…No, not yet the time to shout: ‘Ahoy Rasta!’
It is just a few steps in the right direction, if you are a liberal, and of course towards the wrong direction if you are a deep conservative.
Legislators in the Malawi Parliament have adopted a motion by Ntchisi North legislator Boniface Kadzamira, asking government to legalise the growing and use of hemp in the country. However, it is not the hemp that is popular among most Malawians. It is industrial hemp.
Kadzamira moved the motion considering the enormous economic, medical and nutritional value industrial hemp has.
The legislator said that Marijuana locally know as “chamba” can be used as viable alternative that can help drive in forex into Malawi.
“An acre of [Indian] hemp produces more paper than wood pulp or tree. Apart from paper, you can produce fibre, fabric, soap, lighting oil, medicines, food oil and proteins for both humans and animals,” kadzamira’s motion in the house went.
During the August meetings for the legislators on Thursday, cabinet ministers and Members of Parliament were more receptive of the motion and expressed little misgivings about it apparently giving a green light to the cultivation of hemp in the country.
Leader of the house George Chaponda told the house that Malawians are willing to have Marijuana being legalized in the country.
However some Members of Paliament (MP’s) have demanded for a bill that will be voted for on the issue of legalizing Indian hemp.
Malawi’s Indian hemp is internationally renowned as one of the finest sativa strains from Africa according to an entry on Wikipedia.
The entry claims that its popularity has led to such a profound increase in marijuana tourism and economic profit in Malawi that it is even listed as one of the three “Big C’s” in Malawian exports: Chambo (Tilapia fish), Chombe (tea), and Chamba (Malawi gold).
bomalamalawi lidzakhalaosauka mpakakale kukonkondakubisandalama
Inenso ndine rasta koma chamba sinditsuta ndi anthu ambiri amene amasuta chamba koma si marasta ukhakhala rasta sinde kuti amasuta chamba ai ndi ma rasta angati amene adapengapo ndichamba. Chamba chili ndi zintchito zambiri zimene agwiritsa osati kusutakokha ai. boma liganize bwino akutaya nthawi kukambirana nkhani yachamba mmalo moti akhambirane nkhani yanja komanso kukwera tengo kwa chimanga chambacho sichingapulumutse anthu kunjala apa dzikuoneka kuti nzeru ku boma zikuchepa. Chabwino ndifuseko lamulolo likavomeledzedwa ndi anthu angati angayambe ulimiyo nanga ndidani amene angapite kwanzake kukagola chambacho poti aliyetse ndimlimi dzaukape basi
Zimenezotu apolice
Mhmm MALAWI, inde Malawi ,ona kulotalota kwako, kufuna funa mtendele, Mlengi timveleni a Malawi kulira.
Uloredwe
Kkkkk malawi try to reach in to hight step thats good idea lets try guyz maybe we can change malawi
Sikuti alora niku bema mwausilu silutu ayi azikumanganibe
Ganja farme jah laster allow mybe we can develop malawians people maka ife anthu akumudzi ziri nyatwa hevy
SINSEMILLA FREE THE HERB
Mpofunika boma lililonse kumangidwe mental hospital, chifukwatu ma yuthi apenga ambiri
Camba ici ndicocyana kwambiri ndicomwe ife tmasuta cija
chilimidwe basi, smoking will be an added advantage
Jah bless bless Malawi the warm heart of Africa. In ganja we trust!!
show malawi
Nothing to say
Iyi Nde Nd Dhilu.
Chaka chino chamba tilima takambilana kale ndi saulos chilimaa
Mmmmm kma zipatala za anthu amisala amange zochuluka
Change ur mentality.rasta salimbikitsa kusuta chamba koma kukonda Jahova mlengi wanu.ine ndine rasta koma sindisuta.kololeza ulimi wa chamba sikuti tikunena kusuta ayi.koma chambachi kupangila zinthu zambiri monga momwe maiko ena akuchitila.there4,ma research ambiri ndiofunika.tikhonza kumapanga zinthu zambiri ndikumapanga export kumaiko ena.tobacco is declining.lamulo la chamba ndi la a samunda.this is 21st century,where science is advancing.misala ndimatenda ngati ali onse.misala ili ndi ma causes ake please reasearch.how many rastas are in ur mental hospital and how many rastas smoke?i have sold chamba here and even in zimbabwe.chamba could help grow our falling economy.the debate is long overdue.osasokoneza nkhani,za gay ndiza guy,za ma albino ndi zina.
Yah ya awo nde mawu
Muti zithekadi zimenezi kikikikikikiki mwinatu tidikilebe mwina mkulimako fodya wapogwila pochuluka
zili bobo ndiye yake yoce boo
ndiyee yake zikubweka boo
Jaaaaah>Rastar faraiiii.Das raster family gonner fil yap upon dis ligalised,we can smoke and sale jersy namba 13 wit na fear.Hemp is money and life,try to eat it,KUSUTA KUMAONONGA MOYO
Mmmmmmm apa burley ali madzi
Ine sinsuta ko pamenepo mudya bho not mp s but pple
hehehe koma kumeko
why you allow drags exporting outside of country and you are refuse Hemp to exprt?, iwnna incollege all canabis grower to grow more so that we can Export outside of acountry (mr yellow man) hahaha
Dhilu yabwino tizilima chimenecho
Only #jah_knewz chamba chlimidwe bas
Ever lasting green plant
zili mushe maningi, ndibwelela kumudzi basi ganja ndi dilu
Kulemela basi !!!
We wil Stil remain poor even if we Start exporting hemp it wil b the buyers making prices for the growers Zafodya zimakhala bwanji kuKanengo???Lets wakeup Malawians we have been Used for along time bt nt now…
ndiye tisalime?
thats nice amachedwa ndichan??? mose tinaambila kulima bare osatukuka tisinthekodiapa
Wow zafikapamenepa m paka boma kumvomereza zimenezo wow
It’s Better To Use It Propery (eg use It to make madicine Etc);no Smoking.
Mukamva boma lapenga ndi umphawi ndiye zimenezi layambanso kuchita zachamba
Oh my God
Kkkkkkkkk here we go the future is brighter now am going back home now to grow hectares of chamba and
Oh my word, guys, tobacco is a dying industry. If the ministry can control the growth of hemp, we as Malawians will be able to grow it at least three times a year and help our economy. “Hemp is for industrial use not consumption and smoking Chamba is your choice”
Thumbs up to parliament
This positive reasonin n thinkin,big up.the worl
wow….!gud to hear that
Yayaa boh
Sikut akuloleza kusuta ayi? Chilengedwechit chimagwilitsidwa ntchito njira zabwino zambiri mbiri,nkani pali mawu oti ”use ndi abuse”
ndiyambe ulimi sapano kkkkkk
Ndie panopa tikuembekezera kuti avomereze mukampeza wina ali ndi chaba osamugwira kapena kuotcha zokolorazo, onse anamangidwa adzitulutsidwa mwanchibisira, kusuta adzisuta pena paliponse koma akaona a police adzizimisa poembekeza aproval ya Parliament kkkkkk osaiwala pogulitsa adziikano ma packet a china osati mu pepala la khaki ndipo pomaliza akadzavomereza boma likuenera kudzayakha mafuso ochuluka pazifukwa zoveka bwino pochedwa kuvomereza kuti chamba chidzilimidwa mwa ufulu kutero lidzaenera kupereka chindapusa chopereka mbeu ya Chamba ku banja lililonse mwaurere opanda kugwiritsa tchito makuponi kkkkkkkkkkkkk zikomo
Ok
zachamba
Lord have mercy on us for we know not what we r doing
malawi becoming another Jamaica aaahoooyi
Tachilela nthawi yaitali,tisute basi.
That will be regarded as cash crop, yet we do not have enough resources in the country. I don’t smoke but i agree maybe things will change. Some of those who are in position have their own market. Koma akamupeza munthu wamba nde kumulamula zaka kufanana ndi mlandu wokupha mmmmm. Warm heart of Africa
We the rastafarians are now free,very happy indeed tizingobanda every where without disturbances..
Chamba ndu gold pangani zomwezo tikuguna tilemele ife
Don say ulimi wa chamba so kt anthu aope ayi kma wat z truth.
MULUNGU ngat anasakha kt tzakhala osauku tangovomelezani bac chamba cchngatukule dzoko kma amene azlima chambacho bac FUNDO YOPUSA KWAMBILI
kma ndye amisala achuluka bwanj she!!! zobeba anthu amisala amandsangalatsa kwambili mamaka akavala kamisolo mutu zobeba kwabac kkkkk
Zilibho
Its better to legalize ganja than homosexually
What does homosexuality have to do with ganja. This is like saying it is better to play soccer than dance with a lion. Unrelated issues!
kodi zili apa ndizachamba eti kkkkk
vats agud idea iam allwred big grower koma nimasanja waball sungandiyambe.kakambiranani if tkupanga inu mukungoyesera
Abdullah Muhammad Jr.
Zipatala za mental zionjezeredwe, madokotala akumental aphunzitsidwe ochuluka amene adamangidwa nkhani ya chamba amasulidwe kt akaphunzitseko ena,tikatero chamba chizidzalimidwa mtsogolomu.
The only problem is that the Hemp is still illegal in many Countries.
Chilimidwe basi dziko lili m’manja mwa …………….
moti ine ndiyamba kulima basi cash crop ngati imeneyi
State any two ways of caring for marijuana inorder to produce highest grade (i)watering frequently (ii)removing unwanted weeds around the crop(4 marks) in an essay form…explain 5 importances of marijuana…(20marks) #legalise
mayb People cn stop killing Albinos they cn make money wt chamba
zafika pa mwana wakana phala, Malawi iribe source ya chuma..
If this law works Malawi is going to be rich fast coz Malawian hemp is strong more than any hemp in Africa and its on hie demand
Chamba basi
yah matsiku omaliza
Fans ibande zimenezi mwa mtima biii
Tipezeletu mind a ikuluikulu papa… tiphe makwacha..
Izi ndiye za chamba, akufuna kuti chigwe mtengo eti panopa tikugulitsa K150 bola imodzi ndiye chikayamba kulimidwa mwachisawawa bola tizizagulitsa K20 basi. Zachamba basi.
Kkkkkkk
150 watchipisa koma 200
Shaaaa K200/ bola kuno Ku Zomba kwa Mwambo tikutchipisa etiii. Ndakumvani @ Lawrence wanyerere Luhanga, tikweza basi kkkkk
chonde tiloreni ku parliament tilimetu plz
Ife ku nkhotakota kuno tdayamba kale kulima sizachlendo komaso kuno ndiye tmadya ganja molaptsa
thats a nice development bcoz zosatila za barley taziona&alimi cidwi pa ulimi wafodya chidatha,now its time&time is now to go ahead wit other altarnative 4 de goodness of our beloved malawi.viva ganja! viva maruana !more fire malawian mps togeder we can boost our economy.
rasters tinyadire zimenezi kkkkk
kkkkkkkk Ulimi walero
Eeeee!!!! koma ndiye kuli kanthu. Ine ndikuyang’ana mu 5-10 years za ulimi umenewu kuti kodi miti ya anthu idzakhala yotani? (Sodomu ndi Gomola) Tiye nazoni mwina mkukoza dziko.
Ministry of Agri. Must put chamba as new topic in our secondary xools n universities(like BUNDA) , 4 the country to produce highgrade n highquality weed.
Bola pamenepo mwayamba kuganiza
So Gvt must prepare to build another Mental hospital, bcoz ndasungila highgrade.
Kundendeko munapasidwa mafoni
legalisation fe de ganja herb: rasta need now
Akuchedwa ife mbeu tasunga
Ganja Is Good,ligalize It,is Good For Asthma,multiple Screlosis,glaucoma,cancer,its A Pain Reliever Proved By Scientists,its An Appetiser Too Moti Pano Ndili Mu High Ndabanda Kale Ths Moning,its Not A Drug Its A Healing Of The Nation
That’s gud news 4 us Rasterfarians.Jah!!! Raster Far I !!!
WELCOME
Ziligood tisute basi
with or without the legislation osuta azasuta mpaka kalekale………………….. Why Bother restricting.
Ahooooy
pamenepa ndiye kti amene munatimanga kale ndikhani ya chamba mutimasula kapena ayi
Kaya Wa Mutu Wa Plastic Zako Utola Makoko Amthochi!
smoke and talk fi blessings yehsai blessed is hu knu smokn rizon
Ziko litha kutukuka koopsa ndipo ndi Ulimi okhawo tingapindule nawo
Then Ministry of Agriculture will have an added crop & must redesign Guide to Agriculture booklet•Yes zitha kubeba2 pokayang`ana peji lake kkkkk
Malawi gold indeed ulova umenewu…..its a deal
that’s cute mwina malawi can become the nxt Jamaica to xport nice ganja
eeeeeeeeee paja amalawi,, albino sakukwana ayiiiii koma mugulisekaye chamba, kenako tizigulisana ufitinotu eeeee
Misika nsiyosavuta
bless up
But I believe its licence from Govt will be expensive akulu akulu sikuti aliyense azalima mbanje okhawo agule licence kkkk
there alot of businesses done illigally.
Mot ku mtsonkhano wa president tizika roller eti?
New Jamaica? Mmmmmm.
Takomzeka kulima bola Boma itifufuzire misika yake….kkkkkk
Y?Us Imeneyo Ndiye Dhilu
allow them
Chamba chomwecho kuti wawa may b Malawi can depend on its self than depending on Donner’s MP’s wake up pkz vote for it .Bt first of all deal with ALBINSIM attack. If u don’t do so means ur the one who’s sending people to kill Albinsim people let’s stand to gather to stop this attitude. I supported Kalindo for what he wanted to show to Malawians that’s good leadership. Osamangoyang’anira anthu akuphedwa ayi. But Lucius Banda shame on u yup busy talking of Wi-Fi internet instead of working about Albinsim killed I thaught ur clever bt mmmmmmmm u stubborn. I don’t know what ur people in Balaka they will do when they hear this stupidity mind kkkkkkk komadi ndiwe was SATANIC
Mwina tingabwerere kumudzi koma nde chidyedwa heav ndima Rastafarian
Tiyambe kulima basi .
Chani??!
Malawi Sopano Ndiye Ndikukuvelani Pa 99mhz