The Malawi National Examinations Board (MANEB) says candidates will continue sitting for the 2016 Malawi School Certificate of Education (MSCE) examinations on Thursday even though the day is a public holiday.
According to a statement released by MANEB, the ongoing MSCE examinations will proceed as indicated on the timetable circulated in January this year.
The timetable shows that candidates have a break on Tuesday, 5th July, and Wednesday, 6th July; but the examinations resume on Thursday, 7th July, 2016. “All candidates and examination administrators are, therefore, reminded to unfailingly observe the timetable,” reads part of the statement.
MSCE exams began on 22nd June and they are scheduled to end next week.
The holiday is coming as Muslims will on Thursday mark the end of Ramadhan (Fasting).
Why
Ifeso achristu timatsala holiday yathu ndi liti? That’s between person and our God. If am fasting ican not put a holiday to my family or friends, they can eat , work etc. It between me and my God. Thanks to maneb.
As a Muslim l c no problem coz MANEB showed its respect on Tuesday and the Eid is Today not Thursday. It has bn put on Thus coz it has coincided with that of independence, so the holiday is just honouraly. So ena kaya muziika mu chipongwe but its not kunyoza Aslamufe nor to punish us. Its not politics nor discrimination
zlibe ntchito bola kulemba Gia bax
Ana ena ndi asilamu spanga bwanji koma m’maganiza?
Just shift it if,give them another day off
Hahaha ndiy kutilakwira2
No a problem…. akupita ku world. Long holidy ahead
Tirembe basi hahahaha guyz mwana wa munthu sazatheka
Vuto loyendera Mwezi no date lenileni ayi. MANEB INAPANGIRATU pa 5 july
maneb is nt forcng evrybody 2 wrt, those hu r nt wilng akhar asdzalemb…..
iwowo anapupuluma..anapuma kale Tuesday,so sizingatheke kupumaso Thursday,,ndekuti asokoneza mayeso…
That’s so obvious, …maneb imayenera national calendar, amene saakufuna asazalembe #maneb
hahahah maneb sidzanva!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!1 kuti anyamata amasula kkkkkkkkk kaya bola ine ndukudya nsima mimba yanga paaaaa
dont blame MANEB for that,, just blame the moon for not appearing on time,,,,komaso MANEB cant reverse the plans coz ov the muslims hu r in minority here in #MALAWI,,,,anyway am just jokin’
man xizikugwilizana kaganizidwe kabwin ndikamene kakukuvutan
man xizikugwilizana kaganizidwe kabwin ndikamene kakukuvutan
man xizikugwilizana kaganizidwe kabwin ndikamene kakukuvutan
man xizikugwilizana kaganizidwe kabwin ndikamene kakukuvutan
man xizikugwilizana kaganizidwe kabwin ndikamene kakukuvutan
man xizikugwilizana kaganizidwe kabwin ndikamene kakukuvutan
oky,,thats ur thoughts!!
mtsogoleli adali BINGU osati izi zilipozi,ngakhale ankafoka muzinthu zina komabe amayesetsa
Takozeka kuzalemba lachinayi or anthu mutokota zambiri ife takozeka cz timetable yathu ya MANEB palibe holiday
Rev Levie Nyondo is right i think
Mufune, Musafune kma ife holiday ilpo kale nde munakayamba mwaconsa pa carendara
kkkkk iiii koma guyz ayaaaa sibwino kumayesana ndatha kumvetsa kuti boko hallum inamva kuwawa i thnk ku Malawi itati yabwera eeeeeeee kaya zingathe buanji enafe angathe kutiikira ma bomba ku inbox kwathiku kkk
mi lyk t tithane nazo bas!
Olo musawapase kma wanga yekhayo ndizamupwala bax
Aaaa inu mumati ndisalembe mayeso chifukwa cha midyomba
Den ts not a public holiday,,,wy calling t so?
Kkkkkkkkkk
Musavutike mkumalemba apa an2 alpa holiday bas examination friday
agwa nayo ngati kunali kwayesa a Silamu coz Eid is due tomorrow
Eid ndi mawa kusonyeza kuti Ramadhan yatha 29days; holiday ikhalepo
Its not peter who plans the time table. Pliz zinazi kumaona polemba
pa tym table thursday mayeso alembedwa holiday inal pa 5n6
Mukatelo ndiye kuti mukulakwila ena cause ena mwa macaditate ndi aslam mukadawalola kuka pemphela na eid
ok tathokoza
Musatero Apeseni cz Enawo Analonjeza zibwezi zawo kuti aza wawonesa ku Ndata ku thyolo pa tsikuli ndiye Ayii! musawakhomelere ufulu wawo.
Holiday inalipo lero za thursday zangosinthidwa coz mwezi sunaoneke koma timetable anaika 2days holiday ya id ndi independence
Mwezi waoneka madala musachedwe futulani
Ntchito pasogolo
Eyaka simumamanya kkkkk
Malawi lacks cognitive emplacement of the embittering Calabria !!!!
kkkk what?!?!
Ife Tinabwerera Std 8A , Za Form 4 Zanuzo Sitikuzimanya Bho….. Bho “
Ankolo lemekezani chipembedzo cha amnzanu pali chotukwanira apa amwene
hahahahaha the time table is there every 1 knw7 that mwangosowa cholemba akapuku inu et