Chilima to meet Pope Francis in Rome

179
Saulos Chilima

Chilima: Heading to Rome.

Malawi’s President Vice Saulos Chilima has today left for the Vatican, Rome, Italy for a day long visit.

According to a statement signed by Vice President Press Secretary Pilirani Phiri upon his arrival tomorrow on October 26, Chilima will attend the General Audience at the Vatican where they will also greet the Holy Father, Pope Francis.

According to the statement Dr. Chilima will later the same day meet His Eminence Cardinal Pietro Parolin, Vatican Secretary of State.

“During the meeting, Dr. Chilima will extend an invitation from His Excellency, Prof. Arthur Peter Mutharika, President of Malawi, for Pope Francis to visit Malawi.” Reads the statement.

The Vice President returns home on Thursday, October 27 according to the statement.

 

Share.

179 Comments

 1. God cares Mr vice president. I’m sure has gone their on personal religious reasons. I don’t think it has something to do with the government. Dr. Chilima is a devoted Catholic so there nothing strange for him to pay visit to the Church leader. Take note that pope is just a servant of God and cannot & will never be worshipped. Nobody in Catholic church worships him. He is only the leader of the church world wide.

  • People are crazy, every church has got a leader whether be the pastor, Bishop, Priests others prophets. When someone says I am going to meet the Pastor, Bishop or Prophet then does it mean that he/ she is going to worship the Pastor?

 2. A Malawi a Malawi kumangovomeleza ziri zonse basi zina mzamva nkhwangwa yili mutu kodi kuli chani ku Vatican msakatibweresere zidindo za chilombotu zisayambire pa ife toto takana ,maganizo awo tikuwaziwa kale sitilola

 3. Guys kungogwer kukwapula kapena ayamba kuganiza bwino anamenyedwa ndikale.who pope? instead of asking God for Problem of Malawians.prz God Helping Malawi To Have Wise readers.

 4. otukwana,oweluza,opsa ntima,oganiza moipa.zonse zili mgulu la uchimo.ngati chilima wapita kokapembedza satana nde kuti mwakwela bwato limodzi.komanso mwatsogola ndinu chifukwa njila ndimayankhulidwe anu ndiokhumudwitsa dzina la yesu nkhristu.zonse aziwa ndi yehova ndipo tipemphele kuti tisalowe mmayeselo asatana. Dzililileni nokha.

 5. The only vice president that enjoyed the seat was Dr Joyce Banda koz she became president. And if the president is still alive, vice president alibe ntchto

 6. The only vice president that enjoyed the seat was Dr Joyce Banda koz she became president. And if the president is still alive, vice president alibe ntchto

 7. Pope kkk mavuto alipo kuchivumbulutso anakamb za mkaz wachigololo uja aweluzidwa ndipo adat mkaz wachigololoyo nd mzinda wawukulu omwe ukulamulir dzik lonse omwe nd Rome kwaw kwa pope pamodz nd pope yo kmans mapir 7 aja omwe mkaz wachigololo uja amakhalam .ndalamazo malo mogulira chakudy mkupasa amphawi

 8. Nonse mwalemba zonyoza kaya kutukwana mulungu akukhulukireni chifukwa simukudziwa chimene mukunena.chilima is a catholic member chingamulepheretse chani kukacheza ndimtsogoleri wake?

 9. Nobody hu z perfect in this earth, guyz I hop u knw orede dats wi r living in the last dayz of the world. Dea z no politician who is not under satanic u can jst join into if u want 2 prove it pliz jst pray 2 de Lord in the name of Jesus I pray amen.

 10. maulendo ena amakhala opanda phindu, ndalamazo osangogwilitsa ntchto ina like kumanga ka block kamodzi or tiwiri pa xool ina yake… ana ena akumaphunzira mu zisakasa mmidzi mu!

 11. Malawians are really strange people. Castigating Chilima for visiting the pope? No wonder minyama simakutherani. Idiots.

