Mtsogoleri wakale wa dziko lino a Bakili Muluzi wati ndiokhumudwa ndi imfa ya mkhala kale pa ndale a Gwanda Chakwamba.
A Chakwamba amwalira dzulo pa 24 Okutobala masana pachipatala cha Blantyre Adventist mu mzinda omwewo wa Blantyre atadwala kwakanthawi kochepa.
Sabata latha nyuzipepala ino inakupasilani nkhani kukudziwitsani zakudwala kwa malemuwa omwe amadwala nthenda ya mtima ndipo anagonekedwa pachipatalapo mpaka dzulo pomwe atisiya.
Poyankhulapo pa zaimfayi, mtsogoleri wakale wadziko lino a Muluzi omweso anagwirapo ntchito ndi a Chakwamba, ati ndiokhumudwa kwambiri ndiimfayi.
Muluzi wati adzawakumbukila malemuwa ngati munthu olimbikira komaso osabwelera mmbuyo akafuna kupanga zinthu ndiposo opanda mantha.
“Ndinauzidwa kuti Gwanda wamwalira. Ndimadziwa zoti anali kuchipatala ku Blantyre koma ndimaganiza kuti akhala bwino ndipo nditava za imfa yawo ndamva chisoni komaso ndakhumudwa kwambiri.
Chisoni chikubwera chifukwa ndinawadziwa a Chakwamba zambirimbiri zapitazo, enafe tili anyamata tikuyamba kumene ndale. Tinagwilira ntchito limodzi mu mchipani cha MCP komaso cha UDF ndipo ndikufuna ndipepese kwambiri kumtundu wa a Malawi kamba ka imfayi” wadandaula Muluzi.
Mogwirizana ndi a Muluzi, mtsogoleri wakale wa chipani cha MCP a John Tembo, nawoso ati imfa ya Chakwamba yawakhudza kwambiri.
A Tembo ati ngakhale ndi a Chakwamba nthawi zina samagwirizana, koma malemuwa anali olimbikira pa ndale ndiposo mumchipani komaso amadziwa chomwe amapanga ngati namandwa pa ndale.
A Gwanda Chakwamba amwalira ali Ndizaka 82 ndipo anabadwa pa 4 Epulo 1934 ndipo wasiya mkazi, ana atatu, zidzukulu zitatu komaso zidzukulu tudzi zinayi.
BAIBULO LINATI TIDZAFA NDITHU INU MUKUDANDAULA CHANI. MUNTHUYONSO ANALIBE CHAKUDYA/ POGONA INU MUNALI KUTI
Pepani ofedwa amen
Guyz Ziwani Ichi Mu2 Amafuni Akamwalira Bakili Sanayenera Kudandaula, Ndikupanda Zeru Kwawo Mumva Kt Athandiza Maliro Kusiya Mu2 Ali Kuchipatala.
He is a bg fool Malawi ali pa moto lero coz of him Tabela ma vote ndikulowesa alomwe ake aku dzuza Malawi lerowa.
Ziwani ndale zindikila andale .ndiamozi awa timadana ndife osatila
Dziko la malawi ngati lidasauka ndi chifukwa cha iwe bakili, udagulitsa ma company, udapha anthu ofunikira, udayambitsa kugulitsa ziwalo za anthu, ndiye lero ungave chisoni ndi ifa imodzi.
Chakwamba pa 17 may 1973 ndi amene anamenya mafumu ku nzuzu kuwatibula ameneyo angakhale pulezidenti anatero a tcheya
Rest in peace.
Obvious
nzimu wa gwanda use mtendere ameni
Assaaa asatinamizepo apa nkhani ndi nkhawa kuti who wanner be the next
Choti anthu inu muziwe musiyanise nthawi yaka mpeni ndiya imfa ndi zithu ziwiri zosiyana anthu nthawi yakampeni amayankhula zandale cholinga awine kumbali yawo koma akachoka pa msonkhano anthu aja amagwirizana palibe cholakwika Tempo & Bakili chifukwa si nthawi yandale inu ngati muli mbuli pa ndale ndichifukwa chake mukuyankhula kuti Bakili &Tembo asayankhulepo kathu ndiwe mbuli pandale ndale siwudani ayi mbuzi ya munthu iwe asiyeni anthu akhuze maliro
May soul rest in eternal uncle
Amati azikhalabe moyo mpakana ku?.asampanse minyama Gwanda.siyeni kut naye akapume ndi angelo
Amen!may his soul rest in peace in Jesus name!
Rip mbuya mwana zwele nkhabe wamuyaya tayi
Amalawi tiyeni tisiyanise ndale ndi imfa chodandaulisa ena akunyoza why munthu amamvera chisoni munthu nzake tiyeni tikhudzike ngati amalawi
Rip mbuya mwana zwele nkhabe wamuyaya tayi
Rip mbuya mwana zwele nkhabe wamuyaya tayi
Rip mbuya mwana zwele nkhabe wamuyaya tayi
Mchiyan kod amalawi tidzasiya liti kunyozana nduthenga wamalilo womwe o malawi tikadavutika
Bakile wati wachita bwanji ndi imfa ya Chakuamba? Koma anthufe mulungu azingotikhululukira. Chomwe timayankhula nthawi zina sitimachidziwa, zomvetsa chisoni kwambiri.
Kodi mukamati Mtsongoleri wa kale wadziko lino mukukutathauzanji? Poti ena amene akuwelenga nkhaniyi ali kumaiko akunja. Ndiye adziti Dziko lake liti pofuna kuitsata nkhaniyi?
You are very much aware that the post you are commenting on is Malawi 24 .
Chakuwamba pa 17 septmber 1972 ndiamene anamenya makofi mafumu okwana 19 kwa achikula including amfumu achikumbu ndan sakuziwa bwino. Muse mumtendele madala zimachitika
bakili ndiwabodza suja amkati chakwamba ndimunthu oyipa nde lero chisonicho chilipati
paumunthu ayenela kutelo takumbukilini pakati abingu ndi abakili zinali bwanji? koma kumwalira kwa abingu abakili anakhala nawo zimasiyana ndichidani cholimbilana ufumu wa pamudzi chimakhala chamutima koma zandale zimakhala zanthawi yomweyo akulimbanayo zikatha amayambaso kumwela limodzi inu kutsala tikulumana zopanda tchito
Rip nana
Munthu Akafa Amakhala Wabwino Koama Ali Moyo Sitimukonda Zaonekera Apa
Chakuwamba ndiamene adamenya makofi mafumu 1973
A tembo mukuwanamizila
we are proud of you guys, you did a lot to our country and we still appreciate your presence as retired soja we rilly appreciate and we will still consulting you in different ways, but now give us the room, I mean give the chance to us the youth and let us develop this country technologically, machinery and man power development we have capacity to build this country but our chances are limited and we are here now to break that boundary our slogan is POWER FOR THE YOUTH POWER FOR DEVELOPMEND
muthudi amakoma akafa.RIP Gwanda
Umakhala wabwino ukafa
zakhala bwino kuti mwambo umeneu ukayendetsedwe ndi boma pasakakhale kaka la cipani azipani mumonjeza kulankhula
Pa ndale munthu amaipa ali ndi moyo koma kumwalira dziko lonse cisoni.Tiyeni tizikondana a Malawi ncoonadi.
Bakili muluzi ngakhale atakhetsa msozi kwa ine sindingakhulupirire madalawa amanyoza kwambiri munthawi chisankho nde chakuamba akome lero?????
Bakili simunthu oyenela kunenapo kalikose kokhuza Chakuwamba osangomusiya ause mumtendere bwanji lero Bakili aziti ndakhumudwa ndiliti adakhalapo wabwino Chakuwamba kwa Bakili Mulungu akanachita maye Bakili ngati amava chimunthu choipa chinaononga mtendere wa dziko lathuli samafunika ngakhale kukaponda pakhomo la maliro Bakili
Anamenya makofi mafumu 17 ameneyo angakhale mtsogoreli? Ayiiiiiii kkkkkkkk
Chitsilu Muluzi amangoononga CV ya anzake koma iye amadula ziwalo anthu muulamulilo wake
Chiladzulu
Komaso anamubela ma vote kkkkk ndikulowesa Bingu wa Mthalika.
Komaso anampha matafale bakiliyo
Kkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkk uyo
Anali muthu wabwini zimu wake use mu mtendele
Ndili okhumudwa pakut mfumu ya asena yatisiya ausemumtendele
akhumudwa buanj? iwo amafuna afe ndindan? mlaliki 3:1
Wakoma lelo poti wamwalila?
Ok
It was written that every soul will taste death. Its nt strange thing May his soul rest in peave
Rip
A Muluzi anamubela mavoti Chakuamba kawiri wapita wokhumudwa ndi a tcheya
Aliyense wakhumudwa sizonena za anthu otchuka okha apa mawa mulembe kut Lucius George wakhumudwa ndi imfa ya Gwanda Chakwamba
Apa mpomwe amalawi tiyenera kudziwa kuti andalewa amatipusitsa amaoneka ngati amadana koma kuseri akuchezerana.Ndikudziwa simungadabwe mukaganiza mmene muluzi amkanyozera gwanda koma agwanda anapitanso kukapanga mgwilizano ndi muluzi,tembo ndi muluzi bwa kunyozana wamagazi mmanja pamapeto pake kuzapanga mgwilizano ndi muluzi.Munthalika ndi muluzi bwa?koma ife atimkenaofe bwanji nkhani yomweyi inatchuka ya peter yi ndi chakwera kunali kutukwanizana pano pokomemta koma ayeni akewo akuimbirana ma phone mkumacheza patsogolo muzava apanga mgwilizano opusa mumakhala inu akumudzi mumakangana nkhani zaiii zo lerotu ndi awa
Ya ndikudabwananu a Bakili inu mwaziwa kuti a Gwanda!(ka ya mukuti a shati)alikuchipatala ku Blantyre inu osapita kukawaona anzanu andale ndiye mukuti mwakhumudwa ndichani pamenepo ?mukanakhumudwa alindimoyo ndikupita kukamuona mkulu wakalamba eti?koma uziti ndakonda potisiya agwanda ndiye zimveka ndimau anu oyamba aja
Zikut zakhumudwa chani mbava ziwirizo
Those who stole votes from him during his presidential candidate God is watching just confess
Bakili mene ukamunyozera Gwanda lero akuti anali olimbika pa ndale.tiyeni tizimuyamika munthu akanali moyo. RIP Gwanda Chakuwamba.
R.l.p
Kwasala tchire moto umapita kumeneko…..
AKOMA ATAFA…..
Anamenya mafumu kunzuzu kuphatikixa afumu achikumbu tikusowani
MESA AMADANA NAYE AMUBERA BERA MAVOTI EE NDIYE NYO NYO NYO KUTI CHANI AKAMUPEZA
Ndale ndichoncho siyanitsani ndale ndi umunthu politics its adirty game like wachionandani r.i.p mbuya
Basiakaphume anakula awasatile abaleawo asikapanga sandale enaanaya mba ukapheni awazo akapithilise
Chichewa cha chiyao ndipafb pomwe mdyomba?
Kkkkkkkkk a yao tulo
mau oikira maliro amenewa ngakhare mafumu pamaliro amauza anamalira kut ana tisamala ndiye osadabwa nd mau abakiliwo
Zonsezi!! Ndichifukwa Chakusamvela Kwa Kholo Wanthu Adamu Ndiye Uchimo Unalowa Dziko Ndiye Chifukwa Chake Timafa” Aloma . 5: 12. Komabe Ngakhale Zili Choncho Pali Chiyembekezo Choti Akufa Oose Ali M”munda Adzaukaso .Yohane 5: 28,29. Tilile Ndi Chiembekezo!!!!
Apite akapume adali wakubanso.may hiz soul rest in peace.
Poti chisoni kumatenda pamaliro pamankhala nkhani tiyenazoni.
Tsopano Mr Bakili akhumudwa why? ndimayesa ndi iwo omwewa ankamuotchela mawaya Gwanda kumati adamenya mafumu pa msonkhano?
Kkkkkkkkkkkkkkkk kodi tiunikepo bwino pano akuti akhumudwa che Bakili
Ati nkutelo wati? haaa! aiwala zija ankaliuza dzikoli pamisonkhano yawo
Kkkkkkk m’taya makoko samaiwala man koma m”dya nyemba
Tembo failed to hyd his smile during the Zodiak interveiw…nde mwati heading yanuyo ndi chani?
Thats way how lyf goes osanenedwa palibe pa dziko even our bst frnds talksmore about us bt still wen ths thng comez they can’t rmembr wat they did R.I.P BAA.
Tembo Adalepheretsa Mcp Kulowa Mboma 1999 chfukwa samafuna kulamulidwa ndi GWANDA,bwezi mcp idakali mboma pano.RIP GWANDA
tembo nyie adaononga mcp
tembo nyie adaononga mcp
A hero is not a hero until he dies
muthu ukamwalir zonena kuchuluk. ati ndkumanena kuti R.I.P.koma mwaiwal kuti mumamunyoz adakal ndimoyo. ndkumapitiriz kuti adali ofunika pandale. bushiti
Ndye osamwa tameki bwanji
Akapeza azake amkawapha aja___amkaziyesa shasha akuthira anthu chitedze kukhoma misomali mmitu ya anthu wosalakwa kuwaguza mafumu ena atawayika mziguduli kukhazikitsa malamulo onyasa wakhauka watsala iwe Tembo pamaliro ako anthu adzasangalala
Iwe ndiye chitserekwete chenicheni zitayeni zandalezo.Koma ndalenso suzidziwa.Umadziwa kuti Hwanda chakwamba anali true soildier Msirikali wankulu.Amene uja samaopa amuyesaye kuti amuphe analephera.Anachita kunena kuti ndayesedwa kwambiri kuti andiphe.Koma nkhabe ndinafa ndekha namatenda afuna alandire ulemu waukulu ndi a Malawi Defence Force.Ungafanane naye ameneyo zimene wakambazo adziwe ndi mulungu osati iweyo ayi wamvaaaaaaaaa
Bwanawe ndiye kuti iwee mwana apa palibe ndale koma Nana ndi mzake Tembo ndi anthu awiri ofunika akanalapa asanafe achotsa miyoyo yambiri kuzuza mkatiiiiiiiiiiii
nthawi zina kumango nvetsetsa zikachitika
Mumati atani ngati wakalamba? munthu anakula uyu.
R.l.p mukati pelekele moni kwa bingu
singing……….”Munamugurira suti after mwaona amwalira………”
He was a very dangerous man during one party state sitingayiwale ayi,let trueth be told here.Rest in peace mbuya.
Paja munthu akamwalira amakhala wabwino.Bakili akuyamikira nawo?Tili nawotu ma audio clip a mmene amamunyozera Gwanda.Choncho poti ndi ndale!!
Anatibutira mafumu Ku mzuzu kuphatikizira a T/A chikumbu
R I P
Iwe Bakili bwanji sunakhumudwe ndi infa ya Matafale?iweso John Tembo bwanji sunakhumudwe ndi infa ya Gadama,ndi Aron Sangala?musamatiphimbe mmaso anthu oipa inu.nthawi nde yatha ofunika kulapa basi.
YES
Ai kuweluza kuli kwamwini
iweso ndioipa ukuloza zala azako ulizoipa zako, shame on you. kuweruza kwamwini mulengi, ngati iwowo atero asiyeni
Aliyense amankhala okoma akafa ali moyo pamankhala palibe izi Who is seeds ?
R.I.P
tikulira nawo limodzi, tiyeni tiyiwale zakale mkulira malro.
RIP NANA
Paja O Tembo olipo? Muwawuze tosowa.
Wasintha chapter ? khala serious
Chapter chanji O Ching’ondo?
Uthenga wa imfa ndimatenda ndiye chodabwitsa ndichiyani ngati munthu amadwala? Plus he was old already! Did U guys who shows to the public with your fake glieve soul done some thing better to help him while he was sick? Or its just apolitic issues?
Ndindale man alibe nazo ntchito
M’mene ankamugemulira anthu amenewa, mwina poti ndi pamaliro aliyense amakhala ndi chisoni
Akhuzidwa osati kukhumudwa.