleri asamakhale ndi mphamvu zambiri

 23. Mmmhhh MCP ndi central region only, if DPP is getting some votes in central region then 2019 izalowanso m’boma opanda kupikisana nae. MCP singadzawinenso chisankho cha president koma idzingokhalira kutsutsa basi in the parliament anzao akulamulira

 24. Malipota M C P Ndi A Zbs, Ndamoz Onse Ndo Chewa, 2019 Muzaptanso Ku Khot Cauz Muzafaso, Mot Muone Kt Mwasyana Bwa Kmas Ndi Kwa Mcp, Musamalet Inu Ndamene Mumaymbitsa Chisokonezo

 25. Realy? glad to hear this. mwano siundula ANC ukulira pano chifukwa cha mwano. don’t think people are fools they know they hear they see. inu mukuti 2019 DPP boma m’phunzire poti chipani chanu ndi akaswiri obera mavoti tizawona koma simungabere kawiri tikungoyang’ana

 26. kkkkkkkk amalawi mundisekesa kwabasi or zitavuta maka central singachoke pa MCP muziwe DPP ndiya kumwela ndiye mavote anachitikila kuti mupeza malo ambiri ndi ku central tipite kumangochi UDF kkkkkk

 27. Peter,chakwera Ndi Atupere Alephera.Koma Ndikufuna Mcp Itawinako Mu 2019.Kuno Kumwera Ndayamba Kale Kutchola Mano Ofuna Kundithandiza Tilumikizane.

 28. Momwe ndikuwonera M C P ikhoza kuzachita bwino 2019 ngat atakhala president wina osati chakwera,koma othawa mulungu mcp sizachita bwino ayi mwina ku mp komweko zizakhala better komanso ulamulira wabwanawa aaaah ukuvutirapo
  mavuto alipobe dziko muno

 29. Thus what we call, civilization. .only fools go to pouring station but to vote for failures! A chair said., no body eat politics but development indeed. ….

 30. Mwacisanzo cabe Kuno Zuma akugwa pakalipano cifukwa Cosasatila zimene antu akufuna akumidziko kuma branch ndiye kaya tizamvera momwe zizayendera pazisanko zazikulu 2019 kumeneko koma na maripotio enewo zayamba kuavuta ngatisasinta magiya azagwa mu 2019.

 31. That’s what happens when the ruling party does not lessen to people on the ground and when the leader is selfish

 32. Pepani ndiyerekezera, Mpamvu zachipani zili kumabranch Enafe tinasiya kusapota zipani cifukwa ndinazindikira mocedwa kuti ndikungotaya ntawi yanga m’malo motukula pakhomo ndimakhalira kuyendayenda kumapanga ma campaign, Ndinali mlembi okonza zamisonkano like District organising Secretary, So ndimaziwa kumene kulimpamvu za Cipani.

 33. Even one amanyamula world cup! MCP you beat goverment and oposion UDF! He use goverment resouces, like car, radio, mike phones, and time for goverment, water, ndikuluzanso, Haaaaaaa

 34. ine ndikufuna kuziwa kuti maderawa onse anali achipani chanji? chifukwa apa mukunena ngati kuti onse anali adpp ndiye mcp yalanda Dpp isalamulabe paka kale

 35. The point is that if the ruling part doesn’t gain ground and the opposition maintains its stronghold there is nothing to lose to their part but in the other way i can say that the Dpp government has nothing to offer it will packing bags come next election.

 36. Congratulations to all the players, on the free, fair and credible bi-elections conducted over some parts of the country on 1st November, 2016, It is not easy for the opposition to win, if a playing field was not leveled fairely. Bravo the ruling party for showing maturity, honesty, progressive democracy and rule of law.

 37. Dpp pempho langa ndiloti 3:2 ndipafupi mutha kubweza mukapita ku dressing room mukakoze molakwikamo poti kubweza kumawawa kusiyana ndi kuyamba mukapanda kusamala 2019 akukwapulani osati masewera amalawi anachenjera

 38. Ayi zawonetsa kuti anthu akuona mmene olamula akumapangila zinthu ngati ali wokha kale kukhala chibwelezs chotchi ndie kuti kaya kunaloi otsutsa olamula amatenga basi koma apa mwina olamulawo nimwai kuti awone bwino mngakhale akuti sanatenge wawo komabe ndie kuti anthu ali ni chikhulupoililobe ni otsutsawo

 39. mukati mcp idakalamba ndiye mukunama zd,komaso atso ambiri kuchipanichi ndi anyamata ngati chakwera ndi ena,kuika munthu okalamba kale pampando ndikulakwa zd ndizmene tikuziwona lerf kusowa mfundo yoti ugwirepo ana ndiye apanga bwanji?kumangowombana mizu palibe chanzeru amapanga chomwe walota usiku osati kuganiza.Olamula amafunika azitsogola osati kubwelera mmbuyo ayi chipanichi chapendekera.