 12. Apa ndikutha kuona kuti kumalawi kuli mbuli zadzaoneni munthu apite uku mwati satanic bushiri akuthandizeni mwati wasatanic who is ur holy.to you all inu mudxingokhalira zomwezo azanu akuchita bwino

 13. Iwe VP chitsiru chamunthu ukukatani kumeneko? You deserve insults asaa VP wachamba ngati uyu sindinamuonepo ameneyu akadzakhala Bwampini wa MW azalowetsa za Chiroma kwambiri musavomereze kuti azakhale president

 14. DONT JUDGE UR FRIEND,TO JUDGE IS 4 OUR HEAVENLY FATHER.LEAVE POPE ALONE.KHALANI OLUNGAMANU.WE WERE BORO EACH EACH AND WE WILL BE JUDGED EACH EACH.AMBUYE AKUKHULULUKIRENI COZ CHAMOYO WANU OWERUZA.

 15. I think more than 60% of malawians suffer from “THE NEGATIVITY SYNDROME”. They are happy to apply bad motives to each and every story they come across. The problem is the way they understand personality , traditional beliefs and religion.

 16. Nthawi yatha abale nokha mukutha kuona momwe zinthu zilili.Yesu ali pafupi kubwela chofunika apa nkungolapa machimo basi kuti tsikuli lidzatipeze tili ndi mafuta okwanila munyali zathu.in Christ Jesus amen

 17. Ndiye Akakumana;kuzimazima Kwa Magetsi Ku Kutha?Ee?Madzi Samasiya?Katundu Samakwera Mitengo?Malipiro A Ogwira Ntchito M’boma Awonjezera?Akakakumana Ndi Mtsogoleri Wa Eklesia Yu,ndiye Aika Ma Policy Othandiza Kuti Olo Mvula Itabwera Yochepa,boma Lizatha Kudyetsa Mzika Zake?Akabwerako,mlandu Ya Cash Gate Ya Ma Big Fish Iyamba Kuzengedwa?I Mean,akakumana Ndi Mlowammalo Wa Petro Yu,access To Imfomation Bill Ija Aivomereza Tsopano?

  Sisandikhudze!!Ndangodutsa.

 18. Ukukapangako Cani? Akukatenga Cidindo Ca 666 Kapena? Kodi Nawonso The Vice President Has Joined Satanism? Oh! God Save Us!!

 19. Pa campaign mmatinyengelera nkutilonjeza zambiri koma lero kungokumbutsa malonjezo aja kapena kuzuzula zaulendou ndekuti ulendo kukayankha mlandu!!

 20. Chalima,why Chalima, I was thinking dat u ar agud guy man, now this, my Malawi is going to hell. Pope Francis zoona, Amalawi zovuta zikudza ndithu blv me, Pope mukumudziwa bwino komaaaa( Please God Help My poor Malawi,tikusocheletsedwa zomwe zikubwerazo sitikuzidziwa kuti nzotani,anthu akulowa mnjira yosayenera pofuna zadziko ili,Mutiyang’anile Yehova)

  • iwe nabanda tiziti zoti pope ndi oipa suziwa ??????? zoti analola za same sex marriges mu catholic mwanumo chaka chatha chomwechi suziwa ????,

