Lover’s husband rains blows on Zodiak presenter Joe Mwase

Advertisement
Joe Mwase
Joe Mwase
Joe Mwase got the beating.

Joe Mwase, a radio presenter working with Zodiak Broadcasting Station (ZBS) last night got a beating after he was caught with another man’s wife at his house in Lilongwe city.

According to reports, Mwase has been having an affair with the woman Rita Chaima for some time and Chaima’s husband Arnold Flao heard about the affair but wanted evidence.

On Monday after knocking off from work, Chaima who works at Department of Road Traffic and Safety in Lilongwe went to Mwase’s house in Kawale in the city.

Joe Mwase
Joe Mwase shot while being taken into police custody.

Flao got wind of reports that his wife was at her lover’s house.

The angry man followed the woman and when he caught the two in the act, he rained blows on Mwase who failed to fight back.

After noticing that he would get beaten to a pulp, the disfigured Mwase managed to get into his car and drove away.

Flao was however not done with the lustful Mwase and he chased after him until the broadcaster’s car plunged into a ditch.

The police later detained the three for questioning but Flao was released while Mwase and Chaima spent the night in the cooler.

The law enforcers have since charged Mwase with conduct likely to cause breach of peace.

Advertisement

470 Comments

 1. Holy Ghost fire!!!!!!! Omwase palufunika mulandire Yesu

 2. Haha Joe,ubwereso kwa nieighbour watha nkazi wawo sakana amalandira aliyese adachita ulemba pagate ati all are welcome regardless of height,age,colour,race,origin,weight,size,perimeter,diameter,circumference,radius,speed ni zina zose!24hrs service,nipeze ku inbox nkupatse map!

 3. Tsano o Flao bwanji, mesa o Mwase omapiriliza pomwe inu mmalekeza.Chikondi sokakamiza inuyo ndekuti mudaleka kukoma.

 4. ndamva ma comment anu opusa ndi abwino …onse ndi olakwa ..mayi ndi mtola story yu …ochitanso mnkhalidwe wawumvewu aaaaaa TAKE A LESSON LA 40 likudza posachedwa…….

 5. ndamva ma comment anu opusa ndi abwino …onse ndi olakwa ..mayi ndi mtola story yu …ochitanso mnkhalidwe wawumvewu aaaaaa TAKE A LESSON LA 40 likudza posachedwa…….

 6. koma lita am very much disapointed in you. Why doing that to our very own arnold flao our ex ycw chairman. Choncho munangomuonongetsa mabuku aku church. I know arnold is a good man and he doesnt deserve this. You took him for granted because amakonda kupemphera and you knew kuti azikukhululukirani? Mkazi opusa iwe. Arnold is way better off than your womanizer joe mwase. Walipasula wekha banja and you will not be respected in a community.

 7. Dziko ndi anthu ake,ndalama zitivte,akazinso muvute amuna anu? Shupit

 8. KOMA ANAKAKHALA POLITICIAN, OIMBA, PLAYER BWENZI MUKUTISOKOSA .APA MULI ZIIIIIIIIIIIIIIIII! !!! KACHITSILU KANI KAPANGA NYASI.CHI RADIO CHOKONDELA .THATS WHY I DONT LV YOUR RADIO ! U ALWAYS INSITE VIOLENCE! KUMAZICHEMELELA NGATI ALWAYS MUMAPANGA CHILUNGAMO.IYO NDI NKHOPE! !!!! KHOSWE AKAKHALA PA ZODIAK SAULULIKA! !!

 9. Komano mayi wabanjayi ndiolakwa,chifukwa zomwe wachita apazi zipanga affect even ma Sisters ake omwe ali mmabanja,any mistake azimuna awo aziti watenga mmbale wako.Mapeto ake banja lonse mbeta.

 10. Why not ZBS to air this, paja zikachitika. Pamkhate sapheka……kuonetsa kuti ZBS ndi zokondera ndekuti pali nkhani zina amatero. Ok takudziwani…
  For Omwase, behave urself. U put the station in disrepute…..

 11. More than 300 comments on the fate of Mwase. How many of u amene mwayankhula zakukhosi simunagonepo ndi azikazi a eni ake,kapena amuna a eni ake ?ena mwainu mungoyamika kuti simunagwidwe lanu la 40 lidzakwana.