 40. kkkkkkkkkkkkkkkk koma inu muvutikiranji mu Ntima koma zowona inu mukamakhala mukuganiza kut Dpp muzaigonjesa???? Inu inu musamasausike mu ntima plz.kkkkkkk a mcp mukundisangalasa mwamva. Phuma lake limeneli muzawine inu?? Nanga kachisankho kake kameneka koma kukhala ngati wawina ndi chakwera??? ndie ngati ali chakwera ndie amulumbirisa Liti?? Kaakakakakakakakakakaka kkkkkkkkkkkkkkkkkk zomvesa chisoni. Koma zoti muzimvere chisoni chifukwa choti dpp ikulowa ku chipinda cha mcp simukuona??? Ai ndithu. Isamaleni dpp ndithu izakulizani musakaike

  1. Malawi Queenz yabwelako number chan ku fast5 competition adala inu? Bwanji mmene dziko lasangalila wait and see wat wil going to happen in 2019.

  2. Mutayeni kape uyo man!ukamalimbana ndichitsilu oona sasiyanitsa,mavuto onse abwela chifukwa cha dpp wa alipo yemwe sakuwaonayi?i

  3. Which dpp?mukamakhala ndiganizo loti tikusankha chipani ichi kt chitithetsere mavuto,mudzafa muli amphawi ndithu,pemphani Mulungu akukonxereni mavutowo anenena Yekha kt pempheni ndipo kudzapatsidwa kwainu,ndiye mutukwana zipani zingati popeza boma linalililonse lilindimavuto ake,tidzisankha boma poti ndimwalamulo osati chidwi chathu chonse kwaboma tidzingolira mpaka kale,palibe boma lidzabwere mkudzathetsa mavuto alidziko muno never and never,lets work hard at our level and seek the glory of GOD to guide us,kma kumapanda kutero ndimayo ine mayo ine mpaka kale,zomwe akwanitse akwanitse kma osati boma ili lokha lichepetsa mavuto forget about that my dear friends,akamalowa boma amachita kt eeeya nthawi yakwana yotha mavuto athu,wakuva wava osava akhale thamks

 41. Ndale za Democracy ndi choncho apopo zikusonyezerathu kuti antu akufuna MCP Ibwererenso mboma ndekuti, DPP atopa nayo. Bcz if the ruling party is coming behind it shows exactly that more majority needs MCP to take a rule now. Also we says; you can’t allow to be beaten inside your own house with a strange person. Only he can manage to beat you if you’ve lost power. So in these reports it shows exactly that APM is losing power as of now%#

  1. national election is complicated Owen. MPs and Counselors are voted by relations that know them within those area but a president is voted for the whole nation

  2. national election is complicated Owen. MPs and Counselors are voted by relations that know them within those area but a president is voted for the whole nation. Ask Tembo. He had a majority of Mps but lost presidency.

  3. Zakuti mcp singawine kumwera maganizo ameneo ndi omwe adzakomoketse Dpp 2019 becoz it will be caught by surprise. Pple are now getting matured in democracy, are now tired of ushering crooks into power though own relations. They want trustworthy leaders who will do their best to bail out Malawi from this untalkable poverty for betterment of the future of their children.

  4. Ndale zazigawi, izotu ndfizimene zaika Malawi pangizi, kukavotera Mtshona wakalekale Ku a America, wakwathu wakwithu, wakwidu, sidzidzapindula a Malawi.
   Southern, Central, Eastern and Northern make Malawi not South yekhayo angathane nazo zovuta,
   Izotu zaskukanikani.
   Wakwathu poti ndi professor wa zamaphunziro, zamkanikatu,
   Dikirani, pa2019 May abwereranso Ku America ameneyo

  5. Kma amalawi simupenya maso olo mulinawo,zosankho zachitika chigawo chapakati kudakakhala kt ndikumwera kpna kumpoto mcp idakagwa kwambiri muone masiyanidwe ake.

  6. Anthu ake ati atopawo kodi? A ku Dedza. Mchinji Kaliyeka basi. A ku Kasungu avotera DPP kwawo kwa Kamuzu oamati anthu utatopa iweyo. Kodi anthu unenawo apanga represent what fraction of Malawi? Samalani2w019 ndi mma region as usual. Afe wa ku Thyolo tione ngati Mcp ikapeza mavote

  7. Apa zakhala bwino yawina MCP, tsopano ndi nthawi yoti DPP ikonze molakwika. Ndiye usanyadire lero kuti yawina, chifukwa anzakowono sukudziwa kuti aganizano zotani. Pamenepo, yaperekano mangolomera anaona a Chair ndiye uwone zichitike tsopano.

