Gabadinho Mhango scored a hat trick to inspire Malawi National Football Team to a comfortable 3-nil victory over an Under 20 Angola National Football Team in the on-going Cosafa Castle Senior Challenge Cup in Namibia on Sunday night.
The Flames mentor Ernest Mtawali fielded a strong side no wonder they were the favorites to win the encounter.
Malawi had more chances in the opening minutes through Chiukepo Msowoya who saw his header coming off the upright from an Isaac Kaliyati’s cross.
Minutes later, Mhango had another chance from Kaliyati’s cross but his timing was poor as he headed off the target.
At the other end, the Angolans saw their goal disallowed for offside before missing another chance when Harry Nyirenda cleared the ball before crossing the goal mouth to the disbelief of the Angolan head coach.
However, it was Malawi who took a lead just after the half hour mark.
Mhango’s header from a Stainley Sanudi’s free kick took a deflection before kissing the back of the net, 1-0.
The Flames should have added another goal but wasteful Msowoya headed over the bar from Kaliyati’s low cross drive.
Come second half, the Angolans were composed but Malawi used experience to control their midfield through Rafick Namwera and Joseph Kamwendo.
Mhango almost doubled his lead when released a thunderbolt only to miss the goal mouth with an inch.
Msowoya was having a bad day as he kept on misfiring from all angles.
Malawi doubled their lead through Mhango again.
This time it was a brilliant move from Namwera who released Mhango into the box before slotting past the advanced Angolan shot-stopper,2-nil.
Mtawali then brought in Muhamad Sulumba, Yamikani Fodya and Dalitso Sailesi for Msowoya, Francis Mulimbika and Gerald Phiri Jnr.
Mhango sealed his hatrick from the spot following a handball by Angola’s captain to make it 3-nil and after the end of the regulation time, it ended 3-nil.
Malawi will play Mauritius on Tuesday and a victory will automatically send them through to the quarter-finals of the cup.
CHIUKEPO lero asayambe kumulowetsa atapeza Enerst munthuwina asayambe lero chiukepo mphuma
Mukanena kt muli bwino mudzinyenga nokha otsatira flamez….
Kungokhala ndi mtima wa ufiti osayamika.koma inakaluza?tatiyeni tizikondana ziko lathu.
ine ndikanakondwa ataimenya Zimbabwe ija osati Angola yo ayi kkkkkkkkkkkkkkkkk
zilibe kathu kuno ku south Africa pa radio akuti Malawi beat angola zama under 20 ndizanu administration mdakazanu kwanuko
woza woza Malawi keep up
ine ndikuyera kuyamikira kuti apitirize kuchita bwino!!!!!!
Amalawife zimativuta kuti tizivomeleza pachinthu chikachitika. Ili ndidziko lathu tiyeni tilikonde. Mpila tawina tiyeni tithokoze mulungu kut anali mbali yathu. Mpila ndi win & luz. Thanx to flames & those they post good comments for supportng our beloved team” THE FLAMES”!
I wish titapitiliza kuwina
Thanks fo the victory flames ,do it again with ur equals next time
zili bwino.
zot inali under 20 ukuziwa ndiwe…..ife taidya Angola basi.
kungoatukana
Congratulations our team Angola ndi team yayikulu.sidspange dala imeneyo ndi yomwe anaikhulupirila.
Amalawi kawili kawili tizisiyanitsa pakuti pakalabu ndi team yadziko kulankhulaku kukusonyeza momwe mumacemelela makalabu anthu ai siconco team ikacita bwino tiyeni tiyamike ngati kwa Angola kudali vutomukuti ndi ana sivuto laamalawi ai Iwo amadziwa comwe acita tiyeni tiyamike team yacita bwino sikalabu iyi ai ndi team yadziko lathu
Best speach malawi yagojetsa angola 3-0
Koma Jersey yake sidali imeneyi, idali yakuda and Red guys, ikadakhala ya RED-yi tikadaluza
Koma Malawi tinakhalabwanji osamakonda ziko lanthu
Fulem imadodadada
iyi ndi cosafa
uyo watumiza mwana wazithemba
ndiye mumati tiwanyengelele?
Inu anthu ose mukunena kuti malawi imamenya ndi ana mituyanu sigwila tchito kuyambila lero mukuyeneta kupita ku metulo akakuoneni tiyenera tisapote flames ndi fe amalawi
Achiwukepo osadzamutengaso,zoona nkhalakale ngati ameneyu kumakanika kugwilitsa ntchito timipila tabwino amalandila.Its orkey Brantyre serect.
Guy ndi ana awa ango gwera amalawi
Gaba u ‘ such a blessin
suzgo la ba Malawi mphenepapo apo malawi yiluzenge nga mukuti vichi.?
Sindikuona chosekelera chifukwa ndi chimodzi modzi kuchinya Djibout.Anzathu anaseweretsa ana pomwe ife timu yonse yodalirika ya malawi, Shem!
ine sindikuonapo chachilendo Malawi kugonjesa timu ya Ngola . Dzinali chocho pamene Malawi idatsewera ndi timu yotchuka ya Algearia nigonjesa 3 kwaduuu koma zomvesa chisoni magame onsalawo timu ya Malawi imangogonja
It’s Cosafa senior challenge cup not Cosafa under 20 Ndiye watumiza khanda wazidalira congrats flames
Bravo mw…..makesure madagascar muiphetso….
Under 20 vs Malawi mmmmmm shem
More fire Flames! Angola anaderera kwambiri dzulo
Malwi were playing wth black china jersey, so wy u give us pictures of nike and adidas original jersey? This was for africon only Carlsberg has taken their jersey
Under 14 mkumati tawina malawi sizanva pamene paja panafunika 20 kwa duu
Tinawatu ndie kt abwerese under 20.bola anawa anlimba inakakhala under 25-40 ya Angola ndie zinakakwa 8 kwachilowere
Inu mukuti timamenya ndi under 12 ndinu makape iweso admin ndiweso chitsiru kodi isaac kaliati gaba sanudi namwera gerrald phiri jnr gabeya ndi azibambo? Tamayamikani amalawi chofunika coach asamasinthe sinthe team komaso first 11 ija inalibwino
Mmawa ‘Flames siyidzamva!’ madzulo ‘Gaba iz back’. Nde sapota mapeto ameneyo.
Koma ndidasangalala dzulo ndi mpila wa flames congratulations our boys…. Supporting you our Nerbour flames.
Zomwezi mpaka kukhetsera thukuta,anawo!
Tidzayamba kuikonda ngati ingama wine magemu
kkkk kunena zoona ine tawina koma zigoli zomuchinya mwana wa zaka 15 nde tikachite kunyadila kuti team ilibwino?mmm tidikire kaye akumane ndi akuluakulu anzawo tizawone kuti zitha bwanji
Mwana sitimamuyamikila pamaso amayamba kuzipopa ndikuyamba kulakwitsa
nonse amene mukut gaba wawina coz amamenya ndi ana mpira wamapazi guys mulinawo kutali,,mpira sikukura ingoyamikani bora team yapeza chipambano,inuyo myendo imeneyo ingasewele mpira,bola taphura bas
A Malawi Tatiyeni Tiziyamika Team Yathu Ikachita Bwino…Tikanaluzaso Bweziso Mukuti Taluza Ndi Ana,ku Angola Ko Potenga Team Yao Ija Amaidalira Kut Ikamenya Ndi Team Inailiyose Ku (COSAFA) Ndiy Musamaphweketse Kut Tawina Chifukwa Ndi Ana. Munayamba Mwavako Kut Mwana Amamenya Mpira??? Angora Siingatumize Ana Ku (COSAFA) Ndiy Kut Amaidalira Kut Ikawapangira Zakupsya
Inu flames sidzatheka musaone ngat yayamba kutheka chifukwa dzulo yapanga zotheka
Yaaaa ndidzomwe timayembekedzera ife osati kumangokhalila kuludza dzimaku kanikan bwanji koyenda
Angola under 19 VS Malawi under 40
akanagonjanso pano mukuti achinyidwa ndi ana a U 20,ufiti wakula ku Malawi kuno
wachinyadi koma zinakakwana ten kuphonya ndimzake chiukepo
Malawi moto motoooo
Gaba still under 20?
Mwatichosa manyazi anyamata
The flames on flames
zonyozazo simuzasiya zili m’mangazi anu that’s y zithu zanu sizimayenda bwino azanufe timadya bho zinatiyendela we deserve any situation
Well done flames I did watch it yes of course was good keep on guys
shame on u Admin
amalawi sachedwa kuiwala
The tournament is called Cosafa Castle Senior Challenge Cup so why are you saying about under 20? That is the Senior team of Angola. In football seniority is not necessarily in age but in performance.
