The Blantyre Magistrate court on Friday sentenced a 44 year-old Malawian man to 9 years imprisonment with hard labor for being found in possession of 52 bags of chamba.
Southern Region Police assistant publicist, James Kaledzera, identified the man as Yasin Umali and said he was caught with the bags at Zalewa roadblock.
He said: “After searching him at Zalewa roadblock we recognised that he carried 52 bags of chamba weighing 2000 grams.”
Police have since asked the public to avoid being involved in such cases as they will not stop dealing with law breakers.
Umali hails from Chiwambo Village in the area of Traditional Authority Maganda in Salima district.
Know that dagga is legalised in some parts of the World.
Mmasukeni nsanga palibe chomwe walakwa ameneyu,Mmangeni kaye JB(cash gate)
Bravo Courts! Apanga bwino. Anthu akumasuta chamba ndipa depot pomwe
Fuck Malawi Government Osalimbana Ndi Omwe Akuba Ndalamawo Bwaj
but u will find a murderer gets 2years impreasonment.
Amubera kumumangako akuwopa angawavutitse….
9 years because of weed???????????????????
Unfair,he deserve 3months punishment
Mesa mukut chamba muzilima nde bwanjinso mukumanga munthu wopezaka ndi ganja
Akufun apengetse amalawi anzake
bombcrat vampires they want to suck blood from the sufferes
the first cash gate convict was charged 3 yrs..komanso mwati chamba tizilima.kuli odziwika bwino ogulisa chamba…ku BT kenani..ku salima rasta koma samamangidwa.amphawi mumawawonelera bwanji?
Poor goverment, poor police
Osamanga a cashgate aja? Mukamanga munthu ozithandiza ekha. Nanuso akhothi mmakondera,malamulo amagwira ntchito kwa osauka. Kuli anthu oba mabilioni simukuwamanga bwanji?
Why?he was bringing something in to the country
mudzafa imfa yowawa mukangokhala mao mugulu lomanga anthu ogulitsa kaningina nonse pa pa pa pa panu
Foolish government . FUCK U
Even America legalize Ganja. poor as we busy jailed Man found with remnant seed, after flood of Noah Jah blessed it. Kapokola you will never get rich chifukua mukutsekela billions of kuacha there iz nuh seed in Agriculture that will make man rich rather than Ganja.
Kodi makape inu, mukumugwira muthuyo chifukwa munakumana naye pa loadblock. funso m’kumati kodi kumene kukulimidwa chamba inu simumakuxiwa? bwanji osapita kukatchetcha ganja yonse kumendko km mumalimbana ndi munthu woti wa choka nayo komwe inu ndikumugwira. makape amatha inu otsamawapasa zaka 9 a cashgate koma waganja dziko lokondera ili.km na ife malijuwana tidakadyabe ndpotso chaka chino maliwana alimidwa bas!
aaaaa choncho uyoyo sanabele munthu amalima yekha luyepo anatibera ma billion athu koma munampatsa zaka 5 Ada awowo mwawapaysa zaka 4 ……. nde mukatero mukuti ndichilungamo makape inu
Kodi ameneyu ndi aja a Cashgate oyenera kulandila zaka zambili ndi ndani?
Analipo 82 bags munamubela 30 agalu inu aboma!
chamba chaka chino ife tilima/ takambrana kale nd chilima/ tikzwa a2 ambri mukukayka/ kalata yapta kalexo kwamuthalika,
Why u wnt to put innocent hard working man in prison jst bcoz he’s got what it takes for him to get rich? Tel me what else can u farm that u can make money in malawi than Chamba? Fucken goverment u got pple who r kpn lot’s of gvmnt mny bt u lv them. Open ur eyes poor malawi.
M’malo molimbana ndi za cashgate mukulumbana ndi za chamba? Kodi pa milandu-yi, womwe uli waukulu ndi uti?
kod mesa makape amenewa kufuna apange regalise ganja nde akumumangilanj munthu
Mufuse kuti amati akagulitse kuti akuuzani amapita nacho kumene aphungu akukumanirana.
Why Why now!!!!!!!!!!
Ya mamuna koma ameneyo
akuba zaka zochepa koma wachamba mpka 9yrz wa cashgate 3yrz kkkkkk koma ziko ili mmmmm
Legalise watanixo nanga mukufuna muzigulitsa nonkha abakha inu etiii foools
apolisi amamanga anthu opanda chifukwa bwanji?
sindinamvepo kuti driver anadya chamba ndiye wapanga ngozi,zaka 9 chifukwa cha zinthu zomela zachilengedwe mwamu khomelera
4tsek Chambacho Wachita Kuba,,,,!
big dealer.respect!!9
mumasuleni palibe cholakwa apa
mwamudula geni nzanu sibwino
Inu mumafuna kuti akakudyereni kuti?
Ndili very addicted ku ganja mleken ndi mpulumutsi wa lyf yanga inu mzigwira okuba,jaja azakulanganitu.
Aaa ndi nkhaninso imeneyo? Munthu akupanga zoti azithandizika pa nyasa pano inu mukummanga? Bwanji osakamanga anthu akuba ma million athuwo? Yakulepherani ntchito apolisi
eshhh!ndiyevkumalawi kumene ndimakuziwa ine kumeneko
Mukumanga munthu amene akukhesa thukuta popeza ndrama, koma mukusiya anthu amuboma amene akutibera ndrama zathu zamisonkho.dzitsilu vintchewe imwe mumasulen munthu chonde.
Mwamumanganu,chambacho wakaba kumunda kwanu kapena ndichake? Acashgate smukuwamanga bwanj km adaba ndalama zakhankhan,chamba nkachianiso,nzanu asapange malonda kt azdyako bwno kma inu ndchiphaz chadzkang’acho kumupondereza…bwanj maiko anzathu amalola bznez yajanja? Kanyani ndnu pot ndie mumazwa kunyopola anzanu ai.
Nde kumulakwira akabe chabwino?
Remember! its not ilegal unti you get caught.
Zaka 9 zachuluka kwambiri ndiye ogwirira mumupatsa zingati? Plz mundipatseko thumba limodzi ndizidzasuta kuno chikusowa kwambiri.
52 what???? Guy would be rich by now….. Daafuq is this this Mw Govt?????
I thought govt legalised it so why are you a resting innocent pipo?
Mmmm nkhan zake ndzacamba bax?
naneso ndie mungondimanga2
Kodi Chomwe Boma lavomereza chija sii chimenechocho??
nde mogoyo ili kt?
naye…osandisungitsa ine buanji…ine ndekha nde sakanagwira2
[[.weedicon]] [[.weedicon]] [[.weedicon]] [[.weedicon]] [[.weedicon]] [[.weedicon]] [[.weedicon]] [[.weedicon]] [[.weedicon]] [[.weedicon]] [[.weedicon]] [[.weedicon]]
This is long overdue to be legal.
Anthu wopusa inu anthu akuba ndalama zankhan nkhan zaziko koma simukuwamanga koma munthu kungomupeza ndi chamba basi zaka zankhan nkhan…kupusa basi
Scot…him…free.maluzi,kunjaku
Blessd leaf…..jah fire pon de police officerz….wosamakalimbana nd fanz ya cashgate bwanj!#legaliseIt
Nkhazatu zimenezo zaka zinsezo
Jst get happy coz maridjuana is the biggest ever business wich can make sombody reach easy even to the whole world! Govnm dats nuh a reason for arresting him! Yo job s to keep malawi peace and arrestion who violence not who found wth ganja!
Mmmmmmm kom amulakwira bwanji? zakudyaka zimenezi.
free up the ganjaman
zofuna
tsiku la tsoka