  1. kkkkkk muonepo china chatsopano chani ?khansalayo kapena muona ngati mwatsintha president?moya akulamulirani mpaka 2024 woooo!

 42. Atolankhani akumalawi amenewo,mwatiuza kuti chipani chosusa chapeza ingati nanga cholamula ingati?ndiye mbonaona ilipati pamenepa?apapa zangoonesatu kuti nanu ndi a MCP tu

  1. Nkhani ili apa siyolowa m,boma nkhani ili apa ndiya atolankhani opanda nzeru,komanso olo Mcp yanuyo italowa m,boma palibe chingasinthe chifukwa Malawi ndi Dziko loyima palokha koma lilibe ma resources okwanira kuti lingathe kuyima palokha,even banja lodalira makolo kumakuthandiza akasiya kukuthandiza limathapo.Tikati uyu ndi osusa timatanthauza kuti wa opposition popeza chichewa simumamva ndiye mwina kachizunguka mumvako

 43. Kodi chilipo chipami chomwe chalandidwa mpando? I mean ngati wakaleyo anali wa MCP ndiye watsopanoyi ndi wa DPP and vesa vesa? Anali ndi ma gap (ward and constituencies) ambiri ndani between MCP and DPP. This is well celebrated and the media is so stylish in writing the victory of MCP. Had it been that DPP has won, it could be labeled the rigged elections as we all started hearing of headlines that DPP is rigging elections in mchinji and kasungu. Ndale za masiku anotu ndizowelengera (statistics) osati zotembelera ngati kale.

  1. Come 2019. Dont change the muzik. Must be the same way it is now. Keep APM to help other parties gain vote. Dpp stands for Dictatorship poverty movement kikik. No hard feelings its part of the game. These are just symtoms of kamwadzi.

  2. Mkandawire, every competition has preparations and priority plus winning formula. Let’s draw a small lesson from soccer. When a team is playing for a cup game shifts an objective towards the cup no matter what it takes for them to win as compared to a league game.

  3. Kaliyeka councillor anali wa DPP-meaning kuti DPP won back two seats out of three they held namely-kasungu , zomba and lilongwe.while MCP retained 2 of their seats ( mchinji and dedza)and snatched one from DPP.

 44. Come back mighty MCP with new vision approach, you can’t miss this opportunity out.
  Malawians are lost with no vision and no future.
  Kwaaaaaaacha!

  1. No doubts mighty MCP will bounce back again, believe it or die.
   Come 2019, no any dubious fraud of electoral data capturing tricks, we are awaiting.
   No more burning election storage.
   My vote awaits for a prosperous Malawi.

  2. MCP mukane muvomereze nokha adzawina chisankho chapa 2019, pali anthu odzindikira zinthu bwino mu dzikoli, osati kutengeka ndi mkuntho wa Ku America ayi,
   Malawi Ali pangozi, pamavuto oti mwina ngati sipapedzeka mtsogoleri waphindu woganizira zabwino za dziko kuposa zache, basi tiiwale za ufulu womwe tinaupezera mokhetsa mwazi mu1964, ndipa 1994, kusintha kwa zinthu pa ndale mu Malawi.
   We want change not Mtalika brothers.

 45. Chipani chafuko lose la Malawi!D P P !!!Tilowaso 2019 Nde Muone NU Mmene DPP imanyamulila Mipando Kumangoni! kkkkkk Tiona 2019 Yomweyo! Atcheya APM 2019 Bom kkkkkk !!!

  1. Man mudzidyeratu za Dpp zo coz tambala wakuda akangolowa yese wakumba ndalama za Bom ndi nyakula,kukamuwerengera ma step akamakalowa mumchitokosi and ija ya Red ija idzabwereranso kkkk plus achinyamata akuvutikawa onse akalowa ku Young Pioneer,zonse zidzabwerera,koma.kuweta ng’ona kokha ayi kkkkkk

 46. Kuwina ndi kuwina basi olo utawinira penalty chifukwa DPP ndiyolamula apa ikuyenera yokha izifunse kuti tikulepheta pati ? Otherwise mmmmmmm

 47. Had dpp score hatrick as has done mcp, mbc radio and tv adakayambitsa maprogram onyoza mcp that would have their bootlicker boy PB as the anchor. I feel very sory for this boy!

 48. Mpira umenewu uliponso 2019 uwu unali Friendly chabe koma 2019 ndkulimbirana chikho pakadali pano chikho ikusunga ndi Mighty DPP,,,,pempho langa kwa MCP musatope ndikutrainer poti mwagonjetsa DPP 3-2

 49. Zaonetseratu kuti mcp siingalamuledi pa malawi pano.Sindikuona chomwe mukusangalalira apa cos alibe chomwe chasinthapo apa come 2019 DPP idzawinabe basi.

Comments are closed.