 12. Jesus Forgave A Certain Woman Who Caught Committing Adultary.Jesus Commanded Her To Go And Not to Do It Again. The Same To U 2 Look At His Cross And Ask Forgiveness, He Will Forgive U. There Are Many Pipo Committing The Same Sin But They Are Holy Bcause They Are Not yet Caught. Dont Loose Hop God Forgives U If U Ask Him.

 13. Eeee!mwase apa nde ungomutenga basi cfukwa zikuoneka kuti mwavana sugertu apa,ameneyu anakuosa yotani kapena misionary kkkkk!koma ukangomutenga enanso adzakudyeratu coz nkaziyo ndipalowapalowanso.

 14. Omwase bwanji khaza kwa nzanu kutchuka kapena?mwangoziyalutsapo dziko lonse laziwa ndiwe opusa usazalengenso mpila uzitipatsa minyama potinso suutha

 15. kkkkkk a mikayere moyo wanu wovuta , asungwana omsewa simukuwaona?

 16. ambiri mwaazimuna mwa commenta apa tell me ngati simunafunsirepo mkazi wa munthu. za phweka poti ndiza a Mwase enanu mukufuna kuoneka olungama pano iya sorry Joe zimachitika after all sunayambe ndiwe simply learn a lesson from it

 17. Ngati a Mwasewo samadziwa kti ndimkazi wabanja alibe pulobulemu koma alindi vuto ndimkaziyo. Komanso a malawi 24 pliz every person have his or her own privacy,think twice b4 posting stories to public.

 18. Anthu mukuti mwase amalimbana ndi mkazi wamwini. kodi mkazi wamwiniyo samadzowa kut mzosayenera kunyengana ndi mamuna wina apart from her husband? both chaima and flao are working and we cant say kut amayiwo amatsata ndalama kwa joe mwase, there is something more to it. iwowa agwidwa koma inu ndi ine ndi angelo? ma issues amenewa ali useless. komanso ku police conduct likely to cause a breach of peace kunyenganako? i hope mwawasunga pofuna kuwateteza mwina pano atuluka. tonse tikhale responsible osati mwase yekha. akanapanda kupita kunyumba kwa joe ko bwenzi zonssezi kulibe.

 19. In Zambia the opposite would have been the case. Flao would have arrested for being brut while the case of Mwase shagging Rita would be treated civil. Who knows may be Flao can’t ride far too long and Rita found solace in Mwase who is a good rider.

 20. Kkkkkkkkk zikachitika mumvera kwa ife! Koma izi zokha sitinamvere kwa iwo bwanji?

 21. Eeeeeeee panja masiiku apitawa kunazizira zedi!! Wow, #Joe-Mwase amakatethetsa machine kkkkkkkkkk mmmmmm but wandichititsa manyazi aah #Mwase 😮

 22. mmm amwase!umunthu palibe mpaka mkazi wamwini kuderera kapena kukhwima apopo womenyayo sadalakwitse chifukwa adakapusa akadaphedwa apatu akazako mwana uyu akufunika ku displinary angakhale umve winau ndi obadwa nao

 23. Aliense ndi wakuba. chabe timamuzindikira akagwidwa. Ndipo ngat alipo mwa inu apa emwe sadapangeko zimenezi… Let em start kumugenda JOE. Komanso @ ZODIAK.. Where ar u @ ths time… Monga simudalandile uthenga kapena kumuona atathidtimulidwa mkutziwitsako? Kapena wakwera pa mbiya sangalasike tsopano. Amalawi. Tatieni tisamayang’ane nkhope kapena mbali pochita zinthu. Wy then blame Malawi N24? Nawonso ali pantchito yawo ya utola nkhani. ngat sapelekera zangat zimenezi nde m’mati apelekele ziti? Tikanadziwa bwa. Go harder edditors…

 24. Joe sanalakwe.first thing we have to think About the reasons y the woman was going to hos home living her husband. maybe the husband wasn’t making her satisfied. its not about money or coz joe is a cerebrity.no.its all about family issues. i blame the guy n i support Joe. nane sndkanachitila mwina ndi mphepo ya chilanga mbetayi

 25. Khalidwe lopusa akazi onse akusowa amunawa how can someone go out with somebodys wife?? What special thing you found in that married woman?? Indeed some of u though u went to xul but stll ur educated salvages..nayenso mzimaiyu eish! Ndingayambe kuchimwapo apa

 26. Zochtixa manyaz kwambr,kuxakhutitsidwad madolo mvuto lake nd limenero xo let be proud ov wat we have gyz not kumaononga mbr wekha chonch!!!shame upon Mr mwase.

