Two Mighty Be Forward Wanderers players are persuading Civo United star Nelson Kangunje to Join the Lali Lubani side, Malawi24 can reveal.
The two, Patrick Gunde and Jabulani Linje, played with Kangunje at the Lilongwe based side and they said they have had a conversation with the Flames midfielder to join them at Wanderers.
“We are like one blood we enjoy playing together, it can be more enjoyable to play again at the blue camp,” Linje said.
Linje did not however reveal Kangunje’s response but he said the two are still trying to convince the Civo player that Nomads is the best club for him.
Kangunje’s performances at Civo United last season made him one of the country’s best players and led to interest from the two Blantyre giants, Mighty wanderers and Nyasa Bullets.
The two clubs want to beef up their midfields due to different reasons: Big Bullets want to replace the retired James Chilapondwa while Wanders want to have more midfield players after injuries affected their players last season.
The wise choose Noma. Welcome to the kingdom of the wise
CHOTI MUDZIWE TEAM YA WANDERERS NDI YA ANTHU WOMWE ANAPHUNZIRA NDIPO NDI WOSUNGA KHALIDWE NDI CHIFUKWA CHAKE IMATCHEDWA THE WISE PEOPLE’S CHOICE KOMA VENDOR YAKE NDI NYASA B BULLETSYO NDIYE PALI KUSIYANA KWAKUKULU KWAMBIRI ENAFE SITIMAMBANANO MA VENDORWA MUDZINGOWAMVERA BASI ZATHU PHEEE
Alibe malo position ku Noma after signing Tambe from Fizds Wizzard,and which Nomads Coach is claiming that the guy is in next plans come 2016 season.
ok ndiye mwati ku bibi kunyasa. team yanji yimeneyi last year yinali bibi team ya fungo kkkkkkk koma yaaa
Ndiye yake imeneyo mafanawa ndiozindikila komanso ofewa osati mbuzi zinazi
BB…..kkkkkk koma guyz mumatha bwanj kukond BB???? plz teach me jst bcoz aaaaah ndimakuonani ngat makape….MBFW =nyerere muuuaaaah
Gulani ife soccer timatha NYASA BIG BULLETS mphuma njeeee.
BB????? Ndi kachaninso?????
Eeee zili bwino
BB simafuna maplayer aseason ngati amenewa,ife tinakhanitsa kale, wanjala ndi amene amalowa nkhwokwe.
tikulandila ku nyelele!
tikulandila ku nyelele!
Wina amvekere amulemba ntchito mu Boma, Boma lake liti? boma la mbuyako, Noma imtenga ameneyo
Kangunje u r welcomed
Lol
Players persuading a fellow player to join wanderers , that means you are not sure of yourself? Sixty players on board you are still failing to come up with a winning team?
Ask them bro it seems they are not yet mwina akanapatsidwa mwai oti adzilowetsa 15 mkati bwenzi atasintha nanga m’mene anayambira kugula ndi kungongola ma player muja popanda kusintha kulikonse kkkkk
kd zikho kumalawi kuno zilipo zingati? nde bullets yatenga zikho zingt?
Osazitsata kkkkkkkk
Ur most well come kangunje gud thinking.
WAPITA KUMAVUTO, NDIYE KAYA UNGOLIMBANAZO WAKULAWATHA.
Kodi BB officials mutani pa nkhani ya transfers azanu akutolera ma players in muli phwi bwanji!!
Panga zamanyowa ateam yako&leave my beloved team BB,Titha osagulanso koma ndikukuyabwani heavy,So shutup your mouth&Ukasowa chokamba kulibwino osaikilapo ndemanga apa.BB4 LYF
bb sikutekesekatu ikuona maso ankhono ikufuna zigori zomangoseweretsa mpira ai ikugura koma ikuonetsetsa
ndanyadila
Inu Anoma Kodi Patrick gundeyo nthawi imene mumamutenga amasewera zopusazakezo?mukufuna kangunje mumuonongeso fwesek ameneyu ndiwathu basi wa civo woyeeeeee!!!!
Ctikuopa or atabwera league ndiyathube
Ur most welcome kangunje tithandize potigoletsela zigoli zabwino monga momwe umachitira ku civo
Ndingokuyankha iwe ukuti achina Jabu atha kodi Gunde ndi Jabu ndi Eneya ndi Nikiza watha ndindani abwere kunyasa kotani
Iwe enaya ungamuike pamlingo ndi Jabu kkkkkkkkk Gunde ndkatundu iwe.
Do not force the horse to drink water ok!!
Don’t miss him he wil assist us he agood man.
Sangasiye CIVO 1, Tikumulemba ntchito mu Boma ku!
ANdudu fc akuva bwanji zankhanii
mooost! welcome kangunje
Welcome
Munthuyu ndi wamkulu watsala season imodzi
Ngat fisha eti kkkkkkkk
Ok nkhani yamushe bt chamene tifuna kutenga league
Kangunjeyo azifuse yekha kuti patrick Gunde ali mwakale mommunja kapena walowa mavirus? Nanga Linje? Ngati akufuna sogolo lowala abwere ku Nyasa Bullets osati kwinako akatha ngati katani. Ndiye wina atukwane
Ife kutukana toto koma Abullets.ife tingokuwuzani ngamo baasii,Bullets yanuyo ilibe lutha lozindikira puleya weniweni.ku Noma sikubwera phwepwa. Mwina inu simungavomere zimenezi koma Akuru akuru oyendesa team yanu Amavomera,mboni pa nkhaniyi Ndi SULUMBA Mwamva!!?? ndakutukanani Nyerere ndi Diluu!!!. kawafuseni ACHILUNGA.
wa chingabwe bullets akuziwa kuti palibe player wayambwa last season ngati Lije n iweyo ukuziwa bwino koma sanje Neba imakuvuta imagine amamunyoza Silumba koma lero kadiso kali pomwepo ng’oooooo wauponda kikikiki
Kodi gap yamapoints idali bwanji last season? Nanga chanzeru ndichani kutenga madolo koma lig chitengereni 2006 up to now? Ife ndi manyasa eni soccer pa nyasa.
2016 simuwona mpira a chingambwe iinuu!
Paja inu mumadziwa kuziunjikila ma player ena mpaka kungongola koma League mkuthera pa #4 kkkkkk points gap from the top 21 seven games kkkkkkk pwiti pwiti pwiti pwiti pwiti pwiti #Bullets olo osagula player koma mudzikanda zeni zeni kuposa season yatha
Vuto neba makaka a kit yako achuluka. Black,orange,blue and white. Timu ikulilenji iyi koma madeya enieni
Welcome to the wise peoples choice
Kangunje nyerere yomweyo kuti wawawa
Welcome Kangunje 2 Lali Luban Road.
MANOMA 4EVER 2O16 MORE FIRE KANGUNJE
MANOMA 4EVER 2O16 MORE FIRE KANGUNJE
TIKULANDILA KU NYERERE KUNO.
TIKULANDILA KU NYERERE KUNO.
Kangunje nyerere zonse zikukudikila!
Kangunje nyerere zonse zikukudikila!