Mutharika joins Malawians in mourning Izeki

Advertisement
Izeki

President Peter Mutharika has joined Malawians in mourning the death of the great comedian, John Nyanga.

In a message on his Facebook page, Mutharika said Nyanga contributed a lot to Malawi in his role as an agent of social change.

Izeki
Izeki

“We commence our week on a sad note as a nation following the passing on of comedian John Nyanga popularly known by his stage name ‘Izeki‘. “Besides being an entertainer, Izeki played a huge role to the society as an educator and agent of social change for over three decades.”

“Gertrude and I join all Malawians in celebrating the life of a man who contributed so much to the country. May his soul rest in eternal peace,” wrote Mutharika.

Late Nyanga passed away yesterday at Queen Elizabeth Central Hospital in Blantyre and will be buried tomorrow in the same city.

Advertisement

150 Comments

 1. Ama jelous onse pofunika kuwatengera Bazuka,,,nkupheratu,,,,kkk, machine gun even AK47 sizingathandize,,,,,kubadwa ndi nsanje, kukula ndi nsanje ,paka kuzafa ndi nsanje,,,anthu otani inu??????? Mmmmmmmmmmmmm,,,,,mwina kapena ndi ufiti,,,omapita nawo kotamba nkumayenda wapansi,,,,,

 2. Taluza munthu wofunika kwambiri, Jacob atsala ndindani? Tingoti Madala, moyo wanu uuse mumtendere.

 3. Zoona edi sukunama analikuti pamene amadwala samanena bwanji panopa amwalila nde apezelapo mwayi onena pa fb sibwino chocho amalawi.tizakukumbukila ezek mpaka kalekale.rp.amen.

 4. Chinsime chakuya chimaziwika chikaphwa munthu amathandiza kwambiri ine anandithaziza zitandiphinja transport guualimoto yake pamalilo Amwana wanga,R.IP prophet izeks

 5. Chimenecho chifunilo cha Mulungu ndawiinakwana basi kuti amutenge kwina kulikonse kuli manda palibe kuti akanapita kuti aaa!!! RIP izeki

 6. achisilu awa kukhalangati samadziwa zoti munthu akufunika thandizo uyu kumangomvetsera osampatsa chithandizo apite kuchipatala cholongosoka ayi?getrude and l ndiye kuti chani?watch out bwampini¿¿¿¿

 7. ndinayamba kumvera sewero la izecki ndi jacob ndili std 2 pa namulu primary ku thumbwe ku chiradzulu nde mzimu wake uuuse ndi mtendete amen.izeck Rip.

 8. Pulano iyi ndi yanga ndekha.ndawonjezera mumalawi wina pano.vote yina
  Kodi beleka ndikulakwa? Tikufuna mbumba amalume anu anatero RIP ZEX

 9. Anthu opanda nzeru #John_Nyanga wathandiza anthu ambiri amaudindo awo ena andale kuwapangira kampeni kudzera mudzisudzo koma lero munthu kumakafuwa ku #Queens olo nokha aboma asamutengelako ku Mwaiwathu kapena kumutumiza ku RSA kuti mwina akalandire thandizo lamphamvu iiii mtundu wanga umamukonda nzako uzikuika pabwino koma akadwala mumamtaya mwachipongwe.

  1. Ine ndi mphawi nzake sindingathe kutero koma lero munthu watisiya muona zipepeso mamillion coffin lodula taliona kale mwalephera kumuthandiza ali moyo ndiye mwapindula chani iye kwache kwatha onetsani chikondi nzanu ali moyo”

 10. Tidzamusowa Izeki a Malawi mpaka kale kale ….Inuyo panopa mubalalike ineyo ndithamange ndikaone kut ntaonimo zachitika bwanji ? ..Jacob usakhale sumva zonena munthu ……kungomva kuti kwachitika maliro kuthamanga mukadye osamalira?

 11. Zachamba ngat umadziwa kut
  adali wabwino ngat mtsogoleri wadziko mudapangapo chani?bwanji tsimumamtumidza ku india ngat mfumu ngolongoliwa bwa?mudzioneka abwino mzanu akamwalira,inenso ndizasogolera amalawi kudzachita mourn maliro anu(mr murupare)

 12. Rip lzeki anthu akupha kambirimbiri koma mulungu anakukonda, mzimu wako uuse mu ndintendere!!!

 13. Olengeza:president Wa Dziko Lino Wapepesa Ndi K2,000,000.M’manjamooooo!Kodi Anali Kuti Nthawi Yonse Ija Yomwe Izeki Amafuna Thandizo,lets Say,kupita Kunja Kukalandira Chithandizo Chapamwamba? Uku Ndi Kumene Timati Kup……

 14. Atayesa yesa kulimbana Nako kwabwino kuti apeze Moyo wapa dziko lino,koma Sizinatero cz chamukomela Namalenga kuti amutenge Apumule. ife ndi Ayani!! kuposa kulemekeza chikozelo chake cha Namalengayu. Ngati kumapumidwadi hhhhh!!! Apumedi munthu wazuzika uyu!! Amamvesa Chisoni Awuse Mutendere.

 15. Tataya munthu ofunikila amend amatisangalatsa pamavuto, R.I.P

 16. Edzi Iribe makhwala ndipo ngati ulinayo umwalira basi.. simaona kuchuka, ndalama kaya wayambisa mpingo wako, iwetu upitabasi. anyway rest in peace.

 17. Partly agree with Dixon.

  By the way, why did govt fail to send their fellow Lohmwe to foreign hospital? Thot he was a campaigner for their yellow friends? Atcheya munali kuti Z ali mchipatala? Mmangomufuna nthawi ya kampeni ati?

 18. May hsrip.The man really entertained malawians across the country.We will hardly forget him.Pepani Jacob (Eric Mabed)may God be with u during this trying moment.I know ur devastated because u lived with him since ur youth and u were very fond of each other.

 19. Pakachitika maliro kuchulutsa zonena .Tisayiwale kuti ndichikhalidwe chathu kupepesana mzimu wake tiwulore uwuse mumtendere palibe zandale apa.

 20. Ya I have seen your comments my friends there in Malawi. But first we have to think because we don’t know what is in front of us and what God has prepared for us. When time is over no one can reverse it,let’s not blame someone that one has its own time too. Otherwise he should rest in peace

 21. Amalawi tisakhale ndi Moyo wa chonchitu,,izeki wavutika Ali mchipatala thawi yayitali,,piano wamwalira nde nkumaonesa chikondi ngati zenizeni APA hhhhh,, kapumeni izeki R.I.p

 22. mmmmmmmm dats bad……Izek rest in eternal peace,,,,,,,,

 23. Ndi zoonad kut NTEMBO MWAI izeki wavutika nthawi yaitali ali nchipatala koma chikondi chomwe chikuoneka lerolichi iye atamwalila amachisowa ali moyo.

 24. ma comment a wathu amatewe mwawanva,ati amadikila kuti amwalire kenako apepese.muthu umamulira ali moyo nanga.kuputsa koterokutu muzafa ndi umphawi wa mmaganizo.Cholinga anthu aziti you think more about Izeki more than a president.wake up brothers,mukusalatu ndi fashion yamake dzana.

  1. Muthu oti wabadwa mpaka kukula osadziwa bambo ake amangotukwa ziwaro zoti anatulukila mpopo pobadwa.dats y umangoti Ababa kwa bambo aliyense wamuwona bcz anakuthawa uli mwana.

  1. APM showed love to Izeki when he was alive. He used to invite him to perform at government functions (e.g government reform program). Thats love

 25. #Lone umafuna kt atani naye, munthu alimoyo akamachita zabwino amayamikilidwa kmanso akamwalira amamuyamikilanso ntchito zabwino zomwe amachita… Ndie pamenepo chalakwikapo ndchani.

  1. Anthandize kt chani analibe azibale ake?Iweyo ukazamwalira anthu azizalodza chala Amoya kt sanakuthandize kmanso kunalembedwa kt aliyense azamwalira nthaw yake ikazakwana.Ngakhale amoya mukuanenawo nawo akudikila nthaw yawo.

  2. Hahaha,,,,, so all of u you’re intelligent enough than me,,,,,, but you’re commenting on my stupid comment comment and you call yourself intelligent,,,,, hahaha I knew only fools will comment on this

  3. Kupanda mzeru, aliyense akuziwa kuti moyo wa Zex unalino wapenda penda amati kudwara kuchira kudwara kuchira pano wamwalira mukulimbana ndi moya fo wat? Pamenepa moya akanatani kuti mumuyamikire, kumaganiza kaye zinazi, RIP Izeki

  1. Inu Mukadakonda Adakamuyamikila mwam’tundu Wanji? pamene adali ndi Moyo mukunenawo. kodi akanatero Simukanamunyoza kuti Wagudwa ndi Andale!!? Shame tamaganizani moyenela nthawi zina palibe chalakwika apa!!.

  2. Inu ndiamene mukunena zandale, kodi matumbi powayimbila nyimbo anali wandale? kapena aja akukonza ulendo wa uncle gide wa ku america ndi andale? pulezidenti simunthu? nthawi zonse muzithawira kundale? shame on you too coz chilichonse mumayikapo ndale! #Ngoma

  3. A lone mutu wanu sugwila, kodi onse akumwalirawa amamwalira kamba kakuti sanapite zipatala zakunja. Akati condolence imapelekedwa munthu akamwalira kumene, umunthu ndiye umenewo a president

  4. off point wakamba zachipatala zakunja ndani? uncle gide sakupita kupatala koma koyimba anthu ena amene amayamikila munthu ali moyo ndi amene akonza ulendo umemewu! amisala ndinu amene simukuziwa chimene ndikunena #magalasi

  5. my teacher once said “we all have madness the only difference is the degree of madness” those who misala yawo imaonela ndekuti level of madness is high unlike anthu monga a #Magalasi coz the degree of madness is low ndipo saonekela amaona ngati ali bwinobwino!! musanane anzanu kuti ndi amisala yambani mwaziona kaye nokha!

Comments are closed.