 27. Nokha mukut “Tchimo la chigololo ndiloopsa”….Nokhaso mukut “akazi ali mbwee” advising him to cheat on his wife as well (kwa ma hule) osat akazi apa Banja koz ndiumve….kkkk…

  Ndeee wa pa Banja ndi umve lyk a publik toilet az u say..nanga hule?..ndee wa clean…Nonsense

  The Fact is…ADULTERY IS A SIN….

  Husbands love your wives
  wives love your husbands
  Dont cheat on each other

  why?
  because Sex outside marriage (Adultery) is a Sin regardless of who u hv sex with

  So this Mwase boy and this cheating wife…ngofunika kuwathila “Doctrine”….They shud repent….Ask for forgivess from God..and they shud never do that again…

  Osat ma advice opusa mukuperekawa….oti “Mahule” ali mbweeee…ndeee chan?…thats un-Godly advice….Very Wrong advice…

 28. Is Joe Mwase married/not?? If nt ndie wambwambwana pamenepa, selebu mpaka kumalimbana ndi amayi? Aaaah, kma ngat naeso Joe ndiokwatira no problem pamenepa. Amaflashilanji iyeo.

 29. Where are you zodiak? Paja zikachitika timamvera kwa inu nanga izizo bwa? Any way mwase sioyamba kuchimwa.we all have some weaknesses but this should be your lesson towards a better change Joe

 30. Akakhala pa radio azilangiza za kuopsa kwa matendawa pomwe iyenso apanga zomwezo kupepera kwenikweni. Osangokwatira bwanji? Ukufuna akazi aeni ake chifukwa chani? Chindere

 31. Joe wachita umve kwambiri kt alwayz amakhala akulankhula pa radio popeza wapanga ndi iye zikhala bwanji? monga ali alutsi okangalika ndi nkhani imeneyi apa comittee ya wailesi ya zbs ichitepo kanthu km kumphatikizapo bungwe la atola nkhan……………………….kd mahule onse amapezeka mu mzinda wa LL,BT,MZ It is samawona chifukwatu pali mahule ena ukamawanyengatu amakhala ngati usawasie kuli kukoma ngat sweet ya amazon kuli kutsekemera.km company ya airtel akutipo chian pa nkhaniyi chifukwa ndiwantchito wawo amene amatha kulengeza mauthengatu………………

 32. Zodiak Broadcasting Station ZBS, Zikachitika Mumvela Kwaife…Ha Ha Ha Ha Ha Ha!!! Nanga Iyi Yakuphonyani Bwanji? Mkazi Wa Neighbor Ndi Wako Yemwe Ukachenjera Pakamwa Udya Abuja Kkkkkk! TIDYE BASI ZIMENEZI…

 33. Pepani Joe Mwase kuti zoterezi zakuonekerani ndithu. Infact inu siwoyamba kukumana ndi zoterezi ndipo aliponso ambiri akuchita khalidwe lotere koma sangwidwe. But let this be a lesson to all those who go out wth other people’s wives. Simbiri yabwino iyi ai chifukwa mutha kuphedwa, kubvulazidwa, kuononga nazo nchito komanso koononga banja lanu ndiponso banja lamzanuyo.

 34. A Mwase mpaka mkazi wa mwini?koma akazi onsewo pa company yanu opanda banja ngati kufunsira kwavuta mubwere kwa ine muzatenge mtera(mankhwala)muyambe kufunsira akazi opanda banja

 35. Timadikiratu kuti timvera pa zodiak. Koma kuli chuu. Mesa zikachitika timvera kwa zodiak, nanga iyi yawasempha pati? Khoswe akakhala pa mkhate sapheka.

 36. Anthu otero wongapangira mwase sitimenya timangokoka mlomo wamwambawo ndikudula mano akutunda adziwonekera patali zikatero akazi wokwatira azimuwonera patali

 37. A Jjo mwase kodi mkazi wokongola lilongwe yonseyo ndiyekhayo? Kapena munauzidwa kale kuti ndinjinga? Ku LilOngweko wachuma ndinu nokha kapena mumashayina kupotsa anzanu? Amwase mutengane ndi mkaziyo mkayezese. Mayiyo ndichiphetsa ndinso mdanisi. mukuganiza kuti mchitidwewu alola nokhanu. mukamukwatila kwa inuyo sangazakuzembeleniso? mundiyankhe. Mumene ukuonekela ukadali wachisozera “Uzisamalile makolo ako angazalilire ku utsi. Omfumu Kapelemera Gondwe akulangiza achinyamata nonse amchitidwe woter

 38. Vinnie Moore Wills, Press Gvh Mikule Botha, Issa Donex Mubaraki Mubaraki, Devson Ziyada, Adson Chifundo Chauluka, Thocco Don, Simioni Benati, Eriq Kwanjana, Zsynab Vinnie Moore, Maya Fasten Mbenderah, Elton Ndakanamwano, Devson Ziyada, Felix Nyenyera, Lawrent Kwanjana, Innock Becks Mwanza, George Mwale, Vincent Zunga Wabandulidwa,,kkkkkkkk

 39. Ndyekut a Flao samafkapo pamene amafka a Mwase,Mwase alibe Problem olakwa nameneme amamulondola kunyumba kwake,mamuna weniweni wayenela kudya zimenezi oti zalowa zokha mnyumba.

 40. Ndyekut a Flao samafkapo pamene amafka a Mwase,Mwase alibe Problem olakwa nameneme amamulondola kunyumba kwake,mamuna weniweni wayenela kudya zimenezi oti zalowa zokha mnyumba.

 41. Akamati Mkazi Wopusa Amamasula Banja Ndi Manja Ake Ndiye Zimenezi Komanso Amati Chigolo Ndi Mwini Thako, Mkazi Ameneyi Anayeneranso Kumenyedwanso Kwambiri Ndi Mamuna Wakeyo, Chifukwa Ali Mgulu La Akazi Opusa

 42. imeneyi ikhale vuto lanjalayi paja zitete zatitopetsa nde ife tili ndi ndalama tikungokwasula akazi ayeni akewa koma uchenjele udzapange wa ine udzawone udzakanilila pomwepo ndidzakudula chilawo

 43. The woman is a mere concubine, she isn’t any man’s serious wife otherwise Joe was caught unawares not ready for the bout.

 44. Mnyamata woikonda Malawi wokhala pa bemchi koma osalowa amayang’ana akazi aweni pa bemchipo asaaa akadakugulula mano kuti umkale tiger

 45. Ngati alipo yemwe sanachimwepo ndi odala ,enanu mukukhalangati mulibe uchimo. Tikati tibe uchimo tidzinyenga tokha ndipo mwayife mulibe choonadi.Molo momupepherera mukumuseka anthu oipa ngati inu

 46. Omwase, this portrays bad image on Zodiac and atolankhani onse. Why running after somebody’s wife? If in flao’s shoes, ndikadamukapa ndi chikwanje. Its not unfair kumadya ufa wamuzako. Childish Rita deseves the cooler than any other.

 47. @ news night we would wish to hear from u our listeners on what has happened to Mwase if his custody is not political.”Zikachitika mumvera kwa ife “

 48. Kkkkkk adyooo mwase awapwanyaaa, nyumbaaa apwanyaaa, galimoto apwaanyaaa, achibwesiwoso awapwanyaaa;;;; kuchipanda kudumba adyoo mwazeee adakafaaa mbambadiii

 49. nde osaikapo photo ya muthu womenyedwayo bwanji? apapa zikuonetsa ngati Joe wadya mkazi wa mwindi ndikuswaso mwini mkaziyo2

 50. palibe nkhani apa mulungu wamphavu zonse anakhululukira HULE logwidwa ndi chigololo who is JOE MWASE!!! chitsiru si JOE koma nkazi coz it seems adalumbira mokakamizika poyambilira so take it eazy

 51. A Joe mwase akakhala a zeru sadakamenyenga mkazi wa banja. Umenewu ndi umve! Nyasi! Mkazi oteroyo ali ngati “public toilet” mochita chimbudzi aliyese! Ukamanyenga mkazi wa munthu wina udziwe kuti ndiwe wa nyasi. Akazi opanda banja ali mbweeeeeee. Ndiye chotanganidwira ndi mkazi wa munthu wina ndi cha? Upanda zeru! Upusa! Akazi ndi anthu ofoka pa zambiri. Pamafunika uchita avoid! Upewa! Chifukwa uyenera ulemekeza munthu wina. Tchimo la chigololo ndi loopsya!!!! Umalangidwa pompo! Awaso a Flao sadakamumenya mwaseyo. Adakangu uza ma neighbour. Kutenga awiriwo wa ku Police basi. Zatheka!! Angakhale umenye upindulanji? Mkaziyo sakukonda! Ndiye tanthauzo lake. Muleke!!!!! Osamalimbana nazo! Amuna chenjerani ndi akazi. Amakhala ndi zibwezi 10. Wina tsitsi. Wina ma bill a phone. Wina fuel. Wina kwa telala. Wina transport. Wina sapato. Wina zakudya. Wina othandiza makolo. Wina ogula zibangili. Wina wa pa sterling. Wina airtime. Wina ogula mowa. Wina wa rent. Wina honeymoon ku Salima. Wina wa ku garage. Wina wa bridal shower. Wina wa birthday!!!!!! —————- sinthani…….. akazi ndi abwino komaso ndi oipa. Si onse. Koma ena ambiri khalidwe lawo ndi limenero. Inu akazi abwino. Pitilizani. Osathamangira chuma. Chimatha! Imafika nthawi ya chiweruzo. Mudzakhala osauka.

  1. wekha ukut “Tchimo la chigololo ndiloopsa”….wekhaso ukut “akazi ali mbwee” advising him to cheat on his wife as well (kwa ma hule) osat akazi apa Banja koz ndiumve….kkkk…

   Ndeee wa pa Banja ndi umve.lyk a publik toilet az u say..nanga hule?..ndee wa clean…Nonsense

   The Fact is…ADULTERY IS A SIN….

   Husbands love your wives
   wives love your husbands
   Dont cheat on each other

   why?
   because Sex outside marriage (Adultery) is a Sin regardless of who u hv sex with

   So this Mwase boy and this cheating wife…ngofunika kuwathila “Doctrine”….They shud repent….Ask for forgivess from God..and they shud never do that again…

   Osat ma advice opusa mukuperekawa….oti “Mahule” ali mbweeee…ndeee chan?…thats un-Godly advice….Very Wrong advice…

  2. Tawonaninso ena kufuna kuwoneka amzeru kwambiri mzawo akupereka malangizo iwo akubwera kupanga crush what someone has said a#Pilirane ifetu tamva chomwe mun2yu akutanthauza kuti akazi ndiambiri munthu utha kipeza wako than kumayenda ndimkazi wamwini wake inu chichewa simumachidziwa kapena?? Comment yanuyi kwa ine ndiyopanda mzeru munthuyu wayankhula bwino lomwe comment yanuyi ndiye yopusa chifukwa mukuti wanena kuti mahule ali mbweee zomwemu statement yamunthuyi mukibe wanena kuti akazi opanda banja ali mbweee ndiye inu zinzazo mwazoitenga kuti? I thnk muli ndi mkwiyo chabe pankhani imeneyi i dont know why ndiye osamatenga mkhwiyo wanu kuuika pamunthu wina coz alipo anthu ena amzeru kuposa momwe mumazionela inuyo mapeto ake muzapusa ndinu ngati momwe mwachitila apamu eni ake mumaona ngati mukuchenjera osadziwa mukupusa wake up! be civilised learn to respect other pipo’s views Zikomo

  3. Kodi akazi ndi amuna hule ndindani ? Coz pamakhara kugwilizana asana gonane athuwa dat means amdziwa kale zimene akuchita or ali pa banja kapena ai vuto ndi mtima wa NYere zopandanazo banja kaya nkz or mamuna kufuna kungopeza near sex Doctor mpka neba