Ndiye siize yathu osati Zimbabwe eeee
Chodziwika ndichakuti FlAMES Yawina angola ZinAzo nkusayamika…
Why you say U 20 not Angola National Team………..?
Admin opusa uyu
eya amamenya ndi under 20,wamkulu adali wazaka .19 basi enawose mafana,ndipo malawi ikadaluza ikadayaluka manews asouthafrika adalemba zikhala zamanyazi #malawi ikaluza komaso #angola sidapume ai kuchokela ku game kufikila ku game ina.tiwone akakumana nda akulu akulu azawo zithabwanji
Ndewu ya bambo ndi mwana…. congratulations kkkkkk
Very nice mupitilize flames timakunyadirani
FRAMES YAMVA KKK PITILIZANI TAKONDWERA
Angola anakhulupirira kuti team yao yikachita bwino. Flame inachinya team ya Angola osati under 20. Anthu osayamika inu. Chifukwa chiyani ife a Malawi sitiyamika ena akachita bwino? Sanje basi!!!.
Thats speaking anakaluza bwenzi akuti malawi kuchinyidwa ndi under 20 apa akuchita manyazi poti amadikira kuti malawi iluza ndichifukwa akunyozabe
Malawi under 41 vs. Angola under 12
Ufiti ndiumene wachuluka pamalawi alibe kuyamika kuuluka number one folish
Zoona zake agaba
Mudzipanga choncho amalawi takunyadila mwatichotsa manyazi ku agalu aku zimbambwe sikulina muzawaponda nawotso
Isaac Kaliati probably man of the mutch
thanks guys koma musazatikhumudwise pls
Angola under 20 against mlw so called senior team, kaya chonchobe.
Kaya inali under 14 or 20 koma chidziwika ndi choti flames yathambitsa team ya angola zigoli zitatu kwa chiyambireni, ntchito yabwino imeneyi ipitililre flames…gud luck
That’s gud
This is the same as kuchinya team ya azimai .mxiew mmalo motibula Mashona aja
Ayi coach wayigwila tchito kwambiri
Gabba was best pray tonment in.Malawi Chiukepo’Sulumba ndi a yong kwa Gabba.God bless Flamers.
The next game Mtawali ayambitse Gabba ndi Wadabwa or Sulumba, Chiukepo ayiiiii”!! ku Zimbabwe kujanso anapala ukunso wapalanso!!
Under 20 nxichaninso
Manyaka akunthidwa pompanopa.
Flames moto kuti buu!!!!!! Malawi
Rafik Namwera, isaac kaliati, papa,, stanley sanudi, Dalitso sailesi, Gabeya, Gaba are they senior players? almost 3/4’s of flames are youthful players and thats the more reason we r struggling much wen we r meetin stronger teams. we have won the game impresively Period!!! Be patriotic u’l lose nothing
Congratulation flames mwatichotsa manyazi apa
Ok zayenda bwino zidakatero ndi zimbabweyi zikadakhala bwino
kamwendo is stil a great man, he played very well, but chiukepo, suoumba phumaaaaaaaaa toooo much. chiukepo just did exactly what he was doing in harare last sunday. phuphuphuphuphu, he cant settle down
Playing against teenagers lol
Abg hand 2 Gabaaaah!
Thanks alot ma flams for the victory bt dont forget we were playing against under 15.Work hard in the next games so dat we shall b thankful
palibe choti nkusangalalira apa………Flames sizamva…….akudelera tiana ta angola…….olo HAITI itha kutiswa
Eeeeeee Zili bho
Malawi 24 minde ur statements,a national team z a national team regardless of age,dat shud not b an escapegoat.lets love our team we have won basi.
Kuzolowera kulemba zolakwa zokhazokha eti, gud luck flames!
gaba scores hat trick against 15 year old goal keeper…. kick off magazine kkkkkkkkk
Mwati flames yatani
Amalawi eeeeeh tangoyamikan pazomwe yapanga flames ntchit kunyoza basii muzava chisoni ena akunyozan inu mukuva dzikotu ili oooooh!!! jst say congrats to flamez continue doing zat
TAWINA F COZ KMA AMALAWI NDIKUONA NGAT TILI VUTO LAKUPHONYA DATS WHY MAGAME ENA TIMALUZA CZ EEEEE PAPHONYEDWA MA CHANCES AMBIRI PAMENE PAJA TINAKAWINA ZAMBIRI KMASO MA PLAYER ATHU SACHEDWA KUBALALIKA
Amalawi sadzamvadi kkkk inu mwayiwala kale!
