Mighty Be Forward Wanderers have landed Jafali Chande from rivals Nyasa Big Bullets on a free transfer and the player has signed a two-year contract with the Nomads.
The striker was not training with Bullets recently and he was not in the squad that hammered Red Lions 4-1 over the weekend, prompting speculations that he may seek his way out of the club.
Chande’s contract at the people’s team came to an end after the 2015 TNM Super League in which he scored 12 goals, and Bullets’ attempt to tie him to the club by offering him a new contract has proven unsuccessful.
According to reports, the club – which has been affected by internal wrangles recently – was unwilling to meet the player’s demand for a 4 million kwacha signing on fee.
Chande moved to Bullets in 2014 from EPAC in a deal worth around 2.5 million kwacha and he made over 45 appearances during his two-year stay at Big Bullets where won two TNM Super League titles and a Carlsberg Cup.
wayenda wapita basi kumasinitsa zinthu.
Sulumba anali wanu?
Ok!!!! Zamveka tionana pa turf.
Ok!!!! Zamveka tionana pa turf.
Abale athu a bullets ifetu timakukondani chifukwa timadziwa kuti munachoka mu team yathu yaikuluyi NYERERE, tawonani takupatsani Sulumba osalankhula miseche ngati mukuchitila inumu kuyamba kumunyoza player wabwino ngati ameneyi, tamusiyani muone ayambe kusalala ngati azakewa. Inu kumangodziwa kulongolola koma osawasamala ma player ndiye angaleke kukuchokelani??? Aaaah bwanji kodi,
Troubled Bullets? Mmmmmmmmmm
Kkkkkkk kodi nde mwati chande troubled bullets kkkk
Troubled Bullets? Mmmmmmmmmm
Every player have a choice of the team he wants to plays but a true choice comes from the heart coz u don’t play football if your heart is supporting the other team for example take the performance of Victor Limbani at Bankers. wait until the first round of TNM super league is over. koma afana zabwino zonse bola kulimbikira basis ndizotheka. Once Red Army Always a Bullets fun
Man Chande,what is needed here ndikuonesa luso lako lonse ziwapweteke komanso ife MANOMA timve kukoma
Munya muona bonya bules……. Dilu manoma bas……..
pp wyoeee
Zabwino zonse cande
uyende bwino but know this ;no player has left bb & performs better bola unatitengesa lig chaka chatha
Troubled,,,, yeah! Thats correct, coz the so called pp team is in trouble, cant you see what is going on?
Kodi inu a BB mukulira chani player wapang yekha chisankho anali asakudziwa timu tsono waipeza Noma
Waitha!!!!!!!:D
Waithathathatha!!! Kuli nye kuli nye kulinyelele.
Inde manoma
Welcome to the mighty……….. The richest team in the warmheart of africa……….. Dollar ndosayamba kuno…..
Kuganizakwabwino kumeneko chande
this is stupid reporting .. . which school did you go to?, , ,troubled bullets?
What u shud know is dat player alibe team ichi ndi chisankho chake olo muyankhule olo musayankhule Chande wachoka mmanja mwanu pano ali mmanja mwa Noma basi wakana zomagulitsa chingambwe ameneyu kk wina uyoooooooooooo manomaaaaaaaaaa
Go well, ife league nde tikudifendabe season ino, pitani muzikasuka magalimotowo
Go well u guy,tilibe pulobulemu we the pipos team
Eish guys game 50/50 inu mwatenga sulumba ife Chande ,tione kuti ndani wapanga chisankho chabwino season ino simple
Chande, kuganiza kwa umunthu ndeye kumeneko, welcome to Rali lubani. ine weniweni wa The Mighty Be Foward Wonderers,
Bullets ndichoncho….iwowa amazitenga ngat ndi ampira enawa ndeee ai….kuchoka kwa Zakazaka kupita ku Noma last yr munayakhula zambirirmbiri kumunyuza mwat watha…pano Sulumba wabwera ku BB kma mukuika pa Top mwat ndi player..pano Chande wapanga chisakho chopita ku Noma mwayamba kumunyoza….Demet BB….
Ndimafuna Zamano Manoma ?
Ndimafuna Zamano Manoma ?
Welcome Chande.ndakunyadira ine ndimasowa luso lakolo bcz abullets amakuononga kmaso alibe money amene aja.kungopeza ka sportser basi kuyamba kukokana zamaudindo.anthuopanda khalidwe maule bwanji!!!
apite tilibe naye ntchito…kuchoka player mmodzi sikuti bullets yatha..anachoka madolo bullets ilipobe akafuse vibri victor limbani ankaona ngati akachoka bullets imusowa pano bwanji akuifunaso bullets..team yotha mpira Malawi yose…adzaikumbukira bullets nfana wa chamba yo….apite ku team yosatenga super league yo..mmenemo anzake akutenga league ka 7 paja timatenga 7 times popanda otilandila wina afune kaya asafune…
m like it! big up chande
takulandilani amfumu musavere zinenedwazi ndikukulirani kumeneko muwawonetse zitchito zanu tikakumananawo amenewa nyerere woyeeeee muziona simunati
takulandilani amfumu musavere zinenedwazi ndikukulirani kumeneko muwawonetse zitchito zanu tikakumananawo amenewa nyerere woyeeeee muziona simunati
kwanuko mumamutcha neymar pano wapita ku noma mukuti alibe creativity nsanje yachuluka a malawi
Ndimafuna Zina
zina?
kwanuko mumamutcha neymar pano wapita ku noma mukuti alibe creativity nsanje yachuluka a malawi
Ndimafuna Zina
zina?
Vuto a BB kusavimereza, noma inalandidwa Yobe,ndipo noma inatipo chani ndipo adapita nawo kuti mpira Yobe, munthu akapanga chisankho musiyeni
Vuto a BB kusavimereza, noma inalandidwa Yobe,ndipo noma inatipo chani ndipo adapita nawo kuti mpira Yobe, munthu akapanga chisankho musiyeni
mayazi man
Wonderso ukuyankhula ngati MULENGI chifukwa chani? ndekuti player akapita ku team ina walakwisa? inuyo amwene ndinu osaporter osazindikila mwava
Wonderso ukuyankhula ngati MULENGI chifukwa chani? ndekuti player akapita ku team ina walakwisa? inuyo amwene ndinu osaporter osazindikila mwava
chande alibe creativity pampira…go wel as that we wil not miss your service.
ukunama wapita basi
chande alibe creativity pampira…go wel as that we wil not miss your service.
ukunama wapita basi
osadana ndi chilungamo man, zigoli zake zonse zinali ma rebound okhaokha.
osadana ndi chilungamo man, zigoli zake zonse zinali ma rebound okhaokha.
osadana ndi chilungamo man, zigoli zake zonse zinali ma rebound okhaokha.. ubwino wake tikukumana pa 4 april uzakhumudwa kuti ndi ndowe za bakha.
osadana ndi chilungamo man, zigoli zake zonse zinali ma rebound okhaokha.. ubwino wake tikukumana pa 4 april uzakhumudwa kuti ndi ndowe za bakha.
Kkkkk kunama tu uku kulira ndi mtima,kungonena yenda bwina Chande mmene tinanenela kwa Sulumba
R.I.P Chande tatopa ndikutiluyisa ma game
Kuganiza kwa zeru kumeneko.
Go well boy
Bullets still remains
The most successful club in the land
U ll follow the footsteps of Tizgo and Vibrey as Mapale continue to dominate
Viva Viva Bullets
Bullets ndi timu yaikulu mMalawi muno ndipo wazionera wekha chande timu yawanthu ikugwesa chagada red lions 4 kwa 1 iweyo ulipabench kutanthauza kuti kuchoka kwako palibe yemwe angamange mutu yenda bwino tiwonane mu superleague ndipo ukanakhala wanzeru ukanazifunsa kuti mchifukwa chani Sulumba anathawa kumeneko kubwela ku Bullets akuziwa kuti tsogolo lampira lagona mu Bb ndiye palibe kanthu kaya mwasata ndalama bola musazalilire kuusi !

Kusanka 100% kumeneku Ku bullets ndiwe wekha wanzeru
UOR CHOICE
UOR CHOICE
Kuthawa bench kkkkkkkkkk.bullets won’t be in trouble.coz of chandenga kumeso
Kuthawa bench kkkkkkkkkk.bullets won’t be in trouble.coz of chandenga kumeso
Anayamba ndi sulumba kuthawa thabwa
Chande ndikufunire zabwino zonse,Bullets sikuti ingathe chifkwa cha kuchoka kwako ayi.Bulets iripo inalipo ndipo idzakhalapo.
komabe
Chande ndikufunire zabwino zonse,Bullets sikuti ingathe chifkwa cha kuchoka kwako ayi.Bulets iripo inalipo ndipo idzakhalapo.
komabe
Ndidzimene tinanena kwa Sulumba kuti Noma inalipo ,ilipo idzakhalapo ,
Chisankho chabhooo Chande..kumaona kumene kuli future…. Kkkkkkkkkkkk
Chisankho chabhooo Chande..kumaona kumene kuli future…. Kkkkkkkkkkkk
Rip in advance chande, bullets is for life.
Rip in advance chande, bullets is for life.
Hahaha bullets ikatenga player ku noma mwana wanzeru akapita ku noma ndi kape Rip shame
Kokatha kumeneko, ife tiki ndi Sulumba amene walengeza kuti azikwanisa ma hat trick
Kokatha kumeneko, ife tiki ndi Sulumba amene walengeza kuti azikwanisa ma hat trick
He has left not becoz of what you say is trouble.Why have other players not moved?After all he is not the first one to leave we just wish him all the best.Tikumana naye zikayamba
He has left not becoz of what you say is trouble.Why have other players not moved?After all he is not the first one to leave we just wish him all the best.Tikumana naye zikayamba
Wachita bwino ables umadelela
Wachita bwino ables umadelela
troubled bullets?please reporters simplify your vocabularly sothat readers should be comfortable when reading.there is no troubled team here in malawi
troubled bullets?please reporters simplify your vocabularly sothat readers should be comfortable when reading.there is no troubled team here in malawi
Troubled? Kkkk…koma ma reporter apa nyadsaland…in football There Is no trouble apart from loosing games,full stop!
kkkkkk mwina akupenga
Troubled? Kkkk…koma ma reporter apa nyadsaland…in football There Is no trouble apart from loosing games,full stop!
kkkkkk mwina akupenga
ayende bho, anagwira ntchito bwino, and all the best we had the best players who left still we are the best.
Tit for tat,kwatsala kutenga manyenje ndi chaima
#