  4. Tisawaweluze pakut kuweluza ndikwanamalenga brother afotokoza ma strategical plans 4 women iz 100% sure. Pachikhalidwe chathu mzimayi ayenera kudzipatsa ulemu koma lero bolanso kukwatira hule mkulisintha zochita. Azibambowa tawabwiritsabwiritsa konda ine mkumawathawanso. Joe Mwase ndimakutenga ngati brother wanga coz am a very gud friend of ur ccta wapangiranji izi kuononga reputation motere, wachititsa manyazi banja la Mwase, Zodiac, mafans ako komanso wachimwira Mulungu. Lapani

  5. #Ken…..
   sikut ndikufunika kuoneka wanzeru….thats just the biblical truth….ndawerenga zomwe alemba nkuluyu koma nzopanda Pake….and iweo kuvomereza zimenezo ndee kut ndiwe #wopusa chimozimozi ngat iyeyo…#Kupusa ndee kumeneko-ko

   Apereka maganizo akedi jst lyk many ppo hu hv done the same thing…but the #Wrong #Advice…

   Sunday ku church…lero ukuvomereza zopeperazi?…

   You need to grow up…and start “giving matured-Christian advice”….His advice is un-Godly jst lyk many advice i hv seen on this post…

   “Oti ma hule ali mbweee…yet we are talking about a married man….Yet adultery is sin…”
   Et Nkazi wa pa Banja ndi Umve…lyk a public toilet..Ma hule bola…….ma hule ndee a clean?…Zonse nzolakwika

   What the guys hv done is wrong…Not worth to b supported…and advising the Man to sleep with whores than married women its like asking a #Hard core wizard to abandon his ways and join #Satanism

   Christians don jst #Respect any other ppos views….They shud be Godly….

   If u don understand my above comment…try to focus on the scriptures……

  6. #Ken…
   iweo ndamene sunanve….try to read the whole comment and relate what he says……Not singling out statements…

   Zomwe wanena zot akazi ot sali pa Banja ali mbweee …try to connect that with what he says in his first few sentences…what do u think that means?…

   #Ken…It means…ma hule ali mbweeee…..try to understand the whole comment…#Osamaiwala nsanga..

   and as a christian…i don jst #Respect any devil driven views…Only Godly advice….

 52. Asaaa, ndiye vuto lanu ndichani inu a Malawi 24? mwina. poti ndi radio presenter ndiye mukuona ngati he is vry special kuti safunsila akazi wokwatila?

 53. Mukakhala ndi ndalama doesnt mean u shld mess wit other men’s wives koma poti akazi ena ndi mbuzi u can even catch ’em wit a coin despite havin a man worth millions#LetsBeResponsible

  1. Likewise some men are dogs, they can have a beautiful, faithful loving wife. but still go chasing after dirty filthy prostitutes out of greed .#LetsAllBeResponsible

 54. Hahahahaha!!! Waseweroo chani mutu ngati chibongaa Ntchito kuzembera akazi a eni basi ine ndikanakhalapo ndikanakuphwanya kamutu kako kooouumako!!

 55. Mwase n.nyamata otakataka apatsidwe nyota basi ndiochenjela nkabudula osango mudula nginiyo bwanji ango tsala ndima sapota awili okhawo hahahahaha koma joe adah ndiwe dolo waposa bushilili tu apa

 56. Amene walemba nkhani iyi bwanj sudaikepo zina lako? kapena ndiwe Andrew caan Chilapondwa??? ukuopa kut akakuzindikira kut ukumuipisira mbiri joe mwase akumphwanya eti??? kkkk

 57. Enanu mukhoza kulankhula ngati ndiinu abwino poti simunagwidwe lero Joe akuoneka ochimwa poti wagwidwa. mawa ndiiweyo ukulankhulitsawe. Kulibekoso wabwino Koma kusagwidwa.

  1. Man,ifenso tili ndi zibwenzi koma osati akazi aeni.ndimanyenga ana asukulu,divorced girls amwana mmodzi.Ukanyenga mkazi wamwin,dikilira imfa.angomchepetsanso,akadangomupha basi.

 58. ine ndikuona ngati sanamenyedwe mokwana,akananthyora zolimba athe mwezi ali chigonere! wopusa bwanji sanakakenge ku Taven?

 59. Inu amalawi 24 anachinda wanu,kamaso nanu amwase wanu adatani ndiye mwati sanatuluke magazi koma thovu zilibwino fungo kuti buuu ndiye mwamunayo kkkkk

 60. Aaaaaa!! Chachlendo kwaife ndchan? Akadakhala osatchuka mukadamulemba? Ngat zakuthelan zolemba mukajambule maliseche yazikazianu

 61. Kufera kutchuka azimai amasikwano mmalo mosamala mabanja anu:mukagonana ndi munthu wotchuka mumapeza phindu lanji????? Kufuna kufa basi akuwonekeramu alibwino ameneyu??

 62. Nkat ndiunetsetse apa aliyese analawako chgololo mmene chkomera ndye naye znamuvuta nkaz naye anazipeleka kt athandizane kkkkkk #www.chigololo.com

 63. Mesa amati zikachita timvera kwa iwowo nde iyi bwanji sinamveke Pa Zodiak?Zimakoma nkhani za eni eti hahaha !!!!!!Khoswe akhala wa Zodiak sawululika!!kkkllll

 64. kungwira ntchito ku zodiak ndiy umafuna kut asanyenge? ngat nkaziyo anamusekerera ndiy akadatani? iweyo amene walemba nkhaniyi sunanyengeko nkazi or chibwezi cha wina

 65. Ok komano ndizoona kuti palibe osachimwa.koma tisamachimwe dala pa chifukwa choti aliyense ndiochimwa.kufa saferana.aliyense adzalangidwa yekha malingana ndi machimo amene anapanga.

 66. Azi bambo mpunzilani kusamala azi mai mmakomoku. Mukamapanda kuwaonetsa chikondi, kumawaonetsa ka chikondi kabodza ndiye mkaziyo akazindikira. Nkukumana ndi odziwa chikondi ngati amenewo shaaaa zavuta. Tangoganizani nokha ndiye kuti maiwa amathawa chani nyumba mwawo?

  1. Pali bwino umusiyilatu mwamuna oteroyo usiyana mkumazemba, kenako kubweraso udzakhala pakhomo pompo pa mwamuna wosowa chikondiyo. Chilungamu chimafunika. Osati kuchita uzemba. Nanga tawonani tsopano. Zoti mwamuna, Flao anali oipa sizidziwika tsopano! Oipa akhala wagwidwayo!

  2. Koma azi bambo azipita kunja ndi kubwelanso kwa nkazi wawo. Sichoncho? Azipezeka azimai olimba mtima choncho enanu mutengelepo mpunziro

  3. Maliro akakhala pamdzako umati. Tiyeni tipephe ambuye wachifundo akuthothozeni. Koma zikakugwera panyumba pako umalira koopsa mpakana kulodza mfiti. Mabanja amasiku ano its Made in China. We are living in the world of competition. Akazi onse masiku ano ndiotengeka ndizinthu zachabe.

  4. Mwina vuto ndi abambo anadulitsa nde mayi amamva kuwawa kkkkkkkk tonse titenge phunziro thus a sin ,mwaphwanya lamulo loti usasilire nkaz wanzako

 67. its like a pastor kulalikila mu church!!! akuti chonde ana amulungu musachite chigololo bible limakana mupeza akuti m’busa uja wagwidwa chigololo ndi nkazi wayiniache,, nde munthu otereyo timamukuntha kuti adziwe zoti amapereka tchimo kwa anthu ndiyeyo kkkkkkk mukanamudula mwendo

  1. aise abusa olalikira zachigololo kenako mkupezeka kt agwidwa aja amakhar kt polalikirapo amafuna kt iwe uwasiye asale nawo yekha m’busa yo

 68. Kkk koma wailesi imalemekeza chinthu chonyasa kuteroko ndiwe? Poti ndakuziwa kale koma olo osakuziwa sindikanaluza kanthu!

 69. Mesa ndiwe opanga mafizo 90 minutes koma osatopa bwanji osamubandula mwini mkazyo kkkkkkkkkkkkkkk za zodiak zikachitika timvera a Malawi 24

 70. Kkkkkkkkk why u didn’t kill him?this is the way how virus go all over because of shit people like him,he must sleep with my wife Jacqueline & l will show him how Malawi is.

Comments are closed.