President Peter Mutharika has joined Malawians in mourning the death of the great comedian, John Nyanga.
In a message on his Facebook page, Mutharika said Nyanga contributed a lot to Malawi in his role as an agent of social change.
“We commence our week on a sad note as a nation following the passing on of comedian John Nyanga popularly known by his stage name ‘Izeki‘. “Besides being an entertainer, Izeki played a huge role to the society as an educator and agent of social change for over three decades.”
“Gertrude and I join all Malawians in celebrating the life of a man who contributed so much to the country. May his soul rest in eternal peace,” wrote Mutharika.
Late Nyanga passed away yesterday at Queen Elizabeth Central Hospital in Blantyre and will be buried tomorrow in the same city.
Awuse mutendere!!!!
Awuse mutendere!!!!
REST IN PEACE we are going to miss you IZEKI
Ama jelous onse pofunika kuwatengera Bazuka,,,nkupheratu,,,,kkk, machine gun even AK47 sizingathandize,,,,,kubadwa ndi nsanje, kukula ndi nsanje ,paka kuzafa ndi nsanje,,,anthu otani inu??????? Mmmmmmmmmmmmm,,,,,mwina kapena ndi ufiti,,,omapita nawo kotamba nkumayenda wapansi,,,,,
Alikuchipatala palibeko ndi tsiku limodzi kuti mwakamuona munthu bwanji mkukaona lero patatha
RIP you were the best of the best comedian of all times, we ‘ll miss u so much
Ask manganya pliz
Tili munyengo yowawa tisayiwale amalawi,
Taluza munthu wofunika kwambiri, Jacob atsala ndindani? Tingoti Madala, moyo wanu uuse mumtendere.
another great loss from Malawi
MHSRIP
Autse ndi mtendere…
R.I.P ZEX Dziko la Malawi likusowa
Iam round about iyaaa ukasocherakunosikwanu
Iam round aboout iyaaa! Ukasocherakuno sikwanu
RlP
R…..I……P… WILL MISS U.
Unkalindanji Moyo unkalinda kuteloku
RIP Mbuyanga
mzimu wake uwuse mtendele
Zoona edi sukunama analikuti pamene amadwala samanena bwanji panopa amwalila nde apezelapo mwayi onena pa fb sibwino chocho amalawi.tizakukumbukila ezek mpaka kalekale.rp.amen.
Chinsime chakuya chimaziwika chikaphwa munthu amathandiza kwambiri ine anandithaziza zitandiphinja transport guualimoto yake pamalilo Amwana wanga,R.IP prophet izeks
Kodi TB josha mesa akati peter amwalila nanga bwanji mpaka pano sakufa
R i p
Taluza amuna odyera pakamwa RIP ZEKS.
RIP Izeki
R.I.P. Mr john
Chimenecho chifunilo cha Mulungu ndawiinakwana basi kuti amutenge kwina kulikonse kuli manda palibe kuti akanapita kuti aaa!!! RIP izeki
death z tym
RIP Mr John.
achisilu awa kukhalangati samadziwa zoti munthu akufunika thandizo uyu kumangomvetsera osampatsa chithandizo apite kuchipatala cholongosoka ayi?getrude and l ndiye kuti chani?watch out bwampini¿¿¿¿
Akhundi nkhani ya Maliro kapena zandale,ngati ndindale ,tilekeni tilire Kaye mukakumane pa podium ,
You could laugh by just looking at him.oooh Izeki wanga Rip Alufeyo
Ose akpepesa atafa mbore ya bawo zaphata pa kwinya kumenyesa pasi fo seki!;-(
It is so sad to hear this nad news RIP Izek , its now hard to Jacob u will never have agreat friend like Izek
ndinayamba kumvera sewero la izecki ndi jacob ndili std 2 pa namulu primary ku thumbwe ku chiradzulu nde mzimu wake uuuse ndi mtendete amen.izeck Rip.
Koma infa iyo imango phwasula aaaa!
Zagwa zatha
mumakanika kumusamala pamatenda koma kumalilo kuchita kuthamangilako
R. I. P prophet zeks
#Dickson &Cecilia watch out yur coment mvula ikagwa kuchulaka zoliralira
Pulano iyi ndi yanga ndekha.ndawonjezera mumalawi wina pano.vote yina
Kodi beleka ndikulakwa? Tikufuna mbumba amalume anu anatero RIP ZEX
apm loved prophet z
Sory to Jakob and malawian for loosing Izeki,R.I.P Izeki.
Plan iyi inali yandekha. Mesa nkazi anati ndipezeke ndi matewela.
may his soul rest in internal peace
Anthu opanda nzeru #John_Nyanga wathandiza anthu ambiri amaudindo awo ena andale kuwapangira kampeni kudzera mudzisudzo koma lero munthu kumakafuwa ku #Queens olo nokha aboma asamutengelako ku Mwaiwathu kapena kumutumiza ku RSA kuti mwina akalandire thandizo lamphamvu iiii mtundu wanga umamukonda nzako uzikuika pabwino koma akadwala mumamtaya mwachipongwe.
Ukunena zoona dziko ndi andale omwe alephera kuchita munthu ochuka ngati uyu osamutengera zipatala zabwino esh malawi
Inu munali kuti osamutengera komwe mukunenako bwanji mukuchedwa kuloza chala anzanu pomwe inunso ndimzika zaMalawi……. malabishi……
Ine ndi mphawi nzake sindingathe kutero koma lero munthu watisiya muona zipepeso mamillion coffin lodula taliona kale mwalephera kumuthandiza ali moyo ndiye mwapindula chani iye kwache kwatha onetsani chikondi nzanu ali moyo”
Zoonadi, akanamugulira coffin lodula komanso chipepeso ali moyo, aboma alakwitsa kwambiri
MHSRIEPOG
Tidzamusowa Izeki a Malawi mpaka kale kale ….Inuyo panopa mubalalike ineyo ndithamange ndikaone kut ntaonimo zachitika bwanji ? ..Jacob usakhale sumva zonena munthu ……kungomva kuti kwachitika maliro kuthamanga mukadye osamalira?
R.I.P
Ause muntendere.
Rip
Zachamba ngat umadziwa kut
adali wabwino ngat mtsogoleri wadziko mudapangapo chani?bwanji tsimumamtumidza ku india ngat mfumu ngolongoliwa bwa?mudzioneka abwino mzanu akamwalira,inenso ndizasogolera amalawi kudzachita mourn maliro anu(mr murupare)
autse mumtendele
R I P
Ndipaseni chipepeso ndidyele2 ena adaimba kale! Munthu wadwala nthaw yaitali uyu koma fanz simaoneka .Lero wapita zosokha bweeee koma moyowu ndiokondera.
Jacob kunja sakwera BUS, izeki R I P
Rip lzeki anthu akupha kambirimbiri koma mulungu anakukonda, mzimu wako uuse mu ndintendere!!!
Mzim wake use mumtendele
Ku south Africa sikunja jacob udzinena kuti ndachokapo.kkkkkk.man munali otha zedi
R.i.p izeck
Olengeza:president Wa Dziko Lino Wapepesa Ndi K2,000,000.M’manjamooooo!Kodi Anali Kuti Nthawi Yonse Ija Yomwe Izeki Amafuna Thandizo,lets Say,kupita Kunja Kukalandira Chithandizo Chapamwamba? Uku Ndi Kumene Timati Kup……
R.I.P.
R.I.P.
RIP kma pitala ndi wausilu kumakonda muthu Ali ndi moyo
Mhmmmmmmmmm
R l p
Atayesa yesa kulimbana Nako kwabwino kuti apeze Moyo wapa dziko lino,koma Sizinatero cz chamukomela Namalenga kuti amutenge Apumule. ife ndi Ayani!! kuposa kulemekeza chikozelo chake cha Namalengayu. Ngati kumapumidwadi hhhhh!!! Apumedi munthu wazuzika uyu!! Amamvesa Chisoni Awuse Mutendere.
Wanena zoona mbale ziko ndi andale alephera ndithu esh any way his saul rest in peace
kkkkkkk shaaa! I HATE IT
R.I.P taluza munthu ofunikira ndithu mu dziko lonse la malawi.
Tataya munthu ofunikila amend amatisangalatsa pamavuto, R.I.P
Edzi Iribe makhwala ndipo ngati ulinayo umwalira basi.. simaona kuchuka, ndalama kaya wayambisa mpingo wako, iwetu upitabasi. anyway rest in peace.
Sorry
Partly agree with Dixon.
By the way, why did govt fail to send their fellow Lohmwe to foreign hospital? Thot he was a campaigner for their yellow friends? Atcheya munali kuti Z ali mchipatala? Mmangomufuna nthawi ya kampeni ati?
R I P izeki
Sory to jakob for loosing izek
May hsrip.The man really entertained malawians across the country.We will hardly forget him.Pepani Jacob (Eric Mabed)may God be with u during this trying moment.I know ur devastated because u lived with him since ur youth and u were very fond of each other.
Iam shorkd john myanga hesh God bles him RIP
RIP We will always remember you
Pakachitika maliro kuchulutsa zonena .Tisayiwale kuti ndichikhalidwe chathu kupepesana mzimu wake tiwulore uwuse mumtendere palibe zandale apa.
R.I.P John Nyanga We still Remember U
My condolences to the family and all Malawians.
Mvula ikagwa kuchuluka zolilalila ine ndingoti RIP
Ya I have seen your comments my friends there in Malawi. But first we have to think because we don’t know what is in front of us and what God has prepared for us. When time is over no one can reverse it,let’s not blame someone that one has its own time too. Otherwise he should rest in peace
my comedian RIP
Amalawi tisakhale ndi Moyo wa chonchitu,,izeki wavutika Ali mchipatala thawi yayitali,,piano wamwalira nde nkumaonesa chikondi ngati zenizeni APA hhhhh,, kapumeni izeki R.I.p
Sono umafuna anthandze bwanj? Amathandza ovutka not a ndalama kare……….i
Iweyo wathandiza angati????
Hhhhh zomwezo basi
mmmmmmmm dats bad……Izek rest in eternal peace,,,,,,,,
RIP
R .l .P
Palibe wamyaya RIP
Ndi zoonad kut NTEMBO MWAI izeki wavutika nthawi yaitali ali nchipatala koma chikondi chomwe chikuoneka lerolichi iye atamwalila amachisowa ali moyo.
Unadziwa bwanji kuti amachisowa kuteroko pamoyo akhala akupamga pa maso a president MA comedy
Kodi anthu enanu mumangolemba chifukwa chosowa chochita… Udamva kuti amasowa chithandizo mmmh.
munthalika nd wausilu shit!!!!
Ndi zofunika kutero and izeki nzimu wake uwutse muntendere
RIP pastor …
Lot opusa iwe eti wayesa pa ndale pano osangoika RIP ndikusiya bwanji ndale zakozo kwanu koko
RIP
R I P
ma comment a wathu amatewe mwawanva,ati amadikila kuti amwalire kenako apepese.muthu umamulira ali moyo nanga.kuputsa koterokutu muzafa ndi umphawi wa mmaganizo.Cholinga anthu aziti you think more about Izeki more than a president.wake up brothers,mukusalatu ndi fashion yamake dzana.
pamtumbo pako iwe wazeru iweyo?nyero wako pusi iwe
Muthu oti wabadwa mpaka kukula osadziwa bambo ake amangotukwa ziwaro zoti anatulukila mpopo pobadwa.dats y umangoti Ababa kwa bambo aliyense wamuwona bcz anakuthawa uli mwana.
thx prof for joining us in mourning izeki
Amanyasadi munthu alimoyo R I P …..,……IZEK JOHN NYANGA
My Condolences ndiwakumbukila ineyo Pankhani ya Nyinga chaipa Kodi a Jacob akalipo?
kungomva kuti kuli maliro basi kuthamanga mukadye” R.I.P Zex
Kkkkkkkk yake ija dolo,,,,
Show love when someone is still alive not dead
wat love did you show to him wen he was still alive???
Did I say I loved him? Read again my statement boy
#Lot your statement is pointing fingers, so just correct it instead of getting upset when someone is trying to redirect you.
kkkkkk Baba osamawo ntchire mmunda mwa dzako pomwe nawe ukulephera kupala ntchirero mmunda mwako.Anyway,i cn see you was out of sense.
APM showed love to Izeki when he was alive. He used to invite him to perform at government functions (e.g government reform program). Thats love
“pana tibalalike ndikamvesese kuti zachitika bwanji ntawunimo” R.I.P Zex
#Lone umafuna kt atani naye, munthu alimoyo akamachita zabwino amayamikilidwa kmanso akamwalira amamuyamikilanso ntchito zabwino zomwe amachita… Ndie pamenepo chalakwikapo ndchani.
RIP,
IZEKI is not aware that moya is mourning him,,,,,,, what moya could have done was to assist him while he was alive
Anthandize kt chani analibe azibale ake?Iweyo ukazamwalira anthu azizalodza chala Amoya kt sanakuthandize kmanso kunalembedwa kt aliyense azamwalira nthaw yake ikazakwana.Ngakhale amoya mukuanenawo nawo akudikila nthaw yawo.
Ife tikimati RIP tinamuthandiza chani? Nanga iyeyo anathandiza anthu angati??
Oputsa awa,aleredwa ku orphan care.ndi chifukwa chake comment yake ili yodzidzila chonchi.
koma kuganiza kwa anthu ena pilizi…..nde amoya anakailetsa imfa yo kuti isatenge Izeki? mhsrip …..
aleledwadi mopusa kodi mufuna apresident mpaka azikalimirani mminda .achibale analibe oti nkusamala matenda?
Some people!!!too childish,how can you write this nasty comment,next time think
Hahaha,,,,, so all of u you’re intelligent enough than me,,,,,, but you’re commenting on my stupid comment comment and you call yourself intelligent,,,,, hahaha I knew only fools will comment on this
Ndiwe mbuzi iwe eti ukuweruza bwanji? Uziwa bwanji anathandiza who knowz ndale ndi pa maliro pomwe
Kupanda mzeru, aliyense akuziwa kuti moyo wa Zex unalino wapenda penda amati kudwara kuchira kudwara kuchira pano wamwalira mukulimbana ndi moya fo wat? Pamenepa moya akanatani kuti mumuyamikire, kumaganiza kaye zinazi, RIP Izeki
how did Mr nyanga died
R.I.P
May his soul rest in peace
nce nwz
amadikila kuti amwalire kaye nde aziyamikile. shame!
Tazikharani ndi mzeru penapake, pamenepo chalakwika ndi chani
chalakwika simukuchiona? bwanji samayamikila nthawi yonseyi? tiziti lusolo aliona munthuyo atamwalira?
Inu Mukadakonda Adakamuyamikila mwam’tundu Wanji? pamene adali ndi Moyo mukunenawo. kodi akanatero Simukanamunyoza kuti Wagudwa ndi Andale!!? Shame tamaganizani moyenela nthawi zina palibe chalakwika apa!!.
Inu ndiamene mukunena zandale, kodi matumbi powayimbila nyimbo anali wandale? kapena aja akukonza ulendo wa uncle gide wa ku america ndi andale? pulezidenti simunthu? nthawi zonse muzithawira kundale? shame on you too coz chilichonse mumayikapo ndale! #Ngoma
A lone mutu wanu sugwila, kodi onse akumwalirawa amamwalira kamba kakuti sanapite zipatala zakunja. Akati condolence imapelekedwa munthu akamwalira kumene, umunthu ndiye umenewo a president
off point wakamba zachipatala zakunja ndani? uncle gide sakupita kupatala koma koyimba anthu ena amene amayamikila munthu ali moyo ndi amene akonza ulendo umemewu! amisala ndinu amene simukuziwa chimene ndikunena #magalasi
my teacher once said “we all have madness the only difference is the degree of madness” those who misala yawo imaonela ndekuti level of madness is high unlike anthu monga a #Magalasi coz the degree of madness is low ndipo saonekela amaona ngati ali bwinobwino!! musanane anzanu kuti ndi amisala yambani mwaziona kaye nokha!
Mfundoless i think mumaika mchele mu tea
#Magalasi, bola ine nanga inu kumadya zosanza zanu zomwe!
munthalika ndi kape wheather u lyk it or nt nd zoba
hahahahahahaha
nde mwati mutharika ndi chani?
#Khundi
MHSRIP