52 bags of marijuana land man in prison

Advertisement
Arrested.

ArrestedThe Blantyre Magistrate court on Friday sentenced a 44 year-old Malawian man to 9 years imprisonment with hard labor for being found in possession of 52 bags of chamba.

Southern Region Police assistant publicist, James Kaledzera, identified the man as Yasin Umali and said he was caught with the bags at Zalewa roadblock.

He said: “After searching him at Zalewa roadblock we recognised that he carried 52 bags of chamba weighing 2000 grams.”

Police have since asked the public to avoid being involved in such cases as they will not stop dealing with law breakers.

Umali hails from Chiwambo Village in the area of Traditional Authority Maganda in Salima district.

Advertisement

64 Comments

 1. the first cash gate convict was charged 3 yrs..komanso mwati chamba tizilima.kuli odziwika bwino ogulisa chamba…ku BT kenani..ku salima rasta koma samamangidwa.amphawi mumawawonelera bwanji?

 2. Osamanga a cashgate aja? Mukamanga munthu ozithandiza ekha. Nanuso akhothi mmakondera,malamulo amagwira ntchito kwa osauka. Kuli anthu oba mabilioni simukuwamanga bwanji?

 3. Even America legalize Ganja. poor as we busy jailed Man found with remnant seed, after flood of Noah Jah blessed it. Kapokola you will never get rich chifukua mukutsekela billions of kuacha there iz nuh seed in Agriculture that will make man rich rather than Ganja.

 4. Kodi makape inu, mukumugwira muthuyo chifukwa munakumana naye pa loadblock. funso m’kumati kodi kumene kukulimidwa chamba inu simumakuxiwa? bwanji osapita kukatchetcha ganja yonse kumendko km mumalimbana ndi munthu woti wa choka nayo komwe inu ndikumugwira. makape amatha inu otsamawapasa zaka 9 a cashgate koma waganja dziko lokondera ili.km na ife malijuwana tidakadyabe ndpotso chaka chino maliwana alimidwa bas!

 5. aaaaa choncho uyoyo sanabele munthu amalima yekha luyepo anatibera ma billion athu koma munampatsa zaka 5 Ada awowo mwawapaysa zaka 4 ……. nde mukatero mukuti ndichilungamo makape inu

 6. chamba chaka chino ife tilima/ takambrana kale nd chilima/ tikzwa a2 ambri mukukayka/ kalata yapta kalexo kwamuthalika,

 7. Why u wnt to put innocent hard working man in prison jst bcoz he’s got what it takes for him to get rich? Tel me what else can u farm that u can make money in malawi than Chamba? Fucken goverment u got pple who r kpn lot’s of gvmnt mny bt u lv them. Open ur eyes poor malawi.

 8. Aaa ndi nkhaninso imeneyo? Munthu akupanga zoti azithandizika pa nyasa pano inu mukummanga? Bwanji osakamanga anthu akuba ma million athuwo? Yakulepherani ntchito apolisi

 9. Mukumanga munthu amene akukhesa thukuta popeza ndrama, koma mukusiya anthu amuboma amene akutibera ndrama zathu zamisonkho.dzitsilu vintchewe imwe mumasulen munthu chonde.

 10. Mwamumanganu,chambacho wakaba kumunda kwanu kapena ndichake? Acashgate smukuwamanga bwanj km adaba ndalama zakhankhan,chamba nkachianiso,nzanu asapange malonda kt azdyako bwno kma inu ndchiphaz chadzkang’acho kumupondereza…bwanj maiko anzathu amalola bznez yajanja? Kanyani ndnu pot ndie mumazwa kunyopola anzanu ai.

 11. Zaka 9 zachuluka kwambiri ndiye ogwirira mumupatsa zingati? Plz mundipatseko thumba limodzi ndizidzasuta kuno chikusowa kwambiri.

 12. [[.weedicon]] [[.weedicon]] [[.weedicon]] [[.weedicon]] [[.weedicon]] [[.weedicon]] [[.weedicon]] [[.weedicon]] [[.weedicon]] [[.weedicon]] [[.weedicon]] [[.weedicon]]

 13. Anthu wopusa inu anthu akuba ndalama zankhan nkhan zaziko koma simukuwamanga koma munthu kungomupeza ndi chamba basi zaka zankhan nkhan…kupusa basi

 14. Jst get happy coz maridjuana is the biggest ever business wich can make sombody reach easy even to the whole world! Govnm dats nuh a reason for arresting him! Yo job s to keep malawi peace and arrestion who violence not who found wth ganja!

Comments are closed.