  • Nabanda ndi mbuli yomwe ikodwere kumbuyo potsata zili zonse,kapena ndinene kuti sukhala ndi nthawi yowerenga News kapena kupanga Google ku Internet or just check now ku CNN international uwone zomwe wanthu am’maiko akukomenta za pope wakoyo, iyeyo ndi akulu wena am’dziko I mean ma president ndi ambiri achumawa akupanga zotenga dziko lapansi through their mentor Lucifer, Pope wakoyo ali pa no 2,Powerful men on Earth,pa no one pali Obama,ufufuze why Obama is called the Beast! Check World Order,ukafuna kumva za nkhani ndakamba pamwambayo za Chalima, check illuminati,uwone zomwe akufuna nanga anthu andalewa ali pati ndi mphamvu zawozo,ma pastor atchuka ndi chuma chosanenekawa akuzitenga kuti? Awanso akulowa njira yomweyo to get wat thy want, The world is coming to its destination blv it or not, zochitikazi zafika pena and mu nthawi ya Nowa chisanadze chigumula wenanso ankatero ngati iweyo,kusakhulupilira zonenedwazo,anthu anali kuchita mwakusaweruzika like today,chigololo,kupha,mabodza,kuba,kusaweruzika,kumutaya ambuye kuyanja za dziko kapansi and Mulungu anawatha, kunali ku Soldom ndi Gomola nso wanthu nali kuchita mwakusaweruzika kwao ndipo Mulungu anawawononga,zonenedwazo zinakwanilitsidwa ndipo zikanapitilira koma uku nkumapeto khulupililani Nthawi Yatha iyi,Zadziko zakwanilitsidwa, Pope andi Vatican yonse akutsutsana ndi zolembedwa za Bukhu la moyo and anapanga lawo Bukhu nkuchotsamo ma verse wena,mufufuze mupeza. Osamatha mau ngati musanapange search.

 21. Pitani mukalambire milungu yadziko lapasiyo koma dziwani mululungu wakumwamba akuwona ndipo azawereza # pope ndekt chan to hell wth him ndalezomwezi achilima mpaka mwalowanazo satanic mmmmmmm mwaonjeza

 22. Sizodabwitsa poti pope ndi Mulungu wadziko lapnsi iye amadzitcha mulowa mmalo wa Mulungu sizodabwitsa kukhara antchrist soon apanga control dziko lonse lapansi

  • Or nditakuuza sungakhulupirire koma dziwa kuti pope ndi antchrist 666 panopa akuona ngati mfumu yachipembedzo koma dziwa zimenezo ma president onse adziko lapansi amamugwadira ndikumakhululukira anthu machimo why? Bible linanena kare xa ufumu wa ameneyu ma loto a daniel mu bible ndipo anayamba kare kuonetsa za ufumu wake zina ndi zimenezo fufuza akuuza coonadi anthu yesu asanabwere pope alamula dziko lonse lapansi kuti tipange folo malamulo ake osati aMulungu ai ndipo zambiri anasintha pano anthu akuzivhita mwakusadziwa

 23. mpaka ku Rome ntchito zaboma zavuta pamenepa, komanso mayankhotu ku Malawi kuno akhoza kupezeka mutawakokakoka amene anaba ndalama aja kubweza pang’o pang’ono ndizambiri kugulir a chimanga olo kuwafunsa anzanu a Tembo kuti kuyendetsa chuma cha boma amatani alipo ambiri dziko likhoza kutheka ili , yendani bwino

 24. Anthu enenu mukafuna ku komenta muzikomenta mwa nzeru.Pali chiyani cholakwika apa. Kusiyana chipembedzo kusakupangitseni mkwiyo. Ife timakupatsani ulemu ndi mtimiki wanu.

 25. Aaaaaaaaaa zaziiiiiiiiiiii mxiewww zoti anthu tikulira we’ve lost the regend iye sizikumukhuzayi??? Matama amenewo ngati sadzafa??? Mix akukagwadiraso FANO …SHAMEEE!!!!!!!

 26. kuwapasa azungu zikoli ife amalawi kutiuza tipite kumangalande. zinkhoza kupezeka kuti azunguuno alilemensa zikoli ife nkuka ononga england

 27. Muyende bwino! Kma mukandipemphereko mkanjo kwa Pope coz uja anandipasa uja unathimbira maka chfkwa cha kusowa kwa madzi oyera a pa tap,, plz chonde ambuye akhalee naaaaaaaaanu,, aaaaaaaaame!

 28. akukanyikidwa mu mphamvu yamagazi pajatu ndi Pope amapeleka mphamvu imeneyo kwama president pa dziko lonse lapansi sinanga Pitala akutula udindo wakewu mwezi wamawa

%d bloggers like this: