Chipani chija chikutha anthu akuona.
Mneneri wachipani chostutsa cha Peoples’ amene anakakamila ngalawaya chipanichi ngakhale mtsogoleri wake atachithawa, a Ken Msonda, alengeza kuti basi iwo alekana nacho chipanichi.
A Msonda analengezaizi pa tsambalawo la pa Fesibuku kuti tsopano iwo simmodzi mwa anthu a mu chipanichi ndipo aganiza zopuma kaye mu ndale zachipani.
“Ndakhala ojijilika pa ndale kuyambila 1994, tsopano ndikufuna ndipumulile kaye,” anatero a Msonda polengeza za chiganizochawo.
Koma a Msonda anatsindikanso kuti kutulukakwawo mu chipani cha Peoples’ sindiye kuti basi azitayilatu pansi ndale.
“Nditulukilanso, mu zisankhoza 2019 ndikupita kukaimila ku Rumphi East. Anthu a ku Rumphi musadandaule, ndilinanu,” anatero a Msonda.
Dera la Rumphi East padakali pano phungu wake ndi a Kamlepo Kalua amene ndimkulu wavuta ndiphokoso podzudzula boma la a Mutharika. Iyendiwa chiwiri kwa mtsogoleri wachipani cha Peoples’.
A Msonda akhala mmodzi mwa anthu okhulupilika kuchipani cha Peoples’ anthu ambiri atachitaya kutsatilaku luzachitsankhokwachipanichindikuthawam’dzikomunokwamtsogoleriwachiapnichi.
Pa nthawi ina a Msonda anapeza mavuto atalangiza a Malawi kuti aphe anthu onse ochita mathanyula ati chifukwa Buku lopatulika limaletsa mchitidwe umenewu.
Cchipani chinatha mai anathawa ataba
Curtein pp?
Wangowona kuti Amayi Joice Banda,adaleka kumuthandiza, woooo wagwanayo alowe ku moz…. akayambe ndalezo.
Chipanichi chatha basi, mwini chipanichi saoneka. Ndi ndana amene angakomesere mbiri yachipanichi nkuzawina?
CASH MONEY
Iwenso wa 24 waganiza bwanji?mpaka WERENKHANI
kkkkkkkkk!!koma anthu enawa mawonekedwe awoso nde mngoseketsatu kwambili ,,,ngati achezera kudya mbewa usiku onsewu,,,,
Ndipo mpando wakewo ndimaufuna nkale pita enafe tione zina
Masten where are you?come and rescue your party before it is two late….kapena mukuopa kudzamangidwa…
Werenkhani
awa si ngandale koma ngadyera bwelera ku mpingo wako kuno ku south Lunzu ccap osatiso ndale ayiii!!!
Man changu pamalo kwavunda khola Fisi amapita komweko kkkkk
pempho kwaolemba inu mukungotipasira mitu yokha nangano nkhani yonse tiziipeza kuti?
https://malawi24.com/2016/09/15/kaliati-agwila-nankhumwa-ufiti/
kapumeni Agogo. mwakalamba. kub. PP tikufuna anyamata inu nde mwasala madzi. amodzi muyende bwino xikomo
Alibe Mbiri Yakuba,akuganiza Kut Azakhala Nduna Akazathamangitsa Mbava 7zija Ku Dpp
Atuluke
Pp Lero Ansonda Manyunyu Chani? Chinatha 2014 Ndikale Ndie Iwe Nsonda Sumaona Umangoti Kaka Wagwanazo Bwanji Manyazeee!
msonda umachedwa kuti
Mwachedwa Ansonda Anzanu Anaonela Patali Achena Khumbo Anathawa Msanavote Nkomwe Ndie Apamtani Mlowera Kuti? Poti Zipani Zose Zasedwa Zako Izo Wekha
Nde kuganiza mochedwa
kkkk akuluwa dyera apitaso konkuja ankakunyozaku
PP ilipo ndipo izakhalapo mpaka kale chipani simuthu modzi ai
Munthuyu amawoneka chochi ndimangomva msonda msonda koma ayi basi achoke ndipo asabweleso ayi ndichizake chamunthu.
Pp singathe cz nsonda watuluka apo ndiye mukunama mukamalemba muzuganiza ngat ndinu oohunzira vuto ndilot amalawi ditimaziwa kusiyanisa chabwino ndichoyipa umphawi suzatha munthu wankulu but ubongo nduwa bankha mungaganize zolonhosoka choncho shirt
ndichakutha kale, ndiye chathelatu apa kuchoka kwa die hard ameneyu
Pp mmene yateromu yatha basi mawa timva za enanso akulengeza kuti ndazitaya,,pp ikagwere uko!!!
ya osakwera basi iyo ikufuna makanika amangire gearbox
Wachedwa ndalama adaba kale anzako pano nkhanga zaona palibe kusololanso.
koma umphaw nde wakugagadatu mwna mukanenepe. …Idiot
Pachoka munthu pali malo .Ine tsopano ndalowa PP.Ndirandireni abale onse a Peoples Party.
Msonda ndikhuluku ngakhale umaoneka ngat wangwiro Ku pp pita DPP ukazione wekha usova
pp yanyamuka iyooooo
He Should Go To DPP Where He Will Survive And Be Taught Real Politics.
Nsonda Wachita Bwino.Amai Aja Anathawa Ndiye Sindikuona Chifukwa Chomatetezera Chipani Chakutha Kale As Old Curtains.
Pachisena Timangoti!!! Utumbo Lelele Unamala Sololeka Kkkkkkkkkk Eeeee Man.
Aaaaa Palibe Chodabwitsa Apa Ngati Mtengo Wawuwisi Ukuyaka Kulibwanji Wowuma? Anayambitsa Ndi Amayi Nanga Ana Alowera Kuti Chatha Basi Chipani.
Chipani Chopanda Tsogolo Ife Monga Chipani Cha NASAF Tikulowa M’boma Ku PP Kuli Mbwa Mbwe Mbwi In Shot Mbwelera Kkkkkk
Yonse mkabati zinazi abale mkangamwala. Ine kudabwa nangiliya anachoka koma ena angoti kakaka pamene mwini wake chipani anachithesa welcome baba nsonda to dpp.mcp.udf
Tiwerenkhe?Kodi kuwerenkha ndikutani inu a Malawi24????
Kuzemba Bamp Nkuliwonela Patali Man
Nanunso muzitha kulemba, timalemba kuti “welengani” osati “welenkhani”
Tisadabwe nazo, ndi umboni wakuti maboma wa anthu sangathe ulamulira mwa chilungamo tizingo uyembekezera ufumu wa Mulungu basi.
Zikomo
Zikungo usonyezeratu kuti ndi Ufumu wa Mulungu wokha basi umene ungalamurire mwachilungamo.
Tathokozaaaaaa
sho,ndi yesu yekha adzalamulira wachilungamo
Ndiwo4yila manwa
Kkkkkkkkk pp ndingat mwana olowelera poti msonda waganiza kt abuele kwa atate thats DPP but here u are not welcome jus stay out there .ndalama zimakhala m ‘matumba not under pitcot
Kkkkkkkkk pp ndingat mwana olowelera poti msonda waganiza kt abuele kwa atate thats DPP but here u are not welcome jus stay out there .ndalama zimakhala m ‘matumba not under pitcot
Mickey mouse party
Zoona pp ikuchedwetsa m’bale waganiza chamuna
kkkkkkkkk ine ndisekepo apa osaona anafusa woona kuti ada bridge ili pati ndie ona unja anamuuza kuti ndikafikapo ndikuuza apatu asonda samaona amayi amaona ndie anangoti ndikafikapo ndikuuzani asonda anangoima kudikira auzee malo moti akanango muuza wina alondorere anapezeka agwera madzi inu kumaganiza sonda sunalakwitse koma popeza wanyowa kale ndiebe aaaa pita ku mcp basi utani nanga poti watani kale ndiline aaaa ndikanalowa boma kudyanao basi kosusako iiiiiii azawina ndakaika awoo mulungu anatemberera basi
Kuganiza mwa nzeru osakwera basi yoti yangoima ayi, mwina njoonongeka, muchedwa nazo,,,pp mwaleromunso,, weldone Nsonda osamakhala ngati mwabadwa lero ayi….
Koma ndiye ati aziabakilaso AMAYI ndi ndani pamenepa.? Mumakwanisatu ndinu nokha.. nde mulowera kuti.?
Ngati mwini wake amene anayambitsa chipanicho anathawa ndiye omutsatila angatani? Wanja balalikani.
Malawian politics full of greedy lions who do not even care about the people they represent. Keenly following to see his next move.
Changu pa malo
Everybody knows that Ken Msonda is a political prostitute, let him go where ever he wants, PP will be there even without him. Odi ukooo!
Kapumeni agogo
pp is jst like a without a driver
Pp Inakakhala Kuti Ndi Team Ya~mu Superleag Tikananena Kut Ikupita Ku Division…… Poti Ndichipani, Aisova!
athu adyera awa
Anthu adyela inu Ntaba mutchulayo pano adakwilirika sadzavekaso ena ndi amenewa aNSONDA akana chidodo ngati cha Jumbe tikuva mawa kuti alowa DPP, adalakwitsa anafuta D Kuti ikhale pp.
Chimodzimodzi ndi galu akaona kuti khomo ilo amumutayira mafupa ndikomwe amakakhala kuyiwala khomo lambwiyache sizachilendo
Zo onadi
Kaya ikupitakuti ppp paja akuti yanyamuka
Kkkk inetu mkadakhala wandale mkamagwira ntchito mchipani cholamura basi sazapezekaso wanzeru pandale ngati Mtaba
Mtabat ndidolo ie siwaphuma ndipo ndale ndimwin wake kkk
YANYAMUKA ODI UKOOOOOOO
Akufuna mpando ku dpp ndikomwe pompano we will hear that he is a member of dpp
Timva alowa dpp
well done
Afuna kulowa DPP galu uyo, ndale zmenezo, akukaima ng@ phungu oima payekha kuRumphi akazawina azalowe DPP, aaaaa….