Pantumbo anthu nonse mumayifunila flames zoipa,nkhope ngati agogo anu
kuteloko under 20 yo ndiyomwe ikanachinya amalawi chifukwa ndi anyamata achisozela othamanga magazi ,,tiyeni amalawi tidzikonda timu yathu
kkkkkk ku euro players of under 20 r dangerous players than of more 20,,,,, malawi kuzolowera mpira wa chomanga eti ,ndizija tima uyu asavale sapato m mpira zija
Flames yangogwera,komanso amamenya ndi tiwana ta std7 palibe chopngira celebrate apa
Lets be positive for once congrats Flames!
this tournament is meant for reserve sides not senior squad
Malodza
dont be happy now,remember @ AfCON,anayambanso chonchi but kubwera magame enawo,flames sidzamva.Inu phee tangodikilani muone mmene ikuswereni mtima.Ine mot sindngasangalale bcoz i know kut kukhumudwa ndipompano.
Ena akunyozawo osadabwa ndi mabundi Samalawi. Big Flamez!!!
Zili bwino apapo tingopempha anyamatawa kuti apitilize
.Flames Yandi Kondwesa Chomene
Inu mukuti under 20 anzanu a malawi voice akuti under 17 ikanawina Angola bwenzi mukuti Angola under wear sichoncho yamikilani pofonika kuuyamikila njala nthenda msanje bwanji
Kuno Ku SA ndaifila flames kwa lero
Congratulations Malawi the Flames
I just wish the flames all da best,keep it up.
Flames mwandisangalasa ndtero in short
Za ziii zopanda ndi mchere omwe. I hv followed football from my childhood and beating under 20 Angola i cannt stand up and celebrate. 1988 I REALLy celebrated 4 the Flames not now rather than 28yr ago. Still shame for Malawi!
zopanda mchere walemba iwezi za. ziii malawi woyee or unyasidwe shame on u too
then continue supporting the 1988 flames. ife yathu ndi yomweyi.
ndiponso matchaba ako wamva
Kuzolowera kunyoza team yanu
Wapanga chani cha mzeru chotukura flames?kumangolankhula basi or usapote usasapote ndiwe mmalawi basi
Wanoma mbudzi uyu
osachokako ku malawi bwa ngati ukuti shame… Flamz flamz flamz.. imadodadada
Amalawi tatiyeni tiphunzire kukondaso dziko lathu kumangonyoza bwanji
ifr tabjoya dzulo ngati zakukwana izo ndi zako malawi yawina basi
ndiwe big fool
Anangogwera apa
Timve ziti kodi a Malawi voice nawo apanga post kuti malawi yawina imamenya ndi under 17 ya Angola now inu a Malawi 24 muti amamenya ndi under 20 ndekuti kunali mipila ingati lelo ? Kodi inu mbuli zolemba nkhaninu simudziwa kuti under 17 amamenya chinkho chawo? Under 20 nso chawo? Musawasokoneze anthu ngati mwatopa katambeni nthawi yakwana fotseki iya
Congratulations guys but you might have score more than that at least its a releaf
chomwe ndikudziwa nchoti flames ya pamwantha angola•zoti amamenya ndi ana aunder 15 mukudziwa ndinu.
Mumpira mulibe mwana anasankha omweo, amene mumati akulu akulu anatha akanatani .mwina pitani inuyo ku Angola akakutengeni muzikonda dziko lanu eesh.
Sanavareso Red Jersey,mwangotolapo eti
awonenji apha njobvu ndi buma kkk
all the bet gaba
flames siizamva kkkkkk
against youngstar.,mxi!
Ndie bwanji osaika picture ya jersey yomwe adavala
Black?inu muika red,ndie atolankhani anu Samantha kkkk!.
Lets thank God for that
Yawinabe no matter bad words u can talk to de team…. conglatd to de flames keep it up
Kumeneko ndiye kubwelano sopano
Kungoipezelera Angola under 17 Mxm!
Yeah this is the results now, we have been crying for it so long keep the fire burning Flames!!!!
Ndakhulupilira mwambi woti , masiku sakoma onse. Zimatele zimatele bwenzi nzikoma.
Kaya zanu izo go Gaba go flames ilavu malawi 4eva
Angolan coach was using Van Gaal’ s style kani yaluza
anawo anachepo kwambili
Malawi inagwirisa ntchito mankhwala a kwa sing’anga kuti iwachinye a Angola
Flmz inavala zokuda osati zofiira.
Katundu amanyasa ukachokamo ipaseni ulemu flames bwanji simumanena tisanamenye
select ya under 15, 17 ndi 20 eti. ndimadabwatu kuti Flames yawina bwanji.
Kkkkkk kkkkkk
tawina mudandaule ikaluza mudandaule tinakhala bwanji amalawi
Kkkkkkkkkkk kusangalala chifukwa mwawachina anawo za ziiiiiiiiiii
Congras kwa anyamata athu
Osagonena kut Malawi yachinya Angola bwanji ngati anatumiza under 20 nde kut anaidalila za ntiiii
but thax goes to Gabadihno if he was not there sitikana phula kathu
what i observe in the game mzoti ,,Flames sili bwino kwenikweni,cordination yawo sinali bwino ma.players ena like Chiukepo nsowoya mmmmh ayi ,,cordination ikatheka zikhala bwino koz tisayiwale kut kuli Namibia ,,Madagasca nd John
Our next game is lesotho then moritius
Vice versa boss, lesotho tizamalizila on thursday
this group tidusa am talking about outside this group which is hard if our cordination will be like fis
Angola under 15 and Malawi its under 40 hmmmm shame!
Boys wud do better than olds!congrats to olds 4 beating the energetic squad!kkkkk
Zatelemu yafika semifinal?
ayi we r n group stages
Bola tawina
Lets not be over excited amayamba chonchi ma flames dont forget AFCON in Angola tinayamba 3 nill chonchi nd Algerian koma tinafika nazo kuti..??? Remember history repeats itself, zichitikanso.
Sha!! Ena Aja Tidasiyira Dala
kod tagwera mafana et! that’s y! hmmm. iwz wondering
Apangenso pa Zimbabwe bwanji tangoyamikani apa, chimene mukufunano ndi chiyani inakaluza mukanati chiyani penapake tatiyeni tiziyamika. Munayamba kale kulankhula zachabe-chabe isananyamuke ili kumudzi, lero yachita bwino mukupitilizabe kulankhula mwano ndiye mudzayamika liti?
Ine ndikadakonda akadasunga team imeneyi ndikungo ikoza momwe amalephelamo ndicholinga chakuti kutsogoloku akapange zoposa apa koma akasithaso team ndikutengaso ma player ena mavuto akunenedwa apawa satha coz enawoso adzakhalaso ndimavuto ofunika kuyamba kuwakozaso
Ndakunyadira Ibrahim, maganizo anzeru koma amenewa.
Amwene musatiiwale ife anthu akuda kwathu ndi kuyamikila mkazi wamwini kusiya kuyamikitra wako enawa khalidwe lawo kukonda kunyoza ndi kusayamikira
Kodi ku Angola mukuona ngati kulibe anthu akuluakulu,ngati anatumiza under 20 ndiyekuti amadelera,tiyeni tizikondana abale,tilimudziko lamtendere…..#Flames yatichotsa manyazi…..
Ndiye kuti under 20 ndi imene ikumenya bwino kuposa imene mukuiganizirayo bravo to the flames
NOBODY IN DAT STADIUM
Kumaona Zpanga Post
kungotipezelera tiana hahaa koma Flames Adhaa tikuonani mukupitaku
MA BEST WISHES BWANJ?TAMAYAMIKAN PLIZ
Gaba man of the moment according to the tournament
babies were on the field
babies were on the field
Gaba, Gaba,Gabaaaàaáaaaa
connection ya flems lero inalibwino kwambiri amalawi amachita dala kwambiri sindingati Angola ndimasanje ateam ayi ndiya mphamvu ndinthu ndipo pakadapanda kugwindwa offiside osewela wa ku angola akadapeza chigoli koyambilira aku angola maka mdf ya malawi inagwilana bwino kuma kumbuyo kusamalindwe bwino
against a 15yr Angolan golie; wonder why they put him between the sticks ; anyway we started well in theTournament
indedi abale mmm zisathele pompa Flames mmmm ndkunva kukoma
zodabwitsa
mupira mulibe ana zimenezo ayi mwana sangamulowese mu ground
Osapanga pa zimbabwe paja zmenezi bwanj
Awapezelela bcoz ndiwana,,,paja amalawi amanama zaka,dzao dzeni dzeni
zosangalatsa kwambiri
